Usi musadzitenge Ngati Ochenjera. Pangani za MCP a USI. Mwazionesanso Kuti unapha CHILIMA iwe Manganya mchifukwa chake Nkhunda yako imakana kuuluka. Khalani ndi Umunthu a USI. Mulungu wathu wamoyo. Mulungu wa Abraham, Moses, ndi Isaac imvani kulira Kwa ana anu ndikutionesera ma bvumbulutso Onse akusowesa Mtendere. Comrade Ntanyiwa Stay safe and blessed ✊🙏💕💕
Without beating about the bush, using UTM cloth in Government Functions, is not right. Let such a practice be stopped because UTM has a President now who is supposed to give orders. Dr. Michael Usi is just a Vice President of the Republic of Malawi not any party.
Machennde ake usi kodi mmesa anakana ku mpikisano anzake anapikisana owinawapezeka ndiye galuyi napanyelo chomwrakufuna ndichani ndipo ndimmoxziemwe anatengapo mbali pa imfa ya kuchikangawa galu
I said it ling time kuti icheal ussi di munthu woipa same like chakwera pamaso ngati munthu, kuyankhula ngati wachilungamo koma munthu woipa zedi, mfiti watha ntchito
Akanakhala dolo akanapita ku convesation mesa ukati ukayima, conversation yatha kuzitenga ngati ndi kashasha koma ndewaonetsa uchitsiru wako onse..ndpo umaufunad udindo wa chilima 😮😮😮😮mpaka kumupha pamodz ndi ndi chikangawa party
Kasavuka ka usi apa ndipomwe tadziwa amalawi kuti kanali mugulu lawanthu anapita kukamaliza anthu ku chikagawa ndikafiti kamunthuka kamawoneka kufupikako kamunthu kakupha kagulu kawo kose ka mcp ko
Manganya apapa ndiye waonjeza kwambiri, usamale, achinyamata a utm mosogozedwa ndi Fredo ,u need to do action ,apangilidwe mademo asiye izi galu ameneyi mfiti yamunthu
MAYIKOLO USI NDI SAVAGE WENIWENI.AKUMUSATILA NDI AZIMAI OKHAOKHA AKAPEZEKAPO WAMAMUNA NDEKUTI NDI OYIMBA N'NGOMA KAPENA ACHITETEZO galuuuuuuuuuuuuuuuuu
A MCP komwe mliko, mlungu akukhudzeni mwapadela ,zoona inu lero mngamavale nsalu ya chilima pamene mnamupha ndinuyo.nkumavala nsalu yake nkumavinira galuyo manganya. Shame on you
Waufunatu u vp unya uwona suzaunyatha come next year udyeletu malawi si iwe... kupanda chilima unali ndani iwe unalephelelatu ndi u mp omwe shame on you
Usi musadzitenge Ngati Ochenjera. Pangani za MCP a USI. Mwazionesanso Kuti unapha CHILIMA iwe Manganya mchifukwa chake Nkhunda yako imakana kuuluka. Khalani ndi Umunthu a USI.
Mulungu wathu wamoyo.
Mulungu wa Abraham, Moses, ndi Isaac imvani kulira Kwa ana anu ndikutionesera ma bvumbulutso Onse akusowesa Mtendere.
Comrade Ntanyiwa Stay safe and blessed ✊🙏💕💕
Manganya ngati ndi ufiti udzaziona one day if u think kt ndiwe dolo
Usi ndi yudasi akuwona ngati amalawi sitikuziwa Kuti ndi amene anamupereka chilima
Without beating about the bush, using UTM cloth in Government Functions, is not right. Let such a practice be stopped because UTM has a President now who is supposed to give orders. Dr. Michael Usi is just a Vice President of the Republic of Malawi not any party.
Usi panga momwe ungathere .... Dziwa mulungu akukuona..... Ndipo pangatalike bwanji mudzaziona ......mzimu wa mulongo wanga Biyeni usiyeni ....
Nsalu panga Yako , uikepo nkhope yakoyo !!!
WORDS MAMA.Ndazikonda zomwe mwanenazi
Yudas ameneyu atha moyipa. Lets God take action on Yudas.
