Misonkho ya boma yaphweka; The story of Miguel Elias and his friend Dr Lazarus Chakwera

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 12 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 158

  • @christopherbottoman9131
    @christopherbottoman9131 ปีที่แล้ว +10

    Congratulations 👏👏👏 big brother monga ine top fan I support you

  • @WisdomMwitha
    @WisdomMwitha ปีที่แล้ว +6

    Your doing good work for us and all Malawians , thanks brather

  • @tronygiftmitengo
    @tronygiftmitengo ปีที่แล้ว +1

    Thats good go ahead becoze our opposition is too sleep

  • @user-xc1xt2qd7t
    @user-xc1xt2qd7t ปีที่แล้ว +3

    Much respect 🫡 to you keep up we are knowing a lot of things from your videos

  • @markoviskyhernandez9706
    @markoviskyhernandez9706 ปีที่แล้ว +2

    Agulitsa ma containers amarefuji amene boma rinatenga kwa Ngo'na kuti ndalamayo ipezeke!! 😁😁!! Ndukunena ndalama yoendela ndege ku Ghana!! But it's shameful!! Koma akhulu, m'matha kufufuza nkhanitu!! Thank you very much bro 👊👊🤝🤝👍👍!!

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 ปีที่แล้ว

    Koma ziliko mweee respect you sir matitsekula makutu, 🔥🔥Zofuna iziii timkanena anathera mu siiizi mmmm anthu thawi yaku sadziwa mulungu analekelera ayi zikomo ambuye akuoneni ndinthu mmene anthu

  • @user-hd7wq2yc6m
    @user-hd7wq2yc6m 10 หลายเดือนก่อน

    Aise you are number one in this country Malawi Kodi.achimwene simungakhale ndi wailesi ya public so that aliyesi wakuno kumuzi azimvera aliyese.chifukwa mukutsegila anthu mu maso

  • @user-mo4tv5eu5y
    @user-mo4tv5eu5y ปีที่แล้ว +2

    We should change laws so that youth can rule this country for changes,azibambowa amangoba basi

  • @charlesnkhomah6751
    @charlesnkhomah6751 ปีที่แล้ว

    am in rsa but with you i feel like am in malawi information that you give us very good------long live brother

  • @JenipherAlick-kd8pq
    @JenipherAlick-kd8pq ปีที่แล้ว +2

    Congratulations big man audze ngakhale samamva zonena munthu

  • @ImuraniChinyama-fq6np
    @ImuraniChinyama-fq6np ปีที่แล้ว +2

    Am third for comments.....

  • @EdwardZuze-r7w
    @EdwardZuze-r7w 9 หลายเดือนก่อน

    Congratulation brother for your well done job

  • @ishmaelsadi2710
    @ishmaelsadi2710 ปีที่แล้ว +4

    Tatiuzeni Zaku Poland Ramaposa

  • @thomasgamah764
    @thomasgamah764 ปีที่แล้ว

    Am in Capetown but with this information i feel to forward to Mr chakwera's personal media so that he can really be feeling that his bushirt ppl knows

