Uchitsiru mukupanga nonsenu kuchipaniko zikungosimikidza kuti UTM inali Chilima, ndipo kufa iye palibe chatsala. Udolo ongakhala osokosa mma social media basi, Commission of inquiry la tsegula zipata kuti muka pereke ma umboni mulinawowo koma kuli ziiii, kumango bwetuka pa social media basi. A big applause to Marry Chilima and family for excluding herself from this shit 💩. She remains a woman of integrity and class.
Ma desciples a yesu amene anali ndi yesu sanatengere utumiki patali amene a anate gels utumiki patali anali Paulo amene sanagwire tchito ndi yesu hi mm odzimodzi amene a gapititse patsogolo ndi kabambe koma sanagwire tchito ndi saulosi chilima
NDIPO MANGANYA NDI JUST A VICE PRESIDENT. PRESIDENT WA UTM ANALI SAULOS KLAUS CHILIMA. .NDIPO A BAKILI ANATI VICE PRESIDENT NDI WAPAKALIYALA. IYE WAPAKALIYALA SAYENDETSA NJINGA NDIYE MANGANYU ALHALA BWANJI WOYENDETSA UTM .? PANOPA PRESIDENT NDI DALITSO KABAMBE. BASI AMENE ANTHU MADELEGATES AMUSANKHA NDIYE MANGANYAYU INJUNCTION YAKE ISACHITIKE KULETSA KUTI KABAMBE SIPRESIDENT WA UTM
Beloved HE Dr Chakwera,you are a wise leader.Please reshufle your cabinet immediately or MCP Integrity will be backslided.First MBM out
I agree with you my lovely Malawian citizen
Ng'alulayization part 4. Ndakhutila zonse zomwe mwanena ma Sister ❤❤🎉🎉. My God bless u.
Chemwa mukunena zoona ndithu we need people like you in this movement
I just like u mah received your flowers ❤❤
Well said
You are a good advisor
Very true
Auzeni Chemwa, more 🔥 🔥 🔥 🔥 🔥
Work hard so that tomorrow Wii be better
Mama wayowoya uyu, tiyeni titolepo apo kamoza
Very honest indeed
Osaopa Osafooka ,SKC mentality, ❤❤❤
Love you my sister ❤ 💓
🙏🙏🙏
Mawu
Well organized woman,ndakukondanitu mayi
Bravo Abiti Manile
Mai mwalakhula bwino kwambiri, my good Lod bless you
Mai ndani paja, umayitha dzedi and keep it up
Keep it up
I think zolakhula izi ndizimene zikufunika zomanga osati zomasula
Mai awa akanakhala pafupi ndikanawapatsa 10 thousand kwacha yokha...
Kungobwera poyelatu osabisaso khope ayi
Uchitsiru mukupanga nonsenu kuchipaniko zikungosimikidza kuti UTM inali Chilima, ndipo kufa iye palibe chatsala.
Udolo ongakhala osokosa mma social media basi, Commission of inquiry la tsegula zipata kuti muka pereke ma umboni mulinawowo koma kuli ziiii, kumango bwetuka pa social media basi.
A big applause to Marry Chilima and family for excluding herself from this shit 💩. She remains a woman of integrity and class.
