Zinazonsezo wainena bwino koma poletsa anthu kuswana pokhapo Genisis 9:1 MULUNGU ANADALITSA KUTI ABALANE KUMENE. Eksodo 1:7 ana aIslaeli anaswanadi. Anadana nazo ndi Falawo potero apezeka wachimwira bodigadi wake wamkulu kumwamba. Chifukwa pa verse ya 15 anamwino poopa Mulungu sananvera may oipa a Falawo. SO ZIMENEZO MUSIIRENI CHIKANGAWAYO YEMWE AKUPHAYI. KULERA NDIKUPHA ZOMUYENERA CHAKWERA INU AI BOSI. Kwinako mwalankhula mau amphanvu moimirira aMalawi keep it up Mr boss man .
Ngati ana anu amaphunzira ku India ife musatinyasepo apa ,ku university pano palibe amene akuchosedwa school chifukwa Cha fees ma upkeep aliyense akulandura ma fees including a ODL nthawi yanu munapangapo iziiiiii osangodziwa kulubwalubwa Inu simungazaloweso mu boma
Chilungamo kupweteka , mr suleman big up , we're proud of you .
The way I love this man, Apm my vote
Bwana inuyo dikanakhala ndi nambala yanu bwana mukanakhala vary best friend ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
At zot akamukhululuklaso mulunguyo zikukaikitsa😂😂😂😂😂
Big up mr suleman
Zinazonsezo wainena bwino koma poletsa anthu kuswana pokhapo Genisis 9:1 MULUNGU ANADALITSA KUTI ABALANE KUMENE. Eksodo 1:7 ana aIslaeli anaswanadi. Anadana nazo ndi Falawo potero apezeka wachimwira bodigadi wake wamkulu kumwamba.
Chifukwa pa verse ya 15 anamwino poopa Mulungu sananvera may oipa a Falawo.
SO ZIMENEZO MUSIIRENI CHIKANGAWAYO YEMWE AKUPHAYI. KULERA NDIKUPHA ZOMUYENERA CHAKWERA INU AI BOSI.
Kwinako mwalankhula mau amphanvu moimirira aMalawi keep it up Mr boss man .
Man of the politics of the year.......with he's bordgurd GOD
Mulungu wake wakutiko amene angateteze mbuzi yamunthu ngat ameneyuyu?
Mumaona ngat Mulungu ndiopusa kut akateteze zitsiru ngat izizi?
@@isaacchiwaula731paja iwe ndi wa Chikangawa Party ndiye sungayankhule zabwino za Suleiman.
Umakwana Suleman ndiwe mbambande Good speaker.
Mr Suleman I love you so much mwa Inu muli usogoleri boss
This Boss SAMEER Is Man Integrity ✊✊✊🤙🤙🫒🤸🤸🤸🤸🤸🤸🤸🤸🤸🤣😂😂🤣😂😂😂😂🤣😂😂🤣
This man is genius
More fire suleman🎉
Perfect speaking 🗣️🗣️
God bless suleman he is humble
Iweyo unabwera basi Sulemani😂😂😂😂umandiwaza heve
Mr. Suleman. Ulemu. Want. Mr. Chili ma. 😢😢😢😢
I just like the guy nsaname😂😂😂
Ndipo tikuchita kuwona kuchedwa Siku loponya vote a Peter woyeeeeee
Keep it up boss 👏
🔥 bigup reality talk
Big up big man
Ulemu wanu bossss ❤❤❤❤
I love this man
Atiberanso mvula Mr chikangawa
Kkkk koma yaa
Yipatse moto , good speech
Koma uyuyu gayezi 🙌
Mr Selemani ❤ more 🔥🔥🔥🔥✔️
Iweso Martha i love you
Umakwana Suleiman,,,,, osaopa osafooka osatopa 🔥
Kkkkkkkk it's itsanana wamvuta
Real leaders
Fire nsuleman umativetsa kukoma kwambili
Uyu apweteka gulu la mcp😂😂
Powerful 💪 osawopa
😂😂😂😂😂😂😂 itsanana itsanana
This is our Julius malema in malawi
Saying the truth
Auzeni afitiwa bwana ndipo n,galulani
Keep on the fire 🔥 🔥🔥🔥 burning
Mumakwanadi kwambiri tilipambuyo pano😊
Dr chaponda mupatseni mwanayu Leader of opposition bc
Njala eeee,mvulansokulibe
Our next minister of homeland chaka chamawa bwana muli ndi ntchito yozawamanga, chimwendo, kukuyu, zikhale NG, oma
Machine Sameer koma becareful ndi zikwanje
I am not dpp f
An koma mmm big up Mr suleman
Iweyo umakwana osaopa kumakamba chilungamo hiiya tatopa ife😅😅😅
