Anthu atopa ndi MCP ayamba kuotcha nsalu za MCP

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 38

  • @BawulenLuka
    @BawulenLuka หลายเดือนก่อน +4

    Ine mcp pongopha anthu 9 aja mopanda chisoni😢😢 ayi inandidesa ku khosi

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w หลายเดือนก่อน +1

    Mai wa nzeru kobasi, osangotengeka azimai ngati zitsilu ai.

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg หลายเดือนก่อน +3

    😂😂😂😂😂😂 otchani bas zilibe kanthu ife tatopa ndinkhanza

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d หลายเดือนก่อน +2

    Yakwiya ndi mizimu yomweo chikangawa 😢😢

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 หลายเดือนก่อน +2

    Kulapa machimo kumeneko😂😂😂

  • @ModesterKauma
    @ModesterKauma หลายเดือนก่อน +4

    Nsaluzo mukanapatsa anthu ena Malo mootcha

    • @DKMWALE-ew3lp
      @DKMWALE-ew3lp หลายเดือนก่อน +1

      Apatse ndani zamagazi inu izi

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน

      Akufunira anthu ena zabwino. Sungamuveke mnzako matemberero ayi.

  • @DoreenEmmanuelj
    @DoreenEmmanuelj หลายเดือนก่อน +2

    Asala mabuku a MCP

  • @damianokachingwe3531
    @damianokachingwe3531 หลายเดือนก่อน

    Hule ili lapatsidwa ndalama ndi ma cadet peza zochita azanu boma lomweli zikuenda basi

  • @ThomasHandson
    @ThomasHandson หลายเดือนก่อน +1

    Bola asakupheni muzikhala osamala

  • @TressLuka
    @TressLuka หลายเดือนก่อน +2

    Chauta alinafe osaopaaaa

  • @MussaMalon
    @MussaMalon หลายเดือนก่อน +1

    Akuchitabwino 😂😂😂😂

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน

    Kupha anthu 9 kamba kofuna Chilima? Ufiti chiyani? Ufiti ndi kusapota MCP.

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo หลายเดือนก่อน

    Zauhule basi mukhaula mulavula ndalama mwadyazo

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw หลายเดือนก่อน

    Ineso ndatuma anthu kuti awonche ndale zomphana kuba chinyengo katangale mmmmmmmmm zikhale

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg หลายเดือนก่อน +1

    Masiye masiye taotcha zovala zamalemu mcp 😊

  • @stalickkafera3454
    @stalickkafera3454 หลายเดือนก่อน +1

    Nsalu zonsezo mumavara nokha ndiye kuzikonda komwe sikukufunika kumeneko
    Ndine inuyo u president mungaunthe

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba หลายเดือนก่อน

    Za ulelezo umaotcha palibe choluza .

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo หลายเดือนก่อน

    Midatani kutuluka Kale muona nyekhwe

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo หลายเดือนก่อน

    Mwabaiba ndiye mwaona kuti thawi yakuthelani ndiye mudziotcha salu tsopano

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj หลายเดือนก่อน +1

    Zakalekare izi

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt หลายเดือนก่อน

    Akulu akulu ananena kut chomwe chachita waka chilipopo mcp kuyambila kare makolo afutika nalo boma limenero komaso pither amanena ngakare atupere chimodzimosi athu inu osafa lero

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb หลายเดือนก่อน

    Mwachita bwino mayi.ife tinakuuzani zachita bwino tsopano mwazindikira nokha.

  • @BillyMhone-jp3kn
    @BillyMhone-jp3kn หลายเดือนก่อน

    Mcp si chipani choti chizilamula

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw หลายเดือนก่อน

    mwati ndinu mayi ndani

  • @JullieTsoka-fu2vz
    @JullieTsoka-fu2vz หลายเดือนก่อน

    Zikatero zimatathauza chani osangopatsa anthu ena bwanji?komwe mumkalandilila msalu zonsezo tinaliko? what was the agreement potenga msalu zonsezo?Inunso ndinu woipa wophangila aaaaa

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e หลายเดือนก่อน

    Mwaganiza bwino nkhale mwaganiza mochedwelapo

  • @DoreenEmmanuelj
    @DoreenEmmanuelj หลายเดือนก่อน

    ❤❤❤

  • @user-qn2nu4xs9i
    @user-qn2nu4xs9i หลายเดือนก่อน

    Ng'aluuuu..kkkkkkk

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x หลายเดือนก่อน

    😂😂

  • @MercyMwale-wc4lr
    @MercyMwale-wc4lr หลายเดือนก่อน

    Osangopasa osowa bwanji mpaka kuotcha

    • @AustinChiyembekezo-cx4mz
      @AustinChiyembekezo-cx4mz หลายเดือนก่อน +1

      Azikabvalira kutiko akawapasa enawo?

    • @AchinaKellz
      @AchinaKellz หลายเดือนก่อน +1

      Osaukawo wawaona ngati advertisement ya mcp?

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d หลายเดือนก่อน +1

      Kodi osaukao mumawatenga ngati ndi athu osafunikla azivala m,salu zotemveledwazo

    • @user-rn5ff7fn9c
      @user-rn5ff7fn9c หลายเดือนก่อน

      Osowawo kuti azitani nazo?

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน

      Osauka muwatembererenso ndi ufiti=MCP?

  • @ZazaManda-w5e
    @ZazaManda-w5e หลายเดือนก่อน

    Mumakwana