Mbenjere Kung'alula Mcp? 😳😳 amene akudziwa Za Nyimbooyi Tiuzeni ko pilizi 😂

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 168

  • @KassimIssa-bn3od
    @KassimIssa-bn3od 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +15

    Wazindikila chilungamo ndiyemweyo 😂

  • @GanizaniMaulana
    @GanizaniMaulana 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +6

    Yaaaah bro ndimbenjere ameneyo I know this guy he has also another style of singing

  • @isaacimmantambala5294
    @isaacimmantambala5294 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

    anthutu chilungamo akuchidziwa mutha kuona & mbenjele ndi ozindikila😂😂

    • @symoldicky
      @symoldicky 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kkkkk wazindikila cuz Ali kuchikangawa party? Ndipo Kodi akat kuzindikira nchani ngat sikuchikuta zinthu mwanzeru munthawi yoyenera? So ngat nkuzindikira KO kwagona pati pot posatengera ndale or chipan chosatira koma kuima pachilungamo zinthu sizili bwino pankhan ya umoyo kamba Ka usogoleri ulipo omwe anthu Ake akukhala ngati agontha komaso khungu moti sakuoan ndikunva mmene anthu Ake akuvutukira then kod Munthu ozindikira panthawi iyiyi yomwe anthu akuvutika ndipo akusowa anthu omwe angathe kuwayankhulira zammene uli Moyo angasapote zomwe zikuzunzitsa anthuzo?

  • @AbdulrazaqHussain
    @AbdulrazaqHussain 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Yaphedukadi for real, big up!!!love it

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Ameneyu ndiye timati Legend Mbenjere💪 Not anyapapi omwe akumakayimba ku MCP music Show!

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Zoona Chakwera you must go, watikwana

  • @HarryKandani
    @HarryKandani 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

    Mbenjele kubaya pa liwombo 😂

  • @MussaZimba
    @MussaZimba 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mbenjele katundu wa amalawi uyu 😂😂😂

  • @YamikanAbubakary-my4ie
    @YamikanAbubakary-my4ie 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Inu zimenezo sinzikugwirizana ndi zomwe akumvena pamebepo mix inyimbo imeneyo ndiyakele oro Dr Laz asalowe m'boma
    Komaso mmene ndikumverela mau enawo simbenjere ayi ndiwomwe anyamata olubwalubwa 😂😂😂😂

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    good composition Mbenjere amatha

  • @YamikanAbubakary-my4ie
    @YamikanAbubakary-my4ie 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Km boma ndilomweri stikusintha m'paka 2030 wooooo
    Yemwe akufuna kusintha
    boma angosintha mkanzi oro mwamuna pamenepo ndiyekuti zimunthekera
    😂😂😂😂😂😂

    • @StevoZimba
      @StevoZimba 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Imbwaiwe

    • @AchinaKellz
      @AchinaKellz 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      Mbuzi 😂ndi mbuzi olokuyingenda pompo imaona ngati dzuro

  • @DanJohn-ws5gl
    @DanJohn-ws5gl 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Nice song mbenjele tufuna izizi iyi ndiye sound yanzelu

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    He's the one 😂😂😂, galu wake yomwe wayamba kukuluma

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    M-malawi aliyense akudziwa nkhaza dzimene adapanga a mcp ku Chikangawa.

  • @captainmedia
    @captainmedia 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Akuti ndikavote pa 20 pano. Meaning Nyimbo iyi Mbenjere anaimba dzaka zambuyozo. Chorus ndiya Mbenjere koma wina walowa ma verse`wo ndi kuika zomwe zachitika chaka chino cha 2024.

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Iwe wabodza nyimbo yaimbidwa Pompano usaname

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Uzinva nyimboyo message yake, Kodi mesa zotenga ziphatso Kuti abere mavoti zikuchita pompanopa kumawanamiza anthu Kuti awapatsa chimanga apititse ma ID. Open your eyes big Amalawi ndiochenjera MCP Siingatipusitse

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chorus ndi beat ndi mbenjere koma zinaz ndi wina 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @MayaMilanzie
    @MayaMilanzie 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Anthu alowetsapo zawo apa mbenjere maimbidwe ake timawadziwa kkkkkkk izizi ndingati zomwe zinawachitikira mablacks kungowanamizira😂😂😂😂

  • @khidhwirzaynabadharwashali5873
    @khidhwirzaynabadharwashali5873 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Madobadoba amujudula mbenjere,
    Nyimbo ndi ziwiri zosiyananso

  • @SamuelChiwere
    @SamuelChiwere 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tikumva kuti wamangidwaso anyway Mchinji simagawa kamba😂😂😂

  • @HappyKanyangala-oq1kk
    @HappyKanyangala-oq1kk 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Ndiwe Galu heavy that is old music since 2014 I'm remember ase.

