BON KALINDO LERO 12 AUGUST WANG’ALURA MCP AKUTI AKUPANGA MA PLAN OFUNA KULIMBANA NAYE KOMA SAMUTHA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 24 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 248

  • @Rometcma
    @Rometcma 2 หลายเดือนก่อน +13

    Ndikadakonda bon kalindo utakhala president kwinako Malawi angasithe coz umphawi mumaudziwa bwana🎉🎉🎉

    • @kishasbeatsproduction4944
      @kishasbeatsproduction4944 2 หลายเดือนก่อน

      amaoneka olungama akakhala kunja

    • @Rometcma
      @Rometcma 2 หลายเดือนก่อน

      Kkkkk ndale pa Malawi

    • @eunicemacdonaldkaipsa9705
      @eunicemacdonaldkaipsa9705 2 หลายเดือนก่อน

      ​@@kishasbeatsproduction4944mumwa chan bwana pa bill yanga

  • @GrantNkhoma
    @GrantNkhoma 12 วันที่ผ่านมา

    Mumakwanira boss man ipasen moto🔥🔥🔥🔥

  • @GeorgeMekwana
    @GeorgeMekwana 2 หลายเดือนก่อน +5

    The DC, President wa a Malawi osawuka, Malawi First go deeper

  • @DavieMathyola
    @DavieMathyola 2 หลายเดือนก่อน

    Osaopa osafooka comrade tanyiwa ,karindo again via bakili muluzi tv

  • @allanjosamu
    @allanjosamu 2 หลายเดือนก่อน +4

    munthuyu mutu sugwira ndavetsetsa coz munthuyu akupanga target ma lndividuals😮😮😮

  • @RebeccaNvenya
    @RebeccaNvenya 2 หลายเดือนก่อน +4

    More 🔥 the Deeeeeceeee mwana oophya kwambiri 💪

  • @abe9104
    @abe9104 2 หลายเดือนก่อน

    my brother man for others woman u are number one

  • @GiftMakowa-k9f
    @GiftMakowa-k9f 2 หลายเดือนก่อน

    Ulemu wanu Mr DC timakunyadilani kwambili❤❤❤

  • @Rix297
    @Rix297 2 หลายเดือนก่อน

    He is making total sense.
    Aluza ku convention atiphweteka awa.

  • @ANDIWOTCHIMedison
    @ANDIWOTCHIMedison หลายเดือนก่อน

    Medison usi malawi akudataula kuti
    Palibe amene akusapota
    Akuipa bwino bwanji fanayu akutulusa

  • @HamissMaidaz-x4h
    @HamissMaidaz-x4h 2 หลายเดือนก่อน +1

    The dc mwana owophya kwambiliiiii❤❤❤❤❤❤

  • @martinndawala8125
    @martinndawala8125 2 หลายเดือนก่อน +4

    Tamangooyikani Audio straight basi. Osatinso kummaiyankhulira kaye, voice yanuyo ikumapweteka mkutu.

  • @ChiccoJelly-wp5wj
    @ChiccoJelly-wp5wj 2 หลายเดือนก่อน +1

    We need to have 10 people in Malawi like Born kalindo

    • @GotepoBanda
      @GotepoBanda 2 หลายเดือนก่อน

      Mau koma awawa olo alipo five

  • @HendryChiwezo
    @HendryChiwezo 2 หลายเดือนก่อน +6

    Mmmmm wankali samadzing'amba yekha tsiku lidzakwana akalindo

    • @SanudiMcDonald
      @SanudiMcDonald 2 หลายเดือนก่อน +3

      Iwetu iwe unya ndi chakwera wakoyo

    • @lucianoGeoffrey
      @lucianoGeoffrey 2 หลายเดือนก่อน +1

      Pita ukakumane naye nde uzatiuze zomwe ukazione

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 2 หลายเดือนก่อน +1

      Pamtumbo pako ndi Chakwera wakoyo munapha chilima inu fiti simuwina agulu onukha kuthako

    • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
      @AbdulsharifulKalipinde-m6u 2 หลายเดือนก่อน

      Iweyo koma ndiye uny'a nayo
      Chaka chake sichino

    • @DjshukulanGift
      @DjshukulanGift 2 หลายเดือนก่อน

      Ukanakhara wazelu ukanakhala chete ,😡mwadzi...

