Ndale za Chipani chopsyodza Mafinya Za Uchitsiru. Mukubwera ndi imeneyo mukuona ngati muyiwalisa za Anthu munawapha Ku Chikangawa? Ayitu palibe kuyiwala apa. Munapha Anthu Osalakwa ana a Njoka inu 🐊🐊
MCP VIVA !! DR CHAKWERA VIVA!! BOMA LA MALAWI ILILO NDI BOMA LA MALAWI CONGRESS MIGHTY PARTY LOMWE SILIDZASINTHA MPAKA KALE KALE UCHOKERA PA 6 JULY 1966. UKWATI WA MCP & MALAWI GOVERNMENT SINCE 1966... MONGA MOTHER PARTY IN MALAWI. ZIPANI ZINAZI MZAMADZERA DZERA POPEZA AMBIRI AKATOPA KUZIPANI ZAWOZO AMABWERERA KWAO KU MCP MIGHTY PARTY. MCP NDI CHIPANI CHOKONDA MTENDERE 💞 UFULU☔🌹KOMANSO CHITUKUKO.. ENA MALAMULO CHA DEMOCRANCY SAKUWADZIWA MCHOCHIFUKWA CHAKE ZIPANI ZINAZI ZIMAKONDA KUBERA MASANKHO. POPEZA NKHANGA ZIDAWONA IZO ZIDAWONA !! ZIPANI ZINAZI ZIMAKONDA ZAKUBA !! AKUPHA MA ALLUBINOH !! WOTAYA CHITUKUKO cha MISEU ! NJANJI ! ULIMII!! KUTAYA MTUNDU WA CHIMALAWI.. ✍️MCP MOTO
Mukuyankhulazi Ngati ndizanzeru lero. Koma Kodi zikwanje Zanu munazionetsera ku Lilongwe KO kwa anzanu muyetsa kuti a Malawife sitiludziwa za inu. Dpp iyi mwina yangonena mau amene akuwawani koma inuyo mudazichita idzi ku Lilongwe anthu anaopyedzedwa inu boma Muli konko Y?? Malawi tiyeni tikondane. Chidzadziwe nchipande powomola nsima and This is through voting. Though tikumva zambiri Zama leakages. Tionetsetsa tisanafike povota kuti Kalembelayu wayenda bwanji situlufuna ma vote obera ayi.Malawi ndi wanthu uyu tisazunzike mdziko lanthu lomwe. No nono.
@@IbrahimJackson-i8h Pamene idzathothokere MCP ndipamenepo . MCP with Or Without DPP Koma mudziwe Kuti mukugwa simukuwina Thambani Serial Killers ⚒️🔨⛏️ Chikangawa serial Killers ⚒️🔨⛏️ AKAZIKWANJE mmakwalalamu
The last time I checked, MCP was in the streets demonstrating for the then MEC chair to step down. Have you known the process for appointing the chair just now? Jane Ansah munangodana naye eti?🤔
Ine ndawona chomwe a kumva kuphweteka nachimutuyu sonkhano wakamajekete uja siunazaze anthu ngati mene anazazila ku DPP kamajekete siuja amachita kugawa ma 10,0000 kuti ayankhe kuti kwacha 😂😂😂 lelo a kulila poyela ndiposo guys mongokumbusana a mcp sinawinile man to man inawinila pasewu monthandizidwa ndi chilima lelo kulibe tiyeni nazoni
Mutu ngati phwala la ngamira Iwe ayiseye.... 1.Where is the black box? 2. If the aeroplane had no transponder then how did you know that the aeroplane took the wrong direction? 3. Anamuuza chimwendo kuti ndege yadzadza ndindani? 4. Chakwela anawuza amalawi kuti ndenge inafika kunzuzu ndipo anawuzidwa kuti abwelele, anamuuza ndindani? 5. Where is the black box? 6. Anthu mukuti anafela mmalele, who told you? 7. Mukuti amafika pansi alibe magazi, madzi, nde anawayamwa ndindani? 8. Valentino phiri, nkulu wa asilikali, anawuza amalawi kuti ndege inawomba phili, anamuuza ndindani? 9. Inu ndege kugwa pa kutali kwa 5meters, anakuuzani ndindani?
