MUKAMVA TIMESTV YASEKEDWA MUSADABWE PROGRAM YAKE NDI YA HOTCURRENT YA DZULO ANG'ALURA MOSANYENGELERA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 24 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 134

  • @ChimsyUlemu
    @ChimsyUlemu วันที่ผ่านมา +16

    Well speaking men, chikangawa mwamuyankhula koma samamva za wanthu

  • @geofreydzinyemba6107
    @geofreydzinyemba6107 วันที่ผ่านมา +3

    Well done guys mumalankhula chilungamo keep it up

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka วันที่ผ่านมา +2

    Bravo Times TV continue kuyima pachilungamo

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 วันที่ผ่านมา +2

    It always pains me when we Chewa tribe are taken like fools or all mcp funs. Some Chewaz are exceptional. TTV big up!! Osagawa ma sweet no!! We need leaders who love our Malawi through right decisions and good governance.

  • @GraciumMdala
    @GraciumMdala 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    This was very much impressed n it may b well tanen as to concerned parties

  • @KeraMkandawire-pn5lx
    @KeraMkandawire-pn5lx วันที่ผ่านมา +2

    I can say bravo to the directors of security for both parties of MCP and DPP of what happened in Mzuzu, that was true exercise of a good Democracy. Let peace reigns this is nice. Zikhale choncho Ku madistrict onse especially South and Central regions Ma campaign akhale aufulu. Political tolerance a way to go.👏👏

  • @LehmanManere
    @LehmanManere วันที่ผ่านมา +4

    In that commission of enquiry you should also include some of Chikangawa villagers please anthu akumeneku Aliso ndimau komaso umboni wabwino

  • @shenwaahabdulhakim
    @shenwaahabdulhakim 2 วันที่ผ่านมา +11

    Ku mzuzu ose ndi a DPP awo mukuona ndi amodzi ena angopita ku mcp kufuna ndalama koma vote yawo ndiya Dpp

    • @frankkalambule
      @frankkalambule วันที่ผ่านมา

      Hmmmm ili nde bodza ili

    • @RuthBeyala
      @RuthBeyala วันที่ผ่านมา +1

      𝐞𝐲𝐚 𝐱𝐨𝐨𝐧𝐚 𝐚𝐥𝐨𝐧𝐝𝐚𝐤𝐨 𝐧𝐝𝐚𝐥𝐚𝐦𝐚

    • @AndrewKaira
      @AndrewKaira วันที่ผ่านมา

      Bola MCP DPP ayi tu kumpoto kuno

  • @JeanfatsanJere
    @JeanfatsanJere วันที่ผ่านมา +5

    Good idea times yendani mudziwe zoona ndazikonda❤

  • @MosesLeckson
    @MosesLeckson 2 วันที่ผ่านมา +4

    Ku Mzuzu kuli anthu ozindikira zimenezi ku Lilongwe sizingatheke and always pamakhala special team ya ziwawa so amadutsanawa zaziwawa sizimawakhudzudza.Alipo ma baunsa amene amayenda ndi zikwanje aja

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole วันที่ผ่านมา +3

    Kungong'alura zilungamo pwiiiiiiiiiii!

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma วันที่ผ่านมา +4

    guys yehova akusungeni pobisika mwaima pa chilungamo mokonda dziko lanu mosatengela mbali pitilizani

  • @williammandhlopa
    @williammandhlopa วันที่ผ่านมา +4

    North is special

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka วันที่ผ่านมา

    Congratulations 🎉 Northern region this is what we call democracy

  • @BersonChidziwe-yu9jb
    @BersonChidziwe-yu9jb วันที่ผ่านมา

    Nice speech with very good logic

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm วันที่ผ่านมา +11

    I could be much impressed if all sensitive positions in the country were approved by a parliamentary commission where all parties are involved .

    • @edgarlastone
      @edgarlastone 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      Exactly Malawi can change

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf วันที่ผ่านมา +10

    Kuyankhula kofunira zabwino dziko lanu, zikomo.

