Another concern. Students went to colleges and were certified by the Gvt that they qualified for secondary school teaching, college lecturing, tutoring etc. Why is it that the TCM in conjunction with the TSC are forcing all teachers, lecturers and tutors to register and get their licenses for them to teach in this country at an exorbitant fees of 24,000 in registering and 24,000 in licensing? How, why, where from?
Wake up opposition mukutipanga ife kufooka, komanso ndifunse sizingatheke tsiku lovota ma representative onse azipani kunyamuka nawo mpaka kwa a DC kowelenga mavoti kumaliza aliyense ndikusunga zosatilazo?
Komadi chikuchitika ndi chani ku zipani zotsutsa, anthu oti azakuvotereni ndi awa alibe ma ID koma muli busy kunena kuti olo munthu atamwa ambuye mtengeni sangavotere mcp anthufe zikutinyatsa koma inu andale muli pheeeee
Thanks Mr Dc... Potiziwisa ife pano ....
That's a strong advice ❤❤
Another concern. Students went to colleges and were certified by the Gvt that they qualified for secondary school teaching, college lecturing, tutoring etc. Why is it that the TCM in conjunction with the TSC are forcing all teachers, lecturers and tutors to register and get their licenses for them to teach in this country at an exorbitant fees of 24,000 in registering and 24,000 in licensing? How, why, where from?
Kodi compaign asegulira ?
Komatu anthu azipani zotsutsa pena pake mukumapweteketsa mtima kwabasi aaah tawonani chimunthu chonamiza mtundu wa amalawi kuti wabweretsa mafuta while zinthu sizili chomwechi ayi penapake mukutipweteketsa mtima pliz otsutsa khalan mmaso pliz
Mr DC tikufuna #yanu
Mr DC mmakwana chilungamo chiyende ngatimazi😅
Inuyo ndi one Mr DC
Zimene mwanena ndizoona Bon kalindo ❤❤❤❤❤
Kodizitsilu zikufunachiyani ice chakwelayu watopetsa abonikalindo titaniamalawi? Mukuyesetsa kuimilaamalawi
Mr DC akutimana # yao...km more fire bas chilungamo nde chikubwera poyera...mmakwana mr DC powasegula maso akhutukumve a opposition wo
Inuso ndiyenu adale sumuwasata bwino palibe chilungamo apa bon kalindo walandilapo zake apo
Please GOD open the oppo eyes 😢😢😢😢😢please
The first mumatiimirira
Mr DC tayeaani mulakhule nawo muwafunse mumve kuti opposition wa aliipati zonse zikulakhulidwazi, tsono anthu awasokoneza sadziwa kopitatu, madando onsewa iwo sakuwaona kapena sakumva?
Truly speaking, Mr Dc
Kukoma kwake mizimu yonse 9 ikuona zomweakuchita mr chikangawa
😂😂nde mwat wamisala watikufelanji😂😂😂😂😂
Mr dc
You are aliar. Siunaone mafuta akutsitsidwa relo? Izi sizikuthandizani akalindo ndi Dpp yanuyo.
Ngati adakwanisa kutinamiza za report,angalephere kutinamiza kt mafuta abwera koma ili molasses?
Kod guys osunsawa awapepetula mmm kwangot ziiiii guys wake up pls pls
The best
ndichifukwa anamupha chilima uja anadziwa kuti ndiyekhayo amenealidoro ndipo ndikutha kuona mcp ikuzalamukilaso
Ndipo zoonadi ndithu, Koma anthu amwalira ambiri kungowinaso shaaaaaaa
Akutitaka tikugona kwambri a opposition
Makwana bro
Nyasi za mcp tatopa nazo aaa
Apange test kavotedwe ndiye akuti mavoti amenewo sazampasa wina aliyense azatenga iwowo inu osafunsa funso kuti akasunge ndindani ndipo akapanga nawo chani, auzeni kuti azaochedwe inu mukuona
Chakwela waapha anthu mitima ndi usataniki wakewo
Inu mukuona ngati Mchabe
???
Opposition ikugona kuno kukaronga ambiri sitinalembese,
Amayooooo malawi wanga ine ndipo anthu otsutsa akupsetsa mtima bwanji et avomeleza kut mavoti akayesele kuvota zimenezo zinayamba zachitika
Kond bwana tingayimbe bwanj mafoni
Ndipod amalawi tikuvutika kuno ku South Africa zowophya zafika pot anthu mkumathawa mnyumba mkumakagona mmitengo madera enawa iiiii
Ndipo mayi kodi opposition ikutani kwenikwen ife amalawi tikudalila apportion koma akuwonekadi kuti akungona kwambili
Opposition is too weak
Atigwira m'maso ndi tsabolatu? Opposition nayonso ili busy kuyika ndalama nthumba 😂😂😂😂😂
Opposition DPP, UDF, UTM has already written NRB to flush them with Centra region figures.
