BON KALINDO 28 OCTOBER 2024 KUNG’ALURA PA MONDAY

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 27 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 27

  • @GolosiMalapata
    @GolosiMalapata 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +6

    Bon kalido ine kadakonda anthu amenewa ataziwona chifukwa tatopa nawo akudwalisa mutu omanga munthu azikumanazo ineso ndili okozeka ndimaswa koma sitiwonekela kwa anthu

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The DC'S mwana woooopsa kwambiri akhalise Malawi chilungamo chiyende ngat madzi

  • @TalazanGamah
    @TalazanGamah 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Respect u Mr DC

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Our beloved ministers: defence and home security please safeguard us from cold wars backsliding our democracy.We are no longer at contentment here in Malawi.

  • @CathreenKadwala
    @CathreenKadwala 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Apa ndiye mp wakumachinga anamanga atangolankhula kokha ndi awa awauza anyamata akwasundwe kumenya anzawo nawonso amangidwet

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      Ndipo brother anyanatawa awamangenso apo biii sitiinva

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Awuzeni chilungamo bwana DC we love you❤❤

  • @JohnMeleka-s1t
    @JohnMeleka-s1t 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Timaopatu kumutukwana apa nde andidziwa

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    MCP ikakutchingilani iphanipo awili kapena mmodzi anthu azitenga phunziro, muziyenda mdimipeni or ma screw drivers, this generation a MCP asatsekele njila nzake noooo

  • @khasimMusa-d3w
    @khasimMusa-d3w 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The DC mwana opanda matha tiyeni tithane nawoo

  • @IdahMphaya
    @IdahMphaya 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zowonadi kuno kuphalombe anthu akubwezedwa omwe alibe ld

  • @IdahMphaya
    @IdahMphaya 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma wado wado samanva mmmmmm akufuna ayambise nkhondo ameneyi zonvesa chison ndithu

  • @DoricaGoweka
    @DoricaGoweka 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bon Kalindoooo the DC 😅😅😅😅

  • @jamessheki4293
    @jamessheki4293 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    MCP yatikwana,mpaka nkhondo

  • @Giftjames-k4r
    @Giftjames-k4r 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Live in mocambique

  • @HassanSaid-q8q
    @HassanSaid-q8q 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi amenewa a mcp akufuna nkhondo kapena chani sono mungonenatu tiyambepi kusema zibonga

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi minister ndiwakwathu Kwa mvumbwe

  • @ThoccoChimbali-h6g
    @ThoccoChimbali-h6g 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndipo anali ndani chimwendo, munthu amagulisa samoosa wa ngumbi

  • @BrianMuleke
    @BrianMuleke 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tizawakhudumula 😂😂

  • @JeanKabotolo
    @JeanKabotolo 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😢

  • @AdamAllen-s8p
    @AdamAllen-s8p 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The d c

  • @MikeLodzi
    @MikeLodzi 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    a mcp akufuna ayambitse zipolowe mdziko muno koma sibeino

    • @jamessheki4293
      @jamessheki4293 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Anthuwa ndi oyipa

  • @TapiwaTaulo
    @TapiwaTaulo 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😂 umakwana

  • @AlexanderMateketa-i8l
    @AlexanderMateketa-i8l 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Asambwaze zisilizo tikazichotsa m'boma zikunama manyi a mcp wo tithana nawo mbuzizo