  • @MAFUNSOMOLESI
    @MAFUNSOMOLESI 2 หลายเดือนก่อน

    I like you so much Mr president watu

  • @lovemorembedza9145
    @lovemorembedza9145 2 หลายเดือนก่อน +2

    Aaaaaah inu zachapani zigwirizana bwanji ndi za dziko ndindani angalimbane ndi munthu openga

  • @johnmponda9070
    @johnmponda9070 2 หลายเดือนก่อน

    Koma ine nkhani ya njuchiyo mwinatu nduna zinazi sizikudziwa akusewelatu amenewa😊😊😊

  • @DorisNkwanda
    @DorisNkwanda 2 หลายเดือนก่อน

    The Dc...... Mwana wA line katola

  • @PeturosiNyirenda
    @PeturosiNyirenda 2 หลายเดือนก่อน +3

    Apambaze amenewo 🤣🤣🤣🤣🤣🙆🙆🙆🙌🏽🙌🏽🙌🏽💥💥💥💥💥

  • @DanielNandajester
    @DanielNandajester 2 หลายเดือนก่อน +1

    Awa koma apange resin chifukwa chachani mmmmm tapanga zako Bon

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 2 หลายเดือนก่อน

      Pamtumbo pako galu ndi chakwera wakoyo munapha Chilima simuwina anthu onukha kuthako inu

  • @LameckGamah
    @LameckGamah 2 หลายเดือนก่อน

    Awa kwao kwatha let's see, time is coming amalawi atopa.

  • @TerezaJaenda
    @TerezaJaenda 2 หลายเดือนก่อน +2

    Sazanthekadi mmmmm katundu waboma kkkk🎉🎉😊

  • @PhalesNotta
    @PhalesNotta 2 หลายเดือนก่อน

    Ndipo ayidya momvutadi ameneyoooooo😊

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mwana wa line katole😊😊😊😊😊

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 หลายเดือนก่อน +1

    The DC bon kalindo akunama iyeyo mr chikangawa aziwa chaka chino

  • @GiftNgwira-e8l
    @GiftNgwira-e8l 2 หลายเดือนก่อน +1

    Uyu ndi big man the DC chakwera chakwera ndimwana

  • @DominiqueChitimbe
    @DominiqueChitimbe 2 หลายเดือนก่อน +7

    the DC ❤akamuna muna

  • @mbonilekisebe2286
    @mbonilekisebe2286 2 หลายเดือนก่อน +1

    The DC mwana owoopsa kwambiri... Umakawana aise. Afiti a MCP sakupuma nawe bwino

  • @JessieKholopa
    @JessieKholopa 2 หลายเดือนก่อน +1

    Uyu eee ndi akatundu omanga ndi mawaya👐👐👐

  • @FosterChinzimuBanda
    @FosterChinzimuBanda 2 หลายเดือนก่อน

    The DC mwana ophya kwambili❤

  • @LOUISCHEN-w7u
    @LOUISCHEN-w7u 16 วันที่ผ่านมา

    akufunika uwaphe mkhwala kkkkk

  • @ShukuraniChitanganya
    @ShukuraniChitanganya 2 หลายเดือนก่อน

    Koma Born kalindo ndakakutundu 😂😂😂😂

  • @AndsonAcd-j6i
    @AndsonAcd-j6i 2 หลายเดือนก่อน +1

    GOD BE WITH YOU BON KALINDO

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 หลายเดือนก่อน +1

    Love you Bon kalindo we silute you forever❤

  • @alomuddin8801
    @alomuddin8801 2 หลายเดือนก่อน

    Boni kalindo DC ukumuyiliradi Mmalawi osauka, pitilinzani kuwaunikira azipani zomwe zikufuna kupanga mgwilinzano 2025, kmso kumuunikira munthu wa kumudzi chifukwa munthu wa kumudzi amangovota moti zingomuchoka mosaonetsetsayi mosaonetsetsa

