Brother you are real Malawian who knows the good culture of the Malawians for example you have got good behaviors in questioning the people you are number one I learn more things if am watching this platform God bless You From South Africa
Amalume Asapemba ndi mutu wamitu kwathu kumalawi kusatengera magesi okha tilindimazi ochuluka koma njala ndikumakhalabe vuto losatha ayi asogoleri a ziko lathu palibe ndithu ndipo sindikuziwa kut ndiliti limene tizapeze nsogoleri wanzelu ngat a Sapemba.. this man is not just a man but is a Master Plan
Iam just happy that the divided plastic plates za apple green zimene akudyeramozo zikupangidwa ndi company yathu ku alberton north and yeah tinkadabwa kuti bwanji zimapita kuti mbalezi now we have the answer kkk
Brother you are real Malawian who knows the good culture of the Malawians for example you have got good behaviors in questioning the people you are number one I learn more things if am watching this platform God bless You From South Africa
Iam to make my comment, congratulations to my Brother, we are in the same decision.
You are the man of VISIONARY POWEEER
Jowabu ntchito mumaidziwa very friendly, funny, and serious
Malawi yonse ntolankhani wabwino ndiuyu
I heard the guy died pangozi yapa mseu some weeks ago 😢rest in peace 😢
Yes i witnessed the incident😢
😮which guy akuyankhura apayu?
It's true?😢
@@Geekmus😢 It's true?
May his soul rest in peace Mathews sapemba
Amalume Asapemba ndi mutu wamitu kwathu kumalawi kusatengera magesi okha tilindimazi ochuluka koma njala ndikumakhalabe vuto losatha ayi asogoleri a ziko lathu palibe ndithu ndipo sindikuziwa kut ndiliti limene tizapeze nsogoleri wanzelu ngat a Sapemba.. this man is not just a man but is a Master Plan
Achakhaza mulimkankho kkkkkk alike the programme and am impressed
Joab ndiwe ntola nkhani wabhoo🎉🎉🎉
This guy is living my dreams🙌🙌🙌
I enjoyed the interview ,thanks joab
Great program, Joab! Quite insightful! Thanks 🙏🏻
Now this is substantive
This is Gold
Ur a choice one in this generation, abig chifundo chanu ndi phindu lathu ena keep on doing it ,may the Lord bless you
Thanks mr Mathews to share your story woow
Amwene, Akulu amenewa adamwalila Friday last week pangoz ya galimoto
Aaaaa zosayendatu, zoona koma? Program ikuonetsa 4hrs ago@@MazonMatias
@@MazonMatias Zosakhala bwino ndiye interview imeneyi anayipanga liti ndakhulupira anthu abwino sakhalitsa 😢😢😢😢
Iwe ndi one Joabu mmmmh Ambuye azikudalitsani Abambo awa akapume mu mtendere wabwino sakhalitsa ai ❤❤❤❤❤❤
Ur effort is well appreciated.
Nice motivation ❤❤
Beautiful
This great man passed away on 11th October, He was guy with vision. RIP
What happened to him
Car accident @@ericmarleyMw
😢 so sad
Joab 😅😅😅 iwe ndi role model wanga aise eeeeish journalism mwaiwe idakhazikika
Ambuye ndi wachikondi kukhala ndi anthu ngati amenewa ku Malawi ambuye akudalitseni nthawi zonse chifukwa chikondi Chanu 🤛👏👏
May God bless you
May this great man rest in eternal peace❤
Much interesting🎉🎉
Ndakondwa kwambili kumvela program imeneyi mulungu akudalitseni
I want to learn more Mr joab
inspiring
The guy he is living my dream 😊
Vert impressive big👏👏
Iam just happy that the divided plastic plates za apple green zimene akudyeramozo zikupangidwa ndi company yathu ku alberton north and yeah tinkadabwa kuti bwanji zimapita kuti mbalezi now we have the answer kkk
Congraturation mathews msuliza
I enjoyed this interview
I have learned alot
Ulemu wanu Mr chakhaza
May his soul rest in peace indeed
My dream ❤.
