COMRADE CLIF CHINYAMA - RICHARD CHIMWENDO NDI CHAKWERA SIMUNGANDIOPSEZE

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 72

  • @jowiemhango5058
    @jowiemhango5058 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +14

    Pakhale corabo ya the DC ntanyiwa bakili muluzi tv alexious kamangila and this guy. 🔥🔥🔥🔥

    • @JulietLizziePhiri
      @JulietLizziePhiri 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      Hahaha koma ndipoooo

    • @jowiemhango5058
      @jowiemhango5058 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      @@JulietLizziePhiri zafikapa malawi yufunika anthu olimba mtima ngat amenewawa

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Strong words and takunyadilani mr.Chinyama, a MCP akutitola kwambiri ndi achina Chimwendo Banda.

  • @collinschipala611
    @collinschipala611 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Brave and bigup. I like his courageous!!! Let's work up guys & support these our fellow youths like the likes of Kamangira and others

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +9

    Woke up achinyamata andale atiwonjeza tsopano zafikapa lets fight for our freedom ( Alunta continua 💪)

    • @wisdomsadyalunda2001
      @wisdomsadyalunda2001 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      you do say wake up in your hiding hahahaha no bho

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    100% truth, anyamata a MCP ndi opusa kwambiri

  • @Mobilot2android
    @Mobilot2android 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +7

    Bravo CLIF CHINYAMA
    long live u r more hero

  • @ZioneMkwanda-y6i
    @ZioneMkwanda-y6i 21 นาทีที่ผ่านมา +1

    😅😅😅😅 Brada well done, please tell them the liyaliya more 🔥🔥🔥 a chikangawa party aonjeza

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Another God sender is this guy, ❤Mulungu atimenyera nkhondo tili chete ngati m'mene anachitira Israel. May the almighty God bless and protect you our brother clif chinyama

  • @MCDAISONNKHWAZI
    @MCDAISONNKHWAZI 20 นาทีที่ผ่านมา +1

    Let's support him guys this is enough

  • @AdamKay-q1l
    @AdamKay-q1l ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    I think a chinyamata Les make new group to crean our Malawi

  • @masingatichilumba8263
    @masingatichilumba8263 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +6

    Mcp simbali yanga kuyambira kale kale,

  • @RosetNkhoma
    @RosetNkhoma 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Kkkkk ndimamva chisoni ndi apolice,akungomanga anthu kulephera kumanga nyumba zawo

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda 54 นาทีที่ผ่านมา +1

    Cliff chinyama real man❤

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zoonadi Brother Clif Chinyama, Chakwera ndi chitsiru cha chabe-chabe

  • @wisdomsadyalunda2001
    @wisdomsadyalunda2001 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    this thing when you come to a point where you realize you have nothing to lose
    all the fears go you starting behaving this way, we have alot of them benefiting from these guys hence their voice is taken
    shame, awawa amadya zawo thats kulimba mtimaku.

  • @muhabaulen7912
    @muhabaulen7912 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Come clif my allah guide and protect you all the time allah akbar respect to big up my bro be strong

  • @CathreenKadwala
    @CathreenKadwala ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndipo ine singachose chikhulupilo PA anthu Inu, Clif, Ntanyiwa, Bon, bro sallo ndi Ena onse Bakili TV, tilipambuyo panu

  • @ElsaMalunga
    @ElsaMalunga 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Kd mukuti ndichani mukufuna chani mupha anthu angati inuyo mudzapita kt kd inuyo mukuopseza anthu cz mwachuluka phavu guys zimenezo ayi ingotengani mifuti mutiphe tonse mwava chipani chanji chokhara ndi zigawenga ala Inu zimenezo ayi kd inuyo simuzafa moti simudziwa kt kupha munthu ndichimo kd Inu boma muli nduna zingati kumangoti chimwendo kukuyu osadabwa ng,oma olola kwambiri sichedwa ku sweka musamare Mcp mwava

