MICHAEL USI NAYE NDI MUNTHU LERO WAULURA ZINSISI ZOMWE ZINACHITIKA SAULOS CHILIMA ATANGOMWALIRA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 1 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น •

  • @AndyChakalipa
    @AndyChakalipa หลายเดือนก่อน +13

    Awawa ndi amuna mfundo komanso school,God bless you Mr usi🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @chiogamata2560
    @chiogamata2560 หลายเดือนก่อน +3

    I always say this, mmalawi muno ngat tili ndi one of the smart guys with wisdom, humility and posseses good qualities of leadership, Usi is one of them.
    Am not a UTM member but I just love this guy, and i wish Malawi had people like him as our president.
    I wish you nothing but the best

  • @TressLuka
    @TressLuka หลายเดือนก่อน +22

    Osamukhulupilira uyu Inuuu. Anatigwilitsa fuwa lamoto. Ndani angalore kumakonda ng'ona koma ikukudyera ana 😅😢😢😢

  • @adammwakitalu7959
    @adammwakitalu7959 หลายเดือนก่อน +26

    Dr usi said utm is still on tonse alliance according to agreement. Would you please ask him this question. Will utm rule malawi for the 5 coming yrs according to agreement?

    • @MaxwellZumbu
      @MaxwellZumbu หลายเดือนก่อน +2

      That's exactly what I want to ask

    • @thomaschikondibanda
      @thomaschikondibanda หลายเดือนก่อน

      If UTM is still in agreement with tonse, that's great guestion chakhaza would ask Usiyo

    • @ancientnkhata1137
      @ancientnkhata1137 หลายเดือนก่อน

      Did they show the terms of the agreement ?

    • @twaibupatrick-k1n
      @twaibupatrick-k1n หลายเดือนก่อน +3

      Wausilu ameneyu chilima amafuna kutuluka mwa liance iyeyu bwanji sakufuna kutuluka

    • @RemitterFlik1130
      @RemitterFlik1130 หลายเดือนก่อน

      ​@@twaibupatrick-k1nameneyu ndamene amatenga zisisi zakuti chilima akufuna kutuluka mu mgwilizano wa tonse ku mcp

  • @KassimKajosolo
    @KassimKajosolo หลายเดือนก่อน +20

    Joab you are a good journalist, mwaitenga bwino interview with good questions that we needed to know

  • @EDGARMPIKAMEZO
    @EDGARMPIKAMEZO หลายเดือนก่อน +26

    Joab chakhaza ndiwe mtolankhani wanzeru kwambiri. Sumaonetsera mbali. Big up !!!

  • @CarynSasamala-g5o
    @CarynSasamala-g5o หลายเดือนก่อน +7

    Koma kuona kwanga jelasi ndiyomwe inakula,, pano ndakuvetsa ussi osalimbana nawo zavuta okha😘

  • @EnossDzuwa
    @EnossDzuwa หลายเดือนก่อน +44

    Kmatu Zina zimangovuta kumbari ya Micheal Ussi kma this guy Ali ndi mzeru ndipo penaso kumuyang'anitsitsa ndukumumvetsetsa muliso umunthu keep it up Ussi sindimakutsatirayi kma uli ndi mzeru

    • @thomaschikondibanda
      @thomaschikondibanda หลายเดือนก่อน +4

      Palibe zanzeru apa iwee

    • @BlessingsNyirenda-ru7ss
      @BlessingsNyirenda-ru7ss หลายเดือนก่อน +4

      Vuto ndiloti uyuyu akufuna apitise chipan ku mcp

    • @ahmadajaihdaud
      @ahmadajaihdaud หลายเดือนก่อน

      @@thomaschikondibanda p
      جج
      p
      ppppp
      pp

    • @bornwellkanyoza-nu4iv
      @bornwellkanyoza-nu4iv หลายเดือนก่อน

      Bro ngati mwini wake amafuna kutuluka ku gwilizano ndiye bwanji iye osapangaa zomwe nzakeyo amafuna ndicholinga kuti zithu zikhale monga mene iue amafunira

