For any sober-minded person, the following questions should ring in his head about Usi and UTM about the heading here. Number 1, why now? why is Usi more UTM today after 4 years when Chilima and UTM were being tormented and painted crooks by their partner? 2. Why not explain why he publicly declared that he would stand as an independent MP in Chilimba yet he was UTM and that was even before Chilimas death? 3. Why has he not made a single speech as UTM president on UTM direction, plans, and vision for UTM as Chilima used to do for the party so that UTM members are informed. 4. If he is UTM leader, bwanji sakutuluka nkuwauza otsatila za mmene chipani cha UTM ndi MCP akukhalira after it was announced that the alliance is over? 5. Whom is he working for, he is more Malawi Vp than UTM President that is why UTM members are not happy. 6 Chihana works and speaks for his party, Chakwera works and speaks for his party, JB works and speaks for his party more so Nankhumwa and APM, they both speak for their party, nanga DR Usi works and speaks for who as president? The guy is a chameleon no wonder UTM members do not want him.
"Why now" mumafuna akhale president wachipani Chilima adakali ndi moyo? Funso limenelo should be directed to Kabambe fukwa sanali even member wa utm angofuna kukolora asanalime.
The vice President of the Republic of Malawi 🇲🇼 Dr.Micheal Bisiwick Usi . He is a man of wisdom, a man of Intergrity, a man who knows what he must do at the right time on the right place. He has no power hungry but assisting the Malawi 🇲🇼 National and development in our country. He must be blessed and his family.
Kodi ndalama zimenezi bwanji sizimapezeka a Chilima anenedwawo akali moyo? A Chilima amakhala ngati ali pa corner tu koma a Usi akuoneka kuti akuyenda mukuboolezatu
Ndiye lero bwanji mukuyankhula Za UTM kumbuyoku mumati mukuyendera ntchito ya boma ndiye simungavale Za UTM or kuyankhula Za UTM mutu wako sukugwila now time yatha manganya
😂😂😂😂😂😂 These women do not seem to understand what Usi is saying. He's telling them that he's nothing to do with party cloth decorations and they celebrate about it. Eeeeish!
Azimai A Mcp awa akungovala makaka a UTM musatinamidze iwe Mbuzi Maiko usi Chilima akome lero galu iwe ngongoledzo mukupeleka pano cholinga chovura mavoti wekupha iwe Mr Chikangawa 2 osakapeleka chakudya ku machinga anthu akufa ndi njala
Kwa ine usi si wa UTM and has never been he is just a traitor send to by the enemy chilima anazunzika iyeyu ali mbali ya adani kumwa mkudyelera awawa nga mcp
Inu mukufuna mpaka UTM intheeeee mpaka ndipo ndizamanyazi ossnyoza munthu kumeneko sikulila maliro achilima Ai koma kupasula chipani ndipo anthu ayamba kale kuti chipani cha UTM chintha ndinthu koma inu ndizoona zimenezo mpaka UTM intheeeee ndinthu koma guys ganizani bwino
For any sober-minded person, the following questions should ring in his head about Usi and UTM about the heading here. Number 1, why now? why is Usi more UTM today after 4 years when Chilima and UTM were being tormented and painted crooks by their partner? 2. Why not explain why he publicly declared that he would stand as an independent MP in Chilimba yet he was UTM and that was even before Chilimas death? 3. Why has he not made a single speech as UTM president on UTM direction, plans, and vision for UTM as Chilima used to do for the party so that UTM members are informed. 4. If he is UTM leader, bwanji sakutuluka nkuwauza otsatila za mmene chipani cha UTM ndi MCP akukhalira after it was announced that the alliance is over? 5. Whom is he working for, he is more Malawi Vp than UTM President that is why UTM members are not happy. 6 Chihana works and speaks for his party, Chakwera works and speaks for his party, JB works and speaks for his party more so Nankhumwa and APM, they both speak for their party, nanga DR Usi works and speaks for who as president? The guy is a chameleon no wonder UTM members do not want him.