Anachimutu akulira boma lapita ku DPP Malo mozuzura anyamata ache azikwanje aja akulimbana ndi zaziii. Ziwawa zimene zikuchitika ku chigawo cha pakati akupangitsa ndi CHIMWENDO.
Dpp supporters are indeed good viewers don't mind their comments they're embittered so hard.Hopefully they will control their complete downfall come September 2025.
Mul ndi chibwana inu a mcp, km mutulukabe m'boma, km mukatuluka m'bomamo simuzalowaso m'boma, mesa a police-wo ndi anu, mudandaura chani pot dzikori ndilanu
Are we sure Malawians will change their mindset and transform the nation especially DPP and MCPdiehards with their vile mentality?????!May God intervene!!!!!
Patumbo PANO nonse a MCP. Kod mmesa zomenya anthu munayamba ndinu?? Lero mukufuna ntendele chifukwa chot DPP yayamba kubweza?? Tikuswa kumene agalu okupha Inu. Maka Maka iwe okula mutu iwe chimwendo banda ulipila magazi a anthu aja unawapha kuchikangawa aja
Eèe koma ku MCP kudadzaza anthu a sweet talk but an action is 0 out of 10...Ndiye mumuuze Chimwendoyo kuti akamayankhula anthu amuzungulirawo nkumamuophera manja asaone ngati kunjaku kuti anthu akuombaso m'manja adzalira kkkk
Mene anabwera chisale central region tinamusiya kupanga sokhano ku central region sikuti iyeyo ndiwochenjela koma democracy si nkhondo that's why tikulora kuti zitero
RIP SKC, awo angochemelela kuti awoneke alandile ma 2pin akamwele kachasu. Dpp woyeeeeee💙💙💙
Woyeeee 🎉🎉🎉
Ndale za Chipani chopsyodza Mafinya Za Uchitsiru.
Mukubwera ndi imeneyo mukuona ngati muyiwalisa za Anthu munawapha Ku Chikangawa? Ayitu palibe kuyiwala apa.
Munapha Anthu Osalakwa ana a Njoka inu 🐊🐊
Akunamatu amenewa
Akubisa kupha kumene iwowa adapha chilima ndi anthu ena aja pandege.
Ndipo musakayike 2025 DPP ikutenga Boma chaka chamawa
Olo kumanga otsutsa awinabe same as Senegal
ctingapepese kwanyau agalu inu
Ulendo wa lero muchosedwa ndi anthu aku lilongwe omwewo
Nanga mademo mumalesa ku Lilongwe ndanyamata anu azikwanje aja simaona kuti zimayambisa khondo ndiye rero mwava kupweteka mau okha
Kodi inu a mcp lero ndiye mwadzindikila lero nanga inu zikwanje mumatulusa zija a dpp akanakubwedzelani zosatila zake zikanakhala zotani lero ndiye zakupwetekan
Amene mukupanga nkhondo ndinu a mcp dziko lonse likuziwa bwino chifukwa cha kulephera kwanu
DPP imangolankhula siipanga koma iweyo chimwendo umapanga ndiye bola ndan
Simungawinenso koma, prepare to loose
Mufune musafune dpp ikuzawina
Nanji hule Jessie kabwera ndiye amangondinyasa popanda chifukwa 🤭
😅😅😅😅😅😅😅 ineso ky bwanji ndi chimwendo
Mmmm kuve zolakhula za chimwendo kuononga nthawi bola kumakamwa mowa
Komaditu kungoononga nthawi yako satana ameneyu ali ndi dzeru zomwe
Simudzawina inu mwatitopetsa ngankhare munganene motani koma anyani inu mwainu mulibe umzimu anthu A mcp
Yemwe anakuletsani kukwela ndege nde osamuchula Koma busy zopepela 😢ana anjoka inu 😢😢😢😢
Anthu oipa awa, zakuchikangawa osayankha koma kumayankhq zozizirazi
Dpp my vote
Muja mumatenga zikwanje kumakhapa anthu lero ndiye mukuti chiyani mukunjenjemera ndi dpp inu muli ndimantha mukudziwa kuti kwanu kwatha amalawi sakukufunani dziko lonse
