Kumenya kugwetsa 🔥❤️My personal thoughts I think mkaz wa hyphen azimvalako Kaya msalu mene amapanjira sangie coz yobwereza trouser sizilibwino don't come for me😂 personal thoughts
My couple crush all day ( Ngozo & Patricia ).... However guys zomat dzuwa lindiwalire inunso mumdiwalire sizoona ay...... For how long are we gonna wait for episode 8 to come???😢😢😢😢 Koma have u ever been betrayed in your lives guys?? Do u know the feeling of being betrayed???? Coz this is betrayal guys plz plz take care of our hearts and feelings do not keep us waiting for so long for u to release an episode...on my bended knees..i beg🥰🙏 But all the same 🥰 forever in my ❤️💋
Sangie knows how to act iiih 🙌🙌. Physix also acts Normal ngati its not acting, like he's living a normal life.. Kkkkk... Y'all are good actors and actresses eish 🙌😂
Pa scene Gani ndi Jabu nde mwapanga zamafilm aku India tu A Jabu afila mkazi uja and akumana naye pa gate anamuza kuti akudikila Gani ampase container Nde akuchezamo a Jabu wo mesa anakamuziwisa Gani kuti nfana wake akukuziwaso ndiyemwe anamupasila container 🙌🤣😂 Apa mwa bleyesatu otherwise serie ndiyabho
you guys are good actors...........youtube malawi Would have been useless without USAUVER
Koma ineyo nditha kuchezera kuonela banja ili Patricia ndi amuna ake angozo simatopa nawo take your ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ from mi
Raga moffin 😂💀
ndipo limabhebha@@Jamespangani
ndipo kwambiri or ine ase
Ineso kwambiri
koma Patricia iiiih ayi zikomo ndithu 😂😂😂🙌🤣
Ati simkazi uja ndinamulota uyuu moti sanandikumbukire😅😅😅😅
Koma sangie ..kkkkkkk koma amadekha pokamba nkhani iiii kkkkkkkk
Clean visual I can see the growth amwene respect Media team 🙌🏿🙌🏿🙌🏿🙌🏿🎉🎉🎉🎉
🤣🤣🤣🤣 And I caught "koma munthu mungamutengere yooose" 🤣🤣🤣🤣
I like sangie's voice ❤
Gani iweyo ndichisilu 😂😂😂😂 ndiwe ochenjela mopusa.let's gather here for Gani
Ndiponsooo iiiiiiii ati kumapanga follow zi2 mukabweleketsa 😂😂😂😂
Rule number one don't skip USAUVER ❤❤❤❤❤
To say the truth Gani is a complete actor😂😂
Sangie assy😂😂
Kumenya kugwetsa 🔥❤️My personal thoughts I think mkaz wa hyphen azimvalako Kaya msalu mene amapanjira sangie coz yobwereza trouser sizilibwino
don't come for me😂 personal thoughts
Eish.....😂😂😂😂😂
My couple crush all day ( Ngozo & Patricia ).... However guys zomat dzuwa lindiwalire inunso mumdiwalire sizoona ay...... For how long are we gonna wait for episode 8 to come???😢😢😢😢 Koma have u ever been betrayed in your lives guys?? Do u know the feeling of being betrayed???? Coz this is betrayal guys plz plz take care of our hearts and feelings do not keep us waiting for so long for u to release an episode...on my bended knees..i beg🥰🙏
But all the same 🥰 forever in my ❤️💋
Mtebe, Sengie and Ghani are pure talents. Ati mutu ngati Bus 😂😂😂😂❤
Koma sing'angayo perfect for the role🤣🤣🤣
Reception yawo kodi inu bwaaanjii😂km muthu ungamutengela yooonseee😂😂😂 km sangie😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂 imagine Ali pheee kudandaula modekha esh
Patricia ati village yawo yasowa 😂😂koma banja iyi😂😂mabebesa
😅😅😅😅😅
Sangie knows how to act iiih 🙌🙌.
Physix also acts Normal ngati its not acting, like he's living a normal life..
