ANTHU ANAYAMBA KUWAFUPA ABUSA AWA LERO KU MULANJE ATAYANKHULA KUTI BOMA SILOMWERI PA MWAMBO WAMALIRO

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 19 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 373

  • @lizybanda-u1v
    @lizybanda-u1v 16 วันที่ผ่านมา +13

    Watching from Zambia you know God is speaking in Malawi have you seen without any fear spirit of God is in him 🎉🎉🎉🎉🎉 amen

    • @eunicesaiti
      @eunicesaiti 16 วันที่ผ่านมา

      Amen, Tatorera mwandi and Remain blessed Sis.

  • @LameckNgwira-t6s
    @LameckNgwira-t6s 15 วันที่ผ่านมา +2

    This is original man of God,a very powerful message 💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪

  • @GaretaBailon-rc7xr
    @GaretaBailon-rc7xr 17 วันที่ผ่านมา +25

    Nkhaniyi ndiyoona amen abusa ambuye apitilize kukupasan moyo wautali

    • @HerlixPBanda
      @HerlixPBanda 16 วันที่ผ่านมา

      Zili bwino .kodi AChakwera. Anali ndani? Lero ndi ndani siwa ndale

  • @MaxfordWasili
    @MaxfordWasili 13 วันที่ผ่านมา +1

    Powerful

  • @RaphaelMaunde
    @RaphaelMaunde 17 วันที่ผ่านมา +8

    Tikufuna azibusa ngati awa onena chilungamo mosaopa ... Amen abusa

  • @SimonGulani-w5n
    @SimonGulani-w5n 17 วันที่ผ่านมา +7

    Ohh man of god,mulungu sanatilenge anthu amantha

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 16 วันที่ผ่านมา +2

    I love this Pastor and Amen, Amen Powerful 🙏

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson 17 วันที่ผ่านมา +6

    Muthu wa mulungu, mtengo umaoneka ndi zipatso zake.chilungu sichiopa.Amen

  • @osmanmdala-uh7xw
    @osmanmdala-uh7xw 16 วันที่ผ่านมา +3

    Boma ili labweretsa mkwiyo pa wanthu moti angakhale pa maliro lizing'alulidwa. Amen amen amen

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 17 วันที่ผ่านมา +6

    Koma anthu tatopa di mweee Malilo ngati msonkhano 🙌🙌🙌

  • @besterlumbe4404
    @besterlumbe4404 17 วันที่ผ่านมา +8

    Koma Maliro awa anakoma ngakhale anankufedwa amaseka nawo Amennnnnn😂😂😂😂😂😂😂😂

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya 17 วันที่ผ่านมา

      Ndiponso..anaiwalanso kuti mbale wawo wapita kkkkk

  • @HastingsChinyama-xl1cc
    @HastingsChinyama-xl1cc 16 วันที่ผ่านมา +5

    Abusa apa amangoyenera kumanena kuti Dpp woyeee!! Osati amen amen ndale zalowa mu church apa 😂😂

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 16 วันที่ผ่านมา +1

      Do Morethan what this man speaks

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 17 วันที่ผ่านมา +8

    😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ koditu anthufe tibangula mcp idziwaso pakamwa ndipathu ifeyo tilalikila sanatiyi
    mtumiki santhula mau iwe 😂😂😂😂😂😂