    • @StevoZimba
      @StevoZimba 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Koma anenamo za ndege umu it's like niku chikangawa 😅😅

    • @TrizerKanyemba-ru3lv
      @TrizerKanyemba-ru3lv 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Nde bwez akukambamo za ngozi ya ndege?

    • @AchinaKellz
      @AchinaKellz 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Yabaya kkkk

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mbenjere ulemu wanu big brother be strong 💪 🙏 that is true 👍 🙏 👏 🙌 😄 😆

  • @WillieKalipinde
    @WillieKalipinde 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyimbo waswa iyi eeeeh, mpaka Mr Chi........ atayimva Mmmmh

  • @OretarbadrBwanali
    @OretarbadrBwanali 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    😂😂😂 Nyimbo nd iz zot ukamamvera uku ukunyekhula

    • @giftgama1325
      @giftgama1325 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kkkkk

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndalamazo idyani Koma Vote ili mu mtima Awa akomoka ndithu Komwe tikupitaku

  • @DysonTummiesSajiwa
    @DysonTummiesSajiwa 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ine mbenjele ndimakhala naye kuno uyuyu simbenjela koma amene wayimba nyimboyi wangotengako ma part ena ambenjele anyimbo zakale

  • @Mobilot2android
    @Mobilot2android 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    We are creating the Kamangilas more and more ❤

  • @cleverchikowi
    @cleverchikowi 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    This song ndyakalekale and it's mbenjere himself who sung it

  • @Ahlubyt
    @Ahlubyt 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂😂😂😂Kaya ndi iyeyo kaya si iyeyo nyimbo yi ilibwino😂😂😂

  • @HestingsEdward
    @HestingsEdward ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ati kuli Adani luu akuyimba tidasungira wanthu wasundwe kkkkkkDPP boma

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Big man Mbenjele nyamata wama suit otchena

  • @FladielMwase
    @FladielMwase 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndi mbenjere ameneyo 😂😂😂😂😂😂

  • @ShamilahSaizi
    @ShamilahSaizi 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    Inu ndi mbenjere uyu weni weni

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@ShamilahSaizi 🤣🤣🤣😂😂

  • @andrewmaluwa2713
    @andrewmaluwa2713 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ine Nyimboyi ndidayimvelako tikuyandikila zisankho za 2020 wina wake adapangila TikTok

  • @erickhowoya9894
    @erickhowoya9894 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyimbo yakale iyi, he was singing against APM.

  • @petermsamariamapira8933
    @petermsamariamapira8933 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    I like mbenjere they song sound malawi ❤

  • @macloudluka8158
    @macloudluka8158 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndi yakalè kale ase nyimbo imeneyo

  • @KondwaniBanda-ul8sj
    @KondwaniBanda-ul8sj 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndimbenjela ndithu sangalephe Ku MCP alawoko posachedwapa chifukwa kumbuyoku anayimilako u mp koma ndi UDF

  • @ahmedissah7884
    @ahmedissah7884 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂😂Ndamumva ndiyemweyo

  • @Miko099-x7h
    @Miko099-x7h 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Nyimboiyi amaimba kalekale thawi pp

  • @cmsanyama200
    @cmsanyama200 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uyutu ndibwezi akumangopitiliza kuyimba chifukwa samaguga ngati mmene alili ambili a reggae a ku Jamaica

  • @GoldenNamanguya-q9u
    @GoldenNamanguya-q9u 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Ndiyemweyo

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@GoldenNamanguya-q9u 🤣🤣 afananaditu komaso Bit yo ndiya Mbenjere

  • @BannetMisi
    @BannetMisi 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Palibe amene savakuwawa mbenjele nayendi Muthu mwina achita manyazi

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyimboyi adayimba ndi mbenjere ft symon mu nthawi ya pp kmno zangogwilizana kwa mbiri ndi nyengo ya chikangawa ino kmno pano akuyimba za mcp😂😂😂😂

    • @FalesichiutsiFalesi
      @FalesichiutsiFalesi 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      I think you are right

    • @FalesichiutsiFalesi
      @FalesichiutsiFalesi 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      But he did not feature Symon, it's someone else

    • @AlfRed-i6y
      @AlfRed-i6y 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Komano zandegezi bwanji

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@AlfRed-i6y musaiwale kuti kunali zogulitsa ndege ya air malawi ndi a jb that's y ndege ikutchulidwamo ndithu ineso nyimboyi yandisangalatsa kwambiri kmno anyamatawa akumapita kukayimba ku misonkhano ya mcp.