  • @CathreenKadwala
    @CathreenKadwala 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mitunda yosaopa, thanks bro

  • @FaheemChipojola
    @FaheemChipojola 16 นาทีที่ผ่านมา +1

    Zoona big mumwa chani brother mwayakhula bwino kobas

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    May God proetect u where u r broh always mdima umadana mkuunika koma mawa tisamve kuti china chake chachitika kwamchimwen uyu anthu ongoganiza zokupha inu malo motukula dziko mzaziiiiiiii

  • @lyiemax
    @lyiemax 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Powerful brother Man ❤❤❤

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Akamangila akutulukatu, wina amva 'bebe.

  • @GladysndilimbiraBonongwe-g6c
    @GladysndilimbiraBonongwe-g6c 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    More fire brooh

  • @ChisomoBanda-jo4ix
    @ChisomoBanda-jo4ix 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    koma m c p mwaonjeza kwambiri kod afiti ose adatha kumarawi kuno. bwanji osangorodza amenewa kuti tipumure lfe

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Malawi need courageous young men like you,bravo

  • @francismungu7749
    @francismungu7749 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Guys kumalawi kuli anthu olimba ntima ndaimikamanja. Mr kumkuyu muliso ndifuso? Mumachuluka nzelu kwambili. Man awawa aposa Ntanyiwa, Bakili TV, Man awa ndichida

  • @ThoccoChimbali-h6g
    @ThoccoChimbali-h6g 34 นาทีที่ผ่านมา +1

    Amene amasapota mcp ndi mfiti ndithu

  • @ThokoMsonkho-hy4uc
    @ThokoMsonkho-hy4uc 11 นาทีที่ผ่านมา +1

    Pofikana achinyamata awawa kutuluka ndiye kuti pavuta.
    Ali ndizochita zamphavu koma azisiya zimenezo kumalankhula za ziko. Akuluakulu ziko muno MCP tatopa nayo kwambiri zikuwawa koma zoona zikoli tizingomvera za MCP ndi MEC basi.
    Ife tikati tipereke maganizo athu iwo ati zimenezo ayi, DPP chipani chachikulu ziko muno akanena akuimilira anthu 17,000,000, a MCP akayankhula akuimilira anthu osalawo

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Akutetezeni Yehova man🎉🎉🎉

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 38 นาทีที่ผ่านมา +1

    Ulemu wanu big mukunenedzo zoona

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    More fire morefire wachikulile tiyenawo anyapapi amenewa

  • @BeatrizUlanda-ht2th
    @BeatrizUlanda-ht2th 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zikomo murungu akudariseni

  • @AchiwaNikisya
    @AchiwaNikisya 36 นาทีที่ผ่านมา +1

    Osaopa nchimwene wanga

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Takunyadirani a clif mumatiimilira ife amalawi

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    AKANGOFAT UYU NDIBWEZERA NDINEYO WINA AZAPEZRKA ALIBE ZIWALO WANGOSALA MIMBA PATUNDA NDIY CHIMWENDO BANDA ,ASASOWE UYU ? MCP. MUTISAMALET AMALAWI

  • @LastonMmanga-r2u
    @LastonMmanga-r2u 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kuphatikiza apo malawi siyaku Lilongwe kokha ayi, koma achakwera mwalivula dziko ngati nzimayi oyendayenda kapena kuti hule, malawi Ali PA map a manyazi chifukwa cha ubusa wanu otsogolera amalawi ku mimbulu osati ku nkhosa, malawi ayaluka mochitsa manyazi chifukwa cha a Busa inu and tikuwona Zambiri zowopsa zoti chibadwile sitinaziwone, anthu mpaka kudya chitedze koma olo kulankhula kapena kutenga po gawo ngati kholo, tate wa dziko ayi ndithu abusa???? 😢😢😢😢 Mwachitsa manyazi dzina la ubusa malawi Ali pamoto uyu and dziwani kuti anthu sakukufunani 2025 ndipo mukadakhala Ena kunali kongoimika manja kuti zakuvutani Bola....🤔🤔🤔🤔

