It is a wonderful coincidence that 1979 I also had an epochal dream that was my TURNING POINT and I'm an SDA for over 40 years. I got baptized in 1981. Alleluia
We are waiting for another evangelism efforts from you our PS .We were blessed with those efforts done in Lilongwe , Bangwe and Balaka. The Bible is revealed in it's manner in your preachings.God should continue caring and blessing you . Amen
May God grant you financial breakthrough to buy the mic you preferred to them and many. Can’t wait to hear your testimony how to bought mics to many as a way of serving God.
Poyamba ndinamva kukoma ndi ulaliki wanu abusa, koma mutangololera kusintha logo ya Angelo atatu, kubwelesa ya ntanda, mudasokoneza mpingo wa SDA mudalowesa satana inu
Adawononga mpingo abambowa Ndipo ine ndimawakonda,koma mmmm awa si abusa akuchita mau ayi Ndale za walowa Kusintha Logo ya mpingo Komanso kuvomeleza kusintha tsiku la sabata kulilemba mozembayitsa
It is a wonderful coincidence that 1979 I also had an epochal dream that was my TURNING POINT and I'm an SDA for over 40 years. I got baptized in 1981. Alleluia
We are waiting for another evangelism efforts from you our PS .We were blessed with those efforts done in Lilongwe , Bangwe and Balaka. The Bible is revealed in it's manner in your preachings.God should continue caring and blessing you . Amen
This is so inspiring
Koma nde zovuta zapa dziko,munthu mmodz kukhala mubusa wa mpingo kwinako wandale mmmm bweleran kwa Yesu AY nyirenda pangan chimodz
Strongest honest Malawian Pastor..
Very nice utumiki ochokera kwa Mulungu susowa umayambilad ulimwana that's nice ndaukonda Amen mumandidaritsa zed ❤
Amen my pastor 🙏
We lost hope in you our pastor
Indeed we did up to day am not happy
Mbusa wa mcp akamalalika ngati ngero shame
Yes yes
Amen
Abusa a Nyirenda amandisangalatsa
Tamapezani microphone abwino. Ongopachika aja
Kkkkkkkkk
Basi mic ai
May God grant you financial breakthrough to buy the mic you preferred to them and many. Can’t wait to hear your testimony how to bought mics to many as a way of serving God.
Abusa akwathu ku Lwazi mission
Kweni va ndale ivi ayamba aleki atilengesa ukongwa
Kikiki
Poyamba ndinamva kukoma ndi ulaliki wanu abusa, koma mutangololera kusintha logo ya Angelo atatu, kubwelesa ya ntanda, mudasokoneza mpingo wa SDA mudalowesa satana inu
Aaaaaaaa!!!!
Kukonda chuma kuthandizira kugulitsa Choona. Lero Seventh day ndi mumtima mwa munthu payekha. Mulungu atithandize kuti tonse tikalowe
Achimwene mpingo ndi iweyo kapenamtima wako ndiye chalichi satanikiso ndiwe wekhanso kulandila kapena kukana eeetu chimwene
Adawononga mpingo abambowa
Ndipo ine ndimawakonda,koma mmmm awa si abusa akuchita mau ayi
Ndale za walowa
Kusintha Logo ya mpingo
Komanso kuvomeleza kusintha tsiku la sabata kulilemba mozembayitsa
Mu logo mulibe chipulumutso konzani mtima wanu basi inuyo
Osazanyoza athu okumwa mowo coz you never wat tomorrow bro gs,yokuyenera kuwalimbokitsa anthu a mowa or osita fodya
Amen