THE HOT CURRENT - 24 NOVEMBER 2019

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ส.ค. 2024
  • Land in Malawi is not for Malawians - this is in reference to revelations of public land that has been sold, including Livimbo Primary School in Lilongwe, to Malawians of Indian origin; Brian Banda and George Kasakula discuss this and other issues in this edition of Hot Current.

ความคิดเห็น • 16

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 4 ปีที่แล้ว

    It is unbelievable kuti brian banda anatisiya # times, timutengera ku zodiak koma achite mwambo oyendtsa zisankho. Zabwino zonse Mr banda happy New year

  • @user-hs5xv6bk2f
    @user-hs5xv6bk2f 8 หลายเดือนก่อน

    Brian tachezakoni ndinzimayi uja akutokota zakunyumba yaufumu yathu

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 4 ปีที่แล้ว

    Komatu Times please ma camera anu need to be professionally trained, nthawi imene munthu akuyankhula akuoneka ndi omvetsera, please train them properly.

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 4 ปีที่แล้ว

    Brian banda amùchtsa ntchito akuti amaba. Banja lake litha kutha chifukwa avutika kudyetsa banja lake. Chachikulu ndimoyo malangizo anga kutelo, ntchito ndimuntengo

  • @user-hs5xv6bk2f
    @user-hs5xv6bk2f 8 หลายเดือนก่อน

    Ndzikolidi likulamulidwa ndiasata koma mulungu sakulola kuti satana apitilile kulamulila ndzikoli nchifukwa pano zobisika zonse zikumaululika

  • @alexpeteribrameja1819
    @alexpeteribrameja1819 4 ปีที่แล้ว +1

    Alex Fest1 Always Ndakunyadilan potitumizila Koma mochedwa aTimes mwatani kodi

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 4 ปีที่แล้ว

    Guys osalimbana ndi President cos ndakhalako pa mipando yosiyasiyana ndikudziwa momwe umakhalira busy Munthu

  • @user-hs5xv6bk2f
    @user-hs5xv6bk2f 8 หลายเดือนก่อน

    Mmmmmm mipando yonsele wakhalayo unathandizapo amalawi motani iwenso unangokhalila kuba nchifukwa wakhala mipando yonseyo

  • @katungageorge9124
    @katungageorge9124 4 ปีที่แล้ว

    Ku Kenya akanakhala atapeza kale onse omwe asewera game imeneyi, atawathamangitsa kale m'ma office pano

  • @peterbanda5425
    @peterbanda5425 4 ปีที่แล้ว

    A times poyambilila sinkakuvesesani kama chaka na chinochi mwandisegula mutu pitilizani kutitumizila ndiponso nkhani zanu musamatiyiwalile

  • @jumbradoone4164
    @jumbradoone4164 4 ปีที่แล้ว

    Always say "mwatichapa mmaso

  • @katungageorge9124
    @katungageorge9124 4 ปีที่แล้ว

    Koma ndizoona amalawi ndife otsalira kwambiri. Koma gwero lake ndi atsogoleri athu.

  • @mwasep.296
    @mwasep.296 4 ปีที่แล้ว

    Cubaphidy yemweyoo

  • @ganizaninjaidi4481
    @ganizaninjaidi4481 4 ปีที่แล้ว

    Koma malawi aliyese angoba koma why malawian

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 4 ปีที่แล้ว

    Koma zikupanga boma ili ndi zoipa ife kuno kumulanje tikusowa malo koma agalu amwenye fucken Muslims are taking our land shame on dpp

    • @mouricesaidi5348
      @mouricesaidi5348 4 ปีที่แล้ว

      Waganiza bwanji kunyoza asilamu,,,mmalo mokamba za amwenye okhawo? Why my dear