DR JOYCE BANDA KUFOTOKOZA ZA ALLIANCE |

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 71

  • @johnmwale2047
    @johnmwale2047 หลายเดือนก่อน +1

    I love the truth in JB. The passion and determination she has towards MALAWI. She never get tire working up to date despite not being the president, God bless you Mama

  • @beatricemwale2618
    @beatricemwale2618 หลายเดือนก่อน +1

    Ndenge anagulisa Bingu yoyamba ija ilikuti Jet yakamuzu...ukufunsa iyii chifukwa anagulitsa nzimai...iyi ukufunsa anafotoza kale unali kuti?ndarama zake Dziko linagulira dzithu zadziko...koma tatiuze ya Kamuzu Bingu anagulitsa....Amai Mumagwira ntchito yotamandika...just 100days mavuto onse anatha...Long Live Your Excellency....We are proud of you..❤

    • @Zelinakhisswell
      @Zelinakhisswell หลายเดือนก่อน

      Kmatu tamapangani balance mkamaganiza mukunena kt bingu anagulitsa jet mkubwezeretsapo ndege kuposaso pa jet po, nde iyeyo atagulisa ndege nchani cholozeka chomwe anagura poti ndalama zake mzija anthu amakazipeza mnkhalango za cash gate. Tiyen tingomuyamikira pazinthu zomwe akupanga za charity in communities

  • @user-ru4oi9xv1k
    @user-ru4oi9xv1k หลายเดือนก่อน

    Almighty God continue to bless her excellence Dr Joyce banda, she developed all what a leader need to have , am learning a lot from his hustling, hard work, patriotic to her country Malawi, and dynamic leadership , umu mli umunthu ndi dzeru❤

  • @vitujames53
    @vitujames53 หลายเดือนก่อน +1

    Akudyetsa ana ķu Malawi kuno opotsa 15,000 tsiku lilinse phala...palibenso mtsogoleri amene amayika anthu ovutika pa mtima pake kuposa Dr Joyce Banda

    • @mwale86
      @mwale86 หลายเดือนก่อน

      Ndipo akukwanilitsadi kuti mmela poyamba ana anthu akupita Ku school chifukwa akupezako chakudya kunjaku kuli njala koma ana ambili akuthandizika through Joyce Banda foundation feeding centers

  • @Pembamuhammad
    @Pembamuhammad หลายเดือนก่อน +1

    May Almighty Allah continue to bless her excellence Dr Joyce Banda

  • @HastingsPhiri-ju3yr
    @HastingsPhiri-ju3yr หลายเดือนก่อน +2

    Dr Joyce Banda anapanga zinthu zambiri choyamba:adakwedza salary yaziphunzitsi,analora kutumiza achinyamata kukagwira ntchito kunja komaso kumangira anthu ovutika manyumba just to mention afew

  • @mwale86
    @mwale86 หลายเดือนก่อน

    HE Dr Joyce Banda full of wisdom kuyankhula zowona ndipo ntchito zachifundo mukuzigwila kumangila nyumba anthu with community Development initiative anthu ku kasungu anapeza chakudya mulungu apitilize kukudalitsani

  • @chikondichanza9772
    @chikondichanza9772 หลายเดือนก่อน +1

    Amayi is an amazing creature. I salute 🎉. Zimandipwetekeka day and night amayi tikanawapatsa mpata Malawi could have been another national. I cry for my Malawi

    • @mwale86
      @mwale86 หลายเดือนก่อน

      Ndipo bwezi tili patali kwambili anali ndimasophenya otukula dziko lino

  • @user-oo8cr3vw5s
    @user-oo8cr3vw5s หลายเดือนก่อน +2

    H.E. JB is full of wisdom and plays smart and sophisticated politics

  • @kelvinmphande3754
    @kelvinmphande3754 หลายเดือนก่อน +1

    My role model, continue serving well.

