Kodi akuti atumiza wa Min of Health ndi A Bwana a Police kukanena zoti ndege yasowa. Wa ku Healthy? Mmaganizo anga anayenera kupita ndi a Colleen Zamba
This guy talking first slept through the whole report he missed a few points that were ambiguous Yes apeleka uthenga koma But it’s open ended due to it’s ambiguity
You people Malawian you just make money on you tube for nosence.go out and look and say what Malawian wants about the inccident of chilima What are you hiding in this accident pls Malawian don't take it granted
Kungodyapo ndalama apa palibe chanzeru apa kodi report ranji losakha ma friend kuti apange kafukufuku chilungamo tizaziwa one day dziko lapansi lilibe chinsinsi....
Nkhani ya ndarama Ku ndege mukuwona Kuti sinkhanitso yina yoyipa pa chiwembu cha anthu 9 kkkkkkkkk guys Boma ili kuli anthu osazindikira wochuluka kwambiri zina timangowona taziyamba ndinthu nkhani yili Ku MCP pali mau woti mutiuze kupotsa zabweradzi ife tidakalibe ndi mafunso
Musatipusise😭😭😭😭😭 lamulo ladziko ngat siligwira ntchto ,lamulo lamulungu lizagwira ntchito,ngat sligwira ntchito payinu ,lizagwira ntchito pa ananu ndi zizukulu ndi zizukulu tuvi zanu
Namaniii but God he knows everything 😢😢
Those who are against this report should go and do their own investigation and come up with the report of there wish
Chimata chako iwee mwanaphwaa
Rest in Peace Comrades, you didn't die in vain
Kkkk muziwona simunati mulungu anawonatu chilichose
Anthu awawa atipweteka
This report could not have a negative outcome for the president he has to rely on its outcome to get some form of approval from the public
Kod mesa mumati black box mulinayo koma Mulungu atithandize ndithu muziwona
Whee is black box?
Kodi akuti atumiza wa Min of Health ndi A Bwana a Police kukanena zoti ndege yasowa. Wa ku Healthy? Mmaganizo anga anayenera kupita ndi a Colleen Zamba
Their wish
Kodi chakwera anspita kukanena zaa amene anamuuza zokhuza weather
Moses mumkuyu anaitanidwa kukayakhako za brack box kuti ilikuti??popeza anati anaipeza ndipo inasugidwa
Chimwendo ndindani anamuuza kuti ndenge yadzadza ,mukagowaitana athu amenewa umboni mupeza osati manyi mukutiuzw apawa
It’s not fair with report and why he was without clothes shoes god will panish everyone else
Ndinkana na namiwa anachokamo anadziwa kuti padzakhala kusanena chilungamo
Izi ndi zabodza tingodikira 2025 tidzakhala ndi Report yoyenera
Nde ndi chifukwa chani kuti ndege ya asilikali kuyenda yopanda black box bwanji or ma foni anthu or imodzi sinapezeke mu ndengemo????
Nawononga bundle yanga manyaka alipoti akawerengere kwawokha achikangawa
Mulungu atichotsele utsogoleri oipa umenewu
We need black box that's where there is a pruf
Chakwera ndiwe satana ndipo mulungu akukathe padziko popano ndi anthu onse amane mumafufuza mulungu akukatheni ndithu
This guy talking first slept through the whole report he missed a few points that were ambiguous
Yes apeleka uthenga koma
But it’s open ended due to it’s ambiguity
Where is black box?
Kodi transponder adazimitsa ndi ndani 😢
Kapangeni yanu muli ndi ufulu amene simukuvetsa
Kuzolowela kuti tikayenda chomci timakafika timabwelela opanda vuto koma kosatsata malamulo tikafuna kuyenda ulendo ulionse,coodination amongst needy dipartments.
Zaboza izi
Koma Kunkuyu anati black box anaisunga pabwino. Atiuze kumene ili? Dziko likudikira kuti limve
Chiwembu chinachitika mwachimbuli mbuli apatu bodza likukanikabe
Report limeneli latani kodi silikufotoza za black box ya ndegeyo,tiziti ndegeyo anayipanga yopanda kuyika black box?
