AMAYI OMWE ANALI CLOSE FRIEND WA CHILIMA ALIMBA MTIMA NDIPO ABWERA POYERA NDIKUMUSAMBWANZA CHAKWERA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 243

  • @LezinaBanda
    @LezinaBanda หลายเดือนก่อน +2

    Ulemu wanu mama,,, zimayi olimba mtima ngati inu nsinamuone

  • @BrightonNdalama-x2b
    @BrightonNdalama-x2b 3 หลายเดือนก่อน +5

    Well spoken mama and we understand every single point of ur message and keep it up you're opening our brains

  • @LukasBamus
    @LukasBamus 3 หลายเดือนก่อน +6

    Always on my mind uncle God bless you wisely and continue to reviled more sicrets in this world

  • @jameslifah7909
    @jameslifah7909 2 หลายเดือนก่อน +5

    Strong woman ever,you stand by the truth. Let love lead❤

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 2 หลายเดือนก่อน +6

    I salute you aunt
    The TRUTH eish

  • @LindaMalunjika
    @LindaMalunjika 3 หลายเดือนก่อน +14

    U are right zimene wanena.....anakakhala kuti ndi iweoyo chimwendo unali mu ✈️ ndi anthu ena Chilima anakakhala okathandiza anakakhala SKC.....why coz anali ndi umunthu....ndeeee who did ever did tha to Chilima ili ndi dziko ndipo limatembenuka

    • @HalimaMussa-j6t
      @HalimaMussa-j6t หลายเดือนก่อน

      Mulungu sachedwa azawaika poyela dziko lizadziwa

  • @MercyChimaliro-fi6mv
    @MercyChimaliro-fi6mv 3 หลายเดือนก่อน +8

    Well spoken Aunt ❤️ 💗

  • @howellbandah8211
    @howellbandah8211 2 หลายเดือนก่อน +3

    Be protected ur a blessing mama not just to the Malawian but to whole world ❤

  • @AllanTamula
    @AllanTamula 3 หลายเดือนก่อน +4

    Your comments towards Malawi politics is just great.

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 3 หลายเดือนก่อน +5

    Good message Mayi Chimwendo ndiwakupha ndi Chakwela

  • @EllenKUMWENDA-b2z
    @EllenKUMWENDA-b2z 2 หลายเดือนก่อน +3

    I kove the spirit u hv mamie.Malawi shld hv more ladies like u....💪💪💪

    • @ReyonAndrewBanda
      @ReyonAndrewBanda 2 หลายเดือนก่อน

      She is not in malawi remember.

  • @BrightKuyaka
    @BrightKuyaka 2 หลายเดือนก่อน +2

    Chemwali ndinkanyalanyaza zainu koma ndayamba kukumvetsani, more fire big woman

  • @SpencerKadewere-cd5ok
    @SpencerKadewere-cd5ok 2 หลายเดือนก่อน +2

    You deserve respect mumm continue fighting for the truth until these crocodiles🐊🐊🐊 repent there seens

  • @JosephGama-v7r
    @JosephGama-v7r 2 หลายเดือนก่อน +3

    Mama you are a true freedom fighter

  • @PatriciaTikhiwa
    @PatriciaTikhiwa 3 หลายเดือนก่อน +7

    Ndipo zoona chilima eishiiii ngt zabodza ndege hooooo zosaveseseka😊

  • @WelemuSayizi
    @WelemuSayizi 3 หลายเดือนก่อน +11

    Koma azimayi ngati amenewa ndi mwana wathu koma Malawi ndi yodala mayi uyu ngakhale azibambo 10 muli mu mcp simungafanane naye iron lady more fire!!!

  • @DuncanRashid
    @DuncanRashid 3 หลายเดือนก่อน +6

    I respect you mom good words

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 3 หลายเดือนก่อน +10

    Auzeni mai akuona ngati a Malawi ndi mbuli sitimaziwa kanthu never

  • @danielswaleyi9776
    @danielswaleyi9776 หลายเดือนก่อน

    Well articulated, I have learned slot from you sis.

  • @MascotAnderson
    @MascotAnderson 2 หลายเดือนก่อน +5

    Mulungu abwerese chilungamo pankhaniyi ndipo yehova musalore kt oipayo awine nkhondoyi

  • @RoseChimbwefu
    @RoseChimbwefu 3 หลายเดือนก่อน +3

    Well done mayi awuze chilungamo awa ave

  • @Peter-yz8tm
    @Peter-yz8tm 3 หลายเดือนก่อน +5

    Good lecture. Ine mkazi wanga anamwalira ku queens because anamicheka matumbo pomipanga operation. Bingu saulos pamodzi ndi mkazi wanga akukambirana konko. Kuwani mmene mungathere za olemera izi. Mkazi wanga anakambako palibe....