Kusavukatu uku..akusowa mtendere anthu awa that's u miti ikukhala ngati masala..chitani manyazi manganya
Akuzitenga ngati wanzelu uyu, tsiku lina azapusa uyu, zomwe mukuyakhurazo ndizoona ndithu a comrade ntanyiwa mulungu wathu amava ndithu ndipo tsiku lina azatiyakha, ndithu akuyiwala awa kuti ku kuli mulungu wathu wa mphanvu zonse
Zoona zimene a kupangazi tinaziona kale apite akamufunse man KO, pano mutu wakula ngati wa anduna😳🚶♂️🚶♂️🚶♂️🚶♂️
Nkhunda sizinauluke chifukwa cha usi ,ku ntcheu tsiku linja amazing ulunsa nkhunda
Ndipo zinalitu zodabwisa mwamva osauluka why
Mutu mwamunthu mukadzaza nzeru zasatan or m'busa atameza baibulo or sheikh atameza Quran samamva vinyo wadzaza muubongo Mulungu atimasule anthu mudzanja lasatana
Anapha mzake chifukwa chofuna udindo ndipo iwe manganya ambuye akuone 😢😢
@@JogaJoseph ndipo nayenso atangopanga ngozi amwalile family yake ioneumasiye galu
Uyuyu akudziwa kanthu ndinthu ndipo azanena bwino siku lina ayi ndinthu ,munthu anamuyika papando lero akuti chani awa
Kungoti boma la lelo likuyendetsedwa ndi anthu amazing mutu onse km chekwela ,manganya one day is one day God is around
Ndipo zikudabwitsa kuti akupangiranji izi, to prove what?
Ufiti uyu
Powerful prayer and Amen!!!
Machennde ake usi kodi mmesa anakana ku mpikisano anzake anapikisana owinawapezeka ndiye galuyi napanyelo chomwrakufuna ndichani ndipo ndimmoxziemwe anatengapo mbali pa imfa ya kuchikangawa galu
osadandaula zosatira ndikuzinkhwesa monga yudasi wa lero, osamudandaula akapanda kumvera lamuro amuphaso, taona satana wafupi lero
Bwana Usi, munakadzipatsa ulemu...i used to follow and like u, but from now onwards...ndakusikani..anthu a UTM sakukufunani ankolo...
Pano ndakhulupilila kuti manganya cholinga chake ndikufuna kuononga chipani cha UTM, ndi zonvetsa chisoni zomwe akuchita,,zokhazi zimene achita zaonetselatu mawanga awo onse
Ambuye ngati mumalanga munthu ausi akuziweni kt kuli mulungu
Manganya ngati amafunabe utsogoleri wa UTM akapita ku kokapikisana ku chipani osati ukupanga
Cholinga chake ndichoti bwanji kugwilitsa ntchito makaka a UTM,we don't want you anymore to our party,ndiwe wa MCP
Usi ndi munthu oipa uyu amankhala ngat amamukonda chilima kma ndithu😢😢 continue rest in peace biyeni💔
Manganya mutu wake sugwila ndicifukwa kalindo anamuza kuti za ndalezj adzisiye koma manganya samva musiyeni cilipo cimusata aciona. Osayambitsa cipani cake bwa?
I said it ling time kuti icheal ussi di munthu woipa same like chakwera pamaso ngati munthu, kuyankhula ngati wachilungamo koma munthu woipa zedi, mfiti watha ntchito
Kusavuka kumene akupanga Manganya yu
Manganya ndi mbuzi
Kodi ku utm akukakamilako chani iyeyu osapita azikapanga zake za "odya zake alibe mlandu" bwanji usatitopese
Akanakhala dolo akanapita ku convesation mesa ukati ukayima, conversation yatha kuzitenga ngati ndi kashasha koma ndewaonetsa uchitsiru wako onse..ndpo umaufunad udindo wa chilima 😮😮😮😮mpaka kumupha pamodz ndi ndi chikangawa party
Ndi chitsilu ichi chimkadziona ngati chochejera lero wangwa nayo afune asafune utm ili mmanja mwa Kabambe now
Mtanyiwa imeneyo ndi nyambo 10,000. Alephella from 2021 ankwanisa bwanj amallawi ankuphedwa shinkangawaw 2025samallani👊👊👊🇿🇦
Mtsogoleri alipo kale watsopano yemwe sanayambepo wakhala pulezidenti. Mulungu
anasankha kale zinazi kunena zoona zikhala zokakamiza koma sizitheka.