    • @RitaBan-t7c
      @RitaBan-t7c หลายเดือนก่อน +2

      Uyuuu ndisatana musamamukhulupilire ankanfuna akhare wabwino ndiwe galy kobasi

  • @peterbyson6269
    @peterbyson6269 หลายเดือนก่อน +3

    According to what usi on this interview is saying i have started understanding him and he is the great leader❤❤

  • @JustinKalumpha
    @JustinKalumpha 12 วันที่ผ่านมา

    Great leader indeed afana oganiza boo you deserve next time to rule this country 😊

  • @AnnieMhango-t4w
    @AnnieMhango-t4w หลายเดือนก่อน +1

    The interview is so good and credit is given to the vice president keep up

  • @michaeljenda2421
    @michaeljenda2421 หลายเดือนก่อน +2

    Listen to him with neutral ears you'll hear the wisdom in him
    Usi has umunthu and respect
    We can now understand what's going on with UTM members

  • @innocentsambo9174
    @innocentsambo9174 หลายเดือนก่อน +1

    This is my leader I love him so much bcz I know him beyond the human nature

  • @LaidisiPhiri
    @LaidisiPhiri หลายเดือนก่อน +3

    I like ur speach Dr. Usi

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 หลายเดือนก่อน +3

    sindine wa ndale koma zibambo uyu Usi mulungu azimudalitsa,munthu wabwino wa nzeru komanso wabwino ..kunyozedwa koma samabwezera choipa..munthu ukamamufunila nzako zoipa Mulungu sakudalitsa..

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h หลายเดือนก่อน +13

    Viva Usi u have wisdom big u deserve to b UTM president

    • @JusticeMikondo-i9e
      @JusticeMikondo-i9e หลายเดือนก่อน

      ndili pa mbuyo pa bwana Usi basi

    • @ancientnkhata1137
      @ancientnkhata1137 หลายเดือนก่อน

      Pambuyo pa bwana Usi adha. He is wise

    • @JasonMailos
      @JasonMailos หลายเดือนก่อน

      Manganya opeleka zakeuyu😅

  • @hamzahdael1291
    @hamzahdael1291 หลายเดือนก่อน +3

    Dr usi ndi munthu opilira hvy... Munthuyu waziona hvy....😢

  • @DeborahJimu
    @DeborahJimu 2 หลายเดือนก่อน +5

    The vice president Michael usi is very wise and if everything being said here is true ....then jndeed some people are bitter ...i. Truly see why SKC CHOSE HIM ....
    KOMABE PALIBE YOMWE ALI OLUNGAMA KOMA sanje ndi upo wanu kuwonestsera before convention shows something ....
    I love usi. I love akweni. I love Fredokis i love UTM
    If at all UTM could come together as one ..
    One ❤ to all leaders

    • @TwalikiWisiki
      @TwalikiWisiki 2 หลายเดือนก่อน

      @@DeborahJimu SKC unknowingly due to luck of discernment chose Usi who is so cunning like a snake, he trusted him just like jesus trusted Judas the only difference is that jesus knew exactly who judas was and he knew very very well that one day this fellow would BETRAY him,unlike Chilima he poured out his love and trust in this sell out, not knowing he will betray him, the truth of the Matter is Usi is very very very wicked,no matter how much of good words can come out of his mouth he is a traitor period,

    • @TwalikiWisiki
      @TwalikiWisiki 2 หลายเดือนก่อน +3

      @@DeborahJimu so you call it wisdom when one betrays a person who made them to be who they are today, its wisdom rite, Usi is so cunning like a serpent Chilima did not see this, truly he could have stayed far away too far from this wicked man,when you find a person who claims to be your brother or friend feasting on the same table with your enemies pit a big question ??