  • @PatumaCassimu
    @PatumaCassimu 2 หลายเดือนก่อน +3

    Perfect said👍🔥🔥

  • @LekelenSuwale
    @LekelenSuwale 2 หลายเดือนก่อน

    Well spoken Mom, you deserve respect and I admire you more than ever teach us Mom

  • @JaneMhango-zl6pt
    @JaneMhango-zl6pt 2 หลายเดือนก่อน +2

    Achakwera akudziwapo kanthu pa imfa ya a Biyeni. Mulungu alowelerepo ndithu. Komanso chilungamo chidzawonekele ndithiludi.

  • @giftkanjuchi-qm8hf
    @giftkanjuchi-qm8hf 2 หลายเดือนก่อน +1

    It is making sense mama ndinu di achipatala

  • @pacharokoloviko1694
    @pacharokoloviko1694 3 หลายเดือนก่อน +1

    Big up mama, please tayakhuleni madam Mary ngati nkotheka achitsogolere chipan i

  • @ThomasBlessings-j8k
    @ThomasBlessings-j8k 3 หลายเดือนก่อน +6

    Ineyo kwanga nkupempha amalawi ozindikila Kuti 2025 chikangawa asazakhale m'boma chifukwa kukhala NDI asogoleli ofanana ndi uyu ndekuti tonse tizaphedwa

  • @brendachirwa-u2q
    @brendachirwa-u2q 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zoona kwambr BN anali wochita zimthu moganizira anthu. Thanks

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson 3 หลายเดือนก่อน +1

    Keep doing good work yourselfless be blessed.

  • @FelistasNkasalaMakumbo
    @FelistasNkasalaMakumbo 3 หลายเดือนก่อน +1

    Love you mama mumatiyimirira❤❤❤❤❤

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 หลายเดือนก่อน

    Point of Correction Sisy Mtambo sanachite kuchoka yekha mboma anachita kumuchotsa.

  • @GerladMakayika-on5rt
    @GerladMakayika-on5rt 3 หลายเดือนก่อน +15

    Just point of collection, that was not an accident it was planned for him to go sothat they'll rule again

    • @alexanderduncan9000
      @alexanderduncan9000 2 หลายเดือนก่อน

      Reality talk

    • @LuwizaChika
      @LuwizaChika หลายเดือนก่อน

      Ndipo khaniyo ndiyona mamie sukunama ambuye akupasen moyo wautali mwayakhula chilungamo

  • @FebbieNjewa-g3k
    @FebbieNjewa-g3k 3 หลายเดือนก่อน

    Sure sure Abiti tell them ,,God bless yu more

  • @MosesKamtndo
    @MosesKamtndo 3 หลายเดือนก่อน

    People like this woman must be abandant, keep it up mama

  • @HajiAslam-nd9xq
    @HajiAslam-nd9xq 2 หลายเดือนก่อน

    Big up Mai mukhalise inuyo 💯💯💯💯

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 หลายเดือนก่อน +1

    Another example is Kondwani Nankumwa who was expelled from DPP but alive but MCP will never leave you alive

  • @JamiluSunday
    @JamiluSunday 2 หลายเดือนก่อน

    ❤❤❤ ulemu wanu mama

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 3 หลายเดือนก่อน +2

    Oh yes a woman of truth

  • @NickUpoche
    @NickUpoche 3 หลายเดือนก่อน

    Keep it up mm,proud of u

  • @QueenMoses-c1n
    @QueenMoses-c1n 3 หลายเดือนก่อน

    Big up mama u really encourage us

  • @EmmanuelDanitsa
    @EmmanuelDanitsa 3 หลายเดือนก่อน

    Great message Moom..

  • @ThomasNChinseu
    @ThomasNChinseu 3 หลายเดือนก่อน +1

    Nice touching to u nurse in USA keep it up

  • @RidgieGondwe
    @RidgieGondwe หลายเดือนก่อน

    Well done mamie

  • @ÑaloWemba
    @ÑaloWemba หลายเดือนก่อน

    Wow 😮 chilungamo ichi

  • @KhumboNyerenda
    @KhumboNyerenda 2 หลายเดือนก่อน

    Good message mum

  • @UfuluManondo
    @UfuluManondo 2 หลายเดือนก่อน

    I silute you dear mommy mwaima pachilungamo,ambuye abise Moyo wanu pomwe a mcp isauone❤

  • @EliasManthenga
    @EliasManthenga 2 หลายเดือนก่อน

    Mummy mukazafika ku South Africa zandizwsen tizadye kota limozi, kuima pa chilungamo amalawi aziwe ❤

  • @geeman-p9d
    @geeman-p9d หลายเดือนก่อน

    Abiti mukunena zoona tonse tikudziwa zoti Saulos anaphedwa. Anali ndi ntchito yabwino osati ku chipiku. Tikulirabe ndipo tidzalira mpaka kalekale. Anali wa ndale nde tikukambanso za ndale apapa. Mwayankhula bwino abiti zikomo

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 3 หลายเดือนก่อน +1

    Wise woman.

