Mantha iwe ndiye bwenzi uli vice p bwanji sunakane u vice president wo kulira ndi mtima basi ingothokoza wanyambitako pa imfa ya skc other wise ndiwe chidole ku tikufelanji sumathanso acting apa usandinyase
This one is insane because 20 million anakapereka anakaluzabe. But if he was wise he could have saved utm. Pano muli muli pamwamba olo 20 million simupereka manganya pansana pako
Koma mwati uyuyu akuyankhulayu ndi Manganyadi? ine poyamba ndinkamutenga ngati wamzeru, koma ndi mchabwa wachabechabe. Nkhani zokhudza ngongole Za NEEF mudakawasiyira alangizi a NEEF apange ma awareness campaigns ngati mukuona kuti kuli madera ena omwe sanafikeko, otherwise mwafika potinyasa nazo🚮🚮🤧🤧
That's why ndimati uyuyu sayamika.
UTM inalibe funding ndipo convention was a must, 20million kunali kusonkha kuti convention ichitike ndipo above that ma member amagura chithunzi Cha SKC modula just to raise funds kuti convention itheke yet Usi uli apa mkumalalata ngati zanzeru.
Lets 2025 tione kuti ndale zikakusiya kutiko
Sakuchita bwino bwanawa
Mr nthiko
Chipani chingayende popanda ndalama, 20 million ndindalama zoti zikathandiza chipani
Usi ndiwe satana unangulinsa chilima ndiwe, unaulura chinsinsi kuti chilima akambwera ku North korea achoka mumwingwirinzano usi ndiwe yundasi.
Koma uyuyu ndiwamisala poyamba akati convention sanapange Coz chipani sichimasata malamulo now akut coz of 20 mita ija sakanapeleka coz kuli anthu ovutika ambili ofuna thandizo.
Komanso ndalowa UTM fukwa manganga wachoka😂😂😂
Inenso amandinyansa
Iwe a mcp akupusitsa for them to stay for ever they need to pay more sacrifice end of caught
Uyuyu zomwe amapangazi amaganiza ngati akupanga Tikuferanji samadziwa kuti akuyenera kumakhala serious popanga zadziko ( usi ndi mfiti yopemphera be careful Malawi.)
Maclel usi ndiwaboza akuti sangapeleke k20,0000000 chikhalilecho amaitana anthu Ku nyumba kwake Ku mapasa anthu k200,000 Kwa munthu modzi ndiye zikusiyana bwanji amaziwa kuti aluza uyu asakupusiseni
Zilibe kanthu Ife timamkonda
Mwachita bwino mulekeretu kukakamira dza chipani cha UTM pangani dzanu dza utm dziyiwaleni
ma quality a president alibenso olo olo
Ndi president wandani, mmesa anazusiya analowa kabambe
Usakadye utaka kuti ndani iweyo...mwalowa liti mboma kuti anthu azikakufunsa zautaka...vomerezani kuti simunakawina baba
Apenga awa
uncle short one mulibe mfundo mcp ikubudulani pompano kapena ai muphedwa ngt chilima kumeneko
Team Kabambe ife
Chimunthu choipa mtima ngati ndulu ya ng'ona ichi
Nfundo👐👐🤜🤜👏👏👏 man of the people
Ngati zilibe phindu nanga mnzakoyo chakwela akukakamila chani??
😂😂😂unayiwopera patali iwe
Amaopa kuluza awa, enawa ndi manyazi😊
Mulibemo mfundo umumu
Ndipo chitini cheni cheni
Palibe chimene ndikumvapo apa aaaa
Ndipo nane sindkumva
Mantha iwe ndiye bwenzi uli vice p bwanji sunakane u vice president wo kulira ndi mtima basi ingothokoza wanyambitako pa imfa ya skc other wise ndiwe chidole ku tikufelanji sumathanso acting apa usandinyase
Unaiopa convention usayankhulepo mwano apapa
Iwe vubwe palibe comwe ukunena iwe ndiosokonezabasi
TIME IS TICKING....
Mwadziwa liti kuti anthu akuvutika? Za ziii mwayesa a Malawi ndi opusa eti?