    • @MbiNauli
      @MbiNauli 16 วันที่ผ่านมา

      Inde bro kkkk

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 11 วันที่ผ่านมา

    More 🔥🔥🔥 Malawi tili pamoto tikufuna mupulumusi wathu Peter abwerere

  • @sibomasina330
    @sibomasina330 17 วันที่ผ่านมา +5

    Eish, hiting straight to the point. Uthenga wamphamvu Abusa😢😢😢

  • @llewellynkhungwa4712
    @llewellynkhungwa4712 17 วันที่ผ่านมา +15

    Politics everywhere...... Eshhhh koma utsogoleri wa MCP utionesa zinthu

    • @TonyMhone
      @TonyMhone 17 วันที่ผ่านมา +2

      Ndipo uku ndikuyamba zifika pachiyinde yinde bola Moyo kalikonse tikaona ndithu

    • @TsArKhaii
      @TsArKhaii 17 วันที่ผ่านมา +1

      ​@@TonyMhone Ndaseka😂😂..... Kalikonse mukaona

    • @GetrudMagwira
      @GetrudMagwira 17 วันที่ผ่านมา +1

      Zoona kalikonse tikaona mu 2025​@@TonyMhone

    • @TonyMhone
      @TonyMhone 17 วันที่ผ่านมา +2

      @GetrudMagwira Mulungu si Chikangawa khakhakhakhakhakha!!! Koma amene analenga munthu mu chifanidziro chake

    • @asantemkwinda6658
      @asantemkwinda6658 16 วันที่ผ่านมา +1

      Kali konse tikaonatu kkkkk​@@TonyMhone

  • @MoffatNyanyaliwa
    @MoffatNyanyaliwa 16 วันที่ผ่านมา +3

    Powerful message pastor

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 17 วันที่ผ่านมา +4

    Powerful message 🙌🙌🙌

  • @PetersKondana
    @PetersKondana 17 วันที่ผ่านมา +15

    Kkkkkk anyamata ombwambwana onena kuti " boma ndi lomweli" kkkk ndaseka😂😂😂😂😂

  • @AliceKaliat
    @AliceKaliat 14 วันที่ผ่านมา

    Asasowetu mbusa uyu
    Chilungamo pa chilungamo powerful abusa

  • @Nthambi-zg4nu
    @Nthambi-zg4nu 16 วันที่ผ่านมา +1

    Watching from Angola 🇦🇴 preach on MCP Ichoke DPP BOMA 2025
    Chakwela asekula mmimba

  • @SpencerKadewere-cd5ok
    @SpencerKadewere-cd5ok 15 วันที่ผ่านมา

    Amen 🙏🙏 abusa very powerful message eiiiii 😅😅😅

  • @AlexanderMateketa-i8l
    @AlexanderMateketa-i8l 17 วันที่ผ่านมา +2

    Kkkkkk ombwambwanadi sukunama pastor 👍👍👍👍👍💥💥💥💥

  • @TriggerMataka
    @TriggerMataka 17 วันที่ผ่านมา +5

    Man of God 😅😅😅

  • @EmmanuelThambo
    @EmmanuelThambo 16 วันที่ผ่านมา

    Za mphamvu abusa palidi anyamata ombwambwana. Good preaching.

  • @MayamikoJeke-d5m
    @MayamikoJeke-d5m 17 วันที่ผ่านมา +6

    Amen 🙏

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo 16 วันที่ผ่านมา +1

    Chakwera , chimwendo Banda mutuluka ukweche😂😂😂😂

  • @WysonChilonga
    @WysonChilonga 17 วันที่ผ่านมา +6

    panopa nkhani yake ndi kuswa - kuswa basi,tatopa ife😢😢

    • @LysonKandaya
      @LysonKandaya 17 วันที่ผ่านมา

      Kung'amba kung'amba basi

    • @WysonChilonga
      @WysonChilonga 17 วันที่ผ่านมา +1

      @LysonKandaya eeetu ife zotiputsitsa pa imfa ya Chilima takana

  • @patricksinyala1345
    @patricksinyala1345 16 วันที่ผ่านมา

    No spirit of fear in this Man of God Oooh Glorify God chilungamo chenicheni ndithu