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@FalesichiutsiFalesi komaso imvani za tsiku lovota akuti pa 20 yet vote ya 2025 ndi pa 16 September km anthu sangazindikire chifukwa mind yathu ili ya za ndege ya ku chikangawa.

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Oyimba amene akulowa muchipani cholamula bola nyani angakhale ndizeru pamene wafika Malawi munthu wazeru sangamene kuti boma ndilomweli okhawo womwe nali ndi mizimo yoipa andi amene akuti mboma ndilomweli chifukwa satana or munhamuphuzitse bwanji mawu a Mulungu sadzatembenuka.

  • @hagayichiluwe
    @hagayichiluwe 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyimbo ndiyakalekale iyi 😂 koma cadet ali pa job

    • @MosesChaphuka
      @MosesChaphuka 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Nanga za ndege nzaliti?

  • @BaldwinBanda-gd9zo
    @BaldwinBanda-gd9zo 19 นาทีที่ผ่านมา

    Koma nyimbo iyi ndiyapakanthawi siyatsopano ayi koma ndi yomweyo mbenjere

  • @KondwaniGumba
    @KondwaniGumba 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndikalekale nyimbo iyi kkkkkkk , inu mwaivera kumene.

  • @CollinsChimsendenji
    @CollinsChimsendenji 38 นาทีที่ผ่านมา

    Nyimbo ndya kalekale iyi 2019

  • @AlufeyoBanda-cv2we
    @AlufeyoBanda-cv2we 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mbenjere ya kalekaleyi inuyo mwaimva lero koma kumalawi kkkkk

  • @NoahPhiri-f7m
    @NoahPhiri-f7m 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    More 🔥 🔥🔥🔥🔥

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mbenjere ndi Mp koma wadatuluka Dpp pano ndi wa Mcp ndiye inuyo musamunamizire pa za nyimbozo

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      Mbenjere ndi Mp?????

    • @AmanaHambalie
      @AmanaHambalie 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      ​@@MalawianCamera ineso kudabwa

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      ​@@MalawianCamerabro dont mind him samadziwa.chomwe amakamba nthawi znse awo

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      ​@@AmanaHambaliemukamva kuti ku MCP kuli zisru zokha.zokha musamadabwe nazo zimenez

    • @VioletChandire
      @VioletChandire 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Mp wo akuphirira paborder?

  • @BrianMuleke
    @BrianMuleke 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkk ndiyemweyo😊

  • @HannahTulizoh
    @HannahTulizoh 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    MCP my vote

  • @GraceJailos
    @GraceJailos 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ipase moto mbenjele nyimbo koma imeneyi osati atuluka ukweche ndiye zichani

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    We need some more teachings!!

  • @Moses51
    @Moses51 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Yomweyo mbenjele 😂😂😂

  • @robertkalima874
    @robertkalima874 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Nyimboyi ndi ya nthawi ya Joyce Banda musapusitse anthu

  • @MoffatBinali-pp8hi
    @MoffatBinali-pp8hi 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyimbo yakale kwambiri nthawi ya Joyce Banda amanena zandege idagulisidwa

  • @peterliyapah3844
    @peterliyapah3844 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Title take chani nyimboyi?

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Usanchimwitse

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkkkkkk koma ayi mcp mwanyanayo basi sinchewa ameneyi ayi zikomo

  • @MarthaChigonero
    @MarthaChigonero 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mulungu naye watopatu pano anthu azingo ng'alula basi

  • @FrancisTizola
    @FrancisTizola 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyimboyi ndi ya Mbenjere anayimba 2019 towards 20 May mmenemo DPP ikugawa Chimanga ndi ngongole ya madefu.

  • @thomaswyson-e2q
    @thomaswyson-e2q 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ameneyi ndimbenjele emweyo komansotu paja anaimbakale yatinkat tambalawakuda komandimloza

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Mbenjere at his best

  • @innocentlipita3630
    @innocentlipita3630 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chimozichakwetekwete ndi mutu wanyimboyi ndiyakale ife amene timamvera nyimbo zake imeneyi tilinayo

  • @HaleemaAllie
    @HaleemaAllie 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiya chinkangawa yoo😂😂😂😂

  • @MercyKziphondo
    @MercyKziphondo ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ikhala bwanji yakale atatchulamo zandege ndiyapompa no

  • @HestingsEdward
    @HestingsEdward ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwakalipa amalume DPP BOMA kkkkk

  • @StewardKapoto-u7k
    @StewardKapoto-u7k 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyimboyo angoipanga Remix ndiyakale kale

