Interview ndi Ken Nsonda 27.23

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 190

  • @mkhulukinyata5198
    @mkhulukinyata5198 8 หลายเดือนก่อน +14

    M'dala iwe tamva idzi "
    { 1 } Ndiwe chitsilu kwabasi.
    { 2 } N'kulankhula kwako dzikusonyedzeratu kuti umphawi wakutikita ndiye ukuyesano kuwabakila a Chakwera ndicholinga choti upedzeko Paketi ya Sugar galu iwe..
    { 3 } Kumbali ya mavuto ngati Freddy / Covid ,Idzo nzowonadi kuti it's a natural problem ,.Ndiyeno ntchito ya boma n'kupedza mayankho panthawi yoti mavuto ngati awawa abwera mdziko.
    Ndiyenso since Chakwera ADMINISTRATION yakanika kupedza njira dzothanirana ndimavutowa ", Ndiye kutino bomalo lalephera pamenepo .

  • @Chikulamayembe57
    @Chikulamayembe57 8 หลายเดือนก่อน +7

    This lady is truly brilliant!

  • @ancientnkhata1137
    @ancientnkhata1137 5 หลายเดือนก่อน

    Ndale sizamwanadi adja . Nsonda is genius

  • @user-ti8ds7iq8z
    @user-ti8ds7iq8z 8 หลายเดือนก่อน +2

    Mumazivutisa pomaitana mdala amenei amayamkhula zosemphana ndi ma fuso always

  • @lyiemax
    @lyiemax 8 หลายเดือนก่อน +7

    Dobadoba wa MCP uyu

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 8 หลายเดือนก่อน +1

    Nsonda ndimbuzi yeni yeni, ndiwe galu kobasi

  • @hendrinagama5325
    @hendrinagama5325 8 หลายเดือนก่อน +3

    Chemwali mukungwila ntchito ndi mcp ndakutulukilani nthawi yapitayi machine interview chisale chifukwa anali wa bodyguard wa peter lero mukuchitaso interview nsonda ai akuonengela ntchito mukanvela anthu that's why anthu amakonda Mr brain Banda alibe mbari

  • @user-gj8td8pc4d
    @user-gj8td8pc4d 8 หลายเดือนก่อน +2

    Ndale ndimasewela olikhana, and uyuyu ndiwandaled.

  • @paulnaluso5061
    @paulnaluso5061 8 หลายเดือนก่อน +3

    I like sonda, straight talk.

    • @user-pe7lo1fe9b
      @user-pe7lo1fe9b 8 หลายเดือนก่อน

      Nsonda chitsiru kusaka pofera

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 8 หลายเดือนก่อน +2

    Watching Msonda's interview is not a waste of time at all, anthu awa ndi amene akuyenera kukhala ma presidential advisor.

    • @martinkalaka2667
      @martinkalaka2667 8 หลายเดือนก่อน

      Yes this great man

    • @ancientnkhata1137
      @ancientnkhata1137 5 หลายเดือนก่อน

      Ken Nsonda is a leader and can be a good presidential advisor

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 5 หลายเดือนก่อน

      @@ancientnkhata1137
      Komabe ndi mbava zokha zokha, zipani zonse zandale kumalawi ndi za mbava zokha zokha.

  • @vadokawawa7199
    @vadokawawa7199 8 หลายเดือนก่อน

    Honestly this lady Leah Zodiak has a gold in their hands

  • @kingz-nw3ui
    @kingz-nw3ui 8 หลายเดือนก่อน +1

    Uyu ndosokoneza

  • @kasupeowenpaul
    @kasupeowenpaul 8 หลายเดือนก่อน +3

    Awa ndiachisilu

  • @user-xq5ju2uo9h
    @user-xq5ju2uo9h 8 หลายเดือนก่อน +4

    Amsonda ndi munthu wabwino
    Kwambiri ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-st7lg1io3k
    @user-st7lg1io3k 5 หลายเดือนก่อน