  • @PraiseDuweh
    @PraiseDuweh 2 หลายเดือนก่อน

    Km ichi amwene

  • @RodgersMatola
    @RodgersMatola 2 หลายเดือนก่อน

    DC kuno ku Kasungu tiyankhulireni , akufuna kupeleka ngongole koma chodabwitsa akufuna ma lD ,ndiye kuno anthu akupeleka ma ID maka ife ma MUSLIM, chonde bwana DC tiyankhuleni

  • @agnesschauya7687
    @agnesschauya7687 2 หลายเดือนก่อน

    Aaaa zaziii, ofuna kuzipha salengeza, panga zomwe umatha tiwone

  • @WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un
    @WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un 2 หลายเดือนก่อน

    Tiyeni nawo bon kalindo aña achepa ngt àli madolo tikakumane chikagawa

  • @SARGENTZIMBAMAGABA
    @SARGENTZIMBAMAGABA 2 หลายเดือนก่อน

    UTM koma musitisilizaaa koma mulumgu alowerelepooo

  • @OmkKhongo
    @OmkKhongo 2 หลายเดือนก่อน

    Mfana wammudzi sopano eeeee❤

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 2 หลายเดือนก่อน +5

    ndimakunyadira bon karindo uremu wanu

  • @AllieJonassi
    @AllieJonassi 2 หลายเดือนก่อน +1

    The D.C umakwana and proud of you

  • @AnthonyChirwa-t4g
    @AnthonyChirwa-t4g 2 หลายเดือนก่อน

    The DC mumatiimilila asiyeni agaruwo chao palibe

  • @GreevinWaMugowa-j9c
    @GreevinWaMugowa-j9c 2 หลายเดือนก่อน

    Ndiwe Bon Mwana Owoopsya kwambiri muziko lonse la Malawi

  • @OwenDube-m1h
    @OwenDube-m1h 2 หลายเดือนก่อน

    No to Nyawu party

  • @KondwaniJohn-mm3gk
    @KondwaniJohn-mm3gk 2 หลายเดือนก่อน +1

    Waufiti samazitamandila....awa ndi mantha chabe

  • @MazwaiiMkhize
    @MazwaiiMkhize 2 หลายเดือนก่อน

    Mmm!! Zoonadi, ngathi munthu walephela, obviously it shows that, kwa yiye mphamvu Mulungu wazilanda.

  • @FraserSambo-l1k
    @FraserSambo-l1k 2 หลายเดือนก่อน +2

    Chilipo chikukusata Bon Kalindo

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 2 หลายเดือนก่อน +2

      Simungamuthe Kalindo munama kwambri, munapha Chilima anthu oipa inu simuwina 2025 kumtumbo kwamako galu iwe

  • @KingTroy-t5e
    @KingTroy-t5e 2 หลายเดือนก่อน +1

    Koma kutchuka unakufunisisa 😂😂unayiwelenga boh uli kuti nditchuke ndizingotukwana MCP 😂😂ndiwe dolo

  • @NeemaMatewere
    @NeemaMatewere 2 หลายเดือนก่อน

    Wamisala anaona nkhondo

  • @OssmanAbubaker-t2i
    @OssmanAbubaker-t2i 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ulemu wanu the DC timakunyadilanitu pachilungamo osaopa osafooka osatopa

  • @ehinsupport3217
    @ehinsupport3217 2 หลายเดือนก่อน

    Bon kalindo ndi mbuzi kwambiri. Every day kumankamba dzautsiru basi.

  • @samueljuma4452
    @samueljuma4452 2 หลายเดือนก่อน +4

    Kalindo my guy,thana nawi agalu amenewa athe onse ena atengerepo phunziro achule achabechabe

    • @abe9104
      @abe9104 2 หลายเดือนก่อน

      this is true i know this man

  • @MonicaChanza
    @MonicaChanza 2 หลายเดือนก่อน

    DC amatiyimirira ....ulemu wako....

