ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Moto kuti buuuu🔥🔥🔥
Boma 🎉🎉🎉🎉🎉
❤❤❤❤❤ APM my vote
Victor musowa my mp l will give you my vote 2025
Apm my vote 🎉🎉🎉🎉
Adad my vote 🎉
APM my vote
APM my vote 💙🧢
Zomat peter wakalamba sfundo izo Khan ndikuyendetsa bwno dziko
Zikomo kwambiri mau aphavu
This is where my vote belongs to
Mcp yagwa basi tiyiwale tineneretu pano
A peter a betha loya more faya ambuye aaunge moyo wa a peter apulumutse dziko😊
Moto moto❤
Boma ilo❤❤
Woyeee!
Zobeba ipase moto Dj ukoooooo😅😅
DPP boma basi!!! 🎉🎉🎉🎉
DPP woyeeee ❤❤❤
Pitar anakaramba inu ❤❤❤ msamphe alobinotu kuti mzapange ndiwo pano akukhara muufulu amalawi asakunamizen zaboza izo
Garu iwe ,ma vice president mwapha aja ,nanga nine ku chikamgawa.
Akalamba ndi mabvizi akowo
DPP woyeeee
Dop my vote
2025 boma professor. Auther peter muthalika moto kut buuuuuuu🔥🔥🔥🔥🔥🔥
A c p ❤❤❤❤
Dad woyeeee tilipambuyo pano
Tayahkulani mfundo osati kuyambitsa ziwawa anthu awuzeni mfundo kut mukatenga boma simudzawonongaso anthu a chalbino?
Ndiposo
anthu,a,dpp,mulibe, kukhazikika, nokha, musapote, dpp, komaso, utm, nokhanokha
Ndikumva kukoma ndi apm
sitingavotele, dpp, mcp, tikuyiwona, akatiphele, alobino, ine, aui
Amuchacha ndembela imeneyo siya dziko palibe phindu ndizomwe mukunena tayakhulani fundo
Kuyankhula mupusa ngati kumuneku mungatenge boma,makamaka mp ameneyi ndiwamwano kwambiri
Angopusisana anthu akuba awa, muja ankabera akuona ngati adzabaso?
Nanga mwano amaugeya achimwendo uja bwanji??omwe mwawona ndi uwu
Chabwino a DPP amaba koma angafanane ndi zigawenga za MCP kuba kupha kugwesa kwacha,zinthu zikungokwera tsiku ndi tsiku ndiye mukuti chani inuyo chani
mau, km, ameneo, dpp,idikile, zaka, 26, kuti, idzawine, km, 2025, mukunama
Zikukuwawani tu akamachokako kwanunuko, kuwina ndikomweko dpp 2025 yikulowa boma
Akuti chitani mmomoooo kkkkk
Kumaloku kunakoma heavy
Tiuzeni fundo
mukhululukileni, apm, wakalamba, zolakhula, sizikivekatu tsopano
Za kwacha azikapqnga ku Lilongwe
Mukunenazowona bro a MCP ndiwodelera.
MCP ndi akatundu munya muona, Joyce Banda yemwe uja munamubera uja not MCP
Apm 2025 bomaaaaa
💙💙💙
Bola tamekiNdi zigwe zizakutalkreni 2025 cuz ee mwatengekatu
Zitsiru zakumana inu nokha kwanu kunatha simuzabwereranso boma inu
Ndithu masiku ano anthuwa akamabwera kuzachita misonkhano Awuzeni achitiretu chitukuko chifukwa mbava zokazoka zimangofu kuba
Ati nkazi ofuna mwanatu kkkk
A Malawi kutengeka, kusayamika, kulephera kusiyanitsa that's why we put someone in office who doesn't deserve to be the president and now Malawians are in big problem in their own country
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Iyi ndi land slide mcp paulendo😂😂😂😂
Makape
Chikangawaaaa woyeeeee
Manyaz agwire Satana
Ndava kt aNchacha akupita kwa kabande ku utm
Kkkk amalawi atopa
Mafuta 12500 nkhuku 10 pin bread 2400 sugar 2700 soap wa tablet 700 mayches 150 eeeishh
Mkumati boma ndilomweli, ayi zikomo ndinthu.
@MathewsJanuary eee ndipo mbali zakuno akazi anga amakukonda mbusa amenei
Koma guyz nde kwazaza, imagine kulibeko apm. Nankha akazabwera apm. Kuzakhala bwanji.