    • @JeffreyKambwemba-zs7wy
      @JeffreyKambwemba-zs7wy 2 หลายเดือนก่อน

      Za pankholo eti

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi หลายเดือนก่อน

      Shame

    • @RodgersMwanakhu
      @RodgersMwanakhu หลายเดือนก่อน

      No way we can say ussi is wise muzimuwelenga munthu akamayankha mafunso ,,,uyu akuyankha motchatchalika

  • @JohnAsifathom
    @JohnAsifathom 2 หลายเดือนก่อน +14

    Munthu waboza samasowa munthuyi nditabwali ndinthu ndpo zikumveka kt maudindo ake onse amawapeza munthu akamwalira tshoti ameneyu

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde 2 หลายเดือนก่อน +1

      😂😂😂😂😂😂

    • @faithmagombo3666
      @faithmagombo3666 2 หลายเดือนก่อน +2

      Ndipo live okonda kunog’ona uyu

    • @JeanBetha
      @JeanBetha 2 หลายเดือนก่อน +1

      Aaaaaaah za. Zii 😢

    • @johnlameck8366
      @johnlameck8366 หลายเดือนก่อน +1

      Exactly

    • @MzikaPhiri
      @MzikaPhiri หลายเดือนก่อน +1

      Kkkkkkkkkk

  • @ernestkenamu7956
    @ernestkenamu7956 หลายเดือนก่อน

    Dr Ussi is an intelligent man. He's got too much wisdom

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba หลายเดือนก่อน +2

    A UTM apa za convention palibe komanso mmene wanenera Vice President DR Michael usi very diligent, wise muchenjere mukapanda kuzitenga bwino mutha ngati makatani.

  • @StanleyMzumara
    @StanleyMzumara หลายเดือนก่อน +1

    Chilima sanalakwitse kusankha Michael Usi. Munthuyu nzeru nzosayamba. Katundu waboma ameneyu

  • @dikenzthomo8284
    @dikenzthomo8284 หลายเดือนก่อน +4

    A Usi akukamba zoona koma vuto ndi lakuti a Usi ali ndi ma cadet 2.Ambiri a UTM ndi macadet.Zoona zake ndi zoti UTM ithela ku DPP a Usi akangochoka mu UTM

  • @CarlosChakwana
    @CarlosChakwana หลายเดือนก่อน +5

    Michael ussi nduwa mzelu guys amanganiza asanalakhule

  • @EDGARMPIKAMEZO
    @EDGARMPIKAMEZO หลายเดือนก่อน +3

    Michael Usi ndi wanzeru. Ndimkamupeputsa but he has more Wisdom.

  • @lloydkondowe262
    @lloydkondowe262 หลายเดือนก่อน +1

    Great speech an responses to questions alot has been put on the ground and its eye opening BUT i didnt Hear anything about developing the National or taking us forward as a country Only fights on who has to be the leader and am not conviced why He should be given the continuation of Party Leader.

  • @TembaniMwasanyira
    @TembaniMwasanyira หลายเดือนก่อน +5

    Usi ndakuvesesa kwambiri Ife atu osapota chipani cha UTM ndife ovuta chilima tikamukonda ndimoyowake wolimba tima amakumana ndimilandu km samayakhula Kathu amaziwa zambiri and ngati pamene wayima USI uyime pomwepo

  • @DinaNicholas
    @DinaNicholas หลายเดือนก่อน +2

    Koma chakhaza ndiwe dolo pa kafusidwe, macheael usi wishing u good lucky to success

  • @HagaiChiwer
    @HagaiChiwer หลายเดือนก่อน +4

    Ku utm ayanja alendo Dalitso Kabambe siwa utm ndiwa dpp lero akuti akhale president kusoneza uku mukusala achiyamba kale kuyanja alendo muchifoketsa chipani ndi omwewa ankazuza a Chilima lero mukufuna atsogolere chipani chawo 😢😢😢😢😢😢😢😢😢 chisokonezo

  • @CarolineLiabunya-j8k
    @CarolineLiabunya-j8k หลายเดือนก่อน +10

    Uthenga unakupezani muli ku Blantyre mukuchokera kowaimilira a Chilima ku maliro a Kasambara? Ndiye a Chilima that time amapita kuti?