  • @ruthkundwe7448
    @ruthkundwe7448 2 หลายเดือนก่อน

    No rest for the wicked,DC kachilungamo kalilmo

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 หลายเดือนก่อน

    Ndipo anthu amenewa akuiputa nkhondo kwambiri

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 2 หลายเดือนก่อน +1

    The DC ❤

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 2 หลายเดือนก่อน

    A Kalindo langizani chipani chanu chikupita ku komvesyoni pa 18 August nanga munthu umalangiza zinthu zitachitika kale

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 2 หลายเดือนก่อน

    The DC mnyamata oopya kwambiri, mufatu mkalimbana naye

  • @JOHNMPEMBA-p3i
    @JOHNMPEMBA-p3i 2 หลายเดือนก่อน

    Tamvanao 😮😮😮😮😮

  • @LysonKumwenda-v1m
    @LysonKumwenda-v1m 2 หลายเดือนก่อน

    Ichidi ndichamisaradiiii!!!!!! Wangokura mutu koma zelu aribe

  • @ErickTym-u2m
    @ErickTym-u2m 2 หลายเดือนก่อน

    Kkkk wanyama zing'onozing'ono wagwa mu mtengo wamkuyu

  • @JohnMota-o2u
    @JohnMota-o2u 2 หลายเดือนก่อน

    Ba Bon K nanga mbaa mwakanika bwanji kumuchosapo chakwex yu

  • @JohnMota-o2u
    @JohnMota-o2u 2 หลายเดือนก่อน

    Ba Bon K nanga mbaa mwakanika bwanji kumuchosapo chakwex yu galu oluma samakuwatu

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 หลายเดือนก่อน +3

    aboni kqlindo akuoneka kuti zokamba zawathela

    • @WorriedNdhlovu
      @WorriedNdhlovu 2 หลายเดือนก่อน

      Kod apopo sanakambe or akunveka ngati akuimba nyimbo

    • @DanielNandajester
      @DanielNandajester 2 หลายเดือนก่อน

      @@WorriedNdhlovu akuluwa a kupanga target mcp bac chifukwa adakanikanika kupita Ku embassy mpaka kum@ngonyoza awa nde Kaya ingonenani kuti mufuna dpp osati kumazembera

    • @EstherDebwe
      @EstherDebwe 2 หลายเดือนก่อน

      ​@@WorriedNdhlovu😂😂😂anthu kufika potopa😂

  • @manuelsamuel293
    @manuelsamuel293 2 หลายเดือนก่อน

    We support you Kalindo

  • @EvasonThupilifana
    @EvasonThupilifana 2 หลายเดือนก่อน

    Kom A mcp musamale chifukwa tonsefetu ndife okwiya kwambri chakwela mbuzi yamunthu

  • @SARGENTZIMBAMAGABA
    @SARGENTZIMBAMAGABA 2 หลายเดือนก่อน

    Malawi kung'amba kkkkkk koma DC kkk

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 2 หลายเดือนก่อน +1

    Munthu waufiti samazitama a bon iwe ndiwe saiz yanga osat ungalimbane ndi ziko

  • @ChikhaondIssah
    @ChikhaondIssah 2 หลายเดือนก่อน

    DC alozeni bas

  • @HassanKhebo
    @HassanKhebo 2 หลายเดือนก่อน

    The DC bon kalindo more fire 🔥🔥🔥🔥

  • @MartinChapita
    @MartinChapita 2 หลายเดือนก่อน

    Akhalitse Dc

  • @CharlesWyson-ue5fz
    @CharlesWyson-ue5fz 2 หลายเดือนก่อน

    the dc mwana oophya kwambili

  • @GaryMakhumula-mu3du
    @GaryMakhumula-mu3du 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ati nkatikati mwanyamamo muli nchenga hehehe!!!😂

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 2 หลายเดือนก่อน

    I think akalindo mukamayankhula izizi mumakhala kut mukupanga mantha n ndiwe munthu wamatha. Coz munthu amene saopa kathu sayankhula koma munthu amene akungokuwa amakhala kut akuopa, n inuyo akalindo ndiinu munthu wamatha that's it.

