We sincerely thank God the Almighty for giving Malawians the opportuniy to have Arthur Peter Mutharika as our president from 2014 to 2020. Like any leader, he might have made some mistakes during his tenure of office. But as Malawians, we should not forget that there are many good things that Arthur Peter Peter Mutharika did for Malawi which will always be remembered. As a nation we still have hope for a better Malawi because the future of our country is and will forever be in the hands of God and not in the hands of any human being. Have a graceful peace of mind and good health our former president.
My brother you're right and I have been talking about this I have never seen mcp just start their program without 1mn silence this Dad is agreat man and he always humble himself.Ndaombela mmanja ineyo oa zimwe wachita munthu wamkuluyu.Boma likupita basi chaka cha mawa.
Ndipo inenso pokhapo ndinagoma nawo adad cz mcp convention sanamupatseko silence prayer for the late vice president wathu ndipo a Muntharika aonetsa munthu, chikondi and kukula. Koma uyu m'busa Chakwera zero thinking ndipo l hate him, am not DPP komanso MCP or any party koma zomwe DPP yapanga l wish them well. Koma adad mukanamuika Suleman kukhala president mukadzawina kuti adzayendetse chipani and dziko inuyo mupume mwakula
I will never trust any politician the way I trusted Chilima. This so called professor to me is nothing other than corruption tolerant leader just like Chakwera. So let's not lie ourselves guys, honestly we don't have any politician now who can restore hope for Malawians.
Anthu omwe mumati wakalamba. Shame on you. Listen to how APM clarifies, explains and responds to questions.. he has vast knowledge not only for presidency but also humanity.
Yet the Word of God in Matthew 23 vs 8 is telling you “don’t call any man father on earth…..” And you say that Peter Wa Mutharika is the father of the Nation? Which nation? He is the former president of Malawi not father of the nation. Ndiye Nation ikhala ndi ma father angati????
@@RiteRoderick Zikomo kwambiri inu a Bwana wozindikira kwambiri. So you’re implying that the Word of God is wrong??? If Peter is your Father why do you want to make him the father of everyone. So Kamuzu was the Father of the nation? Muluzi the father of the nation? Bingu the father of the nation? Chakwera the father of the nation??? They’re leaders, presidents not fathers. Kamuzu officially had no child. How can he be a father? He was the leader. Stop worshipping idols.
Transportation is very important in the country ndiye iwowa ngati a DPP alamuli Zaka pafupifupi 13 Koma osabwezeretsa nanji Koma ndikumangura ma track Kuti azipanga ma business a personal awa alipowa angonkha Zaka 4 njanji yabwerela guys njanji ndichinthu chofunuka kwambili mdziko
Akulu awa alibe Nzeru. Akunena zitukuko za achimwene awo, osatchula zawo bwanji??? Signing the Ngongole and implementing the same is a different thing all together. Zanziiii zenizeni.
We sincerely thank God the Almighty for giving Malawians the opportuniy to have Arthur Peter Mutharika as our president from 2014 to 2020.
Like any leader, he might have made some mistakes during his tenure of office. But as Malawians, we should not forget that there are many good things that Arthur Peter Peter Mutharika did for Malawi which will always be remembered.
As a nation we still have hope for a better Malawi because the future of our country is and will forever be in the hands of God and not in the hands of any human being.
Have a graceful peace of mind and good health our former president.
Perfectly said
Well spoken 🎉🎉
Repent
U need to repent
i like this idia
Intelligent and leadership skills in this boss is being proved
The humbleness in Peter should forever be remembered. We love you dad
We proud of you our DAD may the almighty God protect you wherever you shall go❤❤❤ watching from Cape town
Professor Peter ndi munthu ozichepesa cool man keep it up
Wabodza ndi woipa mtima. Moti sakuona miseu ikumamgidwayi nfi mcp? Liar and devil
Kuzichipetsa does not guarantee him to be a good leader.
