This is one of the Malawian songs that we need to export. Great creativity and very very artistic loved everything about it. Receive your flowers 🌹 🌷 guys. Mumatha kwambiri we want more songs like these to reach above and beyond the diaspora. 100% Malawian art
I'm the only zambian who understands this audio from our lovely brother from our new capital city or province which is malawi.... From now own lilongwe and blantyre they are part of 🇿🇲 district. Kumadya anyamata mu zambia osango taya basi 😂😂😂😂 Olo ndiwa soya piece tiyeni tizidya mosafulumila modeka mtima
An insane shot where the green carpet of uneven grass introduces the scene to a young boy, dancing solo, with the subtle sunset giving a general warm effect to the shot, real talent there cameraman and director! 🎉
Ndiye mwati kumadya 🎉🎉🎉bweletsakoni tiichite chipweteko koma phwedo umu mwamuonetsa akulilila kuuna ati bola school days 😂😂😂😂😂😂mphatso ali kuti aone izi Leticia muuze mphatso kuno 😅😅😅😢😢😢ndinaiwala paja adafa moment of silent T shirt ya Mphatso phwedo akabweze madolo ake tituma inuyo mwamuonetsa😂😂😂😂😂 on repeat here
Anyone to like my comment so that I comeback here and listen to this masterpiece😊osayiwalatu kumadya kumeneko ka😂
😂😂😂😂Indee kumadya
Ife tikudya katatu
i hope nanunso mukudya bwino kumeneko
Come and listen 😂😂😂 hope mwadya kumeneko
Ife tikudya zofunika kudya
Ayitu mukafuna Ina munena amene tikufuna Ina let's gather here ❤️
Iyi mwakazinga 🤸🤸🤸🤸🤸💯💯💯💯 , brothers and sisters gather here to support our own celebrities.... 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Tikufuna yina guys
Tadya takhuta
Iyi indithera ndalama iyi
Kkkkk Koma yaaa
Muli boo anyamata aku 25
Sure u r ryt❤❤our very own🇲🇼
Zambia here we approve this song 🌹🌹🌹🌹🌹🌹🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
This is one of the Malawian songs that we need to export. Great creativity and very very artistic loved everything about it. Receive your flowers 🌹 🌷 guys. Mumatha kwambiri we want more songs like these to reach above and beyond the diaspora. 100% Malawian art
I like your union: you have survived for all this time since you started -PLEASE CONTINUE
Zitengera nzeru zako kuti umve nawo nyimboyi 😂🤗 Only for legends
Ndipo only legends can understand the song
Kikkkkkkkkkk kumadya azibambo Kikkkkkkkkk iyi ndi hit kwanga sindikuziwa kwa enanu
Eee ndudabwa nazo 😂😂😂😂🙌
Kkkkkkkk kukhalila kutayaa😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂🤣
The song is deep😂😂😂only legends will understand
Only legends 😂
Koma ndipo😂
U hav gone beyond critical listening 😂
Nanga mpaka kutenthesa mbwanda pakati pa usiku
Nyimbo iyi ikukamba za nsima yomweyi??????😂😂😂😂😂😂😂
The Symon n Kendall Style we know 🔥🔥🔥
Mmatimvesa kukoma
Akendal nda symon ambuye azikudalisani pa ubwezi wanu continue guys mukuitha muvingeso film ija mudapanga zakazpitazo
You're still entertaining us for 2 decades now... We're proud these guys
One of the reasons I love being Malawian 🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤️❤️❤️❤️❤️❤️ culture ...odi ndikaiteleke 😂😂😂😂
No one will compete with you guys❤️❤️💃💃
I like the music coz of it's deepness ,this is the song of heroes inorder to understand it better ...osati zansima muona apazi
Munthu sakhala dolo moyo wake onse ndaonera Phwedo🤣🤣🤣 Nice tune guys!!💥💥
Beautiful and local song "kumadya thupi sitimanga ndi linya 👉❤❤❤❤❤❤