  • @khadijailiyasa5315
    @khadijailiyasa5315 ปีที่แล้ว +1

    I respect you so much brother

  • @user-mz4tk1pw3f
    @user-mz4tk1pw3f ปีที่แล้ว +3

    Timadikirira big

  • @georgechikafutwa1334
    @georgechikafutwa1334 ปีที่แล้ว +3

    Koma zoona Abusa manyazi alibe?kuba ndrama kochititsa manyazi

  • @AhmaduAdini-sq1tl
    @AhmaduAdini-sq1tl ปีที่แล้ว

    Thanks big man timakunyadilani pitilidzani kutiwonikila God bless you thanks

  • @professorsafuta3936
    @professorsafuta3936 ปีที่แล้ว +1

    You're really strong 💪 person on history

  • @user-ks3uw3pq7d
    @user-ks3uw3pq7d ปีที่แล้ว +2

    Mulungu akulukire dziko lamalawi😢😢

  • @user-bl3fm7ji6l
    @user-bl3fm7ji6l ปีที่แล้ว

    Always we proud of you my brother.... Keep fire burning

  • @mustaffahhemmad
    @mustaffahhemmad ปีที่แล้ว +2

    Tionana ku ma vote ameneo poti nthawi yatha kale iyi

  • @George-zd5le
    @George-zd5le ปีที่แล้ว +2

    Chowuruka chizatela ,nkhawi ndikachitsiru

  • @christopherstosherchimbuwi676
    @christopherstosherchimbuwi676 ปีที่แล้ว +2

    ❤❤❤❤❤❤❤ God bless you my

  • @lyiemax
    @lyiemax ปีที่แล้ว

    Big up munthu wankulu kwambiri, keep on updating, I salute you 🔥🔥🔥🔥

  • @wisikitiyesi1224
    @wisikitiyesi1224 ปีที่แล้ว +2

    Big up bro ma3lu

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 ปีที่แล้ว +1

    Tikamati Chakwera ndichisilu palibepo akupanga sitikunama

  • @luciascharles4345
    @luciascharles4345 ปีที่แล้ว +1

    Malawi muno mukufunika ma demo ochosa agologoro amenewa la 40 likubwera guys

  • @clementmwale9222
    @clementmwale9222 ปีที่แล้ว +1

    Big appreciation to you man

  • @fedson2050
    @fedson2050 ปีที่แล้ว +1

    CHIMENE NDINGANENE MCHAKUTI MUZISIYANA NUMBER YANU AS ONE WAY OF SUPPORTING YOU PAZABWINO ZOMWE MUKUTICHITIRA COZ SIBWENZI TIKUZIWA IZI BOSS

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 ปีที่แล้ว +1

    Awa atisenda amoyo ndithuu ndipo chisoni alibe. Olo olo😢😢😢😢

  • @gracetjomane-jj3ib
    @gracetjomane-jj3ib ปีที่แล้ว

    Meny Meny thank you to you my brothers man🤝❤️❤️

  • @ThokiseWiriyam-ws1ec
    @ThokiseWiriyam-ws1ec ปีที่แล้ว

    Bg man keep up good job

  • @user-mz4tk1pw3f
    @user-mz4tk1pw3f ปีที่แล้ว +1

    Ndimakunyadirani big ndiye ponopa nkhondo ya Ku Russia ikiti bwanj big tikudikiratu ife

  • @usg435
    @usg435 ปีที่แล้ว +1

    Mwa inuyo brother ndikhulupilura

  • @johnfarouk8982
    @johnfarouk8982 ปีที่แล้ว

    God bless 🙏🙏 my brother. I like you chanle

  • @MuhamadiIbraima-dr3lz
    @MuhamadiIbraima-dr3lz ปีที่แล้ว

    God bless you bra keep going on we no lot of things from you 👏👏🤝

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 ปีที่แล้ว +1

    Ndalamazo akwanitsadi kuba. Ndipo ndalamazi wazipeza ndithu.

  • @esaumwanza3524
    @esaumwanza3524 ปีที่แล้ว

    Big up brother pitilizani kufukula zobisika ku malawi

  • @ahmedmsume1489
    @ahmedmsume1489 ปีที่แล้ว

    It seems like you can be a good president

  • @frankcholimbirapo262
    @frankcholimbirapo262 ปีที่แล้ว +1

    Ku malawi kuli ndalama 😢

  • @davidmaulana9277
    @davidmaulana9277 ปีที่แล้ว +1

    Koma chithu chimenechi chotchedwa kwa mterechi mmmm

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 ปีที่แล้ว

    Exactly Chakwera ndimbava yothelapo. mbuzi yamunthu

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 ปีที่แล้ว +2

    BIG 👍

  • @tronygiftmitengo
    @tronygiftmitengo ปีที่แล้ว

    All of them cbakwera and chilima are people of mw

  • @humairamalombe295
    @humairamalombe295 ปีที่แล้ว

    Big up bro 💪
    Yamacholowe mwaidojayo tikudikilila

  • @blessingsmasakala3285
    @blessingsmasakala3285 ปีที่แล้ว

    Iwill subscribe u forever ilike ur story to us the trueth

  • @ShyreenKafumbwa-bg2nu
    @ShyreenKafumbwa-bg2nu ปีที่แล้ว +1

    Galu chakwela akupanga ngati ku malawi kuno sakukuziwatu

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 ปีที่แล้ว

    Ndinu the one only!!