School
Ndiwa school uyu munthu wakulu alamula muno uyu
APM ndi deal
May God bless you adad so that Malawi as a whole can be blessed too
The cool, humble and displine man ever I see ❤inuyo mulungu akuze malile amoyo wanu .....ena bwez akungolalata apa
When you know who you are you speak with confidence help is coming the man of wisdom DPP Boma ilo watch from Canada 🇨🇦
❤❤❤
Munthu mulala
Uyu ndi munthu ozindikira one minute silent imene ija wapezeratu ma vote one million
My brother you're right and I have been talking about this I have never seen mcp just start their program without 1mn silence this Dad is agreat man and he always humble himself.Ndaombela mmanja ineyo oa zimwe wachita munthu wamkuluyu.Boma likupita basi chaka cha mawa.
@@Blessings-b7hza ziiii
Ndipo inenso pokhapo ndinagoma nawo adad cz mcp convention sanamupatseko silence prayer for the late vice president wathu ndipo a Muntharika aonetsa munthu, chikondi and kukula. Koma uyu m'busa Chakwera zero thinking ndipo l hate him, am not DPP komanso MCP or any party koma zomwe DPP yapanga l wish them well. Koma adad mukanamuika Suleman kukhala president mukadzawina kuti adzayendetse chipani and dziko inuyo mupume mwakula
Kkkkkkkkkkkk. @@SheenahMwalabu-iz3pr
@@kingsleyhopematchaya5184munayesa kuwonjezela salt😮
The guy's genius. See the way he's taking the questions, so simple and very accurate.
❤Madala got my vote woow!!!!
Exactly mr Peter muthalika is gd leader he knows what poor Malawians need
God is good guys Adad 2025 will be a leader again
Obviously
My lovely president ❤
I wish he could give chance to the young blood. He could be much better if he was just like party advisor.
Exactly 💯
Eeeeee why?
Following the events as they unfold from Falls Estate in Lilongwe city.
APM MY VOTE ❤❤❤❤❤
I love you adad
Power 🎉🎉
professor speech it's more powerful.....
The mn of wise😅
President Dr Lazarus Chikangawa Chakwera ufumu wako unatha pa 10 June, utapha Chilima ndi anthu ena 9 this include Raph kasambala
President wanzeru zoopsa zedi Peter Munthalika mmmmm❤❤❤❤❤❤ DPP my vote mpakana kale❤❤
😂 7:37
Dr raz my vote
Ineso Chakwera ❤️
@@TheophilusKhondowa-m1nchikangawa party
😢😢😢😢😂
I cnt wait to vote for this one again..
Iyeyu anakanika kupitiliza zomwe anasiya Ngwazi Bingu Wamuthalika kwawo komwe ku Thyolo, kuli ma project ambiri anangosiydwa, koma amnzawo akukwaniritsa zomwe iwo akunamiza anthuzo kuti anayambitsazo, komaso munthu akukanika kunenako zomwe anakwaniritsako, mmalomwake akunena zomwe anakwaniritsa Ngwazi
Asteps of A righteous leader are ordered by God
I will never trust any politician the way I trusted Chilima. This so called professor to me is nothing other than corruption tolerant leader just like Chakwera. So let's not lie ourselves guys, honestly we don't have any politician now who can restore hope for Malawians.
Then don't vote
I would give Penjani Kalua a chance. Koma ena sangakondwe mu chipani chake
Ife wathu ndiyomweyi iwe kavotere chikangawa wakoyo
Ndipo zoona palibe chazeru akulankhula mbuzi imeneyi gogo alibe zeru uyu
@@beinhardkausiwa7107 ife nd DPP bas 😅😅 APM vote yanga akutenga popandanso kukambirana
Dr Lazarus McCarthy CHAKWERA number one zinazi ndi nyash
I like the confidence ❤️
Apm my vote
Integrity reader in Malawi,,,God bless this Man❤
The real president 🎉🎉
Wow! Mmmmm! What a comfidence
Anthu omwe mumati wakalamba. Shame on you. Listen to how APM clarifies, explains and responds to questions.. he has vast knowledge not only for presidency but also humanity.