  • @Blessings31
    @Blessings31 หลายเดือนก่อน +1

    Our ambassador to the international community..Mmatiimilira mama

  • @vitujames53
    @vitujames53 หลายเดือนก่อน +1

    Ndale zake ndiza mtendere, amalimbikitsa kuti ndale sitimadya tiyeni tizikondana tonse ndi a Malawi ndipo palibe dziko lomwe tingalilodze kuti ndi kwathu..
    Amalimbikitsa kulemekeza atsogoleri ndikuwopa Chauta.
    Ambuye azikupatsani moyo wautali Amayi

  • @KestherMkandawire
    @KestherMkandawire หลายเดือนก่อน +1

    Mai wamzeru uyu ndipo i wish chipani chake chikanakhala strong ndithu ndikanamvotera ndimamkonda kuyambila pachiyambi ndipo amandilimbikitsa kukhala mzimai olimbikira.

  • @vitujames53
    @vitujames53 หลายเดือนก่อน +1

    Mama JB pa 2 years analamula Malawiyu ìmfa za azimayi pobeleka kunalibe chifukwa amalimbikitsa uchembele wabwino..ndipo anamanga ma guardian shelters muzipatala zambiri za Boma mu Malawi muno

  • @yamizimba4018
    @yamizimba4018 หลายเดือนก่อน

    She's a hope of Malawians and she deserved to be a leader indeed because she didn't stop doing her leadership work despite of her not being on the throne

  • @KhumboPaulos-xb4id
    @KhumboPaulos-xb4id หลายเดือนก่อน

    H.E JB, a woman of integrity. A true leader. I love H.E JB.

  • @dianachabs
    @dianachabs หลายเดือนก่อน +1

    Ambuye adzikudalitsani masten , ntchito zachifundo ndiye mukuzichita

  • @uchizimwale8510
    @uchizimwale8510 หลายเดือนก่อน +1

    HER EXCELLENCY 🙏🏽🙏🏽🙏🏽

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 หลายเดือนก่อน +2

    I love this mama.

  • @vitujames53
    @vitujames53 หลายเดือนก่อน

    Sangagone tulo anthu ena akugona nyumba zodontha ndichifukwa pa 2 years anamanga manyumba almost every district of Malawi under Mudzi Transformation

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo หลายเดือนก่อน +3

    Inunso mayi ndiamene munalipatsa soka dzikoli 😢

    • @dianachabs
      @dianachabs หลายเดือนก่อน +1

      Anasintha zinthu in just 30 days mu office

    • @mwale86
      @mwale86 หลายเดือนก่อน

      Ndipo mafuta ,Forex magetsi kusiya kuzima masten amagwila ntchito

  • @vitujames53
    @vitujames53 หลายเดือนก่อน

    She was born a leader and full of love and passion

  • @kelvinmphande3754
    @kelvinmphande3754 หลายเดือนก่อน +1

    My favorite

  • @vitujames53
    @vitujames53 หลายเดือนก่อน

    She knew what to priotize in her leadership..mankhwala sankasowa mzipatala

  • @mkajikosya-uq5hs
    @mkajikosya-uq5hs หลายเดือนก่อน +1

    Mayi wanzeru anasintha dziko 100days

  • @mkajikosya-uq5hs
    @mkajikosya-uq5hs หลายเดือนก่อน +1

    Munthawi yake anapanga zinthu zimene amuna alephera

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w หลายเดือนก่อน

    Mama J.B. yoù are brilliant, but why can't you tell Chakwera, of which you supported.

    • @kelvinmphande3754
      @kelvinmphande3754 หลายเดือนก่อน

      Anthu ambiri akapeza mipando amasiya kumva

  • @Blessings31
    @Blessings31 หลายเดือนก่อน +1

    Masten 🔥

  • @BeatriceChasima
    @BeatriceChasima หลายเดือนก่อน

    Zowonadi Chilungamo cheni cheni

  • @chanceykalimah1965
    @chanceykalimah1965 หลายเดือนก่อน

    Joyce Banda alibetu size oho!!