"Why now" mumafuna akhale president wachipani Chilima adakali ndi moyo? Funso limenelo should be directed to Kabambe fukwa sanali even member wa utm angofuna kukolora asanalime.
EXACTLY, why NOW??
Ndi mbuzi yamunthu iyi
Mbuzi yamunthu iyi
Chizeleza chindere tiye waka uko
Thanks Mr Michael usi pomakhala mukukumbukira kuti umphawi sizinthu tiyamike mulengi poti wakuchosani kuumphawi kukuikani pamenepo kuti muthandize osauka muli ndi ntima wabwino muthandiza Malawi ndikuziwa ine
Tiganizireni a vice president
@@ImmanuelMatsimbe iwe usi ndiwandalama kuyambila kale
Anali country director wa adra simunthu wamba usi
Komatu ng'oma yolilitsa sicedwa kung"ambika tiyeni tizingoyang'ani,,God z watcing everything
Mwalakhula kwambili bwana khalan pasi chifukwa siyinu koma chilima chifukwa chilichose ndi chilima yiweyo ndiye tsogolo pa malawi ❤❤❤
Utenge ndalamazo za niifi zina mwa izo ukagule chakudya ukapeleke ku Machinga anthu akudya chiteze
Mulungu akudalitseni a vice president pa ndalama mwamupatsa mwanayo, mukhale ndimoyo wautali🙏🙏
The vice President of the Republic of Malawi 🇲🇼
Dr.Micheal Bisiwick Usi .
He is a man of wisdom, a man of Intergrity, a man who knows what he must do at the right time on the right place.
He has no power hungry but assisting the Malawi 🇲🇼 National and development in our country.
He must be blessed and his family.
Chitsiru Ichi cha munthu kungowakokola azimayi azikhala Ngati a UTM
Mulungu akulange Galu iwe
Komanso usiye kugwiritsa ntchito dzina la Chilima R.I.P. pomwe unamupha nawo munthuyo
Akulange ndipo akulange
Thanks so much Mr VP
Chomwe tikuziwa ndiwe yudasi Iskariot ndiamene wapeleka nzako kamba ka udindo
Very good speech VP
🎉Mwayankhula a bwana❤
Koma kumwamba ku kuli mulungu,,,koma ngati alipo amulange usi
Amulange watani Usi, aaaaa ndale tiziyike pambali a Malawi 🇲🇼 zomwe akulankhula apa ndizolimnikisa ,kumanga mtundu wa Amalawi
Mwayi wake Mulungu sayendera maganizo amunthu
Kuyakhula ngt mwaseka mphunotu
Usatana basi Mulunguyo alange iweyo, fukwa usi sanalakwe kanthu
Akulange iweyo?
mulungu kuphatikiza ndizopusazi zovetsa chisoni😪😪😪😪
Ndipodi aliyense amafuna kusangalala🙌🙌
Mr vp speaking is your inborn talent processed
Azimai ngat nawo achite backflip ..😂😂..100k yabaya
Wasala ndi mwezi umodzi mchipani cha utm after 17 november uzikapitilizira zakozo ku mcp
Manganya, you are a friend indeed. I like your talking, you think so much like me
God will forever allow justice to flow like a river .. those who are judging any kinda situation will remain like that forever😪
Anzanga amene mwanvala akuti bwanji ineyo afitsi awa ndikamanva mau awo ndikhoza kuyambapo bp
This guy is the choosen1 .... whatever he's saying here is to develop our country
Awatu mutu wawo sugwila zawo uja anapeleka ndiyeyi atafa muja sanayakhulepo kalikonse pa 10 June anali ndi meeting yachisisi ndi chakwera amafuna udindo ameneyi
Muthu oyipa kwambili iwe usi, ndikakuona ngati ndiye wazelu km ndiye mbuzi yamuthu, dikila apangile kampeni agalu a MCP uwone azakusoweseso ngati chilima tikuonela
Akulira 😂😂😂😂😂😂
Zaziiii Inu mwatembeeleledwa heavy
Kodi ndalama zimenezi bwanji sizimapezeka a Chilima anenedwawo akali moyo? A Chilima amakhala ngati ali pa corner tu koma a Usi akuoneka kuti akuyenda mukuboolezatu
Malawi osokonekela,munthu akuti simuzaona nkhope yanga ilipasalu kotero yachilima izapitilila kukhalapo 😂😂 chosecho akuziwilatu kt nkhope yake sizingatheke kuikapo mkumene anthu mkumanyadila 😂😂 umphawi sizinthu.