    • @HartleyMillion
      @HartleyMillion หลายเดือนก่อน +1

      Amakawaimilira bwanji yet mwini wake amapita konko nzoona zimenezi?.
      Komanso ati uthenga unampeza ku BT akuchoka kumaliro kwa kasambala yet zinamveka maliro asanaikidwe nde zikukhala bwanji pamenepo kkkk

    • @mkandawirem610
      @mkandawirem610 หลายเดือนก่อน +1

      Ndipotu zosamveka apa

    • @thomaschikondibanda
      @thomaschikondibanda หลายเดือนก่อน

      Wabalalika uyuu kkkk

    • @IsaacMasamba-j3h
      @IsaacMasamba-j3h หลายเดือนก่อน +1

      Maliro sakhala mbali imodzi mbuli inu munthu ngati amakhala ku Dera Lina lomwe silakwawo maliro amakhale Malo osiyana kkkkkkkkk palibe kubalalika

    • @vincentlamanmathebulamwana5697
      @vincentlamanmathebulamwana5697 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂 Guys uyu ndiwaboza panyelo pake

  • @PatrickAnusa
    @PatrickAnusa 2 หลายเดือนก่อน +4

    Am not his fan or his member but let's say the truth this guy is talking very sense and it sound good and truth ethen if his rying utm was suppose tain him back just like that without look his frowerd until convention and see how hi is

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p 2 หลายเดือนก่อน +2

    It's the first time I have heard him take ownership of UTM. As a leader, these are the growing pains, can he overcome.

  • @AndrewKadammanja
    @AndrewKadammanja หลายเดือนก่อน +1

    Zinthu zkamatere umangodzwilatu kut munthu wamzeru adadzphatikiza ekha nddzitsiru zmene or ztavuta sdzngapitirize loto lake lamunthu wanzeru yo,,,may Chilima's soul continue resting in eternal peace 😭😭😭😭🙏🙏 your legacy is going to be destroy chfukwa cha dzitsiru dzmene zdakuzunguliran bwana 😭😭🙏🙏

  • @SolomonMagola
    @SolomonMagola หลายเดือนก่อน +1

    Lord have mercy for us
    Truth shall be seen no matter how long it shall take.

  • @JosephBotoman
    @JosephBotoman หลายเดือนก่อน +1

    Mumalakwitsa kumabisa mawu enawo komano chomwe ndatolamo mchakuti dr Usi sinunwandale ndipo khalidwe landale mwainu mulibe so please please please siyani kupanga kugwilizana ndianthu andale chifukwa pang'ono pang'ono mutengela khalidweli,siyani chonde ndale mukapange zina ndipo Mulungu adzakudalitsani

  • @IsabelNkomwa
    @IsabelNkomwa หลายเดือนก่อน +2

    Viva usi kuyankhula mosapsatila

  • @petrosmunthali5562
    @petrosmunthali5562 หลายเดือนก่อน +12

    Manganya fails to run the UTM since the death of SKC coz MCP is using him hence planning to destroy UTM

    • @YOUNGKIDS-k5d
      @YOUNGKIDS-k5d หลายเดือนก่อน

      Ummmm kuwawa kutelo mwava kuti amamuletsa kodi mukanakhala inu mukanatani ngati munthu wokanidwa

    • @thomaschikondibanda
      @thomaschikondibanda หลายเดือนก่อน

      Exactly

    • @franciskammadzi9237
      @franciskammadzi9237 หลายเดือนก่อน

      Wakulurani oipa inu

    • @WisemanMunthali
      @WisemanMunthali หลายเดือนก่อน +1

      I disagree with you broh/ cater. Honestly pa usi apa ndipamene Pali ndale zoopsa kwambiri chifukwa wadzungulilidwa ndi anthu akuluakulu okhwima pa ndale.enawa onse ndi ana.... munthu yemwe wakhala pafupi ndi chilima si munthu wamba.muzavele uyu amati mtumbuka uyu wajoina utm posachedwapa.ameneyi kugwila nthito ndi usi ntchito yawo ikhala bwino kwambiri

