SYMON AND KENDALL ALOWA CHIPANI CHA MCP NDIPO AIMBA NYIMBO IYI KU NSONKHANO WA MCP LERO LIVE LIVE

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 13 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 121

  • @HopeKeyz-pr5pw
    @HopeKeyz-pr5pw 2 วันที่ผ่านมา +3

    Mkasa ndi zanyimbo iiiii kuswakuswa.koma Dpp my vote💙💙

  • @Jane-qb5qf
    @Jane-qb5qf 2 วันที่ผ่านมา +4

    Amalawi osadandaula kumwamba kuli mulungu pomwe lafika dziko lamalawi mkumayimbira mmanja izizi aaaa chizaziwe ndichipande poomola

  • @KhumboNyerenda
    @KhumboNyerenda วันที่ผ่านมา

    Chitsiru kendo ,osakangomwa mankhwala owo.

  • @IdirissaCharles-s8g
    @IdirissaCharles-s8g วันที่ผ่านมา +2

    Dpp my vote ❤❤❤❤

  • @LinlyMatheweKufakwina
    @LinlyMatheweKufakwina 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Utm my vote ❤❤❤

  • @BakhePaliso-h8h
    @BakhePaliso-h8h 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Boma ndilomweli kwanu konko kuno ayiiiii

  • @LameckBanda-gk6ri
    @LameckBanda-gk6ri 2 วันที่ผ่านมา +2

    MCP ndi malonda osavuta kuguritsa kusiyana ndi zakubanjazi ,mutukwana mutopa koma boma ndi lomweri basi

  • @FalesMdemba
    @FalesMdemba 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Utm my vote

  • @YohaneStevenMhone
    @YohaneStevenMhone วันที่ผ่านมา

    Mmakwanila a symon nd a candle

  • @ModesterBandah
    @ModesterBandah 2 วันที่ผ่านมา +1

    MCP my vote

  • @NdaonaSandifolo
    @NdaonaSandifolo วันที่ผ่านมา +1

    Koma kendo ndi sayi eee ndinu madolo

  • @yasitafuphiri-nw2he
    @yasitafuphiri-nw2he 2 วันที่ผ่านมา +1

    Kendal my next mp umakwana ,kuli dzuwa ukoko kkkkk

  • @GenitojosebingalaJosebingala
    @GenitojosebingalaJosebingala วันที่ผ่านมา

    Zinali ku Mozambique afelelimo agwa chatenga ndi chipani changoyamba chaka chomwechino awuzen achakwela akudziwa salu zake zamagazi zomwezo

  • @BashiruKatuli
    @BashiruKatuli วันที่ผ่านมา

    Dpp woyeeee🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @MariaNkhata-i9q
    @MariaNkhata-i9q วันที่ผ่านมา

    💙💙💙💙💙💙Dpp my vote 💙🔵🔵🔵💙🔵💙🔵💙🔵💙🔵💙🔵💙🔵💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙 adad love u

  • @NdaonaSandifolo
    @NdaonaSandifolo วันที่ผ่านมา

    Nkasa ukunena zowona tili pambuyo pa mcp motsogozedwa ndi achakwera dpp sindingayivotele chifukwa inandidyela alubino

  • @AnusaMponda
    @AnusaMponda วันที่ผ่านมา

    U president ndi business guys no one can come and mkutivetsa kukoma ndipo zomangosintha zipanizii ndiye dziko tizingoononga basiii nkhani ndiyomwe ija chipani chimodzi kumangosintha atsogoleri koma zathuziii mmmm aliyense angosiya ngongole kuti nzawo anve kuwawa komwe kuli. Kupweteketsa amalawi kum'bwezelera ngongole wina siii easy apa tili nyengo zovuta basi 😢😢