    Nsonda is a genius

  • @robertchikaonda-mu1bg
    @robertchikaonda-mu1bg 8 หลายเดือนก่อน +2

    Kkkkkk mbava iyi inu

  • @user-nw6ie3xx8b
    @user-nw6ie3xx8b 8 หลายเดือนก่อน +1

    True servant of dpp

  • @user-je5ll8by7m
    @user-je5ll8by7m 8 หลายเดือนก่อน

    Reyaa mafuso aphavu kwambili keep it up ❤❤

  • @user-ur4sj4mk1q
    @user-ur4sj4mk1q 8 หลายเดือนก่อน

    Ok

  • @louisgolden
    @louisgolden 8 หลายเดือนก่อน +1

    Akulu akulu wopanda nzeru Ku Malawi

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 8 หลายเดือนก่อน

    Leah andale akuMalawi ndi amphawi.amalephera kuthetsa umphawi wawo nthawi yomwe ali m'boma.azao akachoka m'boma apita ndikakamapanga ulimi mma farm ndikumatukula dziko.iwo koma kusintha zipani,kumakanirira ntown.agalu kulephera kutukula dziko.anayamba ndi Bakili mpaka pano ndale.

  • @ChamboChange-pq1hd
    @ChamboChange-pq1hd 8 หลายเดือนก่อน +1

    Mafupa Ken msonda ndiwe galu

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 8 หลายเดือนก่อน +2

    Vuto Latsonda ndimomwe amachitila ndiosokoneza yemweyi adatsokoneza UDF, DPP , PP again DPP now MCP watch out this fella

    • @lusunguphiri6418
      @lusunguphiri6418 8 หลายเดือนก่อน +1

      Msonda ndi wa MCP ndakhulupilira sopano eti boma la MCP lakumana ndi minyama kkkkkkk

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 8 หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkkkkk galu iwe ungakhale pusident machende ako

  • @jonathanmakalani-xv5od
    @jonathanmakalani-xv5od 8 หลายเดือนก่อน +1

    Iwe Ndiwa mcp

  • @usumanidaudi
    @usumanidaudi 8 หลายเดือนก่อน +3

    Komaso sindingakuvere iweyo uribe zeru chimene ukuziwa ndi kusokoneza ndiwe chisiru bwanji 😅😅😅😅

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 8 หลายเดือนก่อน

    Kkkk koma musonda umandivetsa kukoma Peter akanakomokadi siukunama big

  • @binalidjeyshabahzombamalawi
    @binalidjeyshabahzombamalawi 8 หลายเดือนก่อน +1

    Nsonda akufuna awasiye anthu mmavuto...in advance rip nsonda

  • @JamalNgumba-pe6xo
    @JamalNgumba-pe6xo 8 หลายเดือนก่อน

    Nsonda mutu wake suyenda bwino

  • @bellemagoldenwalk7767
    @bellemagoldenwalk7767 8 หลายเดือนก่อน

    gogo uyu ndi chitsilu chotheratu mbudzi ya munthu

  • @giftbanda4518
    @giftbanda4518 8 หลายเดือนก่อน

    This man is pure MCP and just causing confusion in DPP

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 8 หลายเดือนก่อน +1

    Machende ako iwe nsonda wachule anthuwo ndiwe galu

  • @user-rd4lf2gg7g
    @user-rd4lf2gg7g 8 หลายเดือนก่อน +2

    Ansonda odya zopepha

  • @JosephyMakunganya
    @JosephyMakunganya 22 วันที่ผ่านมา

    Riah nd black beauty tu koma Ken nsonda at sikuti muzipopetu 😂

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 8 หลายเดือนก่อน +1

    Sister mpapaliseni mafunso galu ameneyo chitsilu chamunthu

  • @AgrementShadreck
    @AgrementShadreck 8 หลายเดือนก่อน +2

    Palibepo chazelu inuso azodiaki muzioona ochezanawo kkkkkk

  • @PaulNyson-fb9ni
    @PaulNyson-fb9ni 8 หลายเดือนก่อน +1

    Mbuzi ya munthu

  • @user-hs5xv6bk2f
    @user-hs5xv6bk2f 8 หลายเดือนก่อน

    Yes brian and leya dinu anthu amamene ife timawafuna kuti muzifunsa mafunso ovuta kwaanthu omwe amati ndioganiza boh ngati amenewa leya uyu ndiye sunamumwese madzi wakumananazo nsonda waziyalusa yekha amaona ngati acheza ndiachina jowabu omangomvela nkhani basi

    • @ancientnkhata1137
      @ancientnkhata1137 5 หลายเดือนก่อน

      Ken Nsonda answered all the questions accurately unless you chose to be deaf

  • @mayamikozimanyeta8633
    @mayamikozimanyeta8633 7 หลายเดือนก่อน

    Leah Leah Leah how many times did I call ur name tikakhala amfana oshota ifeyo Leah???????