Pamatako pinu mose
Anyamata ovala mask komaso onyamula zikwanje awooooo akuchemererawo
Mwangokumana agalu okhaokha inu azikwanje aja munapepesa kutundu wamalawi ndiye apa mukufuna mupepesedwe zaziiiii
Pita asowe asasowe adanena mau amenewa ndani
Kkkkkk kufuna tiyiwale za njala eti muchedwa ur tym is up guys mwatilephera
Hule iwe mcp inapha ofunika kuposa razaro
Mumange a police anaba 5 million aja
Ndinuakupha ndikare simuwina
Chigawenga chowuma mtima, chimapha munthu koma ngati boma lichibwenzera zisiyana pati? Am singing....ndatchula munthu? Ngati uli Mulungu iweyo ndekuti muwinanso koma Malawi wakana
😂😂😂😂😂 chobwezera kuwawa.....mau okha koma mpaka press briefing 😅
Tawauze iwe 😂😂😂😂😂😂😂
😢😢😢 kudabwatu ine
Ndipo inuo ocita okhal iwo😅
Inuyo mukungofunika mchape mumwe mukumva kuwawa kwambili 😂😂😂😂😂dpp umakuwawani chani kodi
MCP VIVA !! DR CHAKWERA VIVA!! BOMA LA MALAWI ILILO NDI BOMA LA MALAWI CONGRESS MIGHTY PARTY LOMWE SILIDZASINTHA MPAKA KALE KALE UCHOKERA PA 6 JULY 1966. UKWATI WA MCP & MALAWI GOVERNMENT SINCE 1966... MONGA MOTHER PARTY IN MALAWI. ZIPANI ZINAZI MZAMADZERA DZERA POPEZA AMBIRI AKATOPA KUZIPANI ZAWOZO AMABWERERA KWAO KU MCP MIGHTY PARTY. MCP NDI CHIPANI CHOKONDA MTENDERE 💞 UFULU☔🌹KOMANSO CHITUKUKO.. ENA MALAMULO CHA DEMOCRANCY SAKUWADZIWA MCHOCHIFUKWA CHAKE ZIPANI ZINAZI ZIMAKONDA KUBERA MASANKHO. POPEZA NKHANGA ZIDAWONA IZO ZIDAWONA !! ZIPANI ZINAZI ZIMAKONDA ZAKUBA !! AKUPHA MA ALLUBINOH !! WOTAYA CHITUKUKO cha MISEU ! NJANJI ! ULIMII!! KUTAYA MTUNDU WA CHIMALAWI.. ✍️MCP MOTO
@@DanielChipasula
👹👹👹🤪🤪😈😈⚒️⚒️🐊🐊🐊
Ng'ona inu
Zaziii muli ndi matha inu..... Ground lake liti mwapondalo 😂😂😂😂😂 DPP simungapange nao mpikisana
Munayamba kale kuvula ndinu,akuyenda Ali ngati maliseche Pano,tachokani apa
Chokani mulile chocho kkkkkkk❤❤❤❤dpp moto
Mau a Musowa okha mwaitanitsa press briefing, zosakwera nawo ndege ya Chilima zija zikuchedwa pat??
@@JohnSemu-c3h eti?kupepera basi
@TamikaKaponya Aaaa ndipo inu, ali mutu gwaa ngat gwafa
Press briefing mmalo mokamba zinthu zopindulira amalawi koma Ali busy miseche ndi mijedo....apatseni mchape amwere😂😂😂😂😂
RIP SKC udalakwitsa kupanga ubale ndi Ng'ona party nanga lero taona zidakudyatu.😭😭😭 panoso tsopano ng'onazotu zalusa zayamba umangotenga zikwanje ndikumakhapa aliyese amene akuzidandaulira ng'onazo pazomwe sizikuchita bwino.
Inu DPP ikuwina 2025 ndipo musakayike ... 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙
🎉🎉
Mukuyankhulazi Ngati ndizanzeru lero.
Koma Kodi zikwanje Zanu munazionetsera ku Lilongwe KO kwa anzanu muyetsa kuti a Malawife sitiludziwa za inu.
Dpp iyi mwina yangonena mau amene akuwawani koma inuyo mudazichita idzi ku Lilongwe anthu anaopyedzedwa inu boma Muli konko Y?? Malawi tiyeni tikondane.
Chidzadziwe nchipande powomola nsima and This is through voting.
Though tikumva zambiri Zama leakages.
Tionetsetsa tisanafike povota kuti Kalembelayu wayenda bwanji situlufuna ma vote obera ayi.Malawi ndi wanthu uyu tisazunzike mdziko lanthu lomwe.