2025❤❤❤❤❤
Father of nationa God bless APM 🔥
Father of the lomwe
😂😂😂😂😂😂@@JoyceGondwe-ve1zu
Mwanva nokha Brian, Calthy and Jona kuti zitukuko ndi ma plan zomwe akutukumuka nazo Chakwera ndi za DPP ndi APM.
Amatani kumanga 6wazs ku capital city chimavuta ndi chyani kt akoze m1? Nanga njaunje inamukanika bwa?
Chitukuko imayamba ndi feasibility study
Inunso ngopepera bwanji iwe kukwatira mkazi osabereka mwana banja Latham wina kubwera kumkwatira kubereka mwana ndiye ungati ndi wako chifukwa anali nkazi wako? Kupusa uku zosamveka
@@StevenLikukutaboma sibanja nanu umbuliwu bwanji,
@@JafferTiles-hp4mu😂😂😂😂😂😂banja ndichapani zosagwirizana
The way forward is the federal system of government basi .
You are very right…
Am proud to you my dad....❤❤❤❤🇲🇼✅✅✅✅2025boma.
Ma vote tasunga ndipo tikukawapatsa adad musakayike achakwera mwakanika nokha
My vote ❤❤❤❤
So the guy needs refresher just after being asked a question. Lets accept abwanawa akula.
D pp bomaaaaaaa 🔥 wosayamikayo ndi nfiti ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ my vote
Jonah usamamuloze chala father of the Nation uzingofunsa basi😂😂😂
Mwayambapo mwano ma Cadet
Jonah has no manners at all
Kusowa ulem uyu,,,,,,ma hater's a DPP sasowa
We heard yu his execellency APM chigwetseni chi pilato munthu oipa ife ngt amalawi tili pa mbuyo panu🥳🥳🥳🥳🥳
What i see is achina Braian akufusa moonetsa kuti akucheza ndi munthu wankulu...❤
Akudziwa kuti akuyankhula ndi president kachikena
Kulakhula kwa phavu my president
❤apita mulungu azimudarisa🎉
A future president adad and wisdom ❤
Father of Malawi ❤lndeed
God bless you APM , we need you to come back 2025 boma ❤
Kuyamba zitukuko ndikosavuta, koma kumaliza...
As for me i don't see any reason yovotelaso DPP, never...❌
Kumaliza motani, Mesa funding imakhala ilipo kale?
Koma Dpp ilowaso ufune usafune
Zitukuko zaboma sizili ngati kumanga chimbudzi, chitukuko chaboma nde chovuta kuyambacho kumaliza nkophweka afana musamazinamize do the recheck
Genius 🎉🎉🎉🎉🎉
Moto kuti buuuuu!!!!!! 🔥 🔥
APM my vote❤
Akagwera pa nsokhano adad anuwa akulephera kumva bwino bwino
Uzisiyanitsa kumva ndi kumvetsetsa he might be old but he is wiser than manyi anuwo
Uyu ndi muthu opa mulungu nďithu kuwina ndikuvomereza kuchoka sizophweka mulungu akudaliseni adadi shalom
Koma yaaaaaa......👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍😮😮😮😮😮😮😅😅😅😅😅😅😅😊😊😊🙄🙄🙄🙄🙄🙄
My vote
Ulemu wanu adadi❤❤❤❤❤
Machine awa only chiyembekezo we have ndi fada wa bas💙
Father of the nation my vote
💙💙💙💙💙💙🔥🔥🔥🔥
APM has got a visionary leadership
Mfumu wa kumalawi❤❤❤
Yehova akusungeni pansi pa mapiko ake adad we love you long live 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙🇲🇼🇲🇼🇲🇼
May God protect this guy mweeee
Father of Malawi❤❤❤❤❤ katundu owopsa zedi APM ❤❤❤❤
Yet the Word of God in Matthew 23 vs 8 is telling you “don’t call any man father on earth…..”
And you say that Peter Wa Mutharika is the father of the Nation?
Which nation?
He is the former president of Malawi not father of the nation.
Ndiye Nation ikhala ndi ma father angati????