  • @ChitaloAbbas-fw2ed
    @ChitaloAbbas-fw2ed 3 หลายเดือนก่อน

    Chonde nose mukutukwananu muziwekuti munthuyu Ali ndi ana and zizukulu chonde Polani Moto ndikutukwana

  • @chimwemwecrispo200
    @chimwemwecrispo200 8 หลายเดือนก่อน +1

    Nsonda mbudzi chopusa kwambili

  • @DanielJuly-dj2ji
    @DanielJuly-dj2ji 8 หลายเดือนก่อน +3

    Excellency Ken Nsonda 🙏😀

  • @TheresaPhiri-ri8fk
    @TheresaPhiri-ri8fk 8 หลายเดือนก่อน

    Lea, mukapangako acknowledge compliment yo

  • @obreykolopo8766
    @obreykolopo8766 8 หลายเดือนก่อน

    munalephera ku wina kwanu kamba ka moyo ngati umenewu wa nsanje. anthu akwanu sanakusankhe kukhala Mp iwe, ukufuna u president koma ulibe mphatso ya utsogoleri iwe.

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w 8 หลายเดือนก่อน +1

    Achikeni nsomba ndimaona ngati ali ndi nzeru koma aaaaaa mbutuma ndichifukwa chake sanakhalepo kansala,mp, even nduna ya mfumu ayi kkkkkkkkkk

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 8 หลายเดือนก่อน +2

    Sangawine over my dead body 😂😂😂

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 8 หลายเดือนก่อน

    mnsonda chilungamo chimawawa at hu akuwabera a muthalika ndizoona

  • @fraserluwemba6364
    @fraserluwemba6364 8 หลายเดือนก่อน

    Nsonda ndi wa pp sitingamumvere

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 8 หลายเดือนก่อน +2

    Anachenjera mofoila uyu

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 8 หลายเดือนก่อน

    Msonda zelu ulibe iwe ukuzikolakola wekha unena kt boma likuyenda bwino zoona galu iwe

  • @kadijachilwan967
    @kadijachilwan967 8 หลายเดือนก่อน +1

    Msonda ndiopanda boza andale ena sangamukonde cz andale amakhulupirila kunama big up msonda

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 8 หลายเดือนก่อน

    Mr msonda, kumpoto kulibe munthu akukufunani inu mutsanamize anthu apa, anthu angafune munthu oduka mutu ngati inu, inu zeru mlibetu, komaso anthu akudziwa kuti munalowa mcp. Amalawi uyu musamvere ndimunthu osokoneza kwambiri madala opanda nzeru uyu.

  • @rashyklaas3930
    @rashyklaas3930 7 หลายเดือนก่อน

    awa ayambe chawo chipani namkumwa dausi ajefry ndi smsonda kapena back to mcpp

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w 8 หลายเดือนก่อน +2

    Dyera awa

    • @user-ld1js7dt3b
      @user-ld1js7dt3b 8 หลายเดือนก่อน

      Kukalamba yet alibezopanga

  • @user-hs5xv6bk2f
    @user-hs5xv6bk2f 8 หลายเดือนก่อน

    Akunama galuyu magazi ake azilemba Hiv postive

  • @David-sf3qj
    @David-sf3qj 8 หลายเดือนก่อน +2

    😂😂😂😂 Nsonda ndi Drama..usazafe aise

    • @nicksonchitenje
      @nicksonchitenje 8 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂😂

  • @user-lz2qb1uz1f
    @user-lz2qb1uz1f 8 หลายเดือนก่อน

    Wamisala uyu, osamuvera akufuna kungosokoneza chipani,Galu wachiwewe.

