JB Vs Dan Lu Kwachemelatu!

แชร์
ฝัง

ความคิดเห็น • 141

  • @JasperWitness-2000
    @JasperWitness-2000 2 หลายเดือนก่อน +2

    Aliyense wabwela yekha pano gather here pano ayi❤❤❤❤❤

  • @FloridaOssy19
    @FloridaOssy19 3 หลายเดือนก่อน +2

    Chakwela Ku menyanya Ku gwesa , 🔥🔥🔥🔥🔥 or wamu tukwane, chakwela aimatso 🔥🔥❤️ I love you Dan lu

  • @KuliKapinga
    @KuliKapinga 3 หลายเดือนก่อน +2

    Ndikona kuli sipani sambili munthu Ali ndi choice kusanga Ngati mzika yamalawi palakwika ndiphati kwa Dani Lu akaliyati sanali Ku DPP lelo Ali kuthi amutalika anapezeka bwanji Ku DPP kuyiukila UDF muziyeni Dani Lu Amenye ndikugwenza kwacha 1-2milion❤❤❤😅

  • @IllenKatota-b4c
    @IllenKatota-b4c 19 วันที่ผ่านมา +1

    We will forever forget you dand krazy may your soul rest in peace we love you all

  • @MofatwilsonJohn
    @MofatwilsonJohn 3 หลายเดือนก่อน +8

    Munthu okonda dziko lake mene mcp ikuendesela dzikoli munthu wanzelu sangalowe mcp

  • @VincentNyabanga-dw9uj
    @VincentNyabanga-dw9uj 2 หลายเดือนก่อน +4

    Mavyete big up

  • @HarieedJumah-m4b
    @HarieedJumah-m4b 16 วันที่ผ่านมา

    Number one bos mn keep up bro

  • @fregiousmablekisi8451
    @fregiousmablekisi8451 3 หลายเดือนก่อน +4

    Choice yake fire Dan lu 😅

  • @johnbanda-v8x
    @johnbanda-v8x 3 หลายเดือนก่อน +1

    Guys Lets think b4 we act ..Dan Lu ukhonza kumadyatu iwe wina akuthatha ndi moyo chifukwa cha njala wosamukalibusa.Zandinyasa kwambiri kuamayamikira kt boma ndilomweri yet zinthu sizikuyenda bwn ndy kt tiziti akudandaulawa akulinamizira bomali kt zinthu sizikuyenda bwn

  • @GeraldNyirenda-j8v
    @GeraldNyirenda-j8v 20 วันที่ผ่านมา

    Chambacho chikulu pweteka ukunyoza mabanja amene anataya abale awo, nde ukufuna lipoti anamize amalawi pangani njira yina yopezela ndalama mizimu yaomwalirawo yiuse mutendele uvutika mtima koma palibe amene akupasa chilimbikiso mbava zizako ndizimene zikuvesa mawu ako😂😂😂

  • @SusanPatel-q2x
    @SusanPatel-q2x 27 วันที่ผ่านมา

    Ambuye Mulungu maso anu asachoke pa mama Mary Chilima🙏🏼

  • @davidbulla5128
    @davidbulla5128 3 หลายเดือนก่อน

    Corruptin'tha Youth 🎶🎵 iz 4 Unifying & ñot fi Divide.
    Use ya powerful voice to empower youth against negative forcez Such Az....

  • @Louisluhanga
    @Louisluhanga 2 หลายเดือนก่อน

    Oo meeen this is more than being superb😮

  • @MosesNyirongo-s4q
    @MosesNyirongo-s4q 3 หลายเดือนก่อน +3

    Dan lu wachitabwino MAKAPE asamamuuze zochita ngati amadya kwawo

    • @HASTINGSKABATA
      @HASTINGSKABATA หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂😂😂 indeed you right 😅😅😅😅

