🎉🎉🎉🎉🎉🎉 Congrats Brian & Cathy for a very cordial interview. At some point i also joined in the laughter. Meaning i enjoyed it very much. Bravo Bravo Aluta Continua!!!!
I feel sorry for his statement "why HRDC is quiet, why, is it because they hated me personally" Kulandidwa chomwe munthu unawina is very painful, This guy won 2019 elections. Panali mfunu kalelo yomwe inaweluza nkhani ya azimayi awiri omwe akalimbilana mwana. He judged kuti mwanayo adule pakati ndipo wina anavomereza and mkazi wina anakana saying basi apereke kwa nzakeyo than kumudula pakati. And mfumu ija inaona kuti mzimayi wakana zogawana mwana, ndiwakedi not uyo anavomera zogawana.... This guy won the 2019 election thats why anavomera kusiyila ena. Nde wa bakili TV amati history is the best teacher
@@user-ii9ch7oz8n Ngati sukudziwa chirichose ukadangokhala, ngati umazitsata go pa ma results a 2019 then go pa ma results a 2020 ukaona Kuti mavote achakwera ndi Chilima mu 2019 ndiamene anangowaphatikiza mu 2020 Kuti amugwetse Mutharika chifukwa adadziwa Kuti payekha payekha sakadaima pa APM.
My opinion: He has great qualities of a leader. Vuto ndi ndale. During his regime he was passive whilst Alot of DPP officials both in the Cabinet n chipani were busy looting public funds and zinthu zambiri zinaonongeka. Don't forget the likes of Achisale, Cash Madame, Dan Lu and the list goes on. Nepotism. Rampant corruption, Violence and all sorts were associated with his presidency. He will get votes cuz he is loved like a Bakili was but Malawi knows that DPP wants to use him to gain power n get back into government to continue stealing. He is in his late 80's and would be easy to control once they use him, they will find a way to get rid of him. Same applies to the current goverment because it's a can of worms. May the Lord Help This Nation. Timanamizidwa n being used.
Uyuyu APM yu nzeru zake ndi zozama kwambiri this guy knows what he is doing and Coz of his wisdom he sees things from a distance uyuyu ndi katakwe and alibe dyera ndi ndalama he wants best for the country
Mr President to error is human to forgive is divine am sure ur late bro Bingu said this. Forgive mtambo and those who are willing to work with u for the betterment of all malawians.l know it pains but the reward to be given will be great. The sooner the better Mr President imvani mau athu Sir.
Thank you APM for your comments about Timothy Mtambo, you have showed true Leadership and maturity, do not entertain these devils. We are in this situation as a country because of them. They are not supposed to be forgiven. Enock Chihana's decision to work with Timothy Mtambo is the greatest mistake he is making unless Enock Chihana is also a devil 👿.
Am sorry APM that when your time is over like this, you will go with the youth that think you are a solution to their issues, not knowing you are for your great fishes alone 😢😢😢
Am agree with you, HRDC hated you personally, where is HRDC today when people are starving , eating chitedze, zinthu zikukwera dairy , corruption, devaluation monthly.
Brian munthu ngati walepjela udindo mu church sizikutanthauza kuti ndiolephela muchilicbonse mu mpingomo ayi komanso samachosedwa mpingo nde ngati ali ndikutjekela kwa ntchito ina yomwe amaziwa amayenela kupasidwa. Analephela ntchito yomwe anthu anawayesapo panonakuyesedwanso ntchito ina.
President opanda phuma much love APM❤
YOU CAN SAY THAT AGAIN👏👏👏
Muthalika is our president forever ❤❤❤
🎉🎉🎉🎉🎉🎉 Congrats Brian & Cathy for a very cordial interview. At some point i also joined in the laughter. Meaning i enjoyed it very much. Bravo Bravo Aluta Continua!!!!
Mulungu asunge APM atulutse amalawi mu umphawi ndi mu uchigawenga 💙💙💙❤️ APM ndi ntumiki wa mulungu uyu
Mmene zililimu you must come back, zativuta bas
Congratulations brian Banda as well as cathy maulidi chidzukulu cha amayiye for the wonderful interview with Adad.
Brian Banda andi Cathy Maulidi you're the best guyz.....APM 🔥🔥
We are proud of you His Exallence, mukamawapanga interview adad ndimanva kukoma.
Ndipo answering in a humble manner honestly this guy mmmmh loves peace...
I feel sorry for his statement "why HRDC is quiet, why, is it because they hated me personally"
Kulandidwa chomwe munthu unawina is very painful, This guy won 2019 elections.
Panali mfunu kalelo yomwe inaweluza nkhani ya azimayi awiri omwe akalimbilana mwana. He judged kuti mwanayo adule pakati ndipo wina anavomereza and mkazi wina anakana saying basi apereke kwa nzakeyo than kumudula pakati. And mfumu ija inaona kuti mzimayi wakana zogawana mwana, ndiwakedi not uyo anavomera zogawana.... This guy won the 2019 election thats why anavomera kusiyila ena.