  • @mtenderemitembe3433
    @mtenderemitembe3433 วันที่ผ่านมา +3

    Amadanitsa anthu ndi ma politicians. Zinachitika ku mzuzu ndizabwino

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy วันที่ผ่านมา

    Powerful massage

  • @clementmondiwa2128
    @clementmondiwa2128 วันที่ผ่านมา

    Waiting for them in southwest and 😊😊

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka วันที่ผ่านมา

    Kachali is a gentleman ❤

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm วันที่ผ่านมา +2

    Pasakhale ndipo pasapezeke ntundu wa anthu ndi umodzi omwe odziona kuti ndiye oyenera kutsogolera dziko la Malawi .

  • @augustMag
    @augustMag 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pa ifa ya Saulos Chilima Ndi Anthu 8 kuchikangawa akuluakulu Inu mwandiuankhulira bwino kwambiri 🙏🙏🙏🙏

  • @BeautyMtambo
    @BeautyMtambo 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Makosanawa Ali ndi mulungu asawope mulungu alipo awamenyela nkondo ine ndili nawo limodzi awawa❤

  • @augustMag
    @augustMag 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Good job times Redio❤❤

  • @GodfreyKamphiripiri
    @GodfreyKamphiripiri วันที่ผ่านมา

    Nice speech ❤❤❤

  • @LastonThelele
    @LastonThelele วันที่ผ่านมา +2

    Ma top positions should not be appointed by the president but should be appointed through parliament like mec chairs, inspector genal , nrb chairs not by the president because president belongs to a certain political party.

  • @GreenBadani
    @GreenBadani วันที่ผ่านมา +2

    💓💓♥️♥️💪

  • @LangsonNyambalo
    @LangsonNyambalo วันที่ผ่านมา

    Gentlemen,khalani serious munkhanizi.Mwina chifukwa mulibe Brain.
    Mukuonjeza kutseka kwambiri.

  • @PollyLysonLutepo
    @PollyLysonLutepo วันที่ผ่านมา +1

    Tipex yili ndi zolinga ziwili.
    Kwa oipa kubera.
    Kwa olungama kukhozera pomwe paonongeka.
    Koma cholinga chenicheni ndi kukhodzera pomwe pa wonongeka.
    Pa nthawi yija anali kukodza momwe m'naonongeka

  • @HassaniKhenge
    @HassaniKhenge วันที่ผ่านมา +2

    ine ndi chewa koma mawu oti dziko ndilachewa nde mmm musasalalkhule wangokhala kuti mtsogoleli uyu ndi onyasa mtima ndipo sakukhalaso pampando

  • @EddieChan-hj2ql
    @EddieChan-hj2ql 2 วันที่ผ่านมา +3

    We can say mzuzu is the most civilized city.

    • @justinmalala-e4o
      @justinmalala-e4o 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Those people who look like mcp supporters are not mcp supporters. Mcp buys people to go to their rallies

  • @JanetMukaka
    @JanetMukaka วันที่ผ่านมา

    This men they are telling the truth

  • @SamuelBillon-i2f
    @SamuelBillon-i2f วันที่ผ่านมา

    Very good

  • @MikeSymon-si8dw
    @MikeSymon-si8dw วันที่ผ่านมา

    It was nice indeed yoooh..😊😊

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 วันที่ผ่านมา +1

    Ayitanise ndithu aaa asazembe

  • @SqueyaHosmane
    @SqueyaHosmane วันที่ผ่านมา

    Congratulations 🎉 wana wakukaya

  • @CathreenKadwala
    @CathreenKadwala 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Atseke Kaye MBC imanenaso zopepera, katsakulaso akunena mwano kumeneko

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Program ya lero ndi the best. Sikuona mbali

  • @JustinMpunga-c8b
    @JustinMpunga-c8b วันที่ผ่านมา +1

    Kmanso mmene mwayamikila ma supporters a MCP ndi DPP apangira liwudzeninso bola la MCP kuti kalembedwa ka ma ID zikhalenso chimodzmodzi ma boma onse mMalawi muno