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Aulule before they try to attack you MCP ndi anthu opanda mzimu

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Nuff respect comrade cliff

  • @stuartsangaloti8461
    @stuartsangaloti8461 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Eish koma zigandangazi

  • @Daniel-cf4tu
    @Daniel-cf4tu 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Kkkkkkk komatu phamvu sumaziziwa wekha
    Athu ali ndi phamvutu kunjaku khope zake osakhalaso ngati zanuzo

    • @OmarJumah-i3f
      @OmarJumah-i3f 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Iwenso ndiye ulimbali ittiyo Bumbu laamako wamva

  • @BirzetScott
    @BirzetScott 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    ❤❤❤❤ comrade more fire

  • @RosetNkhoma
    @RosetNkhoma 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Auze Amvetsetse Chilungamo chimaba mumtima osawabisa asatana

  • @LetshaChirwa
    @LetshaChirwa 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Osamat opyeza musiyen ayankhule chilungamo

  • @besterlumbe4404
    @besterlumbe4404 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ada awa akulankhula zanzeru, wandiwaza

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Tayakhulani leroli baba ayaluke lero LA 40 likakwana yakwana tayakhuleni baba chimwendo wado wado wajaira

  • @JulietLizziePhiri
    @JulietLizziePhiri 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Koma Mulungu akutiyendeladi kuzela mwa anthu ngati awa'mwe

  • @MustafaAbdullah-pb5zv
    @MustafaAbdullah-pb5zv 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Auze bro anyapapiwa dzianthu zokupha

  • @KendrickLuckyc
    @KendrickLuckyc 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Tiyenawoni Makape amenewa atijaila

  • @StuartMatanje
    @StuartMatanje 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkkk koma kumalawi athu achilungamo ndiambili chilima anasegula maso achinyamata aaaaaa amalawi 💪💪💪💪💪💪

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    ❤❤❤❤kuswa kuswa basi

  • @khalifacalvinajass9998
    @khalifacalvinajass9998 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Achinyamata tatiyen tidzuke mzathu wayamba kale uyu

  • @DamianoYohane
    @DamianoYohane 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Koma uyuyu ndikatundu payekha, Kamangila 2 baba

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mfumu iliyonse ikuyenela kudziwa figure ya anthu ammuzi mwake....everythung starts from the local government....where is the youth?

  • @jowiemhango5058
    @jowiemhango5058 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Faka Dadieeee 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Tawauzeni anyapapi amenewo ,, la 40 lakwana basi

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndiwantchito wathu namachende amaneyu nkumatiphaso mdi nzake moses....

  • @KendrickLuckyc
    @KendrickLuckyc 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    The DC 2

  • @jowiemhango5058
    @jowiemhango5058 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Alex kamangila 2 wafika 🔥🔥🔥🔥

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kodi bwanji amalawi munthu akati ayankhule chilungamo akuti tithana naye chifukwa chiyani MCP maganizo akupha basi ayi mani MCP ndatopa nayo ine, nthawi zonse MCP basi

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    ❤❤❤

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Azipanizotsutsa akuzitenga pa n'gono akufuna kutisiya mavuta taonda nawowa, zisithe izizi

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uyuyu mkatundu eee💪💪💪💪💪😂😂😂❤❤❤

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ngati akulephera kupanga passport kuli bwanji kupanga ID ya dziko, padziko lonse ndi dziko lamalawi lochitisa manyazi kukanika kupanga passport. Chiyambire mbiri ya dziko lamalawi aka ndikoyamba anthu kubwezedwa pa border

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiwe dolo timafuna madolo ngati inuyo big

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    BIG MAN ULEMU WANU

  • @blessingssaiti
    @blessingssaiti 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Auze fada

  • @ChrisyMbewe
    @ChrisyMbewe 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zoona.kweni.ipase.moto