  • @ARONYJACINTOTHOM-n3w
    @ARONYJACINTOTHOM-n3w 13 วันที่ผ่านมา

    Keep it up

  • @AlexZimba-e7k
    @AlexZimba-e7k 3 หลายเดือนก่อน +2

    Ati kutuluka UDF kusiya kuchemerera Peter muthalika😂

  • @ModesterSamson-y1i
    @ModesterSamson-y1i 16 วันที่ผ่านมา

    Mama ambuye akhale nafe mcp sichipani lamuchulikila ndidyela

  • @FladielMwase
    @FladielMwase 3 หลายเดือนก่อน

    Jb ndidolo kwabas ❤❤❤❤ ndpo Dan lu anapanga chisakho chonyasa kwambiri kuchoka ku dpp kulowa mcp 😂😂😂

  • @JafaliChiwimbi
    @JafaliChiwimbi 3 หลายเดือนก่อน

    Sam mavitha umatiyimilila kwambili ndipo upitilize kufukula ngani ❤❤❤❤❤❤

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 3 หลายเดือนก่อน +2

    Dan luu more fire

  • @StewartBatret
    @StewartBatret 6 วันที่ผ่านมา

    Sisimveka izi kwa atogoleri tawonani Dziko losauka koma wina kukhala pa nomber one wa athu olemera pa Malawi

  • @marthaalichangamile1424
    @marthaalichangamile1424 6 วันที่ผ่านมา

    Sorry mum may Allah guide you and your family

  • @CristianoAndrews-r4h
    @CristianoAndrews-r4h 10 วันที่ผ่านมา

    I'll I like this song

  • @happynyirenda8790
    @happynyirenda8790 11 วันที่ผ่านมา

    Moto ukayaka kwambiri ziwani kuti uthima thawi iliyose

  • @MatthewsJanuary
    @MatthewsJanuary 2 หลายเดือนก่อน

    Dan Lu ,potengera ndi mmene analili ku DPP, zamanyazi kwambiiiri lero adziti kwachaaa! Amenewa ayenera kuphedwa coz ngosokoneza kwambiri

  • @NjanjiThimopher
    @NjanjiThimopher หลายเดือนก่อน

    Walakwitsa amafunika akhale ku dpp asachok chifukwa chakachamawach tiklowa m,Boma azatfuna ife a dpp azalila😂😂😂🤗🤗

  • @brightonmilanzi8130
    @brightonmilanzi8130 2 หลายเดือนก่อน

    Mbenjere ndi munthu wankhulu simunthu wamba ayi amaona pathali zedi big lorence Mbenjere

  • @Hamzaaustin21
    @Hamzaaustin21 3 หลายเดือนก่อน +1

    Palibe chalakwika dan lu kuimbira chakwera tonse sitingakhale abulets ena ndi a noma ena a silver koma mpira ndiymodzi

  • @JoãoManuel-j8x
    @JoãoManuel-j8x 18 วันที่ผ่านมา

    Boa boa🎉🎉🎉😂

  • @ChembeKaundah
    @ChembeKaundah 3 หลายเดือนก่อน +2

    More fire

  • @HASTINGSKABATA
    @HASTINGSKABATA หลายเดือนก่อน

    Don't judge anyone without understand his reason
    Munthu aliyese Ali ndi ufulu kusankha chipani chilichose akufuna kopanda kumuweruza

  • @andrewbanda99
    @andrewbanda99 3 หลายเดือนก่อน

    Mukunamatu inu, amenewo ndimaganizo awumphawi amenewo mzanu akudya money. Bwela ku mcp kusokoselako ndi umphawi zikuntha zimenezo

  • @MatthewsJanuary
    @MatthewsJanuary 2 หลายเดือนก่อน

    Ndikutseguleni mutu enanu osaganizanu. Dan Lu zomwe apangazi.zili chonchi, mkazi wanu muli naye mnyumba,ndinu olemera kwambiri,banja kumayenda bwino ndithu,aneba anu kumawanyoza amvekere; awanso ndiye kaya basi, kugona ndi njalaaa, samasambaaa,
    After zaka zingapo, mphawi uja nayenso watola chikwama, banja lake nalonso lasauka. Pamenepo mkazi uja wayambanso kudyerera maso anali mphawi uja mkazi ameneyi anthu akamva,mukuona,adziti chanii? Yankho Ianu ndilomwe lionetse kuti ndinudi oganiza kapena opepera