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza วันที่ผ่านมา +1

    Amai aja ananena choncho chifukwa Mcp ndi imene imayambitsa za chiwembu ndinkona ananena kuti Mcp isadzapangitse ku phalombe

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w วันที่ผ่านมา

    Kodi zikutheka kubela masankho? Ndizowina tipex 2019 MRs jean assah Tipex

  • @CharyLand
    @CharyLand วันที่ผ่านมา +1

    Yah Kung,alula

  • @YusufChipojola
    @YusufChipojola วันที่ผ่านมา

    Kosdi zoti ndege idafika ku mzuzu amamvana ndichani kuti ndege izathele? Nanaga mawu amenewo ku control alipo ngati Mundege mudalibe box ,,,yaku control ilikuti sound

  • @TamaraSamidu
    @TamaraSamidu วันที่ผ่านมา

    👋👋 kuyakhula komatu uku

  • @frankiechasokoneza5802
    @frankiechasokoneza5802 วันที่ผ่านมา

    Mayi Yolamu akugwilitsidwa ntchito ndi Chakwera yemweyoi nothing can change as mcp they are commanding Malawi police to favour them

  • @BrendaDimba
    @BrendaDimba วันที่ผ่านมา

    Koma nde kung'aluratu no mantra times kip it up

  • @AboudujanahMawulidi
    @AboudujanahMawulidi 2 วันที่ผ่านมา +2

    Chigawo chapakati sangapamge zimenedzi kwanyawu kumene kuja zitsilu za anthu

    • @TrasizioMlupwa
      @TrasizioMlupwa วันที่ผ่านมา

      Ndipo sukunama,mbuli za anthu

  • @TaweniChavulaKamwendo
    @TaweniChavulaKamwendo วันที่ผ่านมา +1

    Kkkk Koma anthu Inu pulizi 😂😂😂😂😂😂

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer วันที่ผ่านมา +1

    Km kumalawi kuli ntchito eeeesh ai zikom

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 วันที่ผ่านมา

    Kuleza mtima kumeneko kumapezekadi kumpoto kokha ,chifukwa choti Democracy inabwera ndi munthu kumpoto amene anali Chakufwa Chihana,kumwera ndi pa Central regional zikanathera magazi ,sakanatha kudutsana bwino bwino

  • @winfordgondwe7231
    @winfordgondwe7231 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Amadziwa kuti awa ndi anzathu a DPP uku tikudyako kaye ndalama zaphwekazo 😅

  • @GerraldSolomon8
    @GerraldSolomon8 2 วันที่ผ่านมา +1

    Dpp yokhayokha iyi agendana bwanji awo akungopita kukatengako ndalama basi

  • @HamuzahBamusi
    @HamuzahBamusi 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ambuye chonde mukune muliko mupheni chakwera please Please ife ndakapolo anu please chakwera ntengeni chonde

  • @frankmanda639
    @frankmanda639 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Let's pray for the nation not to have blood she'd come 2025 elections

  • @MikeMwale-bw1xw
    @MikeMwale-bw1xw วันที่ผ่านมา

    Achita manyazi aDpp nthawi zonse kuyipaka mbiri zoipa MCP anthu akuonetsanitu.

  • @KONJEC-m8o
    @KONJEC-m8o วันที่ผ่านมา

    I think ikhale Dpp yomweyo zinazi ndizakupha, Kuba .chomwe tikudikira ife Peter akangolowa Ayesetse Anthu amenewa amangidwe basi

  • @edgarlastone
    @edgarlastone 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Apa tizavota chifukwa coz we are out of options koma MCP DPP zose ndi mbola

  • @francissimbani3241
    @francissimbani3241 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ndimkaona ngati times group ndi ya MCP komaa eeeeh! simmene kulili amwene

  • @Thokozanikawanga
    @Thokozanikawanga 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkhani izingokhala chikagawa ife tidzadya chingawa za ziii

  • @BeautyMtambo
    @BeautyMtambo 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndizoona zomwee mwalankula masapota atu pitilizani kalidweli Pali ena amawasokoneza masapotazi athu