    • @gesinasutherland9241
      @gesinasutherland9241 หลายเดือนก่อน

      usi❤

  • @chimwemwemankhusu2491
    @chimwemwemankhusu2491 หลายเดือนก่อน

    I'm learning something from you Dr Usi
    Xool osazayiphweketsa

  • @RaffickAllie
    @RaffickAllie หลายเดือนก่อน +2

    Ngati unaudzidwa kuti usapedzeke ma maliro bwanji suunapangise sonkhano wa Atorankhani ngati njira imodzi yozisatsa

    • @madalitsokachenje5894
      @madalitsokachenje5894 หลายเดือนก่อน

      Ndiye pomwe pali mnzerupo.....sinakapereka picture yotani Ku dziko? I believe you could be the first one kuyankhula kuti mwaona ayamba kumenyana.!!!! Munthu angachite ubwino ena amayankhulabe. Anachita chanzeru.

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba หลายเดือนก่อน +9

    Apa zawonesa kuti USI ndiye wa UTM original with Late Chilimas blessings enawa ndi ma CADET, ndi patipo Chilima anadandaulapo za a USI ali moyo, gulu linali ndi ma CADET amavutisa ngakhale Chilima kungoti Chilima amawasungira ulemu chabe

    • @SamNkhomo
      @SamNkhomo หลายเดือนก่อน +2

      I don't trust this man

    • @Mavisbunny346
      @Mavisbunny346 หลายเดือนก่อน

      He looks not honest

    • @gesinasutherland9241
      @gesinasutherland9241 หลายเดือนก่อน

      more fire abwana

  • @kaitanokagalu
    @kaitanokagalu หลายเดือนก่อน +2

    In my own view of this interview, I have discovered kuti the Team Kaliati and the big UTM knew the death of Chilima before the crash.

  • @PreciousKaptain-kt9zg
    @PreciousKaptain-kt9zg หลายเดือนก่อน +2

    Kusamala mphika waboma apa!! Chirima amayenda yekha bwanj

  • @ColetteMalunga
    @ColetteMalunga หลายเดือนก่อน +3

    Jelasi idakula ku Malawi, nthawi zonse munthu timamulembera malire, kumuyang'anira pansi ndikunyoza. Usi is very wise 👌. Mulungu achite kufuna kwake popereka mtsogolere ofuna kutukula Malawi. If is you Mr Usi, God be with you.

  • @IsaacCloves
    @IsaacCloves หลายเดือนก่อน

    Uyu ndimwana pandale😂😂😂 akumayankha zosiyana ndifuso kkkk

  • @M.shukriAdams
    @M.shukriAdams หลายเดือนก่อน +1

    Ndiwabodza ameneyo siwa utm usi wa mcp palibe chisisi pa dziko lapasa

  • @MphindiraChimwemwe
    @MphindiraChimwemwe หลายเดือนก่อน +7

    Usi ndiwe munthu woipa Kwa mbiri zonse wakambazi ndizaboza

    • @johnlameck8366
      @johnlameck8366 หลายเดือนก่อน

      Am agreeing with you

    • @happychimwemwe-1805
      @happychimwemwe-1805 หลายเดือนก่อน

      Aka ndikabodza kwambr

    • @madalitsokachenje5894
      @madalitsokachenje5894 หลายเดือนก่อน

      You have the truth of him,,, please come forward and say your facts.....nsanje isakuonongeni maso kuona zoipa za munthu...