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 3 หลายเดือนก่อน +6

    Chimwendo banda chakwera kunkuyu namajekete wankulu wa army manganya athu amenewa ndi amene anapha athu onse 9 aja koma thawi yawo yatha sopano mcp yamagazi crocodile 🐊

  • @TITANIMATOLA
    @TITANIMATOLA หลายเดือนก่อน

    True mama osaopa osafooka

  • @solomonkasiya6904
    @solomonkasiya6904 2 หลายเดือนก่อน

    Lankhulan Mai mumatiimilira❤

  • @CHAPITASINGINI
    @CHAPITASINGINI 3 หลายเดือนก่อน +1

    Mwayakhula ndikwanga komwe cct eeeeh moyo kuwawa kwambiri

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 3 หลายเดือนก่อน +4

    Ku MCP amaphana polimbilana udindo. Chakwela anamupha chilima chifukwa amapingidwa kuti aimenso 2025

  • @ChimwemweJoelKajawo
    @ChimwemweJoelKajawo หลายเดือนก่อน

    🤣🤣🤣🤣 Koma ndi osekesa kwambiri apa Pali cha nzeru chilichonse chomwe munthuyu wayankhula, even izizi sizikupeleka evidence or proof yoti munthu anaphedwa kapena Kuti inali movie

  • @jameswajumpha6790
    @jameswajumpha6790 3 หลายเดือนก่อน

    Dan Lu naye imukhuze nkhani iyi kulondola kosekose athu osakhazikika😂😂😂😂

  • @IvanRoux-vl8gu
    @IvanRoux-vl8gu 2 หลายเดือนก่อน +1

    That's true negligence

  • @ChimwemweMuhelliwah
    @ChimwemweMuhelliwah 2 หลายเดือนก่อน

    Anthuwa kupemphera kwawo mkwabodza...minbulu pakati pankhosa...olo nkhope zawo zimawoeka kt ndi anthu oipa ..fiti zopemphera...

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 3 หลายเดือนก่อน +2

    Bravo Chemwali

  • @LuciousChikopah
    @LuciousChikopah หลายเดือนก่อน

    Bravo mama

  • @JosephBanda-ox5rw
    @JosephBanda-ox5rw 3 หลายเดือนก่อน

    Number one Bola asakupheeee

  • @atupelemposa4786
    @atupelemposa4786 3 หลายเดือนก่อน +1

    Sanamukondepo chilima ,they just use him to remove DPP,
    Munthu woti ukumukonda or atadwala umathamangila nayo ku chipatala .

  • @DanielGeorge-l4h
    @DanielGeorge-l4h 3 หลายเดือนก่อน

    May Allah bless you mom eish

  • @FRANKBEULA
    @FRANKBEULA 3 หลายเดือนก่อน +2

    Mai iweo usazamfe umakwana ndipo ukunena zooona

  • @AginesWailes
    @AginesWailes 3 หลายเดือนก่อน +2

    Ndipo pakhare misaaa yot ikachitikire pachikangawa pompooo

  • @GlynLumbe
    @GlynLumbe 2 หลายเดือนก่อน +1

    Muti ineyo Ku Namwera Ndiye kwathu kumudzi kumachemba MOTi timatsikila galimoto pa chesailesi kumapita ku machemba tiyakhulileni Kwa Anthu wathu osowa chikondi wa kuno

  • @gearardphiri6904
    @gearardphiri6904 3 หลายเดือนก่อน +1

    Thanks my sister

  • @gladysmanthimba7851
    @gladysmanthimba7851 2 หลายเดือนก่อน

    Abiti ndinu fire. Mau opanda chigamba. Zikomo kwambiri tili nanu limodzi

  • @MikeMtunduwatha
    @MikeMtunduwatha หลายเดือนก่อน +1

    Zoonazake zimenetikudziwa

  • @AnniePetro
    @AnniePetro 2 หลายเดือนก่อน +1

    Chilungamo mama

  • @franciscomalola92
    @franciscomalola92 2 หลายเดือนก่อน

    aunt sizobisa apa anachita kumupha ndipo umboni ulipo pamene panagwera ndege simalo oti munthu angasake kwa 1 hour ayi ,,