No nono.
Auzeni kwambiri, chimwendo ndi galu wamunthu
Zopanda nzeru zonse mwayakhulazi ndi nthawi yoti muchoke tatopa nanu bola dpp yo ndithuu
Iwe jes kabwira dpp sikukuopan ai ndipo tivotera dpp
Akuphaa inu..munasowesa c hilima agalu achabe inu chokani apaa anyapapii inu
MCP inapha Chilima kamba kandale zomwezo,,, anthu 8 aja samaufuna moyoh?
Alomwe mulipo ochepa kwambili mukafina zipolowe MCP ma bwana athu kungoti go ahead muzathawa kuno ku Malawi
Iwe ukuona ngati ndi alomwe okha amene akudana ndi Chikangawa?, Komanso kuthawa kupita kuti? Poti dzikoli ndi la tonse amalawi
Iwe ukuona ngat achewa onse nga Mcp?
Komanso mulipo angati? 😂😂😂
😅😅😅ine ndizakhara mbali ya alomwe'yo aise ziyanbiseni basi tizawathandizira,,si mumaona ngat achewa onse ndi a MCP 😂😂
Even achewa apaphatawo, mcp sakuifuna.
Iwe ndikape...... Ifeyo ku southern tizatengaso azikwanje mukabwera ku southern
Ndiye aPolice ngati akulephera kugwira okuphawo, ndie kuti munaphana nokhanokha. Ndie mungagwirane?
Awapalibepo chanzeru akunena mamina okha okha
Azikwanje aja bwanji simumayankhula kanthu
Atolankhani mmatha 😂😂😂😂😂
Ndipo kwambiri akuopa
Kodi zisankhozi osati dpp yokha kuli utm,pdp,pp,aford, Ambewe party,udf, zilipo zipani zimenezo ndiye kuti sizizawina
Inenso ndumadabwatu
Akuopa dpp😅😅
Enawo mesa akuti aphatikizana ndi chipani chokupha Cha DPP
@@IbrahimJackson-i8h
Pamene idzathothokere MCP ndipamenepo . MCP with Or Without DPP Koma mudziwe Kuti mukugwa simukuwina
Thambani Serial Killers ⚒️🔨⛏️
Chikangawa serial Killers ⚒️🔨⛏️
AKAZIKWANJE mmakwalalamu
Owoo mwaulula Kuti kalembera mwabera chimwendo waulula pansonkhano watolankhani
Ulira kumene. Ngati umachedwa nkulimbana ndi mec osauza anthu ako kuti akalembetse ulira. Lilongwe yokha 1.4 m. Pamene maboma 5 kumwera 1.2 m multiracial tooooooo
Kkkkk soka lake central regional yo ndiyomwe Iza votele DPP pakwao pompo gada 😂😂😂
Kkkkk ndye azakuvotarani ndani inu
Pathako pawo anthuwa
Bwanji sanalakhulepo zokhuza zikwanje galu ameneyi chimwendo uzafa osadwara nyapala iwe
APM my vote mcp mwatizuza ufumu wanu wagawanika pakati
Awa chiseko chawapana basi😅😅😅😅😅
Ndine wa tsoka pobadwira ku Malawi kwa mcp eny away DPP my vote 🎉
The last time I checked, MCP was in the streets demonstrating for the then MEC chair to step down. Have you known the process for appointing the chair just now? Jane Ansah munangodana naye eti?🤔
Koma amcp mukamapanga zinthu muzidziwa kuti muyeso womwe mwachita mayesela anzako iwenso umayedwela omwewo, ndinu nomwe munatenga dzikwanje dzuwa lilingweee!! Koma simunapepese lero wina wangoti mudziwathamangitsa koma mpaka kuyitanitsa atola. Nkhani??😂😂
Za zili zeni-zeni. Bwanji mulibe manyazi!
Ine ndawona chomwe a kumva kuphweteka nachimutuyu sonkhano wakamajekete uja siunazaze anthu ngati mene anazazila ku DPP kamajekete siuja amachita kugawa ma 10,0000 kuti ayankhe kuti kwacha 😂😂😂 lelo a kulila poyela ndiposo guys mongokumbusana a mcp sinawinile man to man inawinila pasewu monthandizidwa ndi chilima lelo kulibe tiyeni nazoni
Tivindere imwe chimulomo!! mesa iwe ndiwe ukatumanga wanthu navigwandala mbuzi iwe zimilomo ngat chikopa chankhumba
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Sense munapha nokha a MCP. Anyamata aku nchesi umboni tilinao.
