BREAKING NEWS ZACHIKASO KU ZOMBA MOTI TALUZASO ENA KUMENEKU ZA CHISONI

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 27 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 89

  • @AlinaChauluka
    @AlinaChauluka 2 หลายเดือนก่อน +10

    Mulungu wakwiya ndizomwe anachita chakwela pothawa ntchito ya mulungu Sono mawu amati ndizapanga ana chifukwa chakholo ndiye ife tikulangika chifukwa Cha chakwela Malawi amzanga chonde tisavotele chakwela tikatelo mulungu atikhululukila azimulanga yekha ndikusamvera kwake

    • @MaryBanda-n3h
      @MaryBanda-n3h 2 หลายเดือนก่อน

      @@AlinaChauluka kwambiri

    • @Yoxym
      @Yoxym 2 หลายเดือนก่อน

      Awuzeni anyani aanthu enawa😢😢😢😢😢😢😢😢

    • @DL2004-x9q
      @DL2004-x9q 2 หลายเดือนก่อน

      Ndipo tikulangikanso chifukwa choti ndife anthu otengeka kwambili. We’re part of the problem and this is the time to make good decisions

    • @MaryBanda-n3h
      @MaryBanda-n3h 2 หลายเดือนก่อน

      @@AlinaChauluka kutengeka Ngati zing'ono aaaa

  • @JosephBeyadi
    @JosephBeyadi 2 หลายเดือนก่อน +1

    😭😭😭😭😭😭😭Abuye muyichitire chisoni mizimu ya anthu onse atisiya lero kuzera pa ngozi kuti ikause mutendere osatha🧎‍♂️🧎‍♂️Ame

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 2 หลายเดือนก่อน +5

    Bushiri, Chakwera ndi nduna zake ndi afiti oopsa kwambiri ulosi wa Grace Chinga ananena kale

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 2 หลายเดือนก่อน +2

    Mizimu ya anthu aku Zomba iwuse mu mtendere kwathu ku Zomba 😢😢😢😢😢

  • @ephraimphalawala4720
    @ephraimphalawala4720 2 หลายเดือนก่อน +3

    Our Heavenly Father protect our beautiful Nation Malawi 🇲🇼 in Jesus Name. AMEN

  • @IdahMphaya
    @IdahMphaya 2 หลายเดือนก่อน +3

    Mmmmm koma ambuye.tichitilen chifundo ana anu tili pamasawuso akulu kwambili😭😭😭😭😭

  • @EmilyBanjachikwatula
    @EmilyBanjachikwatula 2 หลายเดือนก่อน +6

    Zoona ma driver mukumanyanya kuthamangitsa mukudziwa satana akumalowa njila zosiyana siyana

  • @SueWahna
    @SueWahna 2 หลายเดือนก่อน +1

    RIP grace chinga khondo ija tikuyiwonad ambuye tichitilen chifundo 😢😢😢😢

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 2 หลายเดือนก่อน +2

    God have mercy upon our Nation 🙏🙏

  • @wendaemily3179
    @wendaemily3179 2 หลายเดือนก่อน +1

    Lord have mercy

  • @IssahAluba
    @IssahAluba 2 หลายเดือนก่อน +1

    So sad

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ambuye atithandize

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 2 หลายเดือนก่อน +4

    Abale ngozi zimenezi ndi zamulungu kapena ndi Satana alowererapo ambuye lowereranipo dziko lathu zoona tizitha chocho 😭😭

  • @NoohNowa
    @NoohNowa 2 หลายเดือนก่อน +6

    Chakwela akuziwa bwino zimenezo

  • @StephanoMaganizo
    @StephanoMaganizo 2 หลายเดือนก่อน +1

    Inah lillah wah inah ilaih lajilunah Amen 🙏

  • @GanizaniKamvazaana
    @GanizaniKamvazaana 2 หลายเดือนก่อน +1

    Nda chakwera omwera amenewo Apereka sbe komatu eee ayi zikomo

  • @InnocentNitamanMilanzi
    @InnocentNitamanMilanzi 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zoonadi Anthufe titha chifukwa chakwerayo magazi a bushiri sanamalize kupeleka ambuye mutimenyere nkhondoyi pa ife tokha sitingaikwanitsa