  • @ecksonnjoloma8713
    @ecksonnjoloma8713 วันที่ผ่านมา

    Onsewa akuzavotera chipani chimodzi,alipo akudyeredwa apapa.akudziwana. sizingatheke kungodusana kumalawi kuno.kkkkkk ku mpoto kuli atambwari😂

  • @PatrickMailos-j6u
    @PatrickMailos-j6u วันที่ผ่านมา

    Kwathukuno kummwela sitingalole Kuti MCP tidusane ndimagazi amenewo

  • @HamuzahBamusi
    @HamuzahBamusi 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndege yopanda battery kkkkkkk koma achakwera ai zikomo ambuye pomulenga chikangawayuu

  • @MacdonsonBeza
    @MacdonsonBeza 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pamene akudusanapo ndi pa Ekwendeni po pamo pa nya Hara

  • @GRACEKUMWEMBE-rv2se
    @GRACEKUMWEMBE-rv2se 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tafufuzanidi kuti zomwe anthu akunena za nrb nzoona chifukwa kukana kuvotela I'd atha kukhala ndi zolinga Zina ndipo awona kuti zilepheleka ndi nkhani ya id.

  • @MercyDzonzi
    @MercyDzonzi วันที่ผ่านมา

    Mmmh mukudziwa zomwe akuchita kuseriku awa asakupusitseni ndithu 😂

  • @rashidpoul502
    @rashidpoul502 วันที่ผ่านมา

    Enafe tinapitila kukapeza 2 pin yandiwo koma ife tikavotela dpp

  • @AratonManda
    @AratonManda วันที่ผ่านมา

    Ndikuona ngati malamulo adziko amakhwila tchito kumpoto kokha, chifukwa chake mmaboma Ena ake kumakhala chikulilano

  • @Allan-bk1
    @Allan-bk1 วันที่ผ่านมา +4

    😂😂😂😂😂 guys mwathira nchenga mumpunga wagulu

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole วันที่ผ่านมา +1

      Apapa sungadyeke olo kumezanso ayi😂😂🎉

    • @Allan-bk1
      @Allan-bk1 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@SolomonNjolomole 🤣🤣🤣🤣🤣

  • @CassimTwaliebuMdeleman
    @CassimTwaliebuMdeleman 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Sangaiseke times ife tikufuna zithu zisithe mcp ipakile tatopa nayo yatikwana ndi manyakala awa

  • @ShaibuSmart
    @ShaibuSmart วันที่ผ่านมา +1

    Northern Region ndi anthu ozindikira sapanganawo zopepera

    • @justinmalala-e4o
      @justinmalala-e4o 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Anthu omwe akuoneka ngati ndi a mcp si a mcp. Mcp ikumachita kugula anthu opita kumisonkhano kwawo

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs วันที่ผ่านมา

    Umu nde asambwazadi

  • @MeniyaMikaya
    @MeniyaMikaya วันที่ผ่านมา +1

    Ndinu amanyi nosenu kuli pitala kunalibe nkhaza ? Ndinu zitsilu kwambili mcp singapange naw zaugogo ai

    • @MiracleDamiano
      @MiracleDamiano วันที่ผ่านมา

      Hahaha 😅😅😅 yabayatu mwana wa njoka iwe ndye uphulika chfukwa simunat achikangawa party tikukhwekhwezani asatana inu

    • @giftmabuka3589
      @giftmabuka3589 วันที่ผ่านมา

      Chikangawa ichooo😅😅😅

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi วันที่ผ่านมา

    Ine ndimawayamika anthu aku north amakondana

  • @GuejendraMk
    @GuejendraMk วันที่ผ่านมา

    Zmukamanyoza mudziyamba kuon kut chatsitsa dzaye nchani kut njobvu ithyoke nyanga. Shhaaaaa abale

  • @HedgensChisale-n4b
    @HedgensChisale-n4b วันที่ผ่านมา

    Week ya mawa abishop azakhaleposo

  • @RichardChirwa-em6qj
    @RichardChirwa-em6qj วันที่ผ่านมา

    Chiripo akubisa anthu akuphawa anapha chilima ndi anzake

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi วันที่ผ่านมา

    Kumpoto amantha

  • @MatthewsLex
    @MatthewsLex 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Naa ya gomboi nde iwamalzad abomawa

  • @AndrewChawinga-t1v
    @AndrewChawinga-t1v วันที่ผ่านมา

    Ndazikonda kwambili zimenez

  • @MikeMwale-bw1xw
    @MikeMwale-bw1xw วันที่ผ่านมา

    Kumpoto kuli anthu ozindikila kuti ndale zisawadanitse.