@@chesterphiri7523 Your a bad person and you don't understand bible even the meaning of father
@@chesterphiri7523 Ndiinu opepera zedi, nation ikhala ndima father angati is that a question??? Your mad brother open up your eyes
@@RiteRoderick Zikomo kwambiri inu a Bwana wozindikira kwambiri. So you’re implying that the Word of God is wrong???
If Peter is your Father why do you want to make him the father of everyone.
So Kamuzu was the Father of the nation?
Muluzi the father of the nation?
Bingu the father of the nation?
Chakwera the father of the nation???
They’re leaders, presidents not fathers.
Kamuzu officially had no child.
How can he be a father?
He was the leader.
Stop worshipping idols.
Genius eeish
Machine,my dear,my love my vote
DPP Moto Kuti buuuuuu🔥🔥🔥🔥🔥asakufuna afune adad we love you so much mwawina kale no campain
Transportation is very important in the country ndiye iwowa ngati a DPP alamuli Zaka pafupifupi 13 Koma osabwezeretsa nanji Koma ndikumangura ma track Kuti azipanga ma business a personal awa alipowa angonkha Zaka 4 njanji yabwerela guys njanji ndichinthu chofunuka kwambili mdziko
Chikangawa party zautsilu eti njanje yokha wati basi zatheka anthu akuvutika kunjaku
@@SuzgoMkandawire-ss4kh komatu mu interview mu anakuyankhani kuti zinayambika nthawi yake kaya mukumvera mmapazi i wonder
Zinayambika ndiboza lenileni zimenezo ndizo ndale palibe chimene anganene chabwino kuchokera Ku mcp awawa NDI osusa basi
Wen chikangawa hear this, they going mad DPP my vote 😊
We are with you Mr president be free feel free sir ❤
APM my vote
Proud of you dad
Katundu wa uyu my vote
Komatso seu wa zomba to bt,zomba Vaya jali up to phalombe DPP project well done.
❤
I wish all the best A P M
kuyankha mwanzeru Mr Peter kwa tolankhani
Uyu Mulungu anamdalitsa ndi nzeru osati ziphe zomwe zilipanozi, zikumapzipopa polenga zigawenga kuti azizuna anthu, APM my vote
Agogo mwakalamba zitayen please 🙏🙏
❤❤ peter ndi dadidi
My vote dad
Adadi inuyo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Generalized questions from the interviewers. They must be specific.
Why Brian didn't ask chikangawa those questions kkkkkkk peter my vote am coming there to vote 😂😂😂😂
❤ my vote 🗳 Apm 🎉🎉
Akulu awa alibe Nzeru. Akunena zitukuko za achimwene awo, osatchula zawo bwanji??? Signing the Ngongole and implementing the same is a different thing all together.
Zanziiii zenizeni.
Iwe kape enti mbudzi
Iwe ndi galu anaziyamba 2017
Love Dad
Count my vote
President ozichepetsa kwambyi osabwezera zoipa keep it up Mr president
Long live my President
My president
Akalamba awa
Nde iwe ngat usadakalambe osatenga mpandowo bwanji mxieeee
I❤u dad
Yes bwana phulezidet
The best interview
🎉🎉🎉
Akuti plot number 1
Adad womwewo 🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤
Za ma biggy izi adad 🔥
Koma zoti munthuyu wakula anthunu simukuwona. Ife muoffice timapanga retire pa 60 years nanga awawa bwanji?
Yabani ndare.kugwira ntchito boma ndikugwira ntchito za chipani zosina
Ndie nyamata wanuyo chakwera watipangira chan Malawi akagwere ife tikufuna adad
Fundoless😂
Do you know the US president?
Boss, Mntharika can be old, but he stabilized our country, far better than these young people of yours.
Mukulankhula zotsemphana ndi ndaletu baba... Chakwera sanatenge munthu yemwe anapanga retire kalekale, ndikumpatsa udindo ku lmmigration? Tiziti samadziwa kuti wakula komanso tiziti samadziwa kuti kul achinyamata ambiri omwe ali ndikuthekera pa udindowu?