Koma Moyo ndi ozuzadi ndani wandale adzathetse Mavuto ku Malawi kuno osewa akuba, kupha ndi kuwononga chifukwa Osewa amasamba pa dziwe lamwana wachiwonongeko, wokhulupirira mzanga tiye tichenjere paja paja angakhale Yesu Khristu adakhala moyo wozuzika chifukwa cha ulamuliro womwe tikukhamowu, tsoka wokhulupirira mkono wanyama
Kanthu nkako 😂😂😂😂 ine sindikupanga nayo chikwanje changa ndichophera boma kkkkk sichifukwa kuti ndine mchewa mmmm ay 🔈🎵🎧🎛️🎶📘📹🔵🔷💠🔘🇲🇼 atangoti one party system chipani Nd chomwechi chadziko la Malawi bc the blues
DPP woyeee!!!!,Boma ndilomweli sitikusintha km chomwe tisinthe ndi wolamula bomali bac,2025 DPP ibwelere pa chiongolero bac,APM 16 September 2015 my vote.
Chsnkho chko mum mtima malo relax and enjoy ur life dont angry for nothing koma moopa Mulungu bola zaku famiry osaufe timadya fertilizer otchip koma Chakwera hahahaha kusapotera sstana weni weni
From Lilongwe abetcha Lawyer iyi nyimbo anyapula azimai a sendera keep 🔥🔥 burning 💯🇲🇼💯🔥🔥2025 APM khaa
Or mwana wa dzaka 3 akuwuzani. Kuti chipani cha smart , chokoma , chonunkhira koma DPP l ❤ professor.
Pa 100percent anthu 99 akuti abetcha lawyer ine ndindani kt ndikaleke kukavotera aPeter
Basi abetcha loya yomweyo 😂😂😂❤
Nanga ife ndindan bas gonkonko@@JusticeNyirenda-y9e
Highlights
Abetcha lowyer!! Apm woyeeeeeeeeee
Ineso kuthani kuti isakale abeche lwoya 😂😂😂😂
Apm my vote❤❤
Koma zingatheke wamzelu ngati ine , munthu ozindikila ngati ine ndizikati kwachaaaa 🤣🤣🤣 mutu wanga ukugwila ??.
Asiileni anthu anabadwa mopepelawo azisapotela opepela amzawo
Mbumba za Chakwera ai panja penipeni koma Sendera sisters well organized
Kodi kulibe mankhwala oletsa kukonda Dpp fwa nde eeee its getting out of hand 😂😅😂😂
Kkkkkkkkk
Mmmm abale mu DPP muja muli kenakake ndithu mtima osakhala pansi zoona eee
Ndli nao broh
Inenso zundidabwisatu..thot am alone 😂💙🧢🧢💙
😂😂
A peter abetcha lawyer💙💙💙💙💙
PRESIDENT NDIPITA MUTHALIKA BASI🎉❤😂
Vote for APM
Dpp boma ilo 💙💙💙💙💙💙ndikakhara sindkuona wina oposa peter
I love dpp woman song humble woman god bless you all
Zinazo zakudambwe ingomvani sound azimayi owombera mmanja nyau
Kkkk koma kunena zoona dpp nyimbo zokha ndi one mmm
Dpp boma 2025❤❤❤
Simungafikere wabetcha lawyer
Abetcha lawyer more fire❤❤❤
Amwene chipani chinantha ichii Apeter abecha loya bc palibeso kuchitira mwina adzipakira amenewo nthawi yantha chipani ndi DPP💙💙💙💙💙💙💙💙💙
Chonde azimayi a sendeza aphuzitseni azanu kajambulitsidwe ka nyimbo osati kungotola zithuzi zansonkhano nde zichani 😂😂😂😂😂😂 dpp❤❤❤❤❤❤❤
DPP women good creative and voice well formed
Azimai Achipan changa munapeka nyimbo yabwino kwambiri Excellent
Trump wathu back in office❤❤
A Peter abetcha Loya more 🔥🔥🤣😂🇲🇼💯💯
😂😂😂😂😂 ana achepa APM my vote
A PM my vote
APeter becha loyal no one 100%
Yooo DPP Osanama umati munthu ukamavera nyimbo zake nthupi limachita kugwidwa Dzazi kuti ndinyimbo za chitimu chachikuru Koma zaenawo mmmm zauhule basi mavinidwe ake amenewo DPP mofaya basi📖🙏🏿
Nice ilike it
From BLAZIL dpp More fire 🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤
Abetcha Lowyer on my best song my vote for APM basi
Dpp more 🔥🔥
Lawyer on top
Abetcha loya ndi number 1🔥🔥🔥💪💪💪💪
Abetcha loya my vote
APM my vote
Koma Moyo ndi ozuzadi ndani wandale adzathetse Mavuto ku Malawi kuno osewa akuba, kupha ndi kuwononga chifukwa Osewa amasamba pa dziwe lamwana wachiwonongeko, wokhulupirira mzanga tiye tichenjere paja paja angakhale Yesu Khristu adakhala moyo wozuzika chifukwa cha ulamuliro womwe tikukhamowu, tsoka wokhulupirira mkono wanyama
ADAD MY VOTE 💙💙💙💙
APM MY VOTE
Apm my vote
Abetcher laywer yomweyo akane akane zinaz ndilib nthaw yomvera sndmvera za ana anjoka ine
Apm my vote 🗳
Well organized sendera
Dpp my vote ❤️❤️
Peter muthalika the president 2025 my vote
Chakwera .ndi nyatwa osati khalamba
My vote goes straight to Dr Chakwera not manyaka no opanda mano mkamwa
Chipani chayatsa moto ND Cha dpp or makaka omwe simagazi ayi♥️♥️♥️♥️♥️♥️♥️♥️