Fiti ndinu A MCP muzafziyeletse kamba kandale
Action is louder than words (Inu muatuma adzikwanje pomwe enawo amango Nena ndi pakamwa
MCP zachikwanje mwaziyiwala kulilongwe zakumbowe mwaziyiwala mcp ndinu zisiru
Uyu mayiyu ndi hule,,jess ulira 2025,, you gonna see the world
Zitsiru kupatsa ntchito atolankhani.kodi akutama smartmatic.kupanda Achilima munali ayani inu agankanka.zigaeenga kuyamba 1960s.ng'ona zosekerera
DPP PALIBE KUPEPESA MUYAMBE KAYE INUYO ANYAPAPI AKUPHA MUPEPESE PAZOMWE MUNACHITIRA A MALAWI POWAPHERA SAULOS CHILIMA ,NKHONDOYO MWAIYAMBA NOKHA MESA MUKUMATUMA AZIKWANJE NDIYE ZAKUIPIRANI ? SIMUWINAYI MUNYANAYO
DPP❤❤❤❤🎉🎉
Ku tsungwi ku 25 kungo mvala Cha Dpp amamumenya😮
Tizakutibulanibe😂😂😂😂
Nanunso musiye kubwera ku LL tikutibulani. Paja simuchedwa kuliratu. Kungomuona munthu akunola chikwanje kuti akadule mitengo inu njenjenje kumaganiza kuti afuna akukhapeni. Ngati nkhani yake iri imeneyo muzipanga kwanu konko campaign
@anthonynkhoma4265 Inunso chimodzi modzi
Ayamba kale ayamba kale.....
Simunati mulira mwayiwala kuti munayambisa nokha pamene anzanu akubweza mwayamba kubuula Kodi amayenda ndikukwatire athu kulilongwekuja anali adpp?.mumawona ngati azanu samatha. DPP woyeeee
Mutu ngati phwala la ngamira Iwe ayiseye....
1.Where is the black box?
2. If the aeroplane had no transponder then how did you know that the aeroplane took the wrong direction?
3. Anamuuza chimwendo kuti ndege yadzadza ndindani?
4. Chakwela anawuza amalawi kuti ndenge inafika kunzuzu ndipo anawuzidwa kuti abwelele, anamuuza ndindani?
5. Where is the black box?
6. Anthu mukuti anafela mmalele, who told you?
7. Mukuti amafika pansi alibe magazi, madzi, nde anawayamwa ndindani?
8. Valentino phiri, nkulu wa asilikali, anawuza amalawi kuti ndege inawomba phili, anamuuza ndindani?
9. Inu ndege kugwa pa kutali kwa 5meters, anakuuzani ndindani?
Anachimutu akulira boma lapita ku DPP
Malo mozuzura anyamata ache azikwanje aja akulimbana ndi zaziii. Ziwawa zimene zikuchitika ku chigawo cha pakati akupangitsa ndi CHIMWENDO.
Za ziiiii 😊
10:43 10:44
Chimwendo ngati zambiri umalakwitsa koma apapa wandiyankhulira bwino,tikuyenera kudzudzura potsatira malamulo momwe akunenela
Azikwanje mumawatuma aja zisiru zaathu agalu, u bwno wake opposition ndiimene ikuwina zitsankho mayiko ambili
DPP singapepese.zoti munagula mifuti tikuziwa ndpo zot mwaitanisa mifut yama mp tikuziwa ndithu.
Komatu jezze ankhakale ndi nyini yabwinotu guys 😂😂😂😂😂 DPP moto ❤❤❤❤❤
Inutu musaiware kuti .peter muthalika......nayeso anagendedwapo ku ndilande..... komweko...nde nthawi imene..inja linali ....mcp? Tiyakheni...nde muzingoti ... dpp...mukulakwisa.... zediiii
Iiiii koma MCP 😂😂😂😂😂😂 Ili pa mavuto kwabasi kkkkkkkk 😂😂😂😂😂😂
Mulibe nzeru inu a congress party munayambitsa ziwawa ndinu Ndi anyamata anu azikwanje musadandaule pazomwe a DPP bwanji anu akwa nsundwe
DPP yangoyakhula mwabwela mwayakhulapo km inuyo mukabwela ndizikwanje a DPP ndizipani Zina akandandaula mukuti akulira kt sazawina aaaaaa mwayambisa nokha.