  • @MakawaPartrick
    @MakawaPartrick 16 วันที่ผ่านมา +1

    Ife a Malawi ombwambwana chifukwa tikubvutika tokha mkumatenga bzikwanje😂😂😂😂😂😂😂

  • @KENBILLY-m3u
    @KENBILLY-m3u 16 วันที่ผ่านมา +1

    Abusa alowa ndale kufuna ndalama nankha pa maliro ngat kuukwati kkkkkk😢😢😢😢😢😢

  • @ChrispinTaombe
    @ChrispinTaombe 17 วันที่ผ่านมา

    Powerfull message Habusa athu
    Kuswakuswa bas❤❤❤❤❤❤❤

  • @WisdomChisinga
    @WisdomChisinga 13 วันที่ผ่านมา

    Nice man of God

  • @TiniFrancis
    @TiniFrancis 16 วันที่ผ่านมา

    Apa ma press briefing achuluka ndithu😂😂😂😂 powerful message

  • @amosmuluwane4182
    @amosmuluwane4182 15 วันที่ผ่านมา

    Watching from Ntcheu power full message

  • @BiliatMzungudala
    @BiliatMzungudala 17 วันที่ผ่านมา +2

    Kod azibusa akulalika za chakwela pano satana waonekano ndi maso 😂😂😂

    • @GracieRejoice
      @GracieRejoice 16 วันที่ผ่านมา

      Yea zikuoneka kut satana watulukira poyera 😂😂😂

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 16 วันที่ผ่านมา

    True Man of God,God bless you even more

  • @AgnessMakuluni
    @AgnessMakuluni 17 วันที่ผ่านมา +11

    Koma abusawa sitimva kut akusakidwa ndi wamutu ngat vembe uja😂😂😂😂

    • @TonyMhone
      @TonyMhone 17 วันที่ผ่านมา +1

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 😂😂😂😂😂😂 wa Mutu Ngati vwembe Koma anthu mwafika potopa Ku Malawi

    • @jamesjackson6829
      @jamesjackson6829 17 วันที่ผ่านมา

      Kkkkkkk watero

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya 17 วันที่ผ่านมา

      Akungoyenereka kusakidwa kumene..paja iwo safuna chilungamo tu

    • @AgnessMakuluni
      @AgnessMakuluni 17 วันที่ผ่านมา

      @@TonyMhone 🤣🤣🤣

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 17 วันที่ผ่านมา

      Ndye mwati wamutu ngt choswera malambe km cc

  • @RoseThindwa
    @RoseThindwa 17 วันที่ผ่านมา +2

    Powerful speech

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 17 วันที่ผ่านมา +3

    Ambuye.atithandize 😢😢❤

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis 16 วันที่ผ่านมา

    Big Amen izi ndi zooona zokhazokha na. Pomafuna kuwapha anthu chifukwa. Choti akunena zoona anthu tiyankhula. Kwambiri

  • @topgents4979
    @topgents4979 13 วันที่ผ่านมา

    Go deeper pastor amen!!!!!

  • @LovemoreMuzomera-j4h
    @LovemoreMuzomera-j4h 16 วันที่ผ่านมา

    Yankhula munthu wamulungu that's a good point ❤

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu 17 วันที่ผ่านมา +5

    Koma chakwela akuziwonela eee😂😂😂😂😂😂

    • @TonyMhone
      @TonyMhone 17 วันที่ผ่านมา

      Khakhakhakhakhakhakhakhakhakhakhakhakhakhakhakhakhakha kukhala Wina bola kungodzitaya zitsanafike poyipa

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 16 วันที่ผ่านมา

    Amen And amen wina opepela Ali Kuno akut boma ndilomweri

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 17 วันที่ผ่านมา +5

    Ine Chakwela Amandinyasa olo kumva dzina lake sindifuna Pazomwe analonjeza osapanga komanso pozuza ndikupha chilima

    • @chrissyamanda5510
      @chrissyamanda5510 17 วันที่ผ่านมา

      Same group.inenso amandinyasamotu ndi wamutu ngati matako azimayi aku sasafilikayu amandikwanamo limodzi ndi kamagalasi uyu

    • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
      @HappyAbyssinianCat-xt2bm 17 วันที่ผ่านมา

      Km chakwera amatinyasa ndi anthu ambiri naneso simafuna kumva olo voice yake ngakhare Zina lokha la chakwera mmmm simafuna kumva