  • @ChipiliroSemu
    @ChipiliroSemu 2 หลายเดือนก่อน

    Ameneyu si mbenjele ayi, ngati mukukumbuka padzana panatulukanso nyimbo yonyoza amati ndi Nkasa pomwe sanali nkasa

  • @MangulenjePaulo-j3n
    @MangulenjePaulo-j3n 14 วันที่ผ่านมา

    Atenge ndaramazo azikasiya MMA district anthu tisavutike

  • @PatrickCarol-xe2zb
    @PatrickCarol-xe2zb 2 หลายเดือนก่อน

    Dan lu ni more fire🔥

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 หลายเดือนก่อน +1

    Palib kutuluka ukweche chfukwa chaiyeyo ndindani alibe nzeru vuto lake ndye kulimbana ndi chsru Dan Lu ungapuse ndweyo koz Dan Lu mchsru mchamunthu chabe

  • @FreddieNkhoma
    @FreddieNkhoma 22 วันที่ผ่านมา

    Amadziwa zomwe amanena nthawi imeneyooii lero atiichaani!!!!!

  • @PatrickCarol-xe2zb
    @PatrickCarol-xe2zb 2 หลายเดือนก่อน

    Dan lu ndi more fire 🔥

  • @titusmangazi
    @titusmangazi 3 หลายเดือนก่อน +1

    Mbuzi imeneyi ndiy okonda ndalama

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 3 หลายเดือนก่อน

    Malinga mmene zinthu zikuyendeela pano dl walakwisa kwambiri.nthawi zina ndibwino kukhala opanda mbali.

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 3 หลายเดือนก่อน +2

    Siufulu ena limagokhala dyela

  • @ChimzyWesley
    @ChimzyWesley 2 หลายเดือนก่อน

    JB tikumukonda ambiri bro Dan lu akagwele

  • @SparrowChawawa-g6g
    @SparrowChawawa-g6g 3 หลายเดือนก่อน +1

    Akùru Dan lu ndiiiooiiipa hvy

  • @Daniel-cf4tu
    @Daniel-cf4tu 3 หลายเดือนก่อน

    Eya anapanga bwino ndikumene akupeza thandizo zikankhala ndalezo sitimadyatu paja musaiwale

  • @AbrahamsMlelemba
    @AbrahamsMlelemba 3 หลายเดือนก่อน

    Kulibe zabwino anthuwa akufuna ndalama basi bravo jb

  • @CEE_DAT_NYENGO
    @CEE_DAT_NYENGO 3 หลายเดือนก่อน

    Za ndale sindipanga nawo 🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @LovemoreMandowa-m9y
    @LovemoreMandowa-m9y 3 หลายเดือนก่อน

    Wapanga csakho chopusa jb tien nae athilidwe maphuzo bas mwana opusa

  • @SaidAbian
    @SaidAbian 3 หลายเดือนก่อน

    Yikawina UDF apita kwa atupele😂😂😂😂

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi 3 หลายเดือนก่อน

    JB ndidolotu 🔥🔥🔥

  • @ianmzoche6447
    @ianmzoche6447 3 หลายเดือนก่อน

    Bravo Dan lu chipani ndichomwechi osati mbamva za DDP

  • @Destadentamo-n2p
    @Destadentamo-n2p 3 หลายเดือนก่อน

    Dan lu machende ake km maso ndi wosafinyidw😮

  • @JafaliChiwimbi
    @JafaliChiwimbi 3 หลายเดือนก่อน +3

    Ine ndikuti sanapange chisango chabwino cz iyeyo akuchemelela zinthu zoti sizikuchitka