  • @PreciousBandah-l2r
    @PreciousBandah-l2r หลายเดือนก่อน

    Tyen tziyamikila zomwe wachita munthu amalaw tyen tisinthe

  • @PeterMillimbo
    @PeterMillimbo หลายเดือนก่อน

    We are not Europeans pliz next time ur interview make with Chichewa

  • @FrancisStima-sc7zs
    @FrancisStima-sc7zs หลายเดือนก่อน +1

    Mai amenewa anayesesa

  • @user-ou1od8sx7k
    @user-ou1od8sx7k หลายเดือนก่อน +1

    I am a living testimony, under dynamic leadership of JB and climate justice needs to be reached out in our curriculum.
    Long_live_leadership @H.E JB.
    #necessary_noiz

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p หลายเดือนก่อน

    Joyce NDI ndani galu aneneyo

  • @FlorryVugy
    @FlorryVugy หลายเดือนก่อน

    Our former president she is not yet know,Where she is going to Alliance or not😂😂

  • @user-st4po1yv6r
    @user-st4po1yv6r หลายเดือนก่อน

    Mfit yayikaz

  • @LamieTiger
    @LamieTiger หลายเดือนก่อน

    Mbamva imakhala ndimbaluwe simasewera

  • @maxwellnansongole8744
    @maxwellnansongole8744 หลายเดือนก่อน

    Mama you look young 😂

  • @MfipaKapwera
    @MfipaKapwera หลายเดือนก่อน

    If you want Malawians to trust you bring the money that you sold Jet.

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus หลายเดือนก่อน +1

    Komatu akuonda mayiwa

    • @inessmsiyambiri8517
      @inessmsiyambiri8517 หลายเดือนก่อน +1

      Kukula

    • @cynthiakananji1608
      @cynthiakananji1608 หลายเดือนก่อน

      Komaso it's fine coz kunenepa kumabweretsa mavuto kwa anthu achikulire

  • @Lee-lee-w1r
    @Lee-lee-w1r หลายเดือนก่อน

    Hmmmm🤔🤔🤔🤔

  • @user-rk3jx3kg8i
    @user-rk3jx3kg8i หลายเดือนก่อน

    Mai opanda nzeru

    • @kelvinmphande3754
      @kelvinmphande3754 หลายเดือนก่อน

      Inu muli nazo

    • @mwale86
      @mwale86 หลายเดือนก่อน

      Kuwawona akunenawo kkkkk kuvesa chisoni ndipo ngati iwowo alinazo zeruzo

    • @vitujames53
      @vitujames53 หลายเดือนก่อน

      Mulungu sangakhale opusa kuwapatsa udindo wolamula mdziko muno zinthu ndikusintha pa 100 days..
      Mwinatu munali ku theba mmene iye amalamula.

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9d หลายเดือนก่อน

    Fice iwina uyo

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl หลายเดือนก่อน

    Mbuzi yamunthu iyi

    • @kelvinmphande3754
      @kelvinmphande3754 หลายเดือนก่อน

      When conscious escapes, you talk like this

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 หลายเดือนก่อน

    Ndale zavutatu

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 หลายเดือนก่อน

    Chi mzimayi choyipa chimenechi.

    • @PreciousBandah-l2r
      @PreciousBandah-l2r หลายเดือนก่อน

      Onama iwe

    • @mwale86
      @mwale86 หลายเดือนก่อน

      Koma nde mkwiyotu za ziiiii

  • @JaneMoyo-ws2di
    @JaneMoyo-ws2di หลายเดือนก่อน

    Mh

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g หลายเดือนก่อน

    😱😱😱

  • @user-hd7wq2yc6m
    @user-hd7wq2yc6m หลายเดือนก่อน

    Mama wambula mahala uyu walikutisokezela chalu panyengo yake she was acontributor of troubles in this country during her time stupid

    • @kelvinmphande3754
      @kelvinmphande3754 หลายเดือนก่อน

      Nzeru Mulibe

    • @mwale86
      @mwale86 หลายเดือนก่อน

      Aaaah imwe yoywoyani unenesyo wakasanga charu chanangika no magetsi,Forex mafuta wagalimo kwene wakawezyelapo vyose in 100 days nyengo zinyanke tiyowoyenge unenesyo no soni

    • @mwale86
      @mwale86 หลายเดือนก่อน

      Stupid ndimwe apo ntheee palije nachimoza mulikuvwilapo olo kukaya kwinu

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v หลายเดือนก่อน

    Mbava yikuyankhula ngati zenizeni, ndege yathu yilikuti? You celebrated the death of Bingu, this was not a Malawian culture.

    • @Pembamuhammad
      @Pembamuhammad หลายเดือนก่อน

      Munali ndi ndege?😂

    • @user-jn9tz3li3v
      @user-jn9tz3li3v หลายเดือนก่อน

      @@Pembamuhammad yes, a jet bought by Bingu