  • @WinstonNyadaufe
    @WinstonNyadaufe 2 หลายเดือนก่อน

    Amawopa kumangidwa 😂😂 chifukwa ndi anthu akuba

  • @EkaliKapito-y8q
    @EkaliKapito-y8q 2 หลายเดือนก่อน

    Mwana wa mulanje weniweni

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 2 หลายเดือนก่อน

    DC salute kwanu

  • @GiftMakowa-k9f
    @GiftMakowa-k9f 2 หลายเดือนก่อน

    Koma dc atakhala kuti kumalawi alipo athu 20 ayi futi kumalawi zitalila kale chifukwa ndimuthu wolimba mtima kwambili

  • @LessonBester
    @LessonBester 2 หลายเดือนก่อน

    The DCCCCCCCCCCCCCCCCCCCCCC Mwana oopsa kwambiriiii!!!!

  • @Anordchatha
    @Anordchatha 2 หลายเดือนก่อน

    Mcp manyadzi bwa

  • @sanlakedickson6780
    @sanlakedickson6780 2 หลายเดือนก่อน

    Dziko ndi lathu tiziwopa ndani?

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 2 หลายเดือนก่อน

    Mavoti simayesu tisakole amalawi Kuti tipange mavoti woyesera zayamba liti zimenezi asatipusise

  • @leviecashmere7555
    @leviecashmere7555 2 หลายเดือนก่อน

    Chisankho I chichi mulungu azakhle pa tsogolo

  • @DanChirwa
    @DanChirwa 2 หลายเดือนก่อน

    Ngati amangova mulanje mulanje ayiziwira pa the DC

  • @ThamboWondershellin
    @ThamboWondershellin 2 หลายเดือนก่อน

    Inu ndakatundu big

  • @GaffarMichenga
    @GaffarMichenga 2 หลายเดือนก่อน +7

    💪💪 Viva DC

  • @MabasoMafa
    @MabasoMafa 2 หลายเดือนก่อน +1

    Daily kunyodza MCP chakuntha ichi

  • @StellaCharmer
    @StellaCharmer 2 หลายเดือนก่อน

    Tangomuloza chikangawa man yo

  • @EmaxGraceFanTV
    @EmaxGraceFanTV 2 หลายเดือนก่อน

    Amwene inu ku MCP kulibe kugawikana iweyo uchedwa nazo

    • @GiftMakowa-k9f
      @GiftMakowa-k9f 2 หลายเดือนก่อน

      Ndinu agalu nokha nokha ndi anyani azakowo

  • @MateusEliasluciano
    @MateusEliasluciano 2 หลายเดือนก่อน

    Malume, pangani zanu, alekeni a mcp apange zawo...

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 2 หลายเดือนก่อน

    Chikangawa party

  • @PriscaMalizani
    @PriscaMalizani 2 หลายเดือนก่อน

    Koma nkhani umaziziwa bwanji 😂

    • @EstherDebwe
      @EstherDebwe 2 หลายเดือนก่อน

      My question too
      Coz zimakhala zoonansotu nkhan zake😂
      Ndy iiihm kaya tsono😂

  • @paulphiri-fz9me
    @paulphiri-fz9me 2 หลายเดือนก่อน

    Koma DC kuyankha mopanda mantha zoona 😅

  • @Veronica-o2d
    @Veronica-o2d 2 หลายเดือนก่อน

    Awa ndiye opusa kwambiri azawo zikuwayendela koma iwo😢😢😢

  • @Edward-y3v
    @Edward-y3v 2 หลายเดือนก่อน

    The voice of DC

  • @CharityBanda-lm5cj
    @CharityBanda-lm5cj 2 หลายเดือนก่อน

    Chimene amafuna kalindo sachidziwa oipa ndamene amabweletsa chisokonezo mdziko

  • @HamissMaidaz-x4h
    @HamissMaidaz-x4h 2 หลายเดือนก่อน

    Mwana wa line katole😂😂😂😂

  • @MaduraAlbertoJose
    @MaduraAlbertoJose 2 หลายเดือนก่อน

    Hiiiii chakwela ali male