Kkkkkk big up technical support
Big up
Zoona Fisi ndi Fisi Sure
Malema wathu waku Malawi
Ndipo ya Sadiki Mia Yimandi Wawa💔😔
True vibes mr
Chilungamo live kung,alura basi mpaka kumapeto atasaza
Suleman umakwana😂😂😂
Big boss inuyo ulemu mulandire Mulungu akupatseni moyo wautali
Zowona wagulisa nyanja . Tikuwona kuno Ku south Africa zonse
Kupanda nzeru anthu agulitsa bwanji chimanga ,kuti agule Fertilizer pomwe anthuwo akudya chitedze nyika , kumeko ndikulalatira a Malawi
Bravo suleiman nkaladi azioneka!!!😂
Chilungamo chimamasura😂😂😂
Unabwela kuzakhala Suleman 😂😂😂😂
Big up 😂 ati ndende anamangila anthu
Anajambulisa ndi bebi yake 😂😂😂😂😂😂😂😂
Kkkkkkkkkkkk koma marawi bora
Inutu mr Suleman ndi akutundu
Palibe chomwe timavapo boss komaso zoti akamukhulukila mulungu ndizabodza
More fire 🔥 💙💙💙
Anthu oyela khungunu nthawi zonse mukumabwela ndi mfundo zokwiya muli bho heavy koma chomwe ndapanga note kuvala nyawu kuja umakula ngati nthumbidwa kususuka madyedwe andalama.
Good speech to a normal person osati mbuzi Chakwela. Chakwela ndi manyi enieni.
Kkkkk koma uyu ndi katundu
Km amdaaa awa ndikatundu ulemu wanu big
Chakwera my vote
Malema wa ku Malawi
Enough it's enough wationjeza
Ndinalembetsa chifukwa Cha inu Big
😂😂😂😂 CHAKWERA Is Man Of ITSANANA
More fire
❤❤❤
Fire fire Suleman
🎉🎉🎉🎉🎉😊😊😊
Makwana Big
usi❤
Uyu walusa kkk
Another Malema
😂😁😂😂😂😂 kkkkkkk koma ndaseka ok koma ndiye bebi
Pangolini tiye nazo akhaule agalu amenewa
Boss tilakhuleni
Uyu ndi kape wachabechabe amangofuna kutamika kudziva zeru mix koma ayi ndithu chibakete ,koma boma ndilomweri situsintha Dr Laza sakuchoka
Vuto mukunva chilungamo mumafuna bodza paja like tanks of fuel zili zima dosi
Iweyo ndiye mbuzi yamunthu yeni yeni ndi nyawu yakoyo, zitsiru nonse inu
Zoona zimenezo
ulamulilo,sitikusintha
Katundu weni weni Sameer amandivesa kukoma
Biggy sopano
Ngati ana anu amaphunzira ku India ife musatinyasepo apa ,ku university pano palibe amene akuchosedwa school chifukwa Cha fees ma upkeep aliyense akulandura ma fees including a ODL nthawi yanu munapangapo iziiiiii osangodziwa kulubwalubwa Inu simungazaloweso mu boma
Iweyo ukunama Malawi Congress party kuwinaku izabera mavote osakhala anthu kuikondaso AAA MBUZI ZA ANTHU KUSANGALALA KT AZANU AZIFA NTWI ISANAKWANE
Komad almost aliyense loans board imamtenga, nde uyu asatinamizepo apa ifeyo ndiamene tiliku university kooo
Zowona akulephela kutsogolela
Honorable mponda as minister kugulisa chimanga ku Zambia ,Peter anapangapo chani?
Your say true akusowa fundo zolowela bomamo
Machine mulungu akutetezele ndithu
true
Nice speaking 🔥
At nkumajambulitsa Nd babie yake ija 😂😂😂😂😂
Kuchemerera zopusa amalawi, apapa nfundo ndiyoti chani? Kumangoyankhula nkhani zamabodza basi.
Ndie nkumati Malawi angapite patsogola apaa?? Zovetsa Chisoni kwambiri
Nyanja agulitsa, Admarc idatha chifukwa cha Chakwera, iwe ngati sukumva enafe tamva basi cz MCP ilibe makutu kuphatikiza m'tsogoleri wake Chakwera samamva😂😂😂😂😂
Iwe ndkape ukut chan, chomwe akuyakhula sukumva mboli yako
Ukatero watethedwatu
Ndiwanyawu ameneyo.pwala lake.chilungamo chipotse apa
Umafuna amene kt chan?
Fire fire 🔥🔥🔥🔥 bambo Suleiman please stand for us
Powerful speech wanllah
Makwana bwana chakwera ndichitsiru kwambiri
😂😂😂 at ndye skut tizingoswanatu😂😂
😂😂😂😂😂😂😂