Zopusa basi muzigodya ndalama za MCP chikangawa chilugamo chizaziwika mufune musafu muzayaluka anthu woyipa inu
Kodi Anyani inu ndegeyi inalibe black box ndiyekuti???
Panja kukuyu ananena kt yasungidwa Malo abwino
Angonya ndalama zaboma palibe chomwe achita
Dege inagwa mangozi,kupa Chilima,kungamuthandize bwanji Chakwera????
Ukuonekelatu kut ndiwe mbuli even ma Spelling Ako alakwika Dege ndichan
Nanga bwanji apule akuti samaziwa kut achilima anabwela ku corea
Sete zeni zeni
Kodi za black box siikutchulidwa chifukwa chani?
Kuyambira ko tsirizira kwa nsonkhano
Where isblack box
Pastor Nyirenda are u comfortable with this report? Serious. 7:37
Palibe cha nzeru APA where is black box
Anene chifukwa Chimene abusa a TY Nyilenda anatulukira mu guluri
I'm not interested with this report
Black box ....??????
Where is family's representative
Kafukufuku Winanso ayenera kuchitika after September 2025 Tikasintha boma
Chakwera wa ku gehena
Pastor's by eyes not heart , where is the truth , corruption is a sin mind you pastors
Kodi ndizoona kuti aTY nyilenda sanafufuze nawo?
Bodza ilo,,sangayende osafunsa
Akunkuyu azafotokoza kuti black box yilikuti
Abusa amenewo la 40 lidzakwana palibe wamuyaya
You people Malawian you just make money on you tube for nosence.go out and look and say what Malawian wants about the inccident of chilima
What are you hiding in this accident pls Malawian don't take it granted
Tatanthawuzilani mu chizungu chovekanbwino 😂😂
Foolishness at it's best
Zaziiii
Za ziiiii
Zazi
Ndipephero langa nonse mukunamiza anthu mupenge misara pasababthe mwezi
Akapanda kupenga ndekuti akunena zowona, upenga ndiwe
Black boxs ilikuti zisiru inu
Block box ili kuti
There is no truth in this report,but am very much disappointed with pastor T.Y Nyirenda for being involved in this nonsense.
T.Y anapangatu withdrawal mu committee yakafukufuku
Ndilenda he was not with them
@@hendkachibowo9672 thanks I was not aware of this
Hippocrate he preach what he can't do
Osakhulupiliranso anthu ochedwa azibusa ayika ndalama patsogolo chilungamo pambuyo shame on you all
This is rubbish what you are doing, where is black box
Mukanakangopanga kafukufukuyo ndinu mwina ikanapezeka
Kungodyapo ndalama apa palibe chanzeru apa kodi report ranji losakha ma friend kuti apange kafukufuku chilungamo tizaziwa one day dziko lapansi lilibe chinsinsi....
Ambuye tionetsereni chilungamo chifukwa anthu akonda ndalama mdziko lino coz nkhaniyi ndiya straight
Kkkkkkkk zachisoni kwambiri eeish
Don't fool the Malawians ,,chilungamo chidzadziwika pangatenge nthawi maka, nkhani yaku Thambani inatenga nthawi koma tidadziwa chilungamo chake,bodza lanuli ili nthawi ina mudzayankha
Nkhani ya ndarama Ku ndege mukuwona Kuti sinkhanitso yina yoyipa pa chiwembu cha anthu 9 kkkkkkkkk guys Boma ili kuli anthu osazindikira wochuluka kwambiri zina timangowona taziyamba ndinthu nkhani yili Ku MCP pali mau woti mutiuze kupotsa zabweradzi ife tidakalibe ndi mafunso
Mr inuyo ndi munthu woziwadi chilungamo ife sindikulora zimenezo mpaka muzachoke Kaye ndiye azabwere kafukufuku wina ndiye ndizasiyanitse akuti bwanji zikufanana olo ayi pamenepo ndiye ndazavesa koma pano ndakana izi zikomo kwambiri
Fake pastors rubbish
Kapangeni yanu muli ndi ufulu amene simukuvetsa