What a masterpiece...... Anthu muli ndi luso
Ndipo lusotu
This is 🔥🔥🔥 much love I can see my favorite phwedo 🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Azibambo kungofikira kutaya ndikut kutaya chakudya koma maguyz awawa Kikkkkkkkkk
Since day 1 I realized that there is this dual ,,,never disappointed
Dzanyamata dzakudya💥💥
Mwapha, kupekulira shovelo nsima
Am a Zambian but have understood what ever the song was all About... much love from 🇿🇲🇿🇲
Malawi let's gather here Malawi let's go ya China phwedo mono kumadya
My favorite crew ❤ keep it up guys inuo mumakwana kuposa pa 40 and nyimbo zainu mmafatsa when shooting the vdz .Mmatiyimilira
Yomweyo galu iwe kumadya bas on repeat here😂😂 ❤❤❤❤
Only legends will understand
Komatu phwedo yu munamulakwira aaaash 🙆 Nice one from our very own legengs...Onyamata Onyemba-nyemba 🔥
Komatu phwedo simunamcheze bwino makosana 😂🙌🙌
amuenda pansi
I'm the only zambian who understands this audio from our lovely brother from our new capital city or province which is malawi.... From now own lilongwe and blantyre they are part of 🇿🇲 district. Kumadya anyamata mu zambia osango taya basi 😂😂😂😂 Olo ndiwa soya piece tiyeni tizidya mosafulumila modeka mtima
Ine awawa since day one ....... kumadya or kamudzi kokha... bambo a Juu😅😅😅😅🤣
Brother Symon ofunika kuyamba workout tu achimwene akulu wo bola tinawazolowera.......lots of love from this side......Ina ikufunika
Kudya uku sikwasima, akukamba zogagada pa home,
Big music concert wth powerful meaningful ......l love the song
Big up 🥳 kma uncle Phwedo mwawalakwira😂😂
Mposo etinu Kkkkkk kumangomutuma
Phwedo apa wagwanayo alibe makani kkkkkkkkk
Kulakwadi😂😂
Phwedo phwedo😂😂😂
Ichichi ndichi hit 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Apapa nde mwabweratu zakale zja 🔥🔥🔥
kumadya soya osalira mafuta............................thats goldness
Komatu food yake ndiyomwe kapena inayi kkkkk, zikundivekela mwaaa.... Nice tune
Iyiyi ndiinado
@@EstherZintambira-sq3yy ndipo inu ayi zikomo
Nice tune.Komabe uthengawo siukundimvekera bwinoyi,kudya kwake sichakudyachiyi😁🏃
The duo has survived: congratulations!!!!
An insane shot where the green carpet of uneven grass introduces the scene to a young boy, dancing solo, with the subtle sunset giving a general warm effect to the shot, real talent there cameraman and director! 🎉
This is Greatness on a different level.
Keep the 🔥🔥 burning
Always i respect you guys I'm here in south Africa binoni cloverdene moto kuti buuuu mofaya
I like the drum 🥁 very massive, Man Phwedo ayipatsa moto. This has been cooked, yapsa! 🔥 🔥
Beautiful sounds. The concept is just dope
Ndiye mwati kumadya 🎉🎉🎉bweletsakoni tiichite chipweteko koma phwedo umu mwamuonetsa akulilila kuuna ati bola school days 😂😂😂😂😂😂mphatso ali kuti aone izi Leticia muuze mphatso kuno 😅😅😅😢😢😢ndinaiwala paja adafa moment of silent T shirt ya Mphatso phwedo akabweze madolo ake tituma inuyo mwamuonetsa😂😂😂😂😂 on repeat here
CAN WE PLEASE HIT 1 MILLION IN JUST 5DAYS PLEASE PLEASE PLEASE...WELL DONE TEAM..ONLY .CREATIVITY THAT DAZZLES....CONGRATS TEAM
Kudya ukuku mkomweku koma anyamata Inu,mmmmm pena nduona ngati mwatikuluwika azimayi....big up our own artist.....iyiyi mwaswa eeeee
Masterpiece of all your video songs 🔥🔥🔥🔥❤
Big up to you my brother's.. You really represent south africa music listening from Zimbabwe
Absolutely Beautiful! only 4 the Legendz!!!!!!!!