  • @FunnyKatchenga
    @FunnyKatchenga 2 หลายเดือนก่อน +1

    😭😭😭😭😭😭

  • @AlubiBilly
    @AlubiBilly 2 หลายเดือนก่อน +1

    Timufunse bwinobwino wapita ku Germany uja akudziwa po kathu ngozi zimenezi chifukwa chani tikudziwa kuti kunja kuno mulungu alipo koma . Izi zikudabeitsano

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 2 หลายเดือนก่อน +5

    Timpephe Allah kuti zikuchitikazi kuti zisachitikeso

  • @DanJohn-ws5gl
    @DanJohn-ws5gl 2 หลายเดือนก่อน +1

    Tikupita Ku December N,sembe zipelekedwe ambuye akuendeleni ana anjokainu😢😢😢

  • @MayesoKalupha
    @MayesoKalupha 2 หลายเดือนก่อน +1

    MwaiwA kukasungu Abwana

  • @IdahMphaya
    @IdahMphaya 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mmmmm zovuta nditha koma zonse akuziwa ndiambuye

  • @EllahEllah-hu7hi
    @EllahEllah-hu7hi 2 หลายเดือนก่อน +1

    God have mercy on us malawian

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 2 หลายเดือนก่อน +1

    Chipani Cha nthukuta ndimwazi komwe wapitako ndikomwe akukanthira msembe wapita kopaga zimenezi chifukwa maulendo ake timadabwa kuti ndiwotani apa zikuwonetsano zomwe akukapanga akukatenga mphavu zakumidima

  • @LucyLaisani
    @LucyLaisani 2 หลายเดือนก่อน +1

    Koma ngati ndi munthu akupanga zimenezi akanakhululuka 😭😭

  • @memorybanda9277
    @memorybanda9277 2 หลายเดือนก่อน +1

    Koma abale 😭😭 this is too much

  • @loveshabani8834
    @loveshabani8834 2 หลายเดือนก่อน

    The main problem is poor roads in Malawi

  • @aliwilson7705
    @aliwilson7705 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kwasala chakwera akamabwera kumene aliko naye ndege yake igwe naye afele pompo

    • @EnifaJosafati
      @EnifaJosafati 2 หลายเดือนก่อน +2

      Kkkkk anthu atopa alidi ndikhalidwe loyipa

    • @Priscilla-f9n
      @Priscilla-f9n 2 หลายเดือนก่อน

      Kkkkk it cannot happen

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 หลายเดือนก่อน +4

    Chakwera atule pansi udindo anatenga ndalama kwa bushiri kut abweza mwazi

    • @wizzyamick1696
      @wizzyamick1696 2 หลายเดือนก่อน

      Tikufuna kuno bushiriyo abwelele kuno

    • @Yoxym
      @Yoxym 2 หลายเดือนก่อน

      ​@@wizzyamick1696nkaona peter ankadana naye

  • @YankhoGuza
    @YankhoGuza 2 หลายเดือนก่อน +1

    Chikangawa akupeleka nsembe ndalama zomwe anatengazo ndiye akubweza magazi zovuta sizochokera kwamulungu ayi komano sataniki yalowa mudziko lamalawi chifukwa chachakwera

  • @AlubiBilly
    @AlubiBilly 2 หลายเดือนก่อน +1

    Makamaka chikangawa akudziwapo kenakake maka kumene wapitako akupeleka msembe ku Italy 🇮🇹 kwa papa

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 2 หลายเดือนก่อน +1

    I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa

  • @PeterMPWWailes
    @PeterMPWWailes 2 หลายเดือนก่อน +2

    Paja chakwera Ali kotenga mphavu ku Nice matter tiyembekezere zimenezo tipephere Kwambiri ndipo mosafooka