Nde wa bakili TV amati history is the best teacher
Ndizoonadi nzopweteka kwambiri kulandidwa chomwe wawina ndipo ndigwirizane Nanu ndimakhala ndi kulankhula Kuti APM adawina mu 2019 Koma chifukwa chokonda dziko lake sanafune mukhale nkhondo muno,ndukuuzani Kuti akadakhala munthu wina olo Chakwera yemweyu sakadalola Kuti tipiteso kuchisankho ndikukavomereza Kuti waluza.
Ndiwe wanzeru aseh umaganiza kutali thats great how u have related the stories
Apm ndiwa humble
analuza vote amangofuna kuwapasa mavote atipex
@@user-ii9ch7oz8n Ngati sukudziwa chirichose ukadangokhala, ngati umazitsata go pa ma results a 2019 then go pa ma results a 2020 ukaona Kuti mavote achakwera ndi Chilima mu 2019 ndiamene anangowaphatikiza mu 2020 Kuti amugwetse Mutharika chifukwa adadziwa Kuti payekha payekha sakadaima pa APM.
❤❤❤❤❤ adah from rsa we are together zikumunyasa asaze🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉apm adad athuuuu
Well spoken ADAD may our God continue to cover and protect you wherever you shall go❤❤❤❤❤
Adad you are more wiser than the MCP cabinet
Zomwe anachita mr mtambo akuluwa zimawawa or ine ndakhuzika ndimomwe alakhuliramu
Anapanga nkhaza
Ur right bro
Kod anapanga chani
Peter Muthalika is a real democrat.
Adad💙💙, awona nyekhwe akunenetsadi munthu wamkulu_ akubweretsa zoti chikangawa party singamake
My Vote APM 🎉❤🎉❤🎉❤🎉😂
Dad you are really real intelligent man always proud of you ,plz keep on going like u🎉🎉🎉
MCP izawona nyekhwee yeni-yeni 💙💙💙💙
this mutharika family deserves leadership
My vote APM oh Allah bless and protect APM where ever you are APM ❤❤❤❤
Long live adad 🎉🎉we need you as a president of Malawi ❤❤❤❤
Dedicated president to save malawi
My favorite president in this world
Muthalika is wise in answering questions and very intelligent and experienced
Mtsogoleri azikhala odekha, odziwa chimene akuyankhula ngati ameneyu APM❤❤
President wanzeru uyu AMalawi tidapanga mistake yoooooooophya!
Amandipatsa chidwi peter akamayankha mafuso..
This man he is wise man❤❤.
Long live APM 💙🔥
Brian Banda and your colick Cathy, may God bless you guys
.
Ku TH-cam kuli anthu ozindikira okha congratulations
Alichete sakulangula a HRDC masikoko alinkamwadi A Dad what you're saying it's true.
So sad kwa tengera anthu ku Bagamoyo 💔💔
That's true
Ineso am surprised why HRDC is quiet this time,kapena inafa?
My opinion:
He has great qualities of a leader. Vuto ndi ndale.
During his regime he was passive whilst Alot of DPP officials both in the Cabinet n chipani were busy looting public funds and zinthu zambiri zinaonongeka. Don't forget the likes of Achisale, Cash Madame, Dan Lu and the list goes on. Nepotism. Rampant corruption, Violence and all sorts were associated with his presidency.
He will get votes cuz he is loved like a Bakili was but Malawi knows that DPP wants to use him to gain power n get back into government to continue stealing. He is in his late 80's and would be easy to control once they use him, they will find a way to get rid of him.
Same applies to the current goverment because it's a can of worms.
May the Lord Help This Nation. Timanamizidwa n being used.
Great man may Almighty Allah guide Mutherikah
Mr B mumakwana kucheza ndi adadi muthu omasuka mukanapita kwinako mukanaphedwa😂😂😂
😂😂😂
😂😂😂😂kukalandilako zikwanje@@IsmailBrighton-w6u
This man deserves another chance....without your second opinion .. APM my Vote
You deserve the title APM. Muli future mwa inuyo bwana, as one of poor people in Malawi I wish you all the best next year. DPP WOYEEE!!
The man is more powerful than the party.kikikiki
Timothy Ntambo please munthu uyu akumvabe kuwawa ndizomwe unachita bwelera he's not ready to forgive you
Zoona. Mayankhidwe ake akuwonetsa kuti adakali ndi mkwiyo.
@@modestamhango7737adatirakwiranso ife amalawi kwambiri mtambo apepese kutundu wa Malawi on TV mwina tikhululuk
akamupha naye asamale
Ndipo sanamukhulukire
My Allah will bless you Brian and apm
Beautiful interview Intelligent APM🎉
My beloved Daddy❤❤❤❤❤May The God continue keeping you safe❤❤❤❤❤❤
Peter munthalika ndifi zoona ,akulephera kukhululuka i like this man
Very maturity and peaceful words
APM my vote ambuye azikupansani moyo wautali
Akuluwa amaomesa kuziwa pakudekha kwawo much love my presdent❤❤❤❤
Why are they quit ? Masikono Ali mkamwa indeed! Koma ziwasama
i feel pity for my country Malawi😢😢At this age will he stand the pressure
We hope for the best your excellence APM
The coolest man ever apm we love you
Akuti HRDC sikono yadya ili mkamwa very true why quite Malawi akudya chitedze
Atolankhani athu mantha. How do you start congratulations. Funsani mafunso about what he will and have done with the situations chakwera has faced.
