GWEDEGWEDE WA LERO NDE KUNALI KULANKHULA |

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 1 ก.ค. 2024

ความคิดเห็น • 21

  • @georgesmart3791
    @georgesmart3791 12 วันที่ผ่านมา

    More fire Gwedegwede❤❤❤❤

  • @WezzieChimuzi-ek7bk
    @WezzieChimuzi-ek7bk 10 วันที่ผ่านมา

    Koma naneso ndaseka ine chiphweteeee kuno ati Amen ... a Police naonso ngati asabala chonsecho naonso akuvutika ngipusa kwabasi

  • @JamesLongwe-qz9fd
    @JamesLongwe-qz9fd 13 วันที่ผ่านมา +1

    Ulosi ulipo kale kuti chakwera akuchoka 2025, APM akubweleranso ku State House

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 12 วันที่ผ่านมา +1

    Kuwachosa chipani achita bwino cz anthu akomwe ma mphunguwo akuchokera azizaziwa kuti akuvotela ndani

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 12 วันที่ผ่านมา +1

    Palibe program ya chilungamo ngt iyi ever Ku mibawa osat za achina chawezi amapanga za ndare

    • @owenmulemba5347
      @owenmulemba5347 12 วันที่ผ่านมา

      Ndiposo ine ndimadabwa kuti kodi anthu ena ziimaavuta bwanji kuyankhula chilungamo

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 13 วันที่ผ่านมา +1

    Zamathanyula ayi apo zachita bwino tisalole

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 13 วันที่ผ่านมา

    Good Messnge

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi 13 วันที่ผ่านมา

    Koma menepakukomela pakatsi pakakulowesa patumbo pamamuna Sako koma agalu enawa

  • @gracemaluwa4674
    @gracemaluwa4674 13 วันที่ผ่านมา

    Mulungu ekha ndamene awonetsere chilungamo

  • @alexmkolongo3089
    @alexmkolongo3089 12 วันที่ผ่านมา

    Tikufuna black box

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga 13 วันที่ผ่านมา +1

    Onse omwe achokawo sangapangitse kuti Dpp iludze ayi, ndizopanda tchito APM 2025 akubwelaso 💪💪💪

    • @AnaffSayamika-uh6vg
      @AnaffSayamika-uh6vg 13 วันที่ผ่านมา +1

      Iwe km moyo kumeneko, chakwela nd galu ase kkkkk

  • @NedsonKanjira-qj2ig
    @NedsonKanjira-qj2ig 13 วันที่ผ่านมา

    Zoonadi mwakamba zanzeru zomangana pazithu zaziiii

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 10 วันที่ผ่านมา

    Inu pena simundiwaza anthuwo sakupanga Za Chipani chawo ayenera section 65 igwire ntchito, kodi adawusi akupanga chani kwao, musamayakhulire mantha mwava, muzingokamba zinazo mumakwanitsa

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg 13 วันที่ผ่านมา

    Dpp boma bc, chakwela akapitiliz kuvin nyan wakulu

  • @user-te3ps3kf2t
    @user-te3ps3kf2t 13 วันที่ผ่านมา

    Źoona,ķodi izi amazitenga kuti a mabugwewa,coz it's against with God .

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu 13 วันที่ผ่านมา

    DPP ndiboma kare 2025 ma mp opepera ngt amenewo apite uko zisiru

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 13 วันที่ผ่านมา

    APM 2025 bomba olo mutayikila kumbuyo muzachita manyazi Apm 2o25 boma

  • @IshanieChatha
    @IshanieChatha 12 วันที่ผ่านมา

    DPP always win, take it whether u want it or not

  • @DoreenBanda-hg7oe
    @DoreenBanda-hg7oe 12 วันที่ผ่านมา

    Ngt achotsa ndy Kuti kalipokalipo Koma sikuti angapangitse APM kuluza DPP boma 2025