Chakwera amangodziwa Baibulo sadziwa zachuma Watero Lyton Mangochi

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 52

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 2 หลายเดือนก่อน +5

    A Lyton Mangochi mwayankhula za nzeru kwambiri, Chakwera amangodziwa ma ves basi, mu mutu wake muli mamina wokha wokha. APM abwerere basi.

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ma ARV a muzunguxa mutu uyu

  • @oskidooscar7468
    @oskidooscar7468 2 หลายเดือนก่อน

    A lyton pano ndi the DC Akugwila mtchito limoz
    Pitan bas ku the peoples first baba mukalowe gulu

  • @MoosaDawood-l5c
    @MoosaDawood-l5c 2 หลายเดือนก่อน

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤you right sir iwe Ng,alula

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 2 หลายเดือนก่อน +3

    Mr Mangochi amayankhula chilungamo koma samaziwika kuti ali mbali iti ndi mbewa kapena Mleme 😂😂😂😂

    • @edsonnyasulu5394
      @edsonnyasulu5394 2 หลายเดือนก่อน

      Peter ndiyeso ayi malawi apite kwa axhinyamata

    • @edsonnyasulu5394
      @edsonnyasulu5394 2 หลายเดือนก่อน

      Malawi muli anthu nzeru tiyesepo ena achinyamata

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 2 หลายเดือนก่อน

    Exactly man mutambo ananena kale kuti mcp ndi mfiti

  • @HaroonKampepule
    @HaroonKampepule 2 หลายเดือนก่อน +3

    ، achoke achoke Chakwera achoke

  • @OssmanAbubaker-k9w
    @OssmanAbubaker-k9w 2 หลายเดือนก่อน

    Apapatu Mr Lyton Mangochi mwakwanisa Ulemu wanu apadi mwaima pachilungamo ulemu wanu

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 2 หลายเดือนก่อน

    Amachita Bwino ryiton chifukwa akalowera kwachabe amabwerela mwachangu amadziwa Kuti amalawi amasiku ano anasukusula ..u are Wellcome Mr Mangochi.. Koma abilimankhwe awiri longwe NDI Munro.. ndalama Za magazi zi zikawathera asazabwere apa NDI manyaka siizaveka

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 หลายเดือนก่อน +1

    Pa convention ya MCPigs
    1) ma delegates 60 anakhapana.
    2) ma delegates awiri anapezeka atafa ku room.
    ☝️Ndiye muziti "kwacha, kwacha" zakalekale.

  • @TisopeMkozo
    @TisopeMkozo 2 หลายเดือนก่อน +1

    Bola zikhale zochokera pansi pamtima zomwe ukuyankhurazo

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 2 หลายเดือนก่อน +1

    A very distinguished President, a few among many. Within four years Malawi has changed.

    • @KhooMadex
      @KhooMadex 2 หลายเดือนก่อน

      @ ur home yes not malawians

  • @LucyMachine
    @LucyMachine 2 หลายเดือนก่อน

    Mwayakhula zazeru bro

  • @GiftChitsulo
    @GiftChitsulo 2 หลายเดือนก่อน

    Mwabwela inuyo ❤❤❤❤mangochi

  • @Drmuhammadchiwona
    @Drmuhammadchiwona 2 หลายเดือนก่อน

    Achoke basi apm my vote

  • @CaciousChiwengo
    @CaciousChiwengo 2 หลายเดือนก่อน

    Aaaaaah wapengatu uyu

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 หลายเดือนก่อน

    Lytton mangochi tiuzeni mbale imene muli 😂😂😂😂😂😂😂

  • @jamessheki4293
    @jamessheki4293 2 หลายเดือนก่อน +1

    Bola ukunena chilungamo

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 หลายเดือนก่อน +2

    Pano tayambaso kukonda

  • @Ahlubyt
    @Ahlubyt 2 หลายเดือนก่อน +2

    Mcp ituluke M'boma basi

  • @JohnBanda-bh5gz
    @JohnBanda-bh5gz 2 หลายเดือนก่อน

    Choka iwe wasowa zonena palibe wabwino kulibe ena amene angalamulile malawi? Kupusa
    Peter ndindaninso Peter,,And chakwela zao ndizimodzi
    Bola kusakha ena osati amenewa
    Zitchito zawo tauwona
    Ndiwe opusa ukulakhulawe

  • @MaliGomani-z4k
    @MaliGomani-z4k 2 หลายเดือนก่อน

    😂 Vuto la uyu sachedwa kutembenuka😂😂😂😂 lyton ndimbuziso😅😅

  • @TwayibuChimbama-b8w
    @TwayibuChimbama-b8w 2 หลายเดือนก่อน

    Awa sanawalipire

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 หลายเดือนก่อน

    Ndipo uyu vuto lake kusawuka kwambiri panopa akufuna Dpp koma chilugamo kuti Dpp ndiyomwe iliyabwino

  • @VishonVishon-sj4cx
    @VishonVishon-sj4cx 2 หลายเดือนก่อน

    Apa laitoni mangochi tagwilizana apa basi

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ndalama zatha zomwe anampasa

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 หลายเดือนก่อน

      @@victorauwana7258 🤣🤣akatero akufunaso zina

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 2 หลายเดือนก่อน

    Mutu sumayenda lyrtone

  • @AlexMduladulaMafuleka
    @AlexMduladulaMafuleka 2 หลายเดือนก่อน

    Mwapenga inu Malume

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 หลายเดือนก่อน

    Chakwera ndi mbunzi kwabasi

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 2 หลายเดือนก่อน

    Nanu bible lomwe amalidziwa chakwela ndiliti ?
    Lausatana lomwelo , mumakweza nkhano muntengobwanji

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 2 หลายเดือนก่อน

    Nthawi ija unatiuza kt mcp ikupanga chitukuko 😂😂😂😂😂 Chitumbuwa chamuthela sopano komabe ndazikonda wanena bho

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 2 หลายเดือนก่อน

    Chakwela satana mbuzi sakuzi hata chimozi

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 2 หลายเดือนก่อน

    Komw iyiyi ndimbuzi yamunthu wawona kuti anzako anakuwukira aku mangochi galu iwe wayamba kusintha pitawuko satana wamunthu iwe koma ukunama chitsilu iwe

  • @SueWahna
    @SueWahna 2 หลายเดือนก่อน

    Bola ngat sanatumidwe

  • @BoysonNgwenya
    @BoysonNgwenya 2 หลายเดือนก่อน

    Koma mkationese komwe mkuti Ali chilimako kuchikangawa tiziweko tikamuone

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 หลายเดือนก่อน

    Banzi likakhala chimtuwitsa fanta amachepa. Koma fanta akachuluka banzi limachepa. Likachepa umayamba kunena zoona zokhazokha.

  • @Ahlubyt
    @Ahlubyt 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zatha anampatsa zija?

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 หลายเดือนก่อน

      @@Ahlubyt 🤣🤣😂

    • @JumaKachala
      @JumaKachala 2 หลายเดือนก่อน

      Kkkkkkk. khala ngat

  • @FosterChakanga
    @FosterChakanga 2 หลายเดือนก่อน +1

    Chamisala ichi😂😂

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 หลายเดือนก่อน

      @@FosterChakanga 🤣🤣🤣

  • @imraanJafal
    @imraanJafal 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂😂 Ulemu wanu

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 หลายเดือนก่อน

      @@imraanJafal 😂😂🤣✌️🔥thanks

  • @johnchicoti
    @johnchicoti 2 หลายเดือนก่อน

    Zopusa chitsilu iweyo