DPP alibe fundo mau aZiwawa😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Wukunama kwambiri, wukunena fundo za Chikangawa Congress party zopha anthu mbuli iwe.
Chakwera ndiye Ali ndi fundo ....ndi zisilu zokhazokha zikuchita support chakwera chifukwa amakupasani ndalama zokuba .....iweyo ndi munthu wopusa kwambili ....chakwera wapanga chiyani mmalawi muno cholozeka
Ajomo muja mukampha malubino inu? Mukuona ngati anthu nzisiru?
Kungomva kuti kwacha,kuona mochitira mwache😂😂😂 ajomo eee Palibe chaulemu mukuchionapo apa😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂
Jommo ati Ng'ona ilibe mabere
Musowa umakwana😅😅😅
Musowa wandiwaza akuti ndirande sisunga kape
Koma yaaa chala chikalodza chaloza palibe angadule chala cha yahwe kkkkkkkkk
Fundo palibe
Kkkkkkkkk agogo
DPP can't win this time, mwatuzuza mokwana ndinu anthu oipa, chitipa can't tolerate this nonsense to support DPP, believe u me you can't win over MCP
Ati mukamva kuti kwacha muona mopangila make kkkkkkk.. DPP woyeeee
DPP youse nyapawo
😂😂😂 wagwa nawo iwe pusi
😂😂😂😂 @@alexjeremanuel2541
Ife tavomela chifukwa sitimalimbana ndi zitsiru 😂😂😂
Munthu wa Dpp kulowaso Dpp
Kkkkkkkkk
masapota, a, dpp, fundo, alib, km, kutukwana
Umu uzuozeko panyapake
MBAMBANDE DPP KOMA MUSAMAONJEZE KUYANKHULA NANUNSO , MUKAMATIPASIRA
Oooh tamva. Timangofuna kupeleka zomwe zili mkati. Koma tichepesa
a, dpp, kwanu, km, kudikulila, azimai, povina, fundo,mulibe
nanga,palifundo, yanji, apapa, yoti, mu2, atha kukopekanayo, kulankhula, musiile, mcp, akatundu
Koditu mukana mtulutsa Pita Kaya azikwawa. Munthu adakula bwinobwino azipuma mukakamiza
Ukuona bwanji tidzangokusankha iweyotu
Amayi pangani za kabambe please
Kod anthu ena munakhala bwanji? Zona momwe znthu zikumaonongekera muno mmalawi Inu ndikumakhala kumbuyo kwazopusaz? Ot muzikamba nkhan yoipitsa dpp kumat amampha arubno zamaganizo mwanumo ndikupasiya nkhan yaifa ya chilimo yochita udziwikiratu anthu 9 osewaja adafawa sizikukhudzan ai koma ndikumabakila zoipa ngat iz? AAA kharan ndimanyaz gaizi chipswera Chanyowan ndichomwe chima Wawa.
Chikangawayo siimanamatu
Suleman lelo sanabwele bwanji?
boma, ndlomweli, silikuchoka, olomwanamize, anzanuwo
Boma ndilomweli la malawi timangosintha chipani
Ndiye tiziti akuyambitsa ziwawa ndi ndani pakat pa dpp ndi mcp
Ukamfunse chakwera
Mukafuse chikangawa bwa
Kkkkkkkk fusolimenero uziyakhe wekha
olomutatani, mcp,ndiakatundu,simatekeseka, zaka, 26, ikutsutsa, chipani, osapasuka,,komaso,osatukwa, mu2
Aaa zandale suzitsata ukuonekelamu iwe 😂😂
@@TysonMwenyetasiye akutopesa alipo anthu awiri okha axingo tumiza ma comment osusa paka ka 15
Nde kuyankhula kumeneku koyembekezela kutenga boma
Ayi koma zikwanje zijah ndizimene zikutenga boma. uko!
Iwe umat kkk
@@MuhaShaibu-x5x kkkkk
Iwe umafuna ayakhule bwnaji ....mcp out 2025 Apm my vote❤
Osafunsa Anyatu anu?
Nyimboz ndy zaimbidwa bwino kwabas kkkk
This platform is pathetic
Mudakalinawo ntima uja ete?

Bola tameki
Ndi zigwe zizakutalkreni 2025 cuz ee mwatengekatu