  • @MussaSubeli-bh3ge
    @MussaSubeli-bh3ge วันที่ผ่านมา

    Akatero apatsidwaso ndalama nawo

  • @MangochiJoni
    @MangochiJoni วันที่ผ่านมา

    Dpp noma khanjani is my vote

  • @EdwardAllie-s4m
    @EdwardAllie-s4m วันที่ผ่านมา

    Dpp boma 2025🔥🔥🔥🔥🔥

  • @chipilirombengo4813
    @chipilirombengo4813 2 วันที่ผ่านมา +2

    Nsonkhano ngati ali kumaliro

  • @BakhePaliso-h8h
    @BakhePaliso-h8h 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    DPP woyeeee

  • @ChisomoTrevor
    @ChisomoTrevor วันที่ผ่านมา

    DPP my vote

  • @ChundaLackson
    @ChundaLackson 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    sitisintha boma anyamata achipongwe awa kkkkk

  • @DavieChamasowa-p1g
    @DavieChamasowa-p1g วันที่ผ่านมา

    Zikafika apa umangodziwa kuti ndalama za satanic zaphweka. Dear Grace Chinga. May Your Saul Keep Resting. Still Love You.

  • @MaryChimwala-c5g
    @MaryChimwala-c5g วันที่ผ่านมา

    Adyereni asowa nazo kopita agalu azawo akudya chitedze Dpp ndi boma

  • @AlicksonGoliath
    @AlicksonGoliath วันที่ผ่านมา

    Chakwera deserve my vote again not gogoyu wakula adzikalera zizukulu.

  • @JohnKwapulani-zn7ef
    @JohnKwapulani-zn7ef 2 วันที่ผ่านมา

    Music show nokha a MCP mutha kuona akutha kupangitsa misokhano ndi azipani zotsutsa

  • @FelixWiskesi-d7w
    @FelixWiskesi-d7w 2 วันที่ผ่านมา

    Vote is not going through music but see how we are struggling

  • @EstherKanthungo
    @EstherKanthungo วันที่ผ่านมา

    Olo mutapita oyimba nonse ku MCP ine singakopeke ayi DPP WOYEEE

  • @McdonaldSairo
    @McdonaldSairo วันที่ผ่านมา

    Dpp my vote

  • @thokozanisauti5443
    @thokozanisauti5443 2 วันที่ผ่านมา +2

    koma mumadziwa kukocha nyimbo ana inu ulemu wanu,🔥🔥🔥Boma lomweri

    • @BakhePaliso-h8h
      @BakhePaliso-h8h 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Mbava zimaikilana kumbuyo zokha zokha ngongore zimene mukutenga kumamangila zimanyumba zanu zipatala mukusowa mwankhwala anthu kumamwarira mulungu akulangen pa dziko pompano

  • @MalawiMalawi-q7d
    @MalawiMalawi-q7d วันที่ผ่านมา

    Chaka cha mawa tidzaone mitima yosweka kkkk

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 2 วันที่ผ่านมา +1

    Simon and kendo nkhale akuimaba Mimbazawozo zinaphwelatu panopa ndi njala enawo ngati akudwalatu 😂😂😂

    • @EllenChimera
      @EllenChimera 2 วันที่ผ่านมา

      Kumachita kulira kuimbira mcp😂😂😂😂😂

    • @TinaKazembe-l7d
      @TinaKazembe-l7d 2 วันที่ผ่านมา

      Kkkk komaso iweso

    • @YusufJimmy-v1o
      @YusufJimmy-v1o วันที่ผ่านมา

      😂😂😂

  • @IssackCassimu
    @IssackCassimu วันที่ผ่านมา +1

    Dpp my vote iwe achimwendo mapwala anu🙄🙄🙄🙄

  • @MorganNyirenda-w7c
    @MorganNyirenda-w7c 2 วันที่ผ่านมา +1

    Akumafuna kudya ndarama bas oimbawa nangasi boma ndichisimi chandarama aaaaa musatinamize