Ndipo inu bwampini weni weni
yudas yambachako chipani ndiwe galu
Mbuzi iyi ngati iwe umamulemekeza bwanji inu munadutsa pa chikangawa osapeleka ulemu bwanji
Usagulitse utm ku mcp ubare udathapo Apo mukusangalala chifukwa chilima adaphedwa kuchikangawa
Munthu oipa oyipisisa iwe ndipo ukanakhala Wina sibwe Zi ukumachula dzina la Chilima
Big up mr vp
Nzeru palibe apa .Manyaka okha okha
Ndiye lero bwanji mukuyankhula Za UTM kumbuyoku mumati mukuyendera ntchito ya boma ndiye simungavale Za UTM or kuyankhula Za UTM mutu wako sukugwila now time yatha manganya
Mwayankhula zomanga Malawi Zikomo.
Azimayi yawabaya 100k 😂😂😂😂😂😂
Koma mwazi omwe ukugwirisilao ukuziwa kt anapereka ndi mulungu?muthu oyipa iwe unapanga upandu and mulungu akurange ndi aganyu wako wa mcp
Apo zikomo pokumbukilaso kwa ana a school Dr Michael ndpo mwaganiza bwno kt sakhale chingola dzanja chifkwa makolo amalephera kutenga ngongole
koma kudziwike kuti kumwamba kuli Mulungu ndithu.
Azimayi awa ndi a MCP asatipusitse dzitsiru mbuzi
Ok tadziwa
Sorry ndiye ifeyo tikuwalandila ndiye nanga kutani ife😅
@@blessingsdouglas3 0
Maganya akuononganso ndalama maulendo opanda phindu
Idya nawo k100,000 iyo mwanaaa😊😊
Koma manganya ndalama zathu wapenga nazo koma zoti akudya chitedze ukudziwa iweyo ambuye atithandidze zedi
Well, Mr Michael usi
Garu uyu akufuna kukopa anthu hiya Rlp 😭😭😭 Achirima
Ine ndili zipani ziwiri utm ya Michael usi ndi mcp😅😅😅😅
Big mn ❤❤
Manayotu ayende mwamtendere akufunika MaBodguard Mwanayu 100K, Now Day's
It's not for ever, your days are numbered,wait and see.
Kupusa awa undere uwu
Uzathawa ku Malawi manganya ngati ukupanga masewera
Nkhani si nkhope ya Chilima we want strong UTM. Chepetsa drama.
Ndiponso drama ndi kaduka basi...
Mulibe mfundo bro 😂😂😂😂 kamban zanu osati zamunthu amene munamusogozai 😢
Mapaz ake ameneyu mutu wake sukugwira
Ndipo inu 4yrs yonse osamusata or kamodzi ku court
Zibwana zake 😂😂😂😂
Very good speech
More fire pitirizani kuti bwelesera zambiri zo khuza a Malawi
Nice
Moto buuuu nyumba❤
Watalikanso nthawi yanji uyu😅😅😅
Wa kongelesi uyu,
Chitukuko chikhale NEEF? Mitu yanu why can't you put that money ku ma company mwina zinthu zakwela ngati chakwera zi zitsike pang'ono
Komanso awawa sakuziwa kt ngongole ndiyoyipa basi amalawife tizafa ndi umphawi omwewu😂😂
Chitukuko chimene mukufuna inu ndichiti. Chitukuko cha dziko ndi miseu, zipatala sukulu madzi magetsi.
@@DicksonNyirongo takhonzani economy please zinthu zikhale zofikilika...Inu NEEF yo yakupindililani? Kwacha kugwa daily
Access to financial services such as loans are some development indicators ....period
Galu ngongole za chani galu
😂😂😂😂😂😂 These women do not seem to understand what Usi is saying. He's telling them that he's nothing to do with party cloth decorations and they celebrate about it. Eeeeish!