  • @Marionphuxymw
    @Marionphuxymw 3 หลายเดือนก่อน

    Music is busness nkhan ndi dolla

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 3 หลายเดือนก่อน +1

    Eya anapanga moyenela ndiufuluwake

  • @CharlesMwambira
    @CharlesMwambira 2 หลายเดือนก่อน

    Sakuchiziwa chomwe akuchita kma azachiziwa thawi yikubwela

  • @MartinMoyo-g8f
    @MartinMoyo-g8f 3 หลายเดือนก่อน

    akuluwa akuyang,ana ndalama sakuchita xinthu mwanzelu coz akuonekaso kut ndiodanitsa kuganiza usanachite kumathandiza pochita chisankho ok

  • @FranquehenrinqueHenriquecalrit
    @FranquehenrinqueHenriquecalrit 3 หลายเดือนก่อน

    Ay km iye aluwona kt amalawi Ifé tikuvutika sanayenela ku má sekelela zopusazo

  • @EmilyNyirenda-n8d
    @EmilyNyirenda-n8d 3 หลายเดือนก่อน

    adalu ndiadyela cz ankasapota Dpp ndikumanyoza Mcp nde pot Dpp inaluza nde pano akuchemerera Mcp ndipomwe pa zusa mapir pachigwa cz ngat ingazaluzeso Mcp ndi kuwina Dpp azasinthaso nd kupit ku Dpp nde ndichifukwa anthu akumutuluka alibe chilimbikiso

  • @junasssabiwa1996
    @junasssabiwa1996 3 หลายเดือนก่อน

    Kachimutu tayakhulako za
    p diddy kapena English yimakupena?

  • @WumaruSaid-t2f
    @WumaruSaid-t2f 2 หลายเดือนก่อน

    Jeybi wapangabwino danlu ndichikabudula chopuzakwambili

  • @ApsChap
    @ApsChap 3 หลายเดือนก่อน

    Malvitha iwe .maganizo ako ngotani?

  • @Dayanschirwa
    @Dayanschirwa 27 วันที่ผ่านมา

    Sibwino kumene ukucopo kumanyeramo ai

  • @ElliasShaba
    @ElliasShaba 3 หลายเดือนก่อน

    Am Elias ndimafuna kunena zomwe wapanga Dan Luu sanapange bho coz azibare athu akufa ndinjara iye n,Kumati boma ndilomweri wayamba misara Uyo fack

  • @LazaloChioza
    @LazaloChioza 3 หลายเดือนก่อน

    Jb naweso mapwalaakoso patumbukoso chakwela boma ilooooooooo

  • @FysonKashon
    @FysonKashon 3 หลายเดือนก่อน +1

    ❤❤❤❤❤

  • @EDSONNAKULENGA
    @EDSONNAKULENGA 3 หลายเดือนก่อน

    Diosokoneza musiyeni mumuwona mateloake 2timoteyu 3:1 zoopa zowawa masikuosiliza

  • @ShadeKazota-z2j
    @ShadeKazota-z2j 3 หลายเดือนก่อน

    Naye ndi munthuu Ali ndi zisankho zake ndpo kuyimbaa kwakwe ndi business palibe vuto apa km kungot amalaw Ali ndi vuto

  • @MussaLenard-s2t
    @MussaLenard-s2t 3 หลายเดือนก่อน

    Nkhani ya Dora ndiyovuta kwambir

  • @MenasMarligo
    @MenasMarligo 3 หลายเดือนก่อน +1

    Azazindikira bwino pa songolo zomwe Dan lu akuchita Koma sakupusisa Malawi zikazamubwelera azaziwa choona chake Koma Dan lu ndiwa usiru❤