    • @TinaKazembe-l7d
      @TinaKazembe-l7d 2 วันที่ผ่านมา

      Iweso imba yako udxidya

  • @KennedyBMafedwe-w1p
    @KennedyBMafedwe-w1p วันที่ผ่านมา

    Boma ilo, ndiloyipira waulesi koma olimbikira ndizoyenda

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e วันที่ผ่านมา

    Kkkk ku show

  • @DamianoGabriel-sh2mf
    @DamianoGabriel-sh2mf 2 วันที่ผ่านมา +1

    Mesa anali a mcp kale awa alowaso kangati

  • @JoshuaJombo-ej8pu
    @JoshuaJombo-ej8pu วันที่ผ่านมา

    Dpp woyee molalo wochita kukakamiza abale 🤣😂

  • @MussaLenard-s2t
    @MussaLenard-s2t 2 วันที่ผ่านมา

    DPP MY VOTE 💙💙💙

  • @DalixoulLawrence
    @DalixoulLawrence วันที่ผ่านมา

    Nafe tiyambe kuyimba mwina mkupasidwa kangachepe

  • @JoãoChirwa-n3l
    @JoãoChirwa-n3l วันที่ผ่านมา

    Sono jetu sanamungule bwanji

  • @GeraldMkwewu-gd5eb
    @GeraldMkwewu-gd5eb 2 วันที่ผ่านมา

    Chitukuko akhare oyimba zachisoni nde lfe tilibe Nazo ntchito or mupaseni mabilion adadi 2025 boma kale

  • @ThandiShandu-l6w
    @ThandiShandu-l6w 2 วันที่ผ่านมา +1

    Koma guys dpp ili m'adzi ndiomba akuing'alura palibe akuyi sekelera dpp mcp + oyimba agwetsa dpp ndikawelenga oimba akukwana zipani 9 zinatuluka zija MCP sizatheka zinatha zipani pano moto moto ndioimba

    • @ThandiShandu-l6w
      @ThandiShandu-l6w วันที่ผ่านมา

      ​@augustMagusaname iwe MCP inazula kale Mai sendera mulibe chatsala DPP ndikumanda

  • @giftsululu4274
    @giftsululu4274 วันที่ผ่านมา

    Koma ku opposition tupselerako ife

  • @GeorgeJeremia-dv1sv
    @GeorgeJeremia-dv1sv วันที่ผ่านมา

    Otsutsa ndiomwewa😂😂😂😂😂😂😂🤣🤣🤣🤣🤣

  • @JohnKanyenda-c9e
    @JohnKanyenda-c9e 2 วันที่ผ่านมา

    Mcp my vote

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo วันที่ผ่านมา

    Nyimbo yosabebayo

  • @JalitahKatumbu
    @JalitahKatumbu 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kuvotera mcp mkutaya thawi

  • @EmmyYafete
    @EmmyYafete วันที่ผ่านมา

    DPP my vote !!!!!

  • @StantchuAlex-s9x
    @StantchuAlex-s9x วันที่ผ่านมา

    Boma likhala lomweli bwanji mwini wake waboma anafela ku Chikangawa??😠😠😠😠. Achina Chimwendo note this, this is your time to be happy, 2025 Mukwiya osati masewela😂😂😂😂

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 2 วันที่ผ่านมา

    Oyimba nokha nokha mukapanda kulodzana urendo uno ndakaika

  • @JemaxChibwanazulu
    @JemaxChibwanazulu 2 วันที่ผ่านมา

    Boma ilo, koma mukutha ndi ng'ona bas pokasaka chakudya madzi. Mabvuzi anu mulibe nzeru

  • @richarddoctor4746
    @richarddoctor4746 วันที่ผ่านมา

    Mesa Kamuzu uja munkatinso muzafa naye? Pano mukadali moyo chifukwa chani pamene Kamuzu'yo anamwalira