Mmmmm koma ndizachisoni kumva kuti munthu wamkulu uyu anamwalira 😢
Sapemba is great thinker
Rip MR MSULIZA 😢😢😢
Rest in peace mr sapemba. Mulungu salakwisa
Thanks boss more interested
Joab sambani mmanja mmesa mwamaliza kudya kkkkkkkk msima ikukakamira mmanja❤❤❤❤❤❤
Nice interview
You have inspired me bro
Zomvesa chison kuti akuluwa adatisiya pangozi yagalimoto pakanengo bt he's is grt thinker
Imagine 😢
Nice❤❤
Eeeee awa mindset amayidziwa bwino, aMalawi imativuta ndi mind set,koma mukuti anamwali😭zosakhala bwino akanathanduza ena nzeru
Mwachita bwno kupanga posti kupangira ife amene sitinaonere etu chakhaza umakwana iweyo ulemu wako iwe ndi dolo
Achaza zikom kwambili mwatitengera kwa munthu ofunika kwambili
Fuso limayankhidwa mozonga zedi. koma very helpful anyway
Yes god bless you
Ada awawa amandiwa za Jowabu frack Chakhadza ndi akamuna mulungu akupatseni moyo wa utali
Ndikukusatirani ku choka ku Rumphi
Nice
He was my student at Madisi Secondary School. He was teaching in my home village Kaphaizi.
Oooh really? Powerful
😢so sad and rest internal peace
Brave Man
Achakhaza joab mulungu akusungeni timakunyadira i
I love the man he smokes ganja.
Kma sima iyi ikhaula
Mmm joab is too professional
Am interested with this interview. How can I get him? I have more with him
😢 so sad he was died in October
may his soul rest in peace
Ndumvad kut he was involved in an accident is it true
@@WandaGanunga-bi5ef At it's true coz this program aibweleza dzulo pa zodiac, pokumbukika nzimu wawo
@@MishelleMaseko eeish very bad he was a big brother of my childhood friend
nice bro ❤❤❤❤❤❤
Mtolankhani wozitsata ubwereko kwathu kuno ku Ntchisi.
May your soul rest in peace 😢
Jowab , umaitha koma amakuunikaniyo adya ?
Kukhala ngatidi camera man sanadye nawo kkkk
Koma nanga nchifukwa chani azunguwa amakangalika kumabwela ku Africa kumafuna kuthandiza maiko osauka chonsecho azunguwo nawonso kwawoko ndi osauka?
Chakhaza zilibwino bas mumatiziwisa zambiri
Muthu sungasawuke utavera utasatira izi
Nzungu simunthu
Rest in peace munthuyu anali dolo ka 1000
Ndikanakonda kuti mutinzitseko ntchitoyo Inu ansapemba.
koma ndikumva kuti dhalayu pano ndimalemu eti?
Yes
Koma m'kulu uyuyu ndava zoti wafa pa gozi dzana akuti anaomba track pa Mbaloni mu LL
Kikkkkkk kma yeah
jowabu uku upitaso
Adamwalira2 adha awo akuti
Munabwera ndi njala ajoab
Eeeeeee Zina ukanva anga mwala
Inu ndi one
Nde Wa camera 📸 mwamumana?😏
Kodi anamwalira asapembawa tandiuzani?
Koma Joab;kuwamana aini ake?
Masamba tudyera kuzinziri 😂😂😂😂😂😂
Pa fama pomwepo mwene
Umphawi ndiowawadi
Alendo avekere kodi mwana wachiwiri uja akuphunzira nursing ku Bunda? Akutenga mtanda wachitatu kwathu😅
Ntchunga nidende chaa kkkk
Chakhaza Frank ndi wakumudzi kwathu 😂
Koma muchita kupatsana nselu😊
Pandiwaza pa weed pooo😂😂
Do you smoke weed? Yes😂😂😂😂
Weeds is a herbal 🌿 , is very very important if use it wisely. 😂
Pitilizani ntchito yanu yabwino tadziwa bambowa chifukwa chainu
Joab amaikometsa interview
Big up bro 👌
Masamba anadyeratu ali mwana 😂😂😂😂
Sazikan achakhaza mkutha sima yaeni ake😅😅😅😅
Joab umakwana
Inu mukudya kumasangala ife tagona ndi njala koma a Chakhadza sitimatero😂😅
Is that a feeding scheme project
A Joab basi sambani manja mwankhuta kkkkkk
Ulemu wanu a mateyu