Tolakhani wanga kafe maulid amandiwaza ndaphuzila school kufuna zakhale ngati kafe koma sidzinathek pambuyo pomaliza maphuzilo ndikuno ku South Africa kuthawa umphawi ndimakunyadila kafe kamavela nkhani zowelenga iweyo ine mutima ndimangoti Maloto anga long life kafe❤
My friend, we have been contributing all along. Are you seeing Chimwendo Banda cooperating??? Have we sent suggestions? Haven't Kabambe gave financial advice to the financial advisers of the president????
A Malawi tisayiwale pajatu adanena yenkha kuti tsaziwa zonse azichita kumuuza ndiye amachita kuuzidwatu 😂😂😂😂
Tolakhani wanga kafe maulid amandiwaza ndaphuzila school kufuna zakhale ngati kafe koma sidzinathek pambuyo pomaliza maphuzilo ndikuno ku South Africa kuthawa umphawi ndimakunyadila kafe kamavela nkhani zowelenga iweyo ine mutima ndimangoti Maloto anga long life kafe❤
Chakwera ndi Nkhutukumve ya President,,, koma I hope achoka 2025.
Sangayankhe palibe chomwe angachite
Chimwendo anyamanyi 2025 ndamene akumulakwisa chakwera nde azanyamanyi
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Apule kulithawa funso la munthu was Mai. Eeeeeh!!!!! Paja alibe kanyadzi even kamodzi. Mpaka kuthawa. Uku ndie kuchaya kugwetsa eeeeeeerh!!!
President ndi Chimwendo paja, , , , Chakwera ndi nduna ya Chimwendo.
Aphungu Ku Parliament Kumenya Kugwetsa Chakwera 🤸🏃🏃😁😁😀😀😂
DPP ndi UTM 2025 Boma ilo 💥💥🔥💯🎉
Chamupana chiseko chikangàwa komaso chimwendo ndamene anamuononga chakwela
chakwela. galu. weniweni basi. kumangotosa zithuzi. bass. chisilu chamunthu. mbava kungolowela bomamu kuba galu unali osauka osoka foja kapolo ukuzuza anthu
.
Kkkk yeah siyani mpando madzi asadafike m, nkhosi
Wayenda champeni wamkulu
Kukanika kuyankha funso Koma kupeleka mimba mmakwalalamu hule wachabe chabe chikamgawa manyiake sure
Ndiye kuti chakwera alibe zeru zotse zimene yamashita amaudzidwa ndi chimwendo banda mkaona dzikoli economy ili bad muthu mwa chimwendo mwadzaza mamina okha okha ngati nkhumba
Tatengapo phunzro presdent osakonda anaake
LAST DAYS TIONA ZINTHU ZOOMWE MASO ATHUU SADAZIONEE
Achimwendo kusonyezakuti ukuziwapokanthu momwezawonongekelandala mudzikomuno akukanenakutinthawiyatha nangaenawo atsalilawo nthawiyawo sinathele achimwendobanda asowantendele
athu oipantima awa mm tikumana chaka chamawa
Amalawi tivote mwazeru timuwone chimwendo komwe azipangira zopusa zakozo DPP iloweso kawiri
Chimwendo akupepusa mbuye wake
If we need to develop Malawi, we should not stick to the failures of others,learn to contribute because Malawi is for all.
My friend, we have been contributing all along. Are you seeing Chimwendo Banda cooperating??? Have we sent suggestions? Haven't Kabambe gave financial advice to the financial advisers of the president????
Koma kudachema relo.,...
Koma amarawi mwapunzila Kwa bas ,ntawi ya Mutalika munanena kuti mwatopa naye mugufuna gusintha BOMA la DPP apa pa mwaona .
Km akadafutsa za kupha sangayankhe mutu muli mamina ndikuganiza njila zakuba basi
😂😁
Bola. Azathu. Ife. Wathun Ali. Kusipe
Achina chikangwa mcp machimo
Funso anayankha kale mu presss statement analinayo...