  • @AdamAdamm-b3v
    @AdamAdamm-b3v หลายเดือนก่อน

    Nanga akufuna anene mayina inu.mukubisa bwanji ndiye tivapo cha.mboloyanu nonse 😅😂😂

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym หลายเดือนก่อน +1

    Nde anzake azimusekelere pomwe iye amapanga zathira kuwiri kukanena mabodza kwa chikangawa mpaka chilima wamupha,anthu ena ndiofyafyalika pakamwa kt vimveke bwino kamunthu koipa Aka😮😮😮

  • @LemosBanda
    @LemosBanda หลายเดือนก่อน +1

    Kodi anamenyedwa anthu angati ku Maliro amene aja.?????
    Kodi onse anali ku Maliro amene aja anali a UTM okha okha.?????
    Bodźa ilo pafuka Utsi pali Moto. Manganya munthu oyipa ndi osokoneza. Anapereka Chilima ku imfa uyu dyera la ndalama.
    Zomwe amaona ali ku ADRA panopa sakuonanso ndalama zabweresa Khungu.

  • @SandraChibaka
    @SandraChibaka หลายเดือนก่อน

    No words to express my concerns.... Only Chilima should continue to rest in peace 😔

  • @PatrickChangadeya
    @PatrickChangadeya หลายเดือนก่อน

    Kulankhula molakwika kumeneku muloreni usi agwile ntchito yake❤

  • @ChristianMalingamoyo
    @ChristianMalingamoyo หลายเดือนก่อน +2

    Mr mthilakuwiri

  • @JustinPhiri-kq2bb
    @JustinPhiri-kq2bb หลายเดือนก่อน +1

    Conversation ndiyomwe ikasankhe president wa UTM weniweni

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma หลายเดือนก่อน

    Kulakhula mwazelu kobas ausi mwalakhulakale bwino ndipokhaniyo ndiyoonadi ndipo mwapilila timadabwatu aaaaa munapililadi

  • @LoyceMhango
    @LoyceMhango หลายเดือนก่อน +1

    UTM inatuluka mu mgwirizano.Akukakamilako iyeyu

  • @MikeMoris-zp6yg
    @MikeMoris-zp6yg 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ur wise man usi l follow u

  • @GamizaniBanda
    @GamizaniBanda หลายเดือนก่อน +1

    Manganya ndi machine👏

  • @ElizaSalunda
    @ElizaSalunda หลายเดือนก่อน

    Aaaa ndiye ziti izi zoti utm ndi mcp mgwilizano ulipobe😭😭

  • @mercymalenga1884
    @mercymalenga1884 หลายเดือนก่อน +1

    Usiye kumene iwe ndi wa MCP

  • @SisiliaChaumbwa
    @SisiliaChaumbwa หลายเดือนก่อน +1

    Bwanawo muwamvetsetse akuti amakawayimilira a Chilima which means munthu simapita kukamuyimilira munthu iyeyo akupita komweko ayi ndie amanganya akudziwapo kanthu ndithu

  • @LameckGamah
    @LameckGamah หลายเดือนก่อน +1

    Dr Us. u have to resign😂
    Dr Us umuthu unatha, pando wa u President guys- musazawuphwekese, athuwa amava kukoma akamadya misokho ya amalawi 😢

  • @KamlepoKalua-w7z
    @KamlepoKalua-w7z หลายเดือนก่อน +1

    Why do you edit it?

  • @MartinsilverChirwa-fv9wn
    @MartinsilverChirwa-fv9wn 2 หลายเดือนก่อน +1

    God our heavenly father almighty God help us please

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx หลายเดือนก่อน +1

    Uyu akufuna kupha UTM

  • @chimwemwelimu1670
    @chimwemwelimu1670 หลายเดือนก่อน +1

    The guy is Genius eeeeeeh 😂

  • @RichardZatopetsaManda
    @RichardZatopetsaManda หลายเดือนก่อน +1

    He is wise🔥💯

  • @SamuelNthache
    @SamuelNthache 5 วันที่ผ่านมา

    Mr usi he knows who he is

  • @JamesjnrNahuwo-v1l
    @JamesjnrNahuwo-v1l 11 วันที่ผ่านมา

    Legancy is in work

  • @danccobatson
    @danccobatson หลายเดือนก่อน

    Big man best leader

  • @WilsonFiripo
    @WilsonFiripo หลายเดือนก่อน +1

    M gwilizano wa mcp ndi UTM unatha pomwe Lazarus amanena kut aimanso upule pomwe poyamba anat 5 years for MCP and 5 for UTM ausi ndiwe wadyera mfiti