  • @obedlanken
    @obedlanken ปีที่แล้ว +1

    Zina za zotsatira za "tivotenso"

  • @alicklongwe6375
    @alicklongwe6375 ปีที่แล้ว +1

    Zosakhara Zbwino

  • @chitimbethegreat-pc1bp
    @chitimbethegreat-pc1bp ปีที่แล้ว

    Where is opposition parties in Malawi are they telling me that they don't see this shit? This chakwera man must step down mbava iz zatitopesa

  • @AlexKaunda-ir6rz
    @AlexKaunda-ir6rz ปีที่แล้ว +1

    Vinkhule vao

  • @ismailkhuneya3346
    @ismailkhuneya3346 ปีที่แล้ว +1

    Malawi ikanakhala school tikanangoiseka bas, ma block akewo kusandutsa rest house 😅😅

  • @user-qm1ri6cr6w
    @user-qm1ri6cr6w ปีที่แล้ว

    Iweyo suzatheka❤

  • @nysonchapita595
    @nysonchapita595 ปีที่แล้ว

    Thanks brother ❤

  • @blessingsmimu
    @blessingsmimu ปีที่แล้ว +1

    Adhawa ndi khuluku otheratu dzina lina amachuka kut khizar,ndi mafia kwambiri

  • @Yusufu-Daudi
    @Yusufu-Daudi ปีที่แล้ว

    Ulemu wanu, mumatiimilira 👍👍

  • @ahmedmsume1489
    @ahmedmsume1489 ปีที่แล้ว

    Koma iweyo sungayambise chipani chako, please

  • @mariezorgen7735
    @mariezorgen7735 ปีที่แล้ว

    Praying for you man of God

  • @successngoma
    @successngoma ปีที่แล้ว

    Thank you brother

  • @danielkhinguirossejuliasse6106
    @danielkhinguirossejuliasse6106 ปีที่แล้ว +1

    Yaaah ndizoonadi

  • @Ishmael376
    @Ishmael376 ปีที่แล้ว

    Makometiwa asangokhala oyamikira okha pakufunika kuthandiza nzeru pamomwe likuyendera dziko lathu tsogoleli ameneyu ndichigawenga chachikulu

  • @abisalomchunga6695
    @abisalomchunga6695 ปีที่แล้ว

    Boss I love you

  • @SindiweAllhajih
    @SindiweAllhajih ปีที่แล้ว

    muthu chiloweleb m.boma kumangoyenda yemda ndizaziiiii galu amebeyu ndipo vote yaine galu iwe sudzaiwona ngondolo iwe mwana wahule mboako chigawenga.....nyani iwe......😢😢😢😢😢osamva chison bwanji ufiti chani....kodi asilokali alikut?

  • @banyakolemulenga7072
    @banyakolemulenga7072 ปีที่แล้ว

    I wish seer 1 had interest in Malawi like he has in Zambia.

  • @MussaAli-jw5pq
    @MussaAli-jw5pq ปีที่แล้ว

    Amwene mumaitha kwambiri

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du ปีที่แล้ว +1

    Chikwera watikwana akufuna kumpha amalawi

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u หลายเดือนก่อน

    Enawo amaba koma uyu ndiye wanyanya 150 billion
    Enawo amaba 20 million

  • @edwarddickson501
    @edwarddickson501 ปีที่แล้ว +1

    Kod angatithandize zida zakhondo ndindani tikanalanda boma limeneri by force by 🔥

  • @aggogokina8992
    @aggogokina8992 ปีที่แล้ว

    Akatundu omanga ndi mawaya. Abale munthu uyu ndiofunika kwambiri mdziko la malawi amafukula zinthu za pansi kwambiri nkumatidziwitsa May God Almighty bless you brother.