  • @Peter-yz8tm
    @Peter-yz8tm วันที่ผ่านมา

    Dpp ndidye obera zisankho. Only dpp and their team b utm amakamba za chiavhine.

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz วันที่ผ่านมา

    Kodi imu mesa a ndevu zamwayi milati simutenga information ya social media mde za kumangidwa kwa mtambo munazitenga kuti? Inuyo mukudziwa kuti imali plan ya mvp yomwe imafuna kuipitsa mbiri ya dpp bwanji simukunena?

  • @ClementsKamanga
    @ClementsKamanga 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ae mcp mwawaphumzitsa chikhalidwe

  • @FloraBanda-w7t
    @FloraBanda-w7t วันที่ผ่านมา

    Kod a bishop aja sadzabweraso ??ine amandsangalasa akamang'alula 😂

  • @corretabanda7685
    @corretabanda7685 วันที่ผ่านมา +1

    If the government wanted a fair and transparent election they could have reappointed Mr Chifundo Kachali because he did the last election religiously. But because the current government is aware that they can not win without kubela that's a Ntalimanja was appointed.

  • @donbastora854
    @donbastora854 วันที่ผ่านมา

    Ife si akumwera okonda ziwawa kapena a pakati

  • @YusufChipojola
    @YusufChipojola วันที่ผ่านมา

    Kodi ukakwarila azimayi awili akadwala mozi kumawula ungapitise mzakeyo ?

  • @MercyDzonzi
    @MercyDzonzi วันที่ผ่านมา

    Koma akumanyegererabetu kuwatengera ku china kodi tiwakhulupilire bwanji anyamata wa

  • @AlickJam
    @AlickJam วันที่ผ่านมา

    Anyamatawa mpaka uniform ku ntchito

  • @rashidpoul502
    @rashidpoul502 วันที่ผ่านมา

    Kuyankhula kopusa achewa zikoli ndamene amaliwonga

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chomwe anthu angaziwe ndi chakuti anthu omwe amaoneka ngati a mcp si a mcp. MCP ikumachita kugula anthu opita kumisonkhano kwawo

  • @MasterMwandira-d3k
    @MasterMwandira-d3k วันที่ผ่านมา

    This is northern region, it'll never happen in central and southern region

    • @rodglae6657
      @rodglae6657 วันที่ผ่านมา

      Tisayiwale koma kuti Chakwera was attacked in Mzuzu pa Katoto pompo when MCP was an opposition party. Ku Karonga was almost a no go zone area mpaka was nicknamed Bengazi for its terror nthawi ya DPP. Ndiye Northern Region is not as a holy region as is being speculated.

  • @PatriciaChiwerenga
    @PatriciaChiwerenga วันที่ผ่านมา

    Mpaka ena ayedzedwe 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @FadwukeAfoso
    @FadwukeAfoso วันที่ผ่านมา

    Boma sitikusintha mwayambakale kulira

  • @Thokozanikawanga
    @Thokozanikawanga 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Awa a dpp akudziwa kuti sangawine boma lidawakanika umbuli basi

  • @FrankMsiska-i9j
    @FrankMsiska-i9j วันที่ผ่านมา

    Anthu a kumpoto ndiozindikira

  • @AndrewChawinga-t1v
    @AndrewChawinga-t1v วันที่ผ่านมา

    Ku mpoto kuli anthu abwino okha okhatu

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm วันที่ผ่านมา

    Kusekedwa ndi kutsekedwa ndi zinthu ziwiri zosiyana .