  • @GibsonNyirenda-g6l
    @GibsonNyirenda-g6l หลายเดือนก่อน

    What a genius🔥🔥🔥

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq หลายเดือนก่อน

    Chakhanza you are so brave,mussels ameneyo akusamala mphika wakuboma.

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl หลายเดือนก่อน +1

    Dr mnali mli busy ndi a presdent cz anakulonjezani u vice nkani mnakhala chete

  • @GraciousMkyelu
    @GraciousMkyelu หลายเดือนก่อน +1

    Ask him for me,
    Akuti uthenga unawapedza aliku BT kochoka kudkawaimira achilima Ku malilo a kasambala. How come chilima amapita konko???

  • @JoelMedson-e5x
    @JoelMedson-e5x หลายเดือนก่อน +1

    Joab chakhaza kumasamatu ndi usi uyuyu ndimwara osasweka munthu osunga anthu

  • @Felixcanadad3j
    @Felixcanadad3j หลายเดือนก่อน

    😂😂 manganya 😂😂😂bwerera ku madrama

  • @HildaMbizi
    @HildaMbizi หลายเดือนก่อน

    Angodana naye Usi alibe zifukwa zomuletsela Usi kuti asayime nawo umbuli wachuluka ku UTM angomvela za kaliati INE ndizangovoterako mp osati za mbuli zosokoneza chipani

  • @yamikanikaludzu-g3t
    @yamikanikaludzu-g3t หลายเดือนก่อน

    Love you usi❤❤❤

  • @MonicaMtambalika
    @MonicaMtambalika 2 หลายเดือนก่อน +2

    Being the vise, wat effort dd u put to make sure chipan chisagawikane, Which side are you, how come u leave board members to run the party?

  • @FredModa-k2g
    @FredModa-k2g หลายเดือนก่อน +1

    Dr usi ndinu munthu wosokoneza

  • @StevekassimSteve
    @StevekassimSteve หลายเดือนก่อน +2

    Fuso kumat Kaliyat anamagidwa mochitisa manyaZi chochinja nanga inu bwanji smunalakhurepo kathu bwanji

  • @SylessKamanga
    @SylessKamanga หลายเดือนก่อน +9

    Usi ndiwa mcp komaso ndi fiti alibe usogoleli,uyu azapha anthu kusogolo

    • @thomaschikondibanda
      @thomaschikondibanda หลายเดือนก่อน

      Exactly

    • @gladysmwazaonga1710
      @gladysmwazaonga1710 หลายเดือนก่อน

      Munamatu inuuuu.....bvuto anthu simufuna chilungamo

    • @JasonMailos
      @JasonMailos หลายเดือนก่อน

      Usi anapeleka chilima mulungu amulange munthu uioa ameneyu

  • @user-jv2ur5kh1p
    @user-jv2ur5kh1p หลายเดือนก่อน

    Nyc interview

  • @SamataFlora
    @SamataFlora หลายเดือนก่อน

    All the best Michael ussi

  • @ndawilyznyirenda
    @ndawilyznyirenda หลายเดือนก่อน

    Munthu wazunzidwa uyu, yachuluka ndinsanje ku UTM .

  • @FrankTsoka-q4o
    @FrankTsoka-q4o หลายเดือนก่อน

    Good question excellent

  • @BuleMuhaliwa-dx6wb
    @BuleMuhaliwa-dx6wb หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkkk koma Joab umatha keep it up

  • @RuthMkangala
    @RuthMkangala 2 หลายเดือนก่อน +6

    Kagwere iwe

  • @MarthaBanda-g3s
    @MarthaBanda-g3s หลายเดือนก่อน +2

    1 Samuel 16:7 is operating now had it wasn't God's ✋ Dr. M.Usi couldn't be our country VP and it has to be a lesson to those who doesn't understand why God chooses the unchosen may our living God keep on enlightening citizens of our beautiful country Malawi.