Kkkkk...
Y'all are good actors and actresses eish 🙌😂
Munthu omupemphelera uja wasanduka woswa mtima mpaka kuvula abusa 😂😂😂mtebe pena 😅😅
Sangie mpaka pamenepo😂😂😂ati munthu ungamutengere yonsee😂😂😂😂😂
Omwe sitikuidziwa Raggamofin lets gather here Gani atiuze kuti ndichani...
😂😂😂😂🙌🏻🙌🏻Mpaka mofin
First person to watch🎉❤
❤❤koma Sangie mpaka ungamutengere yonseeee😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Mtebe amafunika pqma awards😂😂🎉
😂😂😂😂😂 Ati reception, village koma u deserve award ase😂😂😂 Sangie iwe nd 1
Sangie n ngauzo aah😂😂
Mtebe maloto anzako mpaka mkwiyo😅😅😅
Ganie ndiwe oipa mtima mmmh
Running out words iyiyi mwapha guys aliyense pamalo pake.❤❤
Sangie yu giving good vibe❤😂😂
😅😅😅😅
🤣😂😅🙌🙌aaah abusa maloto mpaka mikangano zama loto
Anamupatsa service yabwino 😂😂
Sangie aaaaah ati nsing'anga ameneyu ndimfuna. Kayese tione ngati supenga misala koma piksy aaaah
I can't wait gani Kaya zimuthela bwanji akamuziwa kut anatenga ndiwo ndiyeyo
😂😂😂 Gani sanachenjere bwino
Always imatha ikubebabe😂😅 wish mukanama pangs release new episode daily guys
Reception yasowa in Sangie's voice 😂😂😂
Mtebe wangovulidwa nkusiyidwa 😂😂kulakwa iiiii😂
Mnaboweka now my mood is revived.... Sangie😂🙌
Okondedwa ngozo❤ Kodi unasiya kundipatsa ndalama pa Christmas? Kodi tachezetsa? Iwe si mfiti?
Sangie iweyo 😂 kumwamba tikakhale pamodzi umabebetsa 😂😂
Once again, you guys never disappoint. Koma banja la aNgozo anapezana 😅
Fire😅😅🔥
just when i thought i had seen it all then boom abale mpaka reception😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂 km gani ND #1
Ntebe ndi dolo magaye😂😂🔥🔥🔥🙌
KKK koma ndaseka akuti mabodzatu kkkkk keep it up guys mumativetsa kukoma
I regret watching this in the bank....koma sangie🤣🤣🤣🙌
My favoritecomedians after Izeck uja
Ati umangofuna undvule undsye 😅😅😂
😅😅 Koma Sangie ati 'angamutengere yonseee, mmmh pa Malawi panopaaa'😅😅😅😅😅 eeeeeh banja ili limabhebetsa kwabasi 😂😂😂
Tonde, ngani ❤
Kkkkkkk mtebede wavulibwa uku 🤣😂😂😂
😂😂😂 imagine
😂😂😂😂Mtebe amandiwaza ndi mzake tonde@@elizabethkawonga
😂😂😂😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Mtebe kusokosa
Patricia ndi Ngozo 😂😂😂inuyo tsikulina muzangobwelapo nokha basi😂😂,,ati kodi iweyo si mfiti😂😂😂😂
🔥🔥🔥 khani ndi yakotena Gani usaphiphilise😂😂 takondwa lelo wadekha good grill 💥💫
I like sangie kkkk❤
😂😂😂😂ntebe wavulidwa😂😂😂😂😂😂😂😂aaaa😂😂😂😂😂
Sangie ndi ngozooo ai fenks😂😂😂😂😂🙌🏼🙌🏼
Iiiiih🤣😂😂Sangie ati koma iyeyu si mfiti..naye Tonde aaah🤣,Mtebe ukwiya bwanji nanga mesa ndiwe m'busa😂
U guys are the best koma ghani aaah iwe ndi goat😂😂😂
Ntebe for me😂😂😂😂
Kkkkkk koma2 mtebeee!!!!😂😂😂😂😂
Hi hi, zimayambila pompo...😂
Tipatseni Hi ife
😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 Km naye amunake aja samadziwa kt ndi handsome 😊😊........ Anyway ndabwelera hi pano hie hie
😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 Koma Patricia
Kakumaloto kaonekera😂😂
Kodi simungamupezere Malo Bhima Ndalama umumu?