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 3 หลายเดือนก่อน

    Yes timukamba kumene anafa imfa yowawa SKC ndi ena wonse aja ulemu wanu mama

  • @JoyceZimba-pc4du
    @JoyceZimba-pc4du 2 หลายเดือนก่อน

    Good point mama

  • @WakisaNjeghenje-i2n
    @WakisaNjeghenje-i2n 3 หลายเดือนก่อน

    Ndizoona mama❤❤❤❤

  • @dewasicmalunga3374
    @dewasicmalunga3374 2 หลายเดือนก่อน

    I salute you kusyeto wakumangwetu

  • @IvanRoux-vl8gu
    @IvanRoux-vl8gu 3 หลายเดือนก่อน +1

    Thats true Mam

  • @GlynLumbe
    @GlynLumbe 2 หลายเดือนก่อน

    Mama takumvani ndi zoona zake ndipo ku Malawi kuno tikuliladi une so mwanache njenu

  • @Halima-i4x
    @Halima-i4x 3 หลายเดือนก่อน +1

    Zoona mama osaposa 🙏🙏🙏💪💪💪

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa 3 หลายเดือนก่อน +2

    Point point anamumpha chakwela ndi fit anthuwa a MCP

  • @HendrixBrave
    @HendrixBrave 2 หลายเดือนก่อน

    Eeeeeeeeeeeeh Koma yaaaaa ine ndili pheeeeee ena kuseliku akungosegura mmimba

  • @AlexanderKamanga-i2l
    @AlexanderKamanga-i2l 2 หลายเดือนก่อน +1

    Chakwela ndi mbuzi

  • @PercyRoos
    @PercyRoos หลายเดือนก่อน

    That is true mamma

  • @EssauChimpango
    @EssauChimpango หลายเดือนก่อน

    Truth being told

  • @IvanRoux-vl8gu
    @IvanRoux-vl8gu 3 หลายเดือนก่อน

    True ma
    Mamu God be fi

  • @CarolynBandA-bb6cn
    @CarolynBandA-bb6cn 2 หลายเดือนก่อน +1

    True❤

  • @PeterMlowoka
    @PeterMlowoka 2 หลายเดือนก่อน

    Iyayi apa palimbetso zoti bwanji iyi inali plan yao same size Thambani akunga kuti Amalawk ndife opusa ,ifa imakhala ndi malonji

  • @wonganimwase9881
    @wonganimwase9881 หลายเดือนก่อน

    Even if a child is late coming from school, the parents don't wait for an hour to atart searching,, talk less of saying that the search will resume the next day. Every flight has a manifest and a whole pesident couldn't didnt have the correct list of passengers on the plane.

  • @BadwinvanboyMkandawire
    @BadwinvanboyMkandawire 2 หลายเดือนก่อน

    Is true for that

  • @evangelistjacobmithi5061
    @evangelistjacobmithi5061 หลายเดือนก่อน

    Ndinenese pano kuti aliyense okupha or opanga tchimo ngati sanalape sazapeza MTENDERE pokhapokha alapa.

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani 3 หลายเดือนก่อน +1

    Mmmmm mzoopsaaaa zinachitika zija, anthu analimba mtima 9 people mmmmm

  • @MarthaChikandira-yr1ye
    @MarthaChikandira-yr1ye หลายเดือนก่อน

    How can a download this video please

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 3 หลายเดือนก่อน

    Kkkk aaaa za azimayidi ndithu kkkk

  • @Halima-i4x
    @Halima-i4x 3 หลายเดือนก่อน +2

    MCP ndichiman chakupha chifukwa chilowelen MCP boma onan Malawi anthu mene akumwalilila eeeee chakwela akuononga dziko labwino bwino ndi 2 😢😢😢 koma one day is one day

  • @HajiraMustapher
    @HajiraMustapher 3 หลายเดือนก่อน +1

    Chimwendo,chakwera,kumkuyu,zikhale nonse tsiku ili lidzakupedzani mufune musadune

  • @cynthiandekhakatundu6890
    @cynthiandekhakatundu6890 3 หลายเดือนก่อน

    Ndipo kambani Mamie anthu awa anatipweteka ...

  • @YusufGafa-s3j
    @YusufGafa-s3j หลายเดือนก่อน

    Black box inasowa bwanji mundenge ngati inali ngozi chabe eeeee koma a MCP inu mmmmm only God knows

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 3 หลายเดือนก่อน +3

    Auzeni mayi achimwendo ndi chitsilu chopusa

  • @montfortwoka2896
    @montfortwoka2896 3 หลายเดือนก่อน

    Ndipo osamaika mau akuti mwina akanakhala ali moyo akanapita mwachangu ayi answer ndiyakuti anachita kupha awa anthu oipa kwambili tichotsa oipa onse next year ino . SKC anali president wanga.

  • @YammsyZebron
    @YammsyZebron 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo onse anapanga izi apenge