  • @IyshaBakali
    @IyshaBakali หลายเดือนก่อน +1

    Guys mukamati manganya ndiwa nzeru ine sindikuonapo nzeru apa coz sanganene kuti mgwirizano ulipobe zosamveka uyu ndi betrayer

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx 2 หลายเดือนก่อน +9

    Amanganya fuso kod chilima alipo simapita ku Court Kunja komaso simunapangisepo nsokhan

    • @KassimKajosolo
      @KassimKajosolo หลายเดือนก่อน

      Ku court kukatani?

    • @patriciangala8038
      @patriciangala8038 หลายเดือนก่อน

      Azikataniko nanu.....mulandu unali wake?

    • @NoelMsesa-g5d
      @NoelMsesa-g5d หลายเดือนก่อน

      Komasotu wayankha kumva kukukuvuta iwe

  • @TrevorChagoma
    @TrevorChagoma หลายเดือนก่อน

    Ausi sanatithandize panopa tangoti kakasi ife kusowa kolowera .... Ngat Sanalemekezedwe Bwana wake ndi MCP iyeyu ndindan kut MCP ikamulenekeze???

  • @PrimeUpholstery
    @PrimeUpholstery หลายเดือนก่อน

    Some internal issues are not supposed to be touched. Good leadership will always maintain that. What is he doing to reconcile with these figures in order to lead them? . Does he he think if he wins they'll go without a fight? Find a way to bring everyone together no matter what? As a leader he needs to do that and rule. If he does that he is not only bringing the party leaders together but all Malawians who support UTM. Izi sizikuthandizani izi za ma divisions . Anthu amakukana kumene ndithu that's part of kutsogolera and to prove your leadership you bring them to gather by all means. Awo amene akukutsutsa they healp you to shape up and be a good leader.
    Munthu sungalephere kupangisa bata anthu 10 nkumapita kwina komwe kuli anthu 30 nkumati bola awowo Alibwino ndithawatsogolera chifukwa nga bata, No!! Prove that with few.
    I love you Mr Vice president.

  • @BowenRalph-ci4uw
    @BowenRalph-ci4uw หลายเดือนก่อน

    Ati "Ndimavara Nkanjo? Ndimavara uniform yaku church?" Km Ndaseka 😂😂😅😅

  • @LuthandoItcan
    @LuthandoItcan หลายเดือนก่อน +1

    Ok nanga bwanji chilima atamangidwa Ku court sumapitako bwanji tinene kuti chilimayo anali ofoira

  • @DytonChimango
    @DytonChimango หลายเดือนก่อน +1

    Mafunso ngati awa ndikuyankha mosabalalika chonchi mmmm he is a hero

  • @BigBen-r8y
    @BigBen-r8y 2 หลายเดือนก่อน

    The guy is the genius ... UTM needs him

  • @Thatsnotnic
    @Thatsnotnic หลายเดือนก่อน

    Joab, you are special

  • @macdonaldkorea2928
    @macdonaldkorea2928 หลายเดือนก่อน

    Usi ndinyapara weni weni, amkalumikizana mwanseri ndi chikangawa party uyu, ndipo tidikire tione omwe akukhuzidwa ndi kufa kwa chilima kuja uyu apedzekamonso garu

  • @hamzahdael1291
    @hamzahdael1291 หลายเดือนก่อน +1

    Zobisa mawuzo nde zopusatu... Nde why mmaleka kungokambirana kumbali osapanga broadcast bwanji😂

    • @RaphaelMaunde
      @RaphaelMaunde หลายเดือนก่อน

      Eti eti aaaa zopusa