  • @FlorenceBanda-w5s
    @FlorenceBanda-w5s 3 หลายเดือนก่อน

    Kwachema 😂😂😂

  • @EuniseMasuku
    @EuniseMasuku 3 หลายเดือนก่อน +1

    Ndi ufulu wake

  • @LouisKanje
    @LouisKanje 17 วันที่ผ่านมา

    Wakwera yophulika

  • @PatrickCarol-xe2zb
    @PatrickCarol-xe2zb 2 หลายเดือนก่อน

    more Dan lu

  • @KondwaniBanda-ul8sj
    @KondwaniBanda-ul8sj 3 หลายเดือนก่อน

    Wawonetselatu kuti ndiwadyela amafuna komwe kukuyenda

  • @Ntatesibusisombata
    @Ntatesibusisombata 3 หลายเดือนก่อน

    Dan lu adatuluka dpp osati udf

  • @SaniJonathan
    @SaniJonathan 3 หลายเดือนก่อน

    Wachamba Dan Lu ine ndinamutuluka

  • @adeNuramo
    @adeNuramo 3 หลายเดือนก่อน

    Aliyese apange zomwe zamusangalasa bas

  • @evansphiri5951
    @evansphiri5951 3 หลายเดือนก่อน

    JB ndiodwala wamisala

  • @SparrowChawawa-g6g
    @SparrowChawawa-g6g 3 หลายเดือนก่อน

    Grezedia ndihuleee garu oiipa hvy

  • @BarnetGondwe
    @BarnetGondwe 3 หลายเดือนก่อน

    Nde kuti kumwela mumakakamizana zipani?

  • @Chilema-w5l
    @Chilema-w5l 8 วันที่ผ่านมา

    Chifukwa chake anakubera Black Box

  • @GiftYunusu
    @GiftYunusu 2 หลายเดือนก่อน

    Ndi chifukwatu amunyengela

  • @HaneefYusufSaeed
    @HaneefYusufSaeed 3 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂Ukweche

  • @ebinazielkandomo7803
    @ebinazielkandomo7803 2 หลายเดือนก่อน

    Palibe munthu angasankhire mzake chochita kuposa iye mwini.

  • @ShamdanAjangale
    @ShamdanAjangale 2 หลายเดือนก่อน

    Eya chifukwa chakuti siwakumangochi

  • @HopeeNaomi
    @HopeeNaomi 3 หลายเดือนก่อน

    Anapanga chisankho choipa ameneyo

  • @LAXYBRECKFire-o6g
    @LAXYBRECKFire-o6g 3 หลายเดือนก่อน

    Dan Lu Muthu simukugwila

  • @LazaloChioza
    @LazaloChioza 3 หลายเดือนก่อน

    Anakhoza boma ndilomweli vinavi vimaonga dziko lanthu komaso nimava chituko kunalibe

  • @GodfreChayamba
    @GodfreChayamba 4 วันที่ผ่านมา

    Umakwana bwana phpo

  • @Destadentamo-n2p
    @Destadentamo-n2p 3 หลายเดือนก่อน

    Dan lu ndi mapwara ake

  • @CarolChizimba
    @CarolChizimba 2 หลายเดือนก่อน

    Ai Sánayenera

  • @HopeeNaomi
    @HopeeNaomi 3 หลายเดือนก่อน

    Kwachema😮

  • @LeadChanza
    @LeadChanza 3 หลายเดือนก่อน

    Eya

  • @AntonSimony
    @AntonSimony 3 หลายเดือนก่อน

    siwabwino wapara pamenepo

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 3 หลายเดือนก่อน

    Jb more fire

  • @MercyTingo
    @MercyTingo 2 หลายเดือนก่อน

    Anapanga zomusangalasa yekha

  • @GreyJk-i1r
    @GreyJk-i1r 2 หลายเดือนก่อน

    Okay Mr mcp

  • @FelisterBenedicto
    @FelisterBenedicto 3 หลายเดือนก่อน

    Anachita kumugula ameneyo

  • @JackiriniIdeni
    @JackiriniIdeni 3 หลายเดือนก่อน

    Ndi galu dani lu timusamusa kumangochi