  • @Khadija-q9r
    @Khadija-q9r 2 นาทีที่ผ่านมา

    Nsokhano wa Apm rikavinila yomwei

  • @Mpungwe123
    @Mpungwe123 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Anaimba nthawi ya Joyce Banda when she was a president and he was on wanted mpaka anathawa

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Wow thanks for the information timadabwatu

    • @Mpungwe123
      @Mpungwe123 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      @@MalawianCamera 😂😂😂😂I like that song ndilinayo since that time

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@Mpungwe123 koma anaimba bwino coz ikupangaso fit mu nyengo ino 😂😂

  • @TisopeMkozo-h8t
    @TisopeMkozo-h8t 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uyu ndi Mbenjere weniweni

  • @EyobeAyala
    @EyobeAyala 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Umakwanaaaaaaaaaaaaa💪💪💪💪💪💪💪💪💪🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥💯💯💯💯💯💯💯💯🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @HarryKandani
    @HarryKandani 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Sangagule oimba onse ....kuswa kuswa basi

  • @michaelkhunga3676
    @michaelkhunga3676 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ndi mbenjele komaso nyimbo iyo ndiyapakanthawi ndithu osati panopa

  • @YousufuJohn
    @YousufuJohn 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndi mbenjele of course

  • @IslamMapepa
    @IslamMapepa 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akuziziwa ndimwiniwakeyo

  • @fanuelharrison
    @fanuelharrison 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mbenjere Ali ndi mnzake ameneyu

  • @fanuelharrison
    @fanuelharrison 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Amenenu ndi mbenjere koma Ali mnzake

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Auzeni a MCP adziwe okha Mbenjere

  • @TisopeMkozo-h8t
    @TisopeMkozo-h8t 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi in mukumati Boma ndilomweli mumagula zinthu motchipa nde kuti

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyimbo iyi ndiyakale kwambiri

  • @falomoyo1203
    @falomoyo1203 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiyakale koma yimakhala ngati ndiyasopano inali yamunthawi ya joice Banda

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Wawonatu mbenjele😅😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @AnnastasiaChakwiya
    @AnnastasiaChakwiya 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mbenjere yemweyo😂😂😂😂😂😂

  • @HappyChipakasa-g5p
    @HappyChipakasa-g5p 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndiyebweyo ndithu

  • @RaphaelAlfred-s3h
    @RaphaelAlfred-s3h 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uyu waionela patali akuziwa kumene kukupita boma pa 16 sepitembala

  • @RobertTaimu
    @RobertTaimu 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Symon & Kendal uyu

  • @KelvinPhiri-z9d
    @KelvinPhiri-z9d 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Pali colab

  • @SiphelileMwaza
    @SiphelileMwaza 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkk ndimbenjele ndianyamata ake

  • @InnocentMtafya
    @InnocentMtafya 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndale za kwathu kuno zandidziwitsa kuti anthu ambiri mmalawi muno brain nzobooka ,akangomva chinthu osachifufuzanso Basi Ena Ali pa nyimbo ,Ena m'ma social media, kulibe Boma lingadzathetse mavuto athu izo nde kulibe Kaya palowa wins nde worse alipowa sangakwanitsensoyi ,ulesi(n'sanje Ndi katangale) ndiimene utiphweteke

  • @innocentlipita3630
    @innocentlipita3630 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyimboyi ndi yakalekale anaimba munthawi ya joice banda

    • @AlfRed-i6y
      @AlfRed-i6y 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kunaliso zandege kodi nthawi imeneija

  • @HarrisonKalonga-k7p
    @HarrisonKalonga-k7p 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Yemweyo

  • @ChancyMakwinja
    @ChancyMakwinja 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ai simbenjere

  • @KondwaniGumba
    @KondwaniGumba 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyimbo ndi 2014.

  • @ChilekaMoyenda
    @ChilekaMoyenda 39 นาทีที่ผ่านมา

    Mbenjeleeeee❤

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂😂😂😂lpatse moto ❤❤

  • @jeremiasstefano9042
    @jeremiasstefano9042 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Nyimbo yakale iyi

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Alright ndiyakedi?

    • @BrightonEnockEnock
      @BrightonEnockEnock 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      Nyimbo yakalekale iyi nthawi ya Joyce banda muveleso salowa 50​@@MalawianCamera

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@BrightonEnockEnock Thank you brother that's what we wanted to know 👍

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndimbenjere tape yake ine ndilinayo😂😂

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      🤣🤣😂 Serious?

    • @paulpaseli6310
      @paulpaseli6310 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      @@MalawianCamera eya ndiyakale ndithu tikupukusila tape sekela🤣🤣

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@paulpaseli6310 😂😂😂

  • @chifundoKaluvi-ey5uw
    @chifundoKaluvi-ey5uw 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mbenjere yomweyo😅