What had faced bro
Uyu ndikatundu guys am ready 2 vote 4 HIM. DPP moto buuuu
Mfundo kuposa chakwela mkumati wakalamba, kumuopa muona nyekwe 2025 my vote kwadadi
Akufunika atiuze analakwitsa pati nanga akonza pati malawi akuzuzika ndi anthu andale kunena zoona 😢😢😢😢
He know how to answer questions mosakhumudwisa and mwanzeru
Adadiwa APM Simuthu wamba💙💙
My president loves u
The great remembered always ❤❤❤
APM IS A GENIUS MAN
Much love .... Long live
❤❤ l Love you so much Peter mutharika
Adad my vote 💯💯💯💯🎤🎤🎤🎤
Its true masikono alinkwamwa,koma ife tinaona zomwe Anachita nthawiimeneja,ankañgofuna kudzalazitsa mimbazawo
Uyuyu APM yu nzeru zake ndi zozama kwambiri this guy knows what he is doing and Coz of his wisdom he sees things from a distance uyuyu ndi katakwe and alibe dyera ndi ndalama he wants best for the country
My vote 😊😊
Mr President to error is human to forgive is divine am sure ur late bro Bingu said this. Forgive mtambo and those who are willing to work with u for the betterment of all malawians.l know it pains but the reward to be given will be great. The sooner the better Mr President imvani mau athu Sir.
This man has a heart of stone and cannot forgive anyone.
What you are saying please Mr President do in your heart please
President wanji osapisila lilime pang'onong'ono latuluka nkhwilu et?
maturity at its best🎉
Thank you APM for your comments about Timothy Mtambo, you have showed true Leadership and maturity, do not entertain these devils. We are in this situation as a country because of them. They are not supposed to be forgiven. Enock Chihana's decision to work with Timothy Mtambo is the greatest mistake he is making unless Enock Chihana is also a devil 👿.
Ilove u adadi ur indeed the great leader
There's is still potential in APM despite his age .
mdala wakalamba , chakwera my vote
Interview yapamwamba kwambiri ndipo yaulemu ndiyopasa chikoka especially mayankhidwe a Peter
Mwatiyimilira a Times ulemuwanu ❤
He is a real professor
Peter ndiwe wanzeru
Dpp my vote
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ mulungu amudalinse Peter mutalika ❤❤❤❤❤❤❤❤
People we're waiting for you adad
Akunvabe kuwawa APM. Kapepese Mtambo
Komat adad aaaa tima❤❤❤❤ kwambili ndipo mumvesese
Am sorry APM that when your time is over like this, you will go with the youth that think you are a solution to their issues, not knowing you are for your great fishes alone 😢😢😢
Pliz brayan muziyankhulako mchichewa timawatumizola anthu akumudzi
Pliz tomse ndi aMalawi
Proud of dad💙😘💙💙😘
APM my vote💙
Am agree with you, HRDC hated you personally, where is HRDC today when people are starving , eating chitedze, zinthu zikukwera dairy , corruption, devaluation monthly.
mtambo ndi chilima anaonongadi dzikoli😭😭😭😭😭😭
Adad God bless you
Apm my president ❤❤❤❤❤
Its time to regret Malawian please don't do like 2020 my fellow citizens of Malawian
Professor Arthur peter muthalika ndi more
APM must come back please
Brian munthu ngati walepjela udindo mu church sizikutanthauza kuti ndiolephela muchilicbonse mu mpingomo ayi komanso samachosedwa mpingo nde ngati ali ndikutjekela kwa ntchito ina yomwe amaziwa amayenela kupasidwa. Analephela ntchito yomwe anthu anawayesapo panonakuyesedwanso ntchito ina.
To 4give iz blessings adadi just forget and forgive them all they leaned a lot on this mistakes
abryn Muma masukatu kwafusa mafuso adadi Kodi manga enawo bwanji simuwafusa a president akulamulilawa bwanji mudziwafusa nawoso aaaaaaa
My vote APM
Peter Mthalika ndivot yanga
Oleza mtima odziwa democracy,wamasomphenya kungofotokozako zochepa cha
Be
APM my vote 🔥🔥
Ulendo uno juli ndale za nyoooo
Mtambo dzivere mtolo
There is no forgiveness to you and Trapenz by Peter Munthalika😭😊
forgiveness is never available kwaPeter
Brian banda, like aaaah aaaah aaaah when speaking English, can't he speak without aaah aaah aaaah aaah ?
😂😂😂😂😂