Tipemphe Mulungu atisogolere atichosere satan watizungulirayu
Ka nfiti aka 😢
Indeeeee ndi kamfiti
Manganya wasavuka chifukwa mzimu wa malemu Saulos Chilima ukumumenya tsiku ndi tsiku ndiyeno wapenga misala . ndipo posachedwapa apenga misala yeniyeni ndipo ayenda maliseche. ndipo ndipemphe nkazi wake wa Manganya kuti akhale naye pansi amulankhule zinthu zisanafike povutilatu chifukwa apapa Manganya zamuvuta kale .khaya ndi ufiti apa ndiye wayaluka nawo.
Michael usi anabadwa mwa uchitsiru, A Usi mudzafera poyera Mcp sichipani chochifera unayaka wauwisi Chilima,komasoSidiki Miya Inu ndinu ndani.ngati kotheka yambani chipani chanu it's not too late.
Kuyambila lero usatenge nsalu ya utm kuveka azimai a mcp azimai akowo angoti bumbunyini zike😂😂😂
Musiyeni mzimu wa Chilima umukwiyira akuwona ngati akuchenjera, komanso Mcp siyoyifera adziwona pompano sikalenso. Manganya angododedwa angolamulidwa chilichonse
Uchisuru wamukulira usi
Inu anthu omwe mukuyankhula Amalawi mukungoona kutaya nthawi yanu kumalawi aliyense akuyang'ana Malo Ali ndrama zitaye izi
Kasavuka ka usi apa ndipomwe tadziwa amalawi kuti kanali mugulu lawanthu anapita kukamaliza anthu ku chikagawa ndikafiti kamunthuka kamawoneka kufupikako kamunthu kakupha kagulu kawo kose ka mcp ko
Michael Usi achite resign chifukwa is no longer UTM president please
Mmutu mwa Manganya muli mikodzo ya MCP
Usi ndi yudasi, usadzaputenso kuntcheu kumanda a Chilima ndi mfiti uyu ndipo asiye kumanena ma vesi a Bible sizikugwilizana ndi zomwe usi akupanga.
Kd amene ndiopusa kd aridi chipani chake onya zake aribe mulandu iwe tisakhare tikuona zaiwe wanva Mcp yokupha moti mukuona ngati mwana
Apange chake chipani chakutikufelanji ndi MCp
Dr usi chonde musayipise mbiri yanu for the sake of world this world is passing by along with its desires
Angokhala osamva nkului mmh ka amaganiza motani kaya.
This is the end of this rubbish kufupika ndi nzeru zomwe munthu oipa ameneyu
Manganya apapa ndiye waonjeza kwambiri, usamale, achinyamata a utm mosogozedwa ndi Fredo ,u need to do action ,apangilidwe mademo asiye izi galu ameneyi mfiti yamunthu
That's why or sizidamukhudze zokuvota kuja, koma busy kumagwiritsa ntchito salu ya UTM, really manganya ndi munthu oipa heavy
UTM yitenge injuction against this mann
Mzimu wa Chilama uwakathe komanso uyu athibulidwa posachedwa
Ausi mbiri yanu yanyasa ever palibe akukonda olo ukuwaveka mitima ndiyokana koma chifukwa cha ndalama zamwazi
Ntanyiwa musiye Manganya ndi mfiti yachabe iyi aaa convetion wayikana nde lero busy kuvara nsaru
😮😢😢😢😢usi ndimfiti
Manganya akuziwapo khanthu pa nyifa ya chilima akachoka aulula bas
mulungu akuonetsani tchito yake ponga ndawona ausi ndi chakwera chimenecho ndiye ukuru wa mulungu ukuwoneka mwachirendo
Usi ndi munthu oyipa kwambili wansanje wakhanza satana oyenda ndi miyendo
Kodi chimwendo Banda ndi mcp mukapha liti kamanganya nyini yamake timakunyadilani Popha anthu. Nkholo zamanu😂😂😂
Chilungamo
Koma ndipo ndiye kuyipa mtima koopsa Manganya kuyalukatu uku ngati chitsiru cheni chani mbuli yosapita ku school would do better
Kamanganya ndikamfiti aka kotheratu
Komatu penapake atha kukhala ma supporter a MCP achita mokonza kuvala nsalu za UTM.