  • @George-zd5le
    @George-zd5le ปีที่แล้ว +1

    Chakwera ndi pulezident wolephera mimbiri ya malawi.koma muzaona anthu azamuvoteranso iiiiiii Koma ndichifukwa chake ine ndinasamuka Ku Malawi

  • @rechealbracia-vk7np
    @rechealbracia-vk7np ปีที่แล้ว

    Anthu amenene ana votela Chakwela adya bibi yawo ndithu!! Uyu akumalizai

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 ปีที่แล้ว

      Kusamva a atenge ka nawo rent a lesson 🙌🙌

  • @user-td7rn3jw7z
    @user-td7rn3jw7z ปีที่แล้ว

    Mumakwana big up

  • @davenchimadzi6529
    @davenchimadzi6529 ปีที่แล้ว

    Abusa inu mutipha ife nd mtima please 😢

  • @LytonChande
    @LytonChande ปีที่แล้ว

    Respect

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 ปีที่แล้ว

    Eeeeee bro inuyo ndipatali braz iiiiii paka mwamuwelenga Elias congratulations Mr 🤣🤣🤣🤣

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 ปีที่แล้ว

    Wina kungotuluka m,bomamu ecxatry streit wakumaula ndiithu 😢😢😢😢

  • @PaulKwenda
    @PaulKwenda ปีที่แล้ว

    Sanje amalawi bizy mabodza

  • @emmanuelchikonda8053
    @emmanuelchikonda8053 ปีที่แล้ว

    we proud of you

  • @devlinebhema2729
    @devlinebhema2729 ปีที่แล้ว

    This guy si munthu wamba

  • @Misasi19
    @Misasi19 ปีที่แล้ว

    uyu aMW anabetsa

  • @bayview4554
    @bayview4554 ปีที่แล้ว

    Amalawi uyu siprisedent akuphani

  • @bayview4554
    @bayview4554 ปีที่แล้ว

    APA amalawi tiphuzile Kut osogoleli wa choonad umachokela kwamlungu kumuchosa apm uja sanabele sisankho koma anawina kuchokela kwamlungu

  • @user-eg5co3ob7p
    @user-eg5co3ob7p ปีที่แล้ว

    Big up blo

  • @irenechirwa9710
    @irenechirwa9710 ปีที่แล้ว

    Ulemu wanu big

  • @Ishmael376
    @Ishmael376 ปีที่แล้ว

    Ndipo ife amalawi ndi anthu asankho koma losapindula nalo munachosa piter pa pando kuzera muziwoneselo koma lero mfityi mulingo iwonerela akuwononga dziko lathu

  • @dharmeshpatel6370
    @dharmeshpatel6370 ปีที่แล้ว

    Viry puvar country

  • @nenanimayinga716
    @nenanimayinga716 ปีที่แล้ว

    Gud work

  • @josephgabriel1016
    @josephgabriel1016 ปีที่แล้ว

    Exposing all thieves and their connection.

  • @ibrahimjackson-cg6tc
    @ibrahimjackson-cg6tc ปีที่แล้ว

    Koma abale chakwerayu eish salibwino eeeee

  • @JeofreyNamalima-yn4tj
    @JeofreyNamalima-yn4tj ปีที่แล้ว

    Chakwera akankhala nyama titapha kale ndikudya

  • @piliranimphepo1920
    @piliranimphepo1920 ปีที่แล้ว

    Kodi impeachment bwanji?..

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 ปีที่แล้ว

    Komatu ndalama zikudyedwa mopanda chisoni

  • @mimhossan8886
    @mimhossan8886 ปีที่แล้ว

    Chakwera wachepa nazo udindo wakula

  • @ashikalam8616
    @ashikalam8616 ปีที่แล้ว

    Mumatiimilila big

  • @Marialongwe-nzlib
    @Marialongwe-nzlib ปีที่แล้ว

    Osatopa viwanthu vikuba ivi anga khwesi

  • @WakuMalawi
    @WakuMalawi ปีที่แล้ว

    Guys, we must wake up

  • @mussamapira801
    @mussamapira801 ปีที่แล้ว

    Tingomugwi kuponyera kunja Kwa ndende panji 90 minutes itebe

  • @MussaAli-jw5pq
    @MussaAli-jw5pq ปีที่แล้ว

    Timakunyadirani kwambiri