ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Eishiiii nyimbo yabwino zedi Koma eeee Chilima ai zikomo mau ndilibe Chakera oipa chilima pumani bwino misonzi yosatha ife
Yaa good song thanks guy
Strong message to all chikangawa, this is truth ndipo ngakhale mwana knows kut adachita kuphedwa chilima ndipo mulungu wationetsera chinsanzo pandege yagwa Pompano ija opulumuka adalipo ndipo zovala zonse zokwanila pathupi
Powerful msg
That's powerful message song, but truth must be spoken.
Great and powerful message.
Chilima's spirit must not rest until Chakwera and his Chikangawa crew are brought down
Great song boss ❤❤❤❤
Nyimbo zina mukajumbulire pompaja anamuphera chikangawa chilima km lazoro ndi bambo asikono yudasi mumakwana
Ndukhulupilira nyimbo zangati zimenezi zilipo zambiri ndipo zikanatulukabe popeza anthu omwe akawophyeza ku MCP ambiri analuza 😂😂😂😂
iiii zomvesa chisoni kwambiri anthu kupita ngati podza
😢😢zomvesa chisoni
Ndipo ndiye mmm😭😭
Can share me pliz full song
😢😢😢😢😢😢😢
Ndipo live ndipomwe tikadslira
😢😢😢
MCP afiti zed
Chakwela ndi iwe munthu oipitsitsa ZEDI, ndipo mzimu wau munthu ulibe ,kulikonse komwe udziyenda uzisowa ayendele ,magazi a wanthu 9akusowetse mtendele masiku onse amoyo wako.
ai kama amlomwe muli paganyu ndiye poti chakwela sakuchoka mutani?
Sakuchoka umavota ndiwe wekha dziko lonse Peter anachoka bwanji kuyakhula kopanda mzeru ndichani chazeru akupanga chakwera choti anthu amuvotele nacho, mudzilikonda dziko lanu nchifukwa ena tingololela tidzivutika mayiko ayeni chifukwa chamanyaka achakwela
Ine simlomwe km wayakhula zoduka mutu brain yako sikugwila ntchito zandale sizitsata koma wandiyakhulila zoduka mutu
Aa kuyankhula kwabwanji uku kulira akulira anthuku mudziwe zoti Mulungu akumva pangatalike bwanji tsiku lina adzayankha