  • @ibrahimjackson-cg6tc
    @ibrahimjackson-cg6tc 8 หลายเดือนก่อน

    Uyu wau galu

  • @obreykolopo8766
    @obreykolopo8766 8 หลายเดือนก่อน

    inu a Ken Nsonda mwakalamba ndipo mulibe nzeru, mwawonetselatu kuti mu chipani cha DPP mumasokoneza ndiinu ndi anankhumwa, anthu opanda nzeru ofuna kulemera kudzera mukuba mu chipani mukuchulukira. inu ansonda mumayipitsa chipani ndiinuyo. 63 years mukunamanso.

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 8 หลายเดือนก่อน +1

    Fortune seeker,wadyera uyu

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 8 หลายเดือนก่อน

    Kavuwevuwe uyu

  • @petermasenti2084
    @petermasenti2084 8 หลายเดือนก่อน

    One of gready politician in malawi we don't need him in dpp lero ali ku dpp mawa ku mcp he is useless

  • @user-eu1qs1eu5q
    @user-eu1qs1eu5q 8 หลายเดือนก่อน

    Munthu wamisala amakonda kuyenda yenda kwawo kwenikweni sikumaziwika amamuziwa ndiwokhawo kumene amachokera.
    Ada awa zeru ndizochepa kwabasi palibe choonadi pa inu nenani amene amamudyera ndalama apm? Ngati ndi achilungamo. Andale bwanji mukubisala mumawu a Mulungu pa mene ndinu mkango yolusa mukulemphera kuyankha chilungamo.munthu wachilungamo akamufusa sazemba kuyankha.

  • @johnman4619
    @johnman4619 8 หลายเดือนก่อน

    Msonda oyeee

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 8 หลายเดือนก่อน

    Uyu amangidweso ngati chisale kumapeto

  • @user-mx9rq7vz7j
    @user-mx9rq7vz7j 8 หลายเดือนก่อน

    Kaigon msonda kkkkkk

  • @muhammadstaubi4604
    @muhammadstaubi4604 8 หลายเดือนก่อน

    Masala musamazikayikile mutha kukhala pulezidenti staubi

  • @AustinChiyembekezo-cx4mz
    @AustinChiyembekezo-cx4mz 8 หลายเดือนก่อน

    Nsonda just move !!!lots of partys in country takajoineni chipani china wat best for u ,like wat dausi did

  • @MisheckChafikana
    @MisheckChafikana 8 หลายเดือนก่อน +1

    Awa nd achisilu akudwala uyu

  • @user-rd4lf2gg7g
    @user-rd4lf2gg7g 8 หลายเดือนก่อน +1

    Wagwetsa kwacha ndani msonda machende amako

  • @khanilapozo-fj5tq
    @khanilapozo-fj5tq 8 หลายเดือนก่อน

    Kodi conversion amakonza ndi a court kapena achipani komanso crime imeneyi yosapangitsa conversion imatchedwa contempt of court? Why ma administration onse adutsa kumbuyoku asanakakamizidweko ndi court kupita ku conversion?

  • @user-ym6zz2or2n
    @user-ym6zz2or2n 8 หลายเดือนก่อน

    Ndimaonera mwachidwi ndipo nsonda amayankha bwino mafuso koma kumapetoko ndipomwe ndaziwa kuti akutumidwa ndi mcp muvetsetse ku mapetoko

  • @hopeskafumbi2246
    @hopeskafumbi2246 8 หลายเดือนก่อน

    muuzimu wadziwa bwanji iweyo, ntchito ndi chipanu ndizosiyana Mr Ken I think mumango lankhula but you don't know what you mean, now I understand you are good in talking but you don't know what is politics zangochitika kuti muli ndi mwayi okhala nawo pafupi ndi anthu omwe akupanga ndale.

  • @felixmaluku5077
    @felixmaluku5077 8 หลายเดือนก่อน

    Kodi azodick mumachita interview ndi skeleton

  • @Alilevati2994
    @Alilevati2994 8 หลายเดือนก่อน

    Kodi madam alipo akumakutumani?