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga 2 วันที่ผ่านมา

    oyimba oyionera patali amenewo

  • @SusanaMakanga
    @SusanaMakanga 2 วันที่ผ่านมา

    Ku opposition kuja kuri dzuwa🤣🤣🤣🤣🤣🤣🔥🔥Kwa bwana wabwino sitisiya tchito 💃

  • @MartinKawowola
    @MartinKawowola 2 วันที่ผ่านมา

    Chikangawa😢

  • @MaureenBanda-t2q
    @MaureenBanda-t2q 2 วันที่ผ่านมา

    Kodi woyimba wa kumwa ambuye mtengeni onse zaduu

  • @JemaxChibwanazulu
    @JemaxChibwanazulu 2 วันที่ผ่านมา

    Abwasatu inu

  • @anthonylufeyo2505
    @anthonylufeyo2505 วันที่ผ่านมา

    Kunditero ine😂😂😂😂 kukhosi mbeeee

  • @EdithDuncan-s7o
    @EdithDuncan-s7o 2 วันที่ผ่านมา

    Kodi zasanduka za chinalimwali zochita kufupa ngati ukwati inenso ndiyamba kuyimba

  • @alanejaimeluis9209
    @alanejaimeluis9209 2 วันที่ผ่านมา

    Koma nkasa pa ndalama amandiwaza

  • @ChimwemweZgambo
    @ChimwemweZgambo วันที่ผ่านมา

    Boma ndilomweli basi

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 2 วันที่ผ่านมา

    Game ndiwe mwini komatu azikuliprani osati kumakalilira kutseli kwa chitseko.

  • @christophergibson72
    @christophergibson72 2 วันที่ผ่านมา

    Ku opposition mkumanda kkkkkkkkkk

  • @OlivaPhiri
    @OlivaPhiri 2 วันที่ผ่านมา

    Boma iloooo

  • @MastonWatson-g7g
    @MastonWatson-g7g 2 วันที่ผ่านมา

    Umphawi sizinthu mmmmm.

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya 2 วันที่ผ่านมา

      Ndiponso 😅😅

  • @MARRIAMSHAYIB
    @MARRIAMSHAYIB 2 วันที่ผ่านมา

    Bona iiiiiiiiiiiilo

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 2 วันที่ผ่านมา

    DPP woeeeee

  • @MicyThobve
    @MicyThobve 2 วันที่ผ่านมา +1

    Kkkk mkasa wandiwaza hevy

  • @thomphalavi5027
    @thomphalavi5027 2 วันที่ผ่านมา

    Kuli dzuwa chifuwa Dan Lu watha wako koma ife tili komwe kuli dzuwa ko

  • @edsonphangula5817
    @edsonphangula5817 2 วันที่ผ่านมา

    MCP woyeeee

  • @MariaNkhata-i9q
    @MariaNkhata-i9q วันที่ผ่านมา

    Boma losekesa ili

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh วันที่ผ่านมา

    Zazii

  • @LucyMachine
    @LucyMachine วันที่ผ่านมา

    Dpp boma

  • @JosephyKhimbitoni
    @JosephyKhimbitoni วันที่ผ่านมา

    Otsutsa zikuvutani basi

  • @IshmaelJerard-u9w
    @IshmaelJerard-u9w 2 วันที่ผ่านมา +2

    Kuchipan kwangozazana oimba, kodi ndichipani kapen music show

    • @JohnJohn-og8rt
      @JohnJohn-og8rt 2 วันที่ผ่านมา

      Zisilu isi bare

    • @RamseyKamwana
      @RamseyKamwana 2 วันที่ผ่านมา

      Inu simuona kuti akamaimba akumalandira.ankerako zomwezo.kuzisaka kwake ndiye eee iiimh kwa live amwene.kuchita kufupidwa.

    • @kingsleyChisenga-i8g
      @kingsleyChisenga-i8g 2 วันที่ผ่านมา

      Nanga akaimbe ku opposition awapasa chani ndan safuna kuenda ndi boma

    • @ThandiShandu-l6w
      @ThandiShandu-l6w วันที่ผ่านมา

      Omewa ukamva kuti DPP yagwa gulu lake ndilimeneli usali pepuze chakwera wakwera yotentha apapa oimba ndi boma palokha