My late father is smiling,,,, biggest fan ❤❤
Absolutely😂 funy .kkkkkkk phwedo achose mbale😂😂😂😂😂😂😂
Mumakwan in🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Ladies and gentlemen. Its a moment we've been waiting for. Idzidzi ndi dziphe
A touch of class. Well crafted , the concept is just well done. 🎉
Deep fantastic hit!
Not person for under age of 20 this one kumadya💥
Onyamata onyemba yemba nice song
Emptying the whole wheelbarrow is wild 😂😂
I love my country Malawi 😂😂😂
Ma guys I don't disappoint. Message and creativity top class
Kuchoka mu standard 2 npaka pano za school tinayiwalako but ur still entertaining me u guys ndi 1 basi fire 🔥
Amayimba once in a blue moon koma amatulukira ndi chi hit just like B1❤
I just like the way malawi and are supporting our artists these days❤
Apa basi pasapez3ke otulusatso nyimbo Mafumu Azakudya atseka kwa chaka chino😂😂😂😂🎉🎉🎉🎉❤
Very good song ❤❤❤❤❤
Phwedo never disappoint😂😂😂😂
Phwedo amuonetsa. Wakumana ndi man Chaksy ndi mfumu mzake pachakudya. Amaona ngati ndi mphatso machira. Nyimbo ilibwino iyi 🔥🔥🔥
Umumu ndibayemo umu?? Deep meanings
Iyi ndi hit📌
Aah koma phwedo munamupanga nkhaza aaah
This is music belongs to our heritage, bombastic
Kumaphakadi mamuna mpamimba 🔥🔥🔥🔥.Nyimbo yih soh ili bho angoidyera kumodzi 💥💥💥🔥🔥
Kudya kwanji kwapakati pausiku okhwima zeru wamva makanda ose kumazere nyimbo njakulu akulu iyi
Ha ha ha ha ha timva zinthu
Daniel Manduwa, tamamvani zonena amzanu. Malangizo a ululetu awa.😂😂😂😂
My favourite song so far
azibambo kumadya!!!!!!!! ngati mwatopa tikhoza kukuthandizan kkkkkkkk
😂😂😂😂😂very funny😝😝 I like it
Let's appreciate our celebrate our heroes of industry music in malawi you make us proud we need more music ❤❤❤❤
Kumadya zikumveka bwino ndie kungondimana upakila❤❤❤❤❤
J'adore bien ❤❤❤❤ya de l'harmonie
It's Phwedo's move when he was walking away for me. 😂😂😂
Nice music fahda
Koma asee🤣🔥
Very deep song
Nyimbo mwamenya iyi🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 video nde eeeeeee mwala
Awesome video 👍👏🏼👏🏼🤣🤣🤣🤣, you guys making laugh, Watching from America 🇺🇸
I like the creativity in the song and kumudzi simuiwalako ponjambulitsa
Tikufuna ina ndipo tizidya mwachinakodwa
Wow! This what we call Talent🔥🔥🔥
Koma phwedoyo anamupanga chipongwe anabwelela kutumidwa osayitema 😂 munamuwonjeza over wise it's hit song congratulations brothers
Symon and Kendall my favourites. Mumatha guyz. Big up!!!
Mr Phwedo nkudzalowa chamutu pamene paja😂
Koma mukumadya?😂
Mnyamata wakochimeza ndi komasumba nkhunda 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼
I love you guys. Thanks for this piece
Nice song ma guys 😘😘😘
The song is 3000% fine
Classic one boys. Message tamva ndithu. Tiyesesa osamadya kamodzi
This so amazing, I can watch this a million times
Like this song and the performance
Mphwedo sanadyetu.nde.mutilimbikisa bwanji kuday wina mutamana
Best wishes to.u fungisai umatha
❤❤❤My favourite pple,nyc song
Ushasha uja umathadi ndaonera pa phwedo😂😂😂😂😂
My best friends Kendall and Simon I always love you guys God bless you all ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
This is super super i like audio, video as well as actions...keep it up pliz