    • @salmankhanofficiel.5018
      @salmankhanofficiel.5018 17 วันที่ผ่านมา

      Bola ndikulamulila ziko iya😂

    • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
      @HappyAbyssinianCat-xt2bm 17 วันที่ผ่านมา +1

      @@salmankhanofficiel.5018 akalamura kwao kukasiya ife Malawi tamukana sitikumufuna hiyaaa

    • @salmankhanofficiel.5018
      @salmankhanofficiel.5018 17 วันที่ผ่านมา

      @@HappyAbyssinianCat-xt2bm aaaa poti Malawi yose ndizaipha ndizasalako ndekha

  • @CharlesLeo-o7j
    @CharlesLeo-o7j 14 วันที่ผ่านมา

    Watching from RSA,

  • @YamikaniYamikani
    @YamikaniYamikani 16 วันที่ผ่านมา

    zoona mau amveka bwino abusa.mulungu akutezeleni pachilichonse mulungu nkhale kumbaliyanu abusa🎉🎉🎉💃💃💃💃💯💯💯💯🤝💯🤝🤝❤️💯

  • @EnochSamuel-o5e
    @EnochSamuel-o5e 16 วันที่ผ่านมา

    Anyamata ombwambwana, opepera chifukwa cha Sauzande😂

  • @FraserNyozan
    @FraserNyozan 17 วันที่ผ่านมา +1

    Kkkkkk ameni amen amen...mhu Ambuye MULUNGU yemwe anagawanitsa nyanja pakati Ana islayeli mpaka kudusa atithanso kukomza dziko lathu ndipo atithandize kwambri!!! Chifukwa iye ndiye mwini zonse.

  • @IsaacAmiyele-w6y
    @IsaacAmiyele-w6y 16 วันที่ผ่านมา

    Watching from lilongwe azibusa achilungamo ngati awa amasowa and god bless you

  • @JamesBrown-gx8my
    @JamesBrown-gx8my 17 วันที่ผ่านมา +2

    😂uyuyu Akufunika plot

  • @RoseMoses-c9j
    @RoseMoses-c9j 16 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂2025 ija yafika kulizinthu😂😂

  • @g2foods
    @g2foods 16 วันที่ผ่านมา

    One one .....we are towards the truth

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 16 วันที่ผ่านมา

    Unstoppable Voices!!!

  • @AvideOfficial
    @AvideOfficial 16 วันที่ผ่านมา

    Mulungu akulankhula 😂😂😂😅 ndipo MCP ili mazi

  • @HelbertNkolokosa
    @HelbertNkolokosa 17 วันที่ผ่านมา

    Mumakwana abusa osaopa osatopa osafooka man of god

  • @blessingsmwenela1308
    @blessingsmwenela1308 16 วันที่ผ่านมา

    Strong enough 💪 God be with us

  • @JosephEphraim-j9x
    @JosephEphraim-j9x 16 วันที่ผ่านมา

    😅😅😅😅,kumeneku kulibe njala,ikadakhalapo,ndalama amamufupazo,akadagulira ka ufa.

  • @WilsonNedi-s6t
    @WilsonNedi-s6t 16 วันที่ผ่านมา

    Amen my brother, God bless you

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 16 วันที่ผ่านมา

    Za mpanvu man of god🎉🎉🎉

  • @Amunandife3212
    @Amunandife3212 16 วันที่ผ่านมา

    Very powerful

  • @EdenNgulube
    @EdenNgulube 16 วันที่ผ่านมา +1

    Bambowake wa bakili muluzi tv awa😂

    • @ChisomoYosefe
      @ChisomoYosefe 16 วันที่ผ่านมา

      😂😂😂😂😂

  • @CharlesBanda-v8k
    @CharlesBanda-v8k 17 วันที่ผ่านมา +1

    Ine ndasiya sinzanenaso kuti boma ndilomweli 😂😂😂😂😂😂 ikhale dpp yomweyo basi

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya 17 วันที่ผ่านมา

      Simunachedwe...mwazisiya nthawi ya bho bho😂😂😂

  • @BobJoshua-q5n
    @BobJoshua-q5n 16 วันที่ผ่านมา

    Good preaching

  • @chrissyamanda5510
    @chrissyamanda5510 17 วันที่ผ่านมา +8

    Ambuye Yehova mphambe chisumphi Namalenga
    Chita chotheka kuti mwazi akhetsa mu zaka 4 ukhale chida chowakanthìla apite ku Short left tione ulamuliro wina
    Tàtopa