This is smart guy
Nyengu yose iyi ukayakochi leka kupusika wanthu apa Mbuzi iwe meeeee
This is good, Michael usi is talking there is no way someone spend 20 million for position
Kkkkkkkk olokobe utero komabe chakwera wakoyo sawina,so usazivutike kubwebweta ata sizikuthandiza
mmmmm ichi ndi cha mcp
Munthu oyipa kwambr wa MCP fotseki zake
😂😂😂😂zako waphedwa pomwepo iwe ungakhalepopo umatuluka MCP singasithe
I love him...my vote olo asapikisane nawo
Michael Usi is TOO SMART .. enanu simungazimvetse mmene amaganizila.
Mwadulatu dzinalo,, he's smartmartic
I don't think so. He wanted to be a utm president . Too much drama
@@bobkatas1974 🤣🤣🤣🤣
@@emmaculatemenzeiwa yes drama ... We know Him for ma Drama kumene .
EYA PITILIZA ODYA ZAKE ALIBE MULANDUYO OSATI KULIMBANA NDI UTM MBUZI TONKHWE-TONKHWE
Chipandatu udindo sibwezi inu mutakwra galimoto ya Boma,Ngati sufuna udindo muziyendera magalimoto Anu poti mulinawo
Kabambe you have my vote
Uyu alibe nzeru komaso sangawine
Chilima posankha usi as his vice anaona kuthekera.. umu dyera mulibemo..
zazii chosaziwa amene umukonda ndiye mdani wako ambuye akurangeni
Ankaona ngati wabwino aka ndikachitsiru ndipo Chilima kanaziwa sakanasankha pumbwa uyu
Mzeru zatha akulu mwayenda mma office palibe mwachita. Kwatsala 10 months palibe muchute
Achisiru awa magazi achilima akuwavutitsa
Ndipo zoona@@MartinKapito
Manganya waboza umulandile yesu akhale ambuye ndimpulumutsi wako ndipo chomwe ukuyenelakuziwa ndiichi amalawi anapenya
Mr vice nice one
Palibe akuziwa uyuuuu
Kape
So you are very happy that someone lost his life that your dream has come true😂😂😂
Munthu oyipa iwe .. tinalephera ife convention ? Manyazi zinayendatu ...
100% dziko lapansi🎉 silikubwerela mmbuyo ayi,, tili mmasiku otsiliza.
Lero wadziwano kuli azigogo ofunika feteleza kmaso anthu oti aziwalimira.....
😢😢😢😢😢
Usi more fire
Ukhaula wagwanayo bale next year wakundende nose
Kalime fundoless 😂😂
Mukuti chani kwenikweni kodi a VP?
😂😂😂😂 Vp kumenya ma tone agalu
He knew he couldn't win
Mulibe mfundo abwana and ndiumboni wakuti siimu wa UTM, betrayer
Munthu owoopa Mulungu ameneyo azinena chilungamo posayang'anira udindo
This one is insane because 20 million anakapereka anakaluzabe. But if he was wise he could have saved utm. Pano muli muli pamwamba olo 20 million simupereka manganya pansana pako
Umuwudze chakwela wakoyo akungoyda misonkho ya thu
The next sacrifice to MCP ndiwe Manganya. My guy watch out
Munakwanisa bwanji kupanga plan yofuna kupeleka ndalama zambilimbili zowakila chiliza ngati mukuonanso umphawi waanthu?
Koma ndiponso inu aaaa zaziii
A Usi musaoneke abwino popeza palibe amene adakuletsani kuti mukaimile upresident ku UTM ñdipo osati muzichuluka mzeru nthawi mudali nayo yokapeleka maform simu,simudagune nokha osakapikisana nawo ndiye zonyasa ife ayi
Mwalakhula abwana zondisangala
Anapanga bwino osapanga nawo convention coz akanagwa ,akanachita manyazi koopsa kuti VP Wambwita ku chipani
Ukuleka kumuuza chakwelayo bwanji kuti azilapa kukumbukila kuti azafa
Kkkkkk mbuzi yamunthu
Are you at the church service
Sunapang nawo iwee bon kalindo wakuuz kal
Where is your leadership boss😢😢😢
Mapwala ako usi, palibe chanzelu chimene ungatinamize
Kick's from a dying horse.......