😢poyamba nanenso nnapsya mtima koma this is MCP plan
More fire comrade ntanyiwa
Comrade Amen and Amen.
Amanganya kutenga nsaru ya UTM kumawapatsa azimai a MCP 🤣🤣🤣
Manganya unapha chilima chifukwa Cha mpando pusi
MAYIKOLO USI NDI SAVAGE WENIWENI.AKUMUSATILA NDI AZIMAI OKHAOKHA AKAPEZEKAPO WAMAMUNA NDEKUTI NDI OYIMBA N'NGOMA KAPENA ACHITETEZO galuuuuuuuuuuuuuuuuu
Ndimunthu woipa kwambiri koma kumwamba kuli mulungu posachedwa mumva amuthamangitsa ku MCP kwakeko
Kodi Inu simabwera poyera bwanji
Manganya asandichimwitse ine ndipo akundinyasa nsame
Angolimban mtima anuwake anavomeleza kale kd enanu mumazikokomeza bwanj kd mulibw njila ina yopezela ndalama mupezela ndalama pa dzina la chilima bas
Ndipo ine ndikanankhala manganya ndikanatula pansi udindo wa vice president ndikuwasiila okha ngulu la jese kabwila
Koma Inu zovetsa chisoni kwambiri ndipo kwambiri kodi anthu akamane kuti inuyo mumadziwapo kanthu pa ifayi muzikana
Chikangawa party chipani cha anthu opanda umunthu, maonekedwe ngati anthu mitiya ya mikango
Misozi wakhetsa tanyiwa I ngati simukuva inu a manganya mulungu akukanthe ndithu ndiwe amene
Ma results achilima ayamba kuoneka through actions nde tisadabwe koma mulungu akuziyaka poyela
Manganya he know something bout chilima dead
Akugwirisidwa ntchito ndi chakwera
pam.nyapake ameneyu ayike nkhope ya make
Manganya kapitilize chipani chako Cha odya zake alibe milandu bwanji osavomeleza upange zako manganya
Amen and amen
Koma mwati manganya amamudziwa yesu uyu?
Manganya anampajika chilima ndpo nd mnthu woyipa kwambr km nthw yikubera apanga regret chapompano🤓🤓
all in all there is no need for him to use utm slogans
azipanga za mcp basi manganya alibe umunthu that's why amangovina paliponse ngati si mtsogoleri
Ndipo ineyo sindimaziwa kuti man,ganya ndioipa chonchi Koma kumwamba kulimulungu
A MCP komwe mliko, mlungu akukhudzeni mwapadela ,zoona inu lero mngamavale nsalu ya chilima pamene mnamupha ndinuyo.nkumavala nsalu yake nkumavinira galuyo manganya. Shame on you
Zoonadi MCP inkapindula ndi UTM nkaona akuikakamila
And I hope kut anali nayo pa plan yokupha chilima ka mdala kameneka😢😢😢😢😢😢😢😢
Musiyeni manganya analiko anthu ozunguza ali kuti ndiye iyeyo.akuti afika nazo kuti nthawi ndikachisilu
Odya naye mbale imodzi ndiyamene amakupeleka usi ndi oipa ndziwa kuti palibe chisisi padziko
Tamanenakoni malangizo abwino tamusiyeni chilima ause mtendere nsaru ilipo kathu
Waufunatu u vp unya uwona suzaunyatha come next year udyeletu malawi si iwe... kupanda chilima unali ndani iwe unalephelelatu ndi u mp omwe shame on you
Ambuye bwanji mumalola anthu amitima yoyipa kumawasungaso? Chosecho akuzuza anthu a
Asiye kugwiritsa ntchito nsalu ya nkhope ya Chilima apange nsalu yake , galu usi
Chitsilu usi. Chomwa madzi. Ometela ndevu.
Eihhhhhh zomvuta usi ndikupepera kwambiri akukhara ngati osaphuzira
Usi is a savage
Ubwino wake amcpndo akumuona kah zonwe akuchitanzo nanga mesa amcp akumuphunzira
Koma ngati Conversation yatha iweyo si president nso wa UTM
Komano kut tinenezoona zimeneakupanga manganya sizabwino anayenelakumapanga zinthu ngat ndimalawi kut tsikulina anthu azamulemekeze chifukwa pamwamba pamenealipo tsikulina azatsika nkuyenda wapas ndiyeasazitenge ngat ndidolo