Gani ...kuzitsekeleza za container 😂😂😂
😅😅😅 koma sangie ati munthu unga ungamutengere zonse😂😂😂😂
Kkkkkk Koma banj'a la angoza ndilama bodza aaaaaa 😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤❤❤
Mtebe wabalalika ndi maloto a neba. Asa 😂koma ndaseka aaaaah. Nthawi yomweyo phone call eeeeeh mtebe wakwiilatu
Ghanni is the biggest natural talent we'll ever have after Izeck 🎉❤
Straight up bro 😅👐
@khukujrk7890 ichi chimakometsa zosakakamiza 😂
@vincentbankam6406 😅😅🤌
Ndidolo koma don't compare him with izeki
Angozo ndi Patricia ❤🔥🔥
Ati nanu tisacheze😂🤣🤣mtebe usamale reception yako itha kusowaxo🤣🤣🙌
😂mphwake wa Tonde Ben10 wayamba kubhebesa😂😂😂😂
Hahaha koma Sangie ndi Dolo kwambiri 😅😅
Kkkkkkk koma mayi gozo amakometsa zithu😂😂
The best show on planet now
It's the kodi unasiya kundipatsa ndalama pa Christmas for me😂
Ganizan kupanga control nkhan ya containe 😂😂😂😂😂😂😂😂
I like banja la Ngouzo n Patricia❤❤
Koma sangie iweyo😂😂😂😂😂ayi ndithu......kodi inu bwanji
Ndipo Patricia ndendende mayakhuridwe ake ndi mkaz wanga 😂
Ooo noo,guys eee mmabebetsa!Gani😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂 koma nafwaa aaaah! Sangie ndi Pirksy mmatha 🔥 🔥 🔥 ati engine yasowa ndi gear box yomwe? 😂😂😂
😂😂😂sanjie❤️
❤❤❤❤❤❤ my favorites
Aaaah choka!!😂😂
Abusa kuno ayamb zisamba😂😂😂😂😂
Ndimfitidi 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Pa scene Gani ndi Jabu nde mwapanga zamafilm aku India tu
A Jabu afila mkazi uja and akumana naye pa gate anamuza kuti akudikila Gani ampase container
Nde akuchezamo a Jabu wo mesa anakamuziwisa Gani kuti nfana wake akukuziwaso ndiyemwe anamupasila container 🙌🤣😂
Apa mwa bleyesatu otherwise serie ndiyabho
Engine yapita¿ Giya box ilipo km¿ Sangie siyani zoimba pitilizani izi mukuitha kwambili mukumatimvetsa kukoma kwambili 😂😂❤❤❤
Gan ndi 1❤❤
Koma Patricia ndi ngozo😂😂😂😂😂
The family that know how to gossip 😂😂😂
Family that gossip together stays together 🤣
@shamirac5293 yooo no body like this family eeh 🤣🤣🫡
Great 🎉
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Sangieeeee
Sangie eeeeee😂🙌🙌🙌🙌🙌
akuswera bwanji mtima yet your role is just to pray for her😂😂
waiting 4 u akometsi🔥🔥🔥
Mamunaso amavulidwa mkusiyidwa😂😂😂
Zolalata zomwe zijaa?? 😂😂😂😂
Nkhaniyi ineso ndachita kumva ndie mumafuna muzikanena ukooo 😂😂😂😂😂 my patricia 😂😂😂😂
3:18 koma munthu ungamutengere yonse 😂😂😂
Moti iweyo ndiophweka choncho aliyense amangokulot mmene angafunile😂😂
Wandiswela mtima nsaname 🤣
Mtebee🤣🤣