Dr ussi 😊
Moto buu ku ma chende a Usi ko😢😅
Anthu sakufuna kumva za chakwera 😂😂😂
Abwana kunokukasungu anthu madipoziti anaperekakarekare sakurandira mpakapano murindewu mmidzimu kozani anthu ariramokwana ngatindaramakuribe asavutikekumarembetsa anthu
muyankhura mawa Azeri a vip
Mbuzi iwe ukamulemekeze Chilima lelo kkkk ufiti ulipodi eti
Alibe mbalume malumewa. Tikudikira convention ya UTM basi. Amange adzipita
Anakusankha popanda vote pano tikasankha ku convetion. Ngongole mwachedwa nayo ukawauze a president akowo.
Kumalawi ndalama zasataniki zabuka kungovina ee100.000 kuonesa china chake 100pin
Alengeze naye kuti azapikisane nawo pa u president ku Convention momwe achitira Dr kabambe ndi Dr Mtumbuka.
Azimai A Mcp awa akungovala makaka a UTM musatinamidze iwe Mbuzi Maiko usi Chilima akome lero galu iwe ngongoledzo mukupeleka pano cholinga chovura mavoti wekupha iwe Mr Chikangawa 2 osakapeleka chakudya ku machinga anthu akufa ndi njala
Dziko la pansi ndi lonyenga 😭😭😭😭
Ndi we opus a USI, chifwamba nd gulu lako
Mmmmmm manganya za ziiii bwanji osathandiza ku chifunga
Za ngongole ya Neef zopanda chikolezo mukunama, ife akhala akutibweza kuti tikafune zikole, kenako akuti zachepa mukaonjezere, tikawafunsa kuti mesa akuti chikole mwachotsa akumati ife malamulo athu salora kutenga ngongole popanda chikole, ndiye inu ndi a Neef mukunena zinthu zosiyana
Kwa ine usi si wa UTM and has never been he is just a traitor send to by the enemy chilima anazunzika iyeyu ali mbali ya adani kumwa mkudyelera awawa nga mcp
No mfundo, nde aike nkhope yanu inu ndi president wa UTM? No mfundo yolongosokayi asimeyi
Uyuso ndichitsilu a president ake ati akut anthu alandile ngongoleyo kupusa uku
Azikazi andani awa😅😅😅
Ati alibe showbiz 😂😂
Ausi lekani nkhani yanifi tikudziwa kuti mwatenga azimayi a mcp
Kodi ku UTM ko ndaanthu angati ayimila wu president ndufuna kuziwa nawo
Wapolice nde qlandile 5pn tsiku lonse pmwe mwanayo within 2mins 100pin😢😢
Munthu yemwe amamukonda chilima sangapite msonkhano wa usi mmm ndi a MCP amenewo
Pa Neef pokhapo nde zilibwino kwambili
Aaaa chisilu ichii manganya manyi ake
Mukumutamanda nzanu poti anafa😢😢😢, shame!!
Lero ndie mwaphatikiza za ndale ndi ntchito za boma? Never be trusted Mr Usi
Munthu oipa iwe. Ndiwolotse nkakutafune. Chimunthu chopanda mfundo galu iwe. Waatenga Aganyu kumati aUTM.umaleka kuyankhula za imfa ya Chilima ija galu iwe. Lero ukuntchula chifukwa wapanga mpando wake. Pamnya pako mmxxeew
Opusanso iwe eti wakhutaaaa
Vp tapitani ku Machinga anthu akudya chiteze ukuu.
Ndiye atakusankha adakuwuza kuti umuphetse ku mcp sikusinja ndi gwenembe wachabe chabe iwe
Koma azimayi olo Yudas akanamululutila ndithu kumusiya Yesu
Dziko aliyense kumangodalira ngongole basi usi mutu wako ndi nzako chakwera yo.
Kuzikolatu😂, nenani mcp chabe bwana.

Shuwa 💪💪💪🤸