MCP never again, and your Chakwera is not clean. Where is our Chilima? There is no police in malawi rather, Mcp thugs in police uniform.
Bwanji press briefing ya report ya ndege
Dpp supporters are indeed good viewers don't mind their comments they're embittered so hard.Hopefully they will control their complete downfall come September 2025.
Ngati mcp muli ready ndiye nenani tiuzeni siku musaone ngati amalawi akukuopani ndinu upusa kwabasi ngati mukufuna kuvula vulani akape inu mumalo monena chimene chalakwika basi kumazitama kuti nafeso tivula ngati mp wa ddp walakwisa muzuzuleni chabe osati kuti ife ndife tinayamba malawi kuyakhula kopusa orton chirwa ndi amene anapangisa nyasaland kukhala malawi inu ndinu olanda chilima akuyikani pabwino pano mwalanda ubwino wachilima. Apumbwa nose
Aaaaa..😂😂😂😂😂😂 koma agalu awa zikwaje zija mayenda nazo Town ndi anyamata aku 24 zija anali a DPP
Mwaiva ku dowa amayimbira a dpp 😂😂😂😂😂a Malawi ayembekeza atopa mvuuuuuuu
MCP 2025 Boma. Nafe kuthekera kobwexera tili nako km ife stikufuna kubwexera ayi. Inu aDpp km dziwani kt nafe tidzatopa nazo zimenezo. Ambuye akukhululukiren inu aDpp.
Amcp mwalephela kulamula dziko kupha anthu ku chikangawa amene sakuidziwani ndindani mumatuma azikwanje
Mul ndi chibwana inu a mcp, km mutulukabe m'boma, km mukatuluka m'bomamo simuzalowaso m'boma, mesa a police-wo ndi anu, mudandaura chani pot dzikori ndilanu
Atolankhani mulephela kuwakumbusa za ku mbowe bwanji komanso anyamata azikwanje nanunso mwadya chi banzi
Let MCP and DPP presidents meet and reconcile or they will cause wrangles in Malawi of which we donnot want
Are we sure Malawians will change their mindset and transform the nation especially DPP and MCPdiehards with their vile mentality?????!May God intervene!!!!!
Patumbo PANO nonse a MCP. Kod mmesa zomenya anthu munayamba ndinu?? Lero mukufuna ntendele chifukwa chot DPP yayamba kubweza?? Tikuswa kumene agalu okupha Inu. Maka Maka iwe okula mutu iwe chimwendo banda ulipila magazi a anthu aja unawapha kuchikangawa aja
Kodi lelo a mcp a kulila ndimau aja oyamba kumenya mayesa munali inuyo ndizikwanje aaaaaa khonya yobwezela kuwawa mumva peni kumene
DPP UDF my vote
Kod mcp mukudziwa kuti anthu omwe alembetsa kuti avote 2025 ndi okawo owawidwa muntima kuti achose chakwera pampando ndiye mukamamunamidza mumuonongetsa ndalama wabadzo mudzagwa ndi bp dzisamalika ndi kunena mbwereradzo
Koma ndiye mukunamizanatu muzidya komaliza mudzaona 2025 titular nkhuku imeneyo, Boma ndilomweli koma tisinda apule ndi chipani
May God have Mercy upon us😢we are not safe as county 😭
Eèe koma ku MCP kudadzaza anthu a sweet talk but an action is 0 out of 10...Ndiye mumuuze Chimwendoyo kuti akamayankhula anthu amuzungulirawo nkumamuophera manja asaone ngati kunjaku kuti anthu akuombaso m'manja adzalira kkkk
Koma DPP imangoyankhula, MCP ndiomwe imadziwa kukoza.
Koditu umunthu wamunthu umadziwika ndi źochitika zake osati zoyankhula zake.Ndiye awawa a MCP akuwatenga amalawi ngati ogona koma adzazindikira bwino patsongolo nthawi itatha kale.😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Mene anabwera chisale central region tinamusiya kupanga sokhano ku central region sikuti iyeyo ndiwochenjela koma democracy si nkhondo that's why tikulora kuti zitero