  • @ShamilahSaizi
    @ShamilahSaizi 2 วันที่ผ่านมา

    Koma oimba akumalawi kuchititsa manyazi kwake

    • @TinaKazembe-l7d
      @TinaKazembe-l7d 2 วันที่ผ่านมา

      Uchita nanyazi ndi iweyo

  • @shupikayintuwaluwa-5899
    @shupikayintuwaluwa-5899 2 วันที่ผ่านมา

    Pipo need ur promises to be fulfilled not bringing musicians to political rally as if it's music show. Wat a fuck I mean an2 akufq mjala kaamba kodya ziteziwa km muwaona anapwala nonse kuphiriko tiyambire chakwerawe mareport sakumakupezan😊

  • @DicksonLutere
    @DicksonLutere 2 วันที่ผ่านมา +4

    Koma mcp mulichikokatu

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 2 วันที่ผ่านมา

    Wamisala iwe mkasa.

  • @LadenNuz
    @LadenNuz 2 วันที่ผ่านมา

    Koma guyz ndarendiufitidi iwowa anyamatawa amadandaura zanazanali kuti a mcp sanawapase kathupanyimbo yawo yoyamba ija apa aimbaso ina?😂😂😂😂😂😂😂

  • @TinaKazembe-l7d
    @TinaKazembe-l7d 2 วันที่ผ่านมา

    Mkasa wandikumbutsa nyimbo zakale congrats

  • @PulayaKalaka
    @PulayaKalaka 2 วันที่ผ่านมา

    😅😅😅😅😅 Koma khansa

  • @JemaxChibwanazulu
    @JemaxChibwanazulu 2 วันที่ผ่านมา +1

    Or mutapita nose ku MCP ko, ine ndiye singakutsatirenibe

  • @Yafetimota-mc2cs
    @Yafetimota-mc2cs 2 วันที่ผ่านมา

    Mutu ngat botolo

  • @AbdulsalamMussah
    @AbdulsalamMussah 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Boma ndilomweli ❤❤❤❤❤❤❤

  • @MorganNyirenda-w7c
    @MorganNyirenda-w7c 2 วันที่ผ่านมา

    Mimba zinu

  • @FebbieNjewa-g3k
    @FebbieNjewa-g3k 2 วันที่ผ่านมา

    Zaziiii

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov 2 วันที่ผ่านมา

    I don't mind of others but uyu wankulu mutu uyu nkasa alibe manyazi ndipo manyi ake I think ndionunkha kwambili kwasala kut amuphe anamuthibula kare ku dowa

    • @TinaKazembe-l7d
      @TinaKazembe-l7d 2 วันที่ผ่านมา

      Ukhalira yomweyo ukatero ulandira mphoto

  • @OwenNyangu-nv1yt
    @OwenNyangu-nv1yt 2 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkkkk

  • @JoelKacheche-x6i
    @JoelKacheche-x6i 2 วันที่ผ่านมา

    Mcp ndi boma kale mpaka 2030❤❤❤❤❤❤❤

  • @RaheemNgoma-pk1ev
    @RaheemNgoma-pk1ev 2 วันที่ผ่านมา

    Zadziiii

  • @AbdulAzizBaluti
    @AbdulAzizBaluti วันที่ผ่านมา

    Odi ndiphike chitedze changa ndidye ndi ana ine

    • @ClifordNyanda
      @ClifordNyanda 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Mulibe zelu inu ndalama mwagula bandleyo mesa mukanagula chakudya? Musamathandize afumu kuledzera alipo anthu amene akudya chitedze osati inuyo

  • @LingsonManda
    @LingsonManda วันที่ผ่านมา

    Mcp my vote2025

  • @Justman34_dislike
    @Justman34_dislike 2 วันที่ผ่านมา

    Anali a MCP ndikale

  • @YohaneStevenMhone
    @YohaneStevenMhone วันที่ผ่านมา

    Mmakwanila a symon nd a candle

  • @BakhePaliso-h8h
    @BakhePaliso-h8h 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    DPP woyeeee

  • @GeorgeMakwinja
    @GeorgeMakwinja วันที่ผ่านมา

    DPP my vote