  • @racheldongolosi2252
    @racheldongolosi2252 2 หลายเดือนก่อน +2

    Eshiiii Koma abale zomvetsa chisoni 😭😭😭😭😭😭😭Ifeso kwathu Kukasungu TA santhe kwapangikaso Ngozi mmawa walero anthu 26 amwalira pompo onse😭😭😭😭

    • @FloraBanda-w7t
      @FloraBanda-w7t 2 หลายเดือนก่อน +1

      😢

    • @OmexAkim-ww9nd
      @OmexAkim-ww9nd 2 หลายเดือนก่อน +1

      Sorry kwambili

    • @eunicesaiti
      @eunicesaiti 2 หลายเดือนก่อน +1

      Pepa Rachel, Ambuye akukhuzeni ndi mizimu ya abale iwunse mu mtendere. 😢😢😢

  • @Mavitoabdulla
    @Mavitoabdulla 2 หลายเดือนก่อน +1

    Chamanga chimene mumalandi komaso dzikolo likulamulidwa ndi BOMA lamagazi

  • @ColbyNkhambala
    @ColbyNkhambala 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zaonjeza mulungu alowelelepo

  • @IbrahimUseni-p8f
    @IbrahimUseni-p8f 2 หลายเดือนก่อน +1

    Satanic chakwela akufuna magazi,,president wachilowere miliri,,,frede,covid,njala,ngozi,,eee koma amalawi tiona zoopsa

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf 2 หลายเดือนก่อน +2

    Mulungu akhale ndi onse okhudzidwa. Mulungu achiritse dziko lathu. 😰😰😰

  • @marthaP-o2o
    @marthaP-o2o 2 หลายเดือนก่อน

    Tikulangidwa chifukwa chazitsogoleri even ana a Israel anakathidwa ndi nthenda tchifukwa cha utchimo wa Davide

  • @AlickJinamu
    @AlickJinamu 2 หลายเดือนก่อน +1

    pepani mizinu yazibale atuyiwuze mutendele

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mu dziko muno mwalowa mizimu yachabe

  • @eliaskachali-xn2ve
    @eliaskachali-xn2ve 2 หลายเดือนก่อน +3

    Malawi wakana eish tili pamasuzgo yakulu

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w 2 หลายเดือนก่อน

      Mmmmmmmm chimenechi ni chani Malawi walakwa chani tinalakwanji 😂😂😂

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 2 หลายเดือนก่อน

    tiyeni timuthamangitse bushiri ndi chifukwa chake peter wamunthalika amamukana kubwera ku Malawi komanso kuyambitsa church chake koma anthu amaona ngati angomuda komanso nonse amene munalandila zolandila zake za bushiri mudziwe kuti zomwe amanena boni kalindo kuti osamango susuka chifukwa choti tikuvuka zina mukulandilazi ndi za asatanic pano azathu aku South Africa anapumatu zangozi bushiri atamuthawitsa chakwela

  • @OnyxNyirenda
    @OnyxNyirenda 2 หลายเดือนก่อน +1

    Eish Chikangawa is a big vampire 😠

  • @JoyceBanda-k8t
    @JoyceBanda-k8t 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mcp ikufuna mamagazi akapereke kumidima

  • @khalifacalvinajass9998
    @khalifacalvinajass9998 2 หลายเดือนก่อน +1

    Eeeeeeeeee zosayenda

  • @MalitaKapesi
    @MalitaKapesi 2 หลายเดือนก่อน

    Mmmmm why malawi!!!! Ambuye tichitileni chifundo

  • @MahometAli-e8w
    @MahometAli-e8w 2 หลายเดือนก่อน

    Ngati ngoziyo yochokera kwa Mulungu basi tengani abwinoo mukhale nao tengani oipao avindikireni pansi kulisadabuza dzikoli lipangeni upset mukhale nao abwinoo