Anadzidziwa ekha manganya kuti sakanamaka pa mr kabambe ,
Mwinanso bola mai Kaliyati anapeza 21 votes
Ndipo TNM anamvana zochita kale some of the candidates know u president upita kwa kabambe they still competed kuti asokoneze osokonezawa
@@EUGINEMWADALA ukunama
Truth
Kodi bwana Usi 20 million yo ndiye muyipeleka kwandani ndipo liti?
😂😂😂😂wapenga
Kuyakhulitsa
Nanga inu usi mukuthandiza ndani??? Pamene mukudyelela mu MCP??
I remember,bambo anga akayambana ndi anzawo,olo kumenyedwa kunjira,amangolusila aliyense,kuli kupsa mtima.....Mwana asayankhule,amapatsidwa khofi😂😂😂...Umangodziwilatu kuti zinthu zawavuta komwe aluchikeraku.....Vomelani kuti madzi achita katondo.....Udindo mulinawo kale inu......Mudziwa chomwe muchita......Udindo mulibe nawo ntchito,kodi kupanda udindo mungamapange zinthu?
Nokhanso mukuti ukakhala mtsogoleri....Utsogoleri umabwera opanda kuikidwa pampando?! Nanunsotu mupole motoo.....
Tilibe naye ntchito uyuuuuu palibe chobwe akuwathandiza amalawi ngati wapambuyo pa president
Choka iwee usi mulungu akuungokusunga kut ulape koma ukupitilira zousa uona polekera
Mkape iwe uso
Koma mwati uyuyu akuyankhulayu ndi Manganyadi? ine poyamba ndinkamutenga ngati wamzeru, koma ndi mchabwa wachabechabe. Nkhani zokhudza ngongole Za NEEF mudakawasiyira alangizi a NEEF apange ma awareness campaigns ngati mukuona kuti kuli madera ena omwe sanafikeko, otherwise mwafika potinyasa nazo🚮🚮🤧🤧
Mun2 opanda nzeru zoyankhuraso mwana wen wen adyele mcp yomweo
Aaaaaa zaziii nde 20 million ndi chani ukhaula iwe wasowa chinene usova yudas
Koma chilima anamulakwila pomuthetsera odya zake alibe mlandu pano omwe anasiya mmmmm
Munthu uyu alibe mtima oipa ai
Kodi mukupanga kampeni ya chipani chanji mr?
????
😂😂😂😂😂😂😂Chikangawa
Opusa iwe anthu mukuwapasa ma million kuti akakhape anthu aja ndiye uziyakhula ngati wa nzeru
Sindipanga now comment guys koma aaaaaaaaaa basi sikhale choncho eeeeeishhhh 😢😢😢😢😢😢
Palibe Chazeru chimene akunena,
Anthu amatemedwa ku LILONGWE aja iwe unali kt
Palibe ndikumvapo za mzeru ataaaa
Nkhani Siya 20m kunama sukwabwino nkhani ndi 21 votes imene mumaopa nzake Ali ku 600 something 😅
Manganya ndiwe wausilu ku utm sitikukufuna ayi,
Muuzeni sakumvatu kkkk
Muuzeni chakwera abwerere kuubusa asiye zandale kuti akalowe kumwambako komanso inuyo a usi mukumayenda kut muwapatsa ngongole koma ndalamazo sizikuperekedwa nkomwe iyaaaa
Ndiye anthu asakambe zakulephera kwaboma kuopa funso lopusalo
Koma iwe nzeru zikuvuta ::palibe fundo :: a nthu alipadzuwa awuzeni fundo::bodza ngati mkadzi
Kuononfa ndrsma kuyenda ngati ajawa
Palibe chomwe ndikunva chamzelu apa iyaaaaa
chilungamo chikumususa yekha uyu, fundo ikakhale ya Thako Pali nzelu apa???
Ineyo ndikuyesela kuti ndimvetsetse koma ataa mwina adzanga wa mcp uumva
Mfundo zanzeru 👍✊
Ine ndye sindikuvesa ukungolowerana khan zopanda fundo