Munthu akuti tikusatira wamisala koma nayenso ali pompa kutsatira wamisalayo😂😂😂😂😂
paja inu mumagwira ndi opposition ntchito. kkkkkk muliratu, Boma ndilomweli bwana
inuyo ka imileni mwina mudzakhale president inuyo ka
Tinadziwa kut ndi empty train
Tiyeni tiyende pasewu chakwera achoke
Nde inu mufuna iramulire dpp bwana dc
Penapake kumanvetsesa, boma la South Africa likumanga anthu omwe alibe mapepala okhalila mzikomo osati winaaliyense . Dziko la Malawi limanyengelera anthu omwe amakhala mdziko muno popanda chilolezo uko ndikupusa kwa dziko lino
Ndipo mulibedi mafuta asatinamize sife ana
Wabodza galu iwe
😂😂😂tinadziwa kut chakwera sangabweretse mafuta
I'm khuzid
Dolo anali chilima uja basi zasalazi ndi mbuzi zokha zokha
❤❤❤❤
Aaaa anthu awa akutiputsitsa ndipo angona kwabas ndie awina bwanji tilimba mtima bwanji aaa
Mr nyooooo
Kod zipani zotsutsazi zikutani
Opposition yausilu heavy bola ndzipta ku america
Mulungu azikudalisani
The DCcccccccccc mwana oopsa kwambili
Tilibe opposition man aaaa onse ndiopoyila
Chilima uja anali dolo RIP panopa asala ndimakape okhaokha basi, mavuto adakalipobe unfortunately
Ndimafuta abwela musasokoneze anthu apa kambani za opposition ya gogoyo
The DC❤
President uyuyu koma ngochimwitsa mbamba
Ife chikangawa atipulula
Akalindo avekendwa zinyau onsewa chinyau nd choopsa
Vuto kosusa kuli azigogo okhaokha ndie iiiii zativuta basi
Wake up opposition mukutipanga ife kufooka, komanso ndifunse sizingatheke tsiku lovota ma representative onse azipani kunyamuka nawo mpaka kwa a DC kowelenga mavoti kumaliza aliyense ndikusunga zosatilazo?
Komadi chikuchitika ndi chani ku zipani zotsutsa, anthu oti azakuvotereni ndi awa alibe ma ID koma muli busy kunena kuti olo munthu atamwa ambuye mtengeni sangavotere mcp anthufe zikutinyatsa koma inu andale muli pheeeee
Ndi osamva amenewa zina ndi izi at I chisakho choyesera aaaaaaaa
Ndipo akugonadi zoona ine ndipo zikundiwawa bwanji akufuna kugulisa ziko zoona ndi chakwera
Inu NDi wamisala uyu ,Kodi anthu mumamutsatilabe uyu NDi misala yake?
sikuti abela tilipo odzavotera
Msanje mau abodza mafuta asowa liti
Koma muli thobwa? NDi nandolo eti?opposition ya masiku ano hahaha
Tanzukani achaponda mukugona tulotu muzalila
Km iwe umagona? Ndipo mutu wako sukugwira uli ndichimtima choipa
Aww🇨🇭🇷🇸🕛
The DC mwana wowophya kwambiri Bon kalindooooooo
Inu tangomuchotsa ni chakwela chaka chatsalachi alamulile asilikali aaaaa
Asilikaliwo ndiomwe akusokonezaso zithu
😂🤣 koma ku Malawi kuno
Asaaaaa apa tafa basi.
Azipani zosusa agona tulo zedi, mkonono mkati rhiiiiiii,,,, rhiiiiiii,,,, rhiiiii
Ndipo akupwetekesa mtima zedi
Haha 😂😂😂😂😂 Koma akulu inu Mmmm 🙌
@@MatthewKanyenda kkkkkkkk, amwene zikupwetekesa mtima zedi
@@VictoriaWilly kwambiri tu mmmmm 🙌 zachilendo kobasi zomwe zikuchitika ndi otsutsa awa. Even Ku parliament Kuli quite no active.
😢
kumalawi mkokoma😂
Zabwino zose mulungu akudalisen koma ndimafunako number yanu chonde
The Dcc
The dangerous child
DC
😂
Not good at all
Please GOD open the oppo eyes 😢😢😢😢😢please