    • @ArnoldSefasi
      @ArnoldSefasi 16 วันที่ผ่านมา +1

      A chri bho bho

  • @NelsonMd-x5h
    @NelsonMd-x5h 16 วันที่ผ่านมา +1

    Trust me ngakhale azibusa kaya azi bishop ata tokota motani. CHAKWERA awinaso.
    Nkhondo zake sizimenyèdwa ndi anthu.
    Pitilìani ndithu ku yankhula mmene munga kwanisilemo.
    Mothandizidwa ndi social media, ndi zina.
    Mwa chepa nayo nkhondo simunngamu gonjetse Chakwera

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 16 วันที่ผ่านมา

      Pajadi mphavu za satanic zili ndi chakwera mulungu akuchepa, simwatero operekera magazi pansi panyanja??

    • @veronicagullo9373
      @veronicagullo9373 16 วันที่ผ่านมา

      Ndipo achepadi

    • @BeatriceSaulosi
      @BeatriceSaulosi 15 วันที่ผ่านมา

      Aaaaa inuyo ndi mulungu??? Chifukwa choti inu mukuba ndalama za Malawi nkona mukuyakhula mopusa ana a njoka

  • @MariaNkhata-i9q
    @MariaNkhata-i9q 16 วันที่ผ่านมา

    Abusa koma inuyo mwamva ❤❤❤

  • @AllunaBenjamin
    @AllunaBenjamin 16 วันที่ผ่านมา

    God bs paster cholakwika chizuzulidwe kuti aziwe choona

  • @EvanceSungani-cv9jk
    @EvanceSungani-cv9jk 17 วันที่ผ่านมา +4

    Eeeeeee koma wagagada😂😂😂😂😂😂😂

  • @AnnaMarverous
    @AnnaMarverous 12 วันที่ผ่านมา

    Ndizabwino bwino Ali ndi ufulu olakhula nawoso ndi ovotawoso Ali mmipingo momwemo

  • @MchachaGift
    @MchachaGift 17 วันที่ผ่านมา

    Powerful message

  • @SymonMakanya
    @SymonMakanya 15 วันที่ผ่านมา

    Koma lazaro wa umphawi wanvera nawo ulalikiwu😅

  • @ChimtamboWiliam
    @ChimtamboWiliam 16 วันที่ผ่านมา

    Amen god is good

  • @Godwin-xy9rg
    @Godwin-xy9rg 16 วันที่ผ่านมา

    Amen chilungamo chichiona malo m'busa koma uyu

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 16 วันที่ผ่านมา

    Azibusa akuLilongwe kozekelani Press Briefing!!!😂😂😂

    • @TiniFrancis
      @TiniFrancis 16 วันที่ผ่านมา

      😂😂😂😂😂

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 15 วันที่ผ่านมา

    DZIKO LATHU LAFIKAPA LIKUFUNIKA AZIBUSA NGATI AWA OSAKONDA DYERA

  • @Jonas-v8y
    @Jonas-v8y 17 วันที่ผ่านมา +2

    Lelo kumachinga kuno chimanga mpaka 7000 chigoba, tikuona kutalika September atipha basi galu ameneyu, eeeh ayi ndithu, ife ndiye tikuti tili ntawuni nanga akumudzi

    • @goodieschiwaula2756
      @goodieschiwaula2756 16 วันที่ผ่านมา

      Kodi zilipobe zomagula chimanga? Zaulesi eti?