  • @user-yt2op5rl2q
    @user-yt2op5rl2q 8 หลายเดือนก่อน +1

    Hahaha sangawine skeleton uyu kkkk

  • @user-ur4sj4mk1q
    @user-ur4sj4mk1q 8 หลายเดือนก่อน

    😮😮

  • @osmanmailosi6654
    @osmanmailosi6654 8 หลายเดือนก่อน

    Usasowa pogwira nyapapi ngati iweyo

  • @user-eu1qs1eu5q
    @user-eu1qs1eu5q 8 หลายเดือนก่อน +1

    63 yopanda zeru 5 years atha kukhala ndi zeru 😂😂😂😂 adawa wosokoneza Ali ngati mayi woyendayenda ameyo Leah ongotaya naye nthawe

    • @user-ld1js7dt3b
      @user-ld1js7dt3b 8 หลายเดือนก่อน

      Alibechochita, amadyera mommo but ndalezinasintha azatamasoka one day nkuluyu

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 8 หลายเดือนก่อน

    Ai msonda, kuchepa thupi kwako siuli ngati Lea please Msonda you're too much ghost

  • @levisonmoyo1306
    @levisonmoyo1306 8 หลายเดือนก่อน +1

    Malawian politicians are funny Koma

  • @innocentmusuli7380
    @innocentmusuli7380 8 หลายเดือนก่อน

    Tandikonzeni kugwa kwa kwacha ndi natural disaster

  • @wapenyapatali5849
    @wapenyapatali5849 8 หลายเดือนก่อน

    Nsonda kkkkkk! Dausi weniweni

  • @Renzel0234
    @Renzel0234 8 หลายเดือนก่อน +1

    KADHALA AKAKA SIKAKULA BWINO😂😂😂😂

  • @user-kf5th5zy6m
    @user-kf5th5zy6m 8 หลายเดือนก่อน +1

    This politician speaks truth

  • @sydneyngoma2356
    @sydneyngoma2356 8 หลายเดือนก่อน

    Mbali wanga mwa Ambuye Yesu Christu Keep fighting for the truth

  • @leonardjika2100
    @leonardjika2100 8 หลายเดือนก่อน

    A NEW VERSION WILL GOVERN OUR LAND SO HELP ME GOD GIVE ME THE WAY TO SAVE MY PEOPLE DURING THIS DIFFICULT TIME WHEN MY PEOPLE ARE STRUGGLING THEIR LIFE IS DETERIORATING LIKE A LOCKET SO HELP ME GOD TO SAVE MY PEOPLE

  • @user-xm1mp2bn4s
    @user-xm1mp2bn4s 8 หลายเดือนก่อน

    Best journalism❤❤😂

  • @user-vb6ug4zt3q
    @user-vb6ug4zt3q 8 หลายเดือนก่อน

    Ozayamba chipani chanu bwanji mukutinyasa kwambili

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 8 หลายเดือนก่อน

    Dunderhead, nincompoop,I don't have any kind word for you

  • @goldenbanda6757
    @goldenbanda6757 8 หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkk ine ansonda mulungu akudalitseni

  • @user-mt1iw2bb8y
    @user-mt1iw2bb8y 8 หลายเดือนก่อน

    Msonda ndiwe mbuzi ulibe mfundo Koma ife tili pamboyo pa APM

  • @265mww
    @265mww 8 หลายเดือนก่อน

    Leah ndimakufuna

  • @user-sv4vk2bf8r
    @user-sv4vk2bf8r 8 หลายเดือนก่อน

    Boza

  • @fraserluwemba6364
    @fraserluwemba6364 8 หลายเดือนก่อน

    Leah amakhala interested ndi mayankho abodza

  • @user-yt2op5rl2q
    @user-yt2op5rl2q 8 หลายเดือนก่อน

    Uyundicnisilu akukulakukamwa yet alive ndalama convertion ndalama za apm? Ntumbo wamako nsonda

  • @chifundokumbali-nv7fz
    @chifundokumbali-nv7fz 8 หลายเดือนก่อน

    Azibambo adyera awa

  • @usumanidaudi
    @usumanidaudi 8 หลายเดือนก่อน

    Komaso inuyo atora ngani mukamafuna kuyangura ndi andu osamafusa mafuso ndi amisara omwe nsonda ndi wamisara

  • @user-rd8vw1pc4b
    @user-rd8vw1pc4b 8 หลายเดือนก่อน

    🎉

  • @MAYGOSPELALBUMSChawawa
    @MAYGOSPELALBUMSChawawa 8 หลายเดือนก่อน

    Kodi sakuziona kuti watha anayenera kukapuma mphamvu zatha and nzeru zathanso palibe cha nzeru angokhala chete basi