  • @ZioneMkwanda-y6i
    @ZioneMkwanda-y6i 2 หลายเดือนก่อน

    Ngozi izi osati chifukwa Cha speed Ntanyiwa ayi satanic yakula akufuna mwazi Bushiri nda china Chakwela ndi gulu lawo pamodzi ndi ma Artist achinyamata satanic ndaame akupanga izi

  • @LucyKamoto-li9ob
    @LucyKamoto-li9ob 2 หลายเดือนก่อน

    May the departed rest well in Jesus Christ name

  • @binalidjeyshabahzombamalawi
    @binalidjeyshabahzombamalawi 2 หลายเดือนก่อน +1

    Abwerere ku south Africa atitha

    • @DanJohn-ws5gl
      @DanJohn-ws5gl 2 หลายเดือนก่อน +1

      Ndipo ine ndayankhula kale Kuti zinalakwika amuthamangisa Ku Jonz kuja atimaliza 😢😢😢😢😢

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 2 หลายเดือนก่อน +1

    Chifukwa timamukana bushiri ku malawi ngati simukudziwa mudziwe kuti bushiri ndiowopwa musatsekeke maso amalawi, olo chakwela akumaelekedwa simukudziwa kodi?? Zimenezo ndizasataniki bushiri wayamba zionetselo zakeno, atanyiwa muzidziwe Zimenezo

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 2 หลายเดือนก่อน

    simbo yomwe wakagwila chakwera komwe wapita kuja ngat mwaonetsetsa tisamale

  • @marthamusukwa7935
    @marthamusukwa7935 2 หลายเดือนก่อน

    May their souls rest in peace, Jesus comfort the families please.

  • @MacsJafali-d1m
    @MacsJafali-d1m 2 หลายเดือนก่อน

    iwe waymba kunama et ku Zomba kuli 8mls???

  • @GiftHaward
    @GiftHaward 2 หลายเดือนก่อน +1

    Koma kumalawi zikukhala bwanji

  • @MaryBanda-n3h
    @MaryBanda-n3h 2 หลายเดือนก่อน +2

    Malawi tiyeni tisale kudya Mulungu ndiwazisomo

    • @eunicesaiti
      @eunicesaiti 2 หลายเดือนก่อน +1

      Ndikugwilizana nazo , prayers needed in Malawi 😢😢😢

    • @EnifaJosafati
      @EnifaJosafati 2 หลายเดือนก่อน +1

      Zowonadi ndithudi simukunama ndazikonda kwambili

    • @SaloDavie
      @SaloDavie 2 หลายเดือนก่อน +1

      Ndipo zoonadi tikuyenera kupemphera ambuye atichitile chifundo ndithu

  • @jfj-bu5wz
    @jfj-bu5wz 2 หลายเดือนก่อน +1

    😢😢😢zovuta kwabass sorry

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zomvesa chisoni dziko rathu zonsezi koma ndi chakwera amene akupangisa zonsezi

  • @ashankagwa668
    @ashankagwa668 2 หลายเดือนก่อน

    President asatulukeso kunja , nsembe

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 2 หลายเดือนก่อน +1

    At wanjinga

  • @fidelixdezembro4599
    @fidelixdezembro4599 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mwachuluka a satanic ku Malawi

  • @KachaliKaunda
    @KachaliKaunda 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zomvesa chisoni

  • @luciarashid1961
    @luciarashid1961 2 หลายเดือนก่อน +1

    😢

  • @MaryJefry
    @MaryJefry 2 หลายเดือนก่อน

    Chakwera atitha ndithu

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde 2 หลายเดือนก่อน

    RlP 😭😭😭😭😭🙏🙏🙏🙏

  • @DKMWALE-ew3lp
    @DKMWALE-ew3lp 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mmmm

  • @MaryBanda-n3h
    @MaryBanda-n3h 2 หลายเดือนก่อน +1

    Koma yaaaa

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g 2 หลายเดือนก่อน

    😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @nessiemfunie
    @nessiemfunie 2 หลายเดือนก่อน +1

    😭😭😭😭😭

  • @spargomw
    @spargomw 2 หลายเดือนก่อน +1

    😭😭😭😭😭