My sister ❤❤❤❤❤
Zoona zache mama ndakunyadani kwambiri
Mai mumatha heavy
Uyu nde ndi akweni eni eni
Koma eeeee
Eeeeeee iwe umatha
Ufiti anthuwa sister
Eeeee lovely mom ❤❤ ulemu wanu ... Ndeno mwati amavina gule wanji paja
Kadigong'o
Kadii kadiii
💯
Ma desciples a yesu amene anali ndi yesu sanatengere utumiki patali amene a anate gels utumiki patali anali Paulo amene sanagwire tchito ndi yesu hi mm odzimodzi amene a gapititse patsogolo ndi kabambe koma sanagwire tchito ndi saulosi chilima
Ndasitha maganizo
Ulemu wanu mama mwayankhula bwino
Rest well Biyeni
Atsogoleri akumalawi amaziwa kuti anthu ambiri ndi ambuli kuziwa zinthu ndi chifukwa chake amatiseweletsa iwo amazitenga ochenjera
Sister mwanena mau chilimbikiso, Akabambe akukwanila manganyayu ndi dyera
Malawi wanga
Yebo
Osati kumoto, koma kuntoso, osamaphwekesa manganya. PA , sindikuziwa manganya amugula
Mumakwana sister magule nose mukumakhara mundare ya MCP mwazolowera kudya khuku yongoitokosa konyera ndikumadya ndi chifukwa chake chilope chimakupangani ndiye uziaopsesa anthu ziko lino ndi lagure tazingodyani nkhuku zobisalila achaene ake akudwa chiteze inu muli busy kuwabera ndipo gule Alibe chisoni ndichifukwa chake namapwala chakwera sakuopa panalipo osaopa alikuti ndizosiilana iwe chikangawa usinthe manyi ukudyawo reka Niti reka asa pajatu pali mwambi oti ng.oma yosona tsichedwa Kung.ambika wasala pang.ono
mumakwana mama ndipo simukunama mumwa chan pa bill yanga
Empty vessels makes a lot of noise
Mofaya sister
Manganya akulankhula za kuswa malamulo pa convention
Chilungamo chenicheni mama
A police ake ofoila ngati amenewa makape azilandila mk50.000 pamwezi basi osauka
Usitu samakondedwa Ku mj central palibe amene amamkonda ndi osokoneza
Mayi mwanena chilungamo
Aunt mukunena zoona mcp ikuononga cina ciliconse dziko muno ciliconse angolowetsa ndale.Ndipo mcp ndi cipani ca a fitidi.
KKKKK next conversation muzaimile sg wathu or pablicty mayi inu ndi 1 kkkkkk
Pitilizani mai kukamba chilungamo osafowoka osatipa
Koma amayi inu muri ndizelu kwambiri mukunena zoveka manganya ndi fisi wapenga ndi drama hule yamuthu
Akulankhula chilungamo
Auzeni ngati akufuna akanangotuluka chipani ichii
Iwe,.. tazngoplayer ma videos,. Zolongolora zakozo sizikoma,..
Zoona
Mayi wabwino uyu
Muuzeni Manganya avetsetse
usi analowa chiwanda
Eeeeeeesh
Kadigong'o kkkkk ndazikonda
NDIPO MANGANYA NDI JUST A VICE PRESIDENT. PRESIDENT WA UTM ANALI SAULOS KLAUS CHILIMA. .NDIPO A BAKILI ANATI VICE PRESIDENT NDI WAPAKALIYALA. IYE WAPAKALIYALA SAYENDETSA NJINGA NDIYE MANGANYU ALHALA BWANJI WOYENDETSA UTM .? PANOPA PRESIDENT NDI DALITSO KABAMBE. BASI AMENE ANTHU MADELEGATES AMUSANKHA NDIYE MANGANYAYU INJUNCTION YAKE ISACHITIKE KULETSA KUTI KABAMBE SIPRESIDENT WA UTM
That's it mama
Channel chako ukumapeza nkhani mochedwa
Nkhaniyi ndiyakale taponya Chifukwa zomwe akamba zephelezela apapa
Amai Abiti William nkhani yabwino
Inu osaponya nkhan zakale inu azanu anaponya kale tinaionela
Eti eti amwene,inetu ndimaona ngati ndi latest kkkkkkkk
Kkkkk sorry
Kkkkk sorry zativuta tivomele
Mukutinyasatu mukuponya nkhani zakale
😮 zakarekare izi zikumveka
Ndizakale ndipo tanenaso poyamba. Zomwe analankhula zaphelezela nde taona kuti tiponye
Prophet kwayani aaa ndi hule uyu nanuso aaa
MCP is a mighty party. It is not a facebook party. Watch ur space madam.. musathe mau muchita manyazi mawa lino mama
15:56