❤❤❤❤
Adadi abetcha royayo ndi vibe 🙌🙌🔥😊
Kwambiri
❤😂😂😂❤❤❤❤ nyimbo za bwn ndi za DPP
💙💙💙💙💙💙is better than others 2025 APM my vote DPP yomweyo 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Abetcha lawyer is namba 1 ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ zinazo zipite kuchikangawa 😂😂😂😂
😂😂😂 Gogo ati mulu wa somba uli pa 10000k chakwera alibe vote
Ndife ana a dad🔥🔥🔥🔥
Loya waketu ndi Yes akufuna kutisimikizira amene anawoma chisankho chomwe amati chinaberedwa chija
Kkkkk koma zoopsa tikapuma kumwamba...ambuye atithandize matsiku osilizawa
Apeter omweo dpp woyeeee❤❤❤
Ndili ku Mozambique koma abetcha loya DPP number 1❤❤❤ osayiwara
Dpp💙💙💙💙💙💙💙💙
Abetcha loya ndi one Kkkkk inayo ikindivekera ngati ya azimai achisamba nyau😂😂😂😂😂
Apa simwadziwano Kuti abecha Loya sinyimbo wambayi DPP
Apwetekana sure 😂😂
Kanthu nkako 😂😂😂😂 ine sindikupanga nayo chikwanje changa ndichophera boma kkkkk sichifukwa kuti ndine mchewa mmmm ay 🔈🎵🎧🎛️🎶📘📹🔵🔷💠🔘🇲🇼 atangoti one party system chipani Nd chomwechi chadziko la Malawi bc the blues
Olo mwana woti ali mmimba mwamayi ako atha kuchunga ndi voice yokha kuti DDP ndi number 1
A etcha lawyer nyimbo yabwino kuchokeraso ku chipani chabwino ndi president wabwinoso..DPP moto kuti Buuùù!!!
Angavotele mcp mutuwake sugwilantchito ay
Nde tivotere nkhalamba Yanu yopanda Mano yija ukunama boma stikusintha ili
A betcha lawyer ija mmm sizaphada
Kkkkk chipani chomwecho chakwera my vote 🎉
🎉🎉🎉🎉🎉 moto ku apm ❤❤❤
DPP woyeee!!!!,Boma ndilomweli sitikusintha km chomwe tisinthe ndi wolamula bomali bac,2025 DPP ibwelere pa chiongolero bac,APM 16 September 2015 my vote.
From Namibia 🇳🇦 DPP ❤🎉🎉🎉
Ine Dpp nde sindingayisiye 🎉🎉🎉
Abetcha lawyer nyimbo yovuta kwambiri
A betcha lawyer oyeeeeee!!!!!!!!
Abetcha loya yemweyo kkk Dpp boma 💪
Ife Mr busy za music tilipenazo tchito 2025 dpp ukulamula oroko yamikani ufune usafune ndipo simuzabereso vote kulibe
Abetcha lawyer mbambande
Palibe chomwe dpp angabweletse cha nzeru mcp idalowa chifukwa chakulephela kwa Peter lero tivotelens Peter, tipite chitsogolo munthu uja wakula
Kanthu nkakodi osamangokhalolira kupempha ndalama za kunja nkumangobanso😂komanso kuimba za nkhalamba zagwirizana bwanji😂😂
Koma ine DPP inandidyesa kondaine live😂😂😂😂😂😂😂
watching from Zambian Dpp number one .muthalika in states house next yrs
Kodi a congress akuyimba zichani nyasi zenzeni abetcha lyer nomber one❤❤
Dpp tokuti bhuuuuuu
Muyamike malemu Chilima munali ndani?
Agalu inu dzinyau.
Dpp ikutenga boma ndipo zobera ma vote musaganize ife sitikulora.
Ndipo mwene simukunama anali ndani agalu amenewa
Ñdipo kulibe kubera akhauladi
Broh fuula mwina amve kupnda Chilima asatan awawa km amudzwe Mulungu
Enawa ndi chioda osati nyimbo
Abetcha lawyer is the best 👌
E komatu azimayiwa amayimba jerous down
Peter wabetcha roya yomweyooo
Ndili ku Moçambique koma abetcha loya moto moto DPP
Wamisala samadziwa kuti iye ndi wamisala amamuuza anthu ndiduse nawo mchika ngawa
Sindimasapota zipani zakubannja chakwera it's my vote
Tiyeni uko 😂😂😂
That's why mukufa ndinjala😅😅😅😅😅😅 dpp my vote 😊
Chsnkho chko mum mtima malo relax and enjoy ur life dont angry for nothing koma moopa Mulungu bola zaku famiry osaufe timadya fertilizer otchip koma Chakwera hahahaha kusapotera sstana weni weni
Ambetcha ndi one😂😂😂
Ndipo live apeter 2025 boma oloooo🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Kanthuuu mkakooo❤️❤️❤️❤️🔥
Ndene wa mcp koma ndiza votera dpp 😂😂😂
Dpp ndimene ikubeba not zanyawu za chikangawazi😂😂😂😂
A pm My vote
Ndipo zoona mcp idatha apa siizawonekanso... Odi ukooo adadi aduseeee
Abetcha loya❤❤❤❤
More 🔥 BLUE!!!!!!!!!
Adad my vote 🔥🔥🔥
Aaaa za kudabweizi DPP ndi number one
Posatengela udani Dpp nimo to🎉🎉 ine waa!! mcp
Nice song from DPP woman
Kod akati kwacha amayakha bwanji ana abingu tapunduka😂😂😂😂❤💦💦💦💦🗨️
Nyimbo za DPP moto kuti buuuuu dpp ndichipani chafukodi or m'zimu wa Big ukukondwa uliko kut chipani changa muli moto osowa othimitsa