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 17 วันที่ผ่านมา +2

    Abusa nawo ndi anthu ....Atopa

  • @WilliamMasudi
    @WilliamMasudi 16 วันที่ผ่านมา

    Koma zinazi mesa ombwambwana ndiyeyo analandila makobili apa akunena azake kuti opepela eish awa 🙄

  • @WilliamMisoya-g3z
    @WilliamMisoya-g3z 17 วันที่ผ่านมา +1

    Sanalakwe muthuyoo❤❤

  • @MathewsMandutu-q9l
    @MathewsMandutu-q9l 16 วันที่ผ่านมา

    Abwere kuno tikuwafuna abusawo mmm anthu akuziwa kulinganiza ..

  • @JosephEphraim-j9x
    @JosephEphraim-j9x 16 วันที่ผ่านมา

    Tsoka m'busa,komanso anthu omwe sadziwa,kapena kusakhulupirira mau a pa Mateyu Chapter 24

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 17 วันที่ผ่านมา +1

    Chakwela watha basi Ali moyo Magazi awanthu 9 akuyenda paliponse pa malawi mpakana azamwalila chikangawa mozunzika ndi mizimu ya anthu anawapha aha mwadI wa munthu ndiwoopsya ngati si iwowo ana ake kapena zizukulu zake zizalipila mwadzi omwe anaukhesa chifukwa cha dyela

  • @Witness-t7d
    @Witness-t7d 16 วันที่ผ่านมา

    Fire 🔥🔥🔥🔥

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 17 วันที่ผ่านมา +2

    Abusa andisangalatsa ponena kuti ANYAMATA OMBWAMBWANA aaah uwu nde mutu wa ulalikiwu chifukwa akunena zoona.

  • @SamMoyo-o8h
    @SamMoyo-o8h 16 วันที่ผ่านมา

    Amen 😊

  • @ShillahLawrence
    @ShillahLawrence 16 วันที่ผ่านมา

    Uyu amauza Nkhosa zake , kusiyana ndiopanda Mpingo aja chifukwa amauza Dziko

  • @Benrabson
    @Benrabson 16 วันที่ผ่านมา

    A ena akuthawapo nga MCP bwanji😢😮

  • @VeraChirwa-c5n
    @VeraChirwa-c5n 17 วันที่ผ่านมา +2

    Ambuye kumwambako pulumutsani Malawi

  • @SymonJowabe-y1q
    @SymonJowabe-y1q 17 วันที่ผ่านมา +2

    Apabasi zathapo DPP woyeerere

  • @UchiziMwakilasa
    @UchiziMwakilasa 16 วันที่ผ่านมา

    Ndiwonere bwino,,,,Malawi yanga yikupita kut 🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @paulnyirongo7876
    @paulnyirongo7876 17 วันที่ผ่านมา +1

    Diluting the gospel

  • @CrytontwalikiManyungwa
    @CrytontwalikiManyungwa 16 วันที่ผ่านมา

    Go deeper poster❤❤❤

  • @Zainabu-o1c
    @Zainabu-o1c 17 วันที่ผ่านมา +2

    Komatu azibusa mwamasuka kwamba Ka bishop msusa

  • @GladysMagadi
    @GladysMagadi 16 วันที่ผ่านมา

    Kakakakaka apa ukhozakuyiwala kt ndiwe nafwedwa shaaaaa ulaliki imenewu wandiwaza

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 16 วันที่ผ่านมา

    Anyamata Ombwambwana aboma ndilomweli😂

  • @SMARTLEVIEKAMANGA
    @SMARTLEVIEKAMANGA 16 วันที่ผ่านมา

    Watching from TZ mumakwana abusa ulemu wanu

  • @JustinKondowe
    @JustinKondowe 17 วันที่ผ่านมา +4

    Chaka chino tiona zanthu kkkkkk

  • @AzencoNjirima
    @AzencoNjirima 17 วันที่ผ่านมา

    very good