@@courageouslondo1986 aise iweyo ndiamene u have to open your eyes and see ...that guy leadership in him his desire is just the same as SKC that why he was chosen. Adha the rest yachuluka ndidyela if they were good they supposed to let him, respect him as there president...mkuzamuchosa Ku convention....as i am saying mai kaliat amati she doesn't know kuti usi ndi president wa UTM....crazy how malawians don't want leaders than these idiots
A Micheal Usi adawonesta mtima wopanda chikondi pa nthawi ya zobvuta za SKC,and through out he actions has been speaking for its self tonse Malawi tawona tokha
Does Makosana view Usi as UTM leader?....kkkkkkkkkk......What has he done as UTM leader to show he is our leader?...he is not one of us. To answer your question, UTM will stand after the convention.
Aaa iwetso wamitsala nkhani ya mcp uphatikidza bwanji ndi za utm ifetu mcp yakoyo ayi KOMA NKHANI YA KU UTM ANTHU AKUPANGA CHIBWANA CHIPANI CHITHA PA 17 APA ANTHU 6 OFUNA PRESIDENT KKKK KOMA NGATI CHILIMA ALI MOYO CHIPANICHI CHINALI PA # 3 NSONO PANO KUKOKANA KWAKE UKU NDE MUCHITA BWINO AAAA ZAMATSIYE DZOMVUTA KUGAWANA ATI
Mau amenewa akuwopa kabambe ,koma asaiwale kut ndi omwewa amat khomo ndilosengula Ndipo akhoza kulowa,ndiye Lelo anthu anja alowa akumat ndi alendo aaaaaaa utm ndi ya anthu amene ali kumuz ndiye atipase pata tikasakhe tokha ku conversation,kay ndi mulendo tikasakha koma tikasata fundo zake
Anthu awa akunena zoona. Mukaonetsetsa muona kuti ambiri akubwera nkumati Chilima anali nzawo sanafune kumuthandiza Chilima nthawi imene idza ndipo anali bize kufuna u president ku dpp kapena ndi ma business awo. Mngakhale pamene Chilima amakumana ndi zokhoma ku dpp ndi ku Alliance awawa sanatulukile poyera. Atulukira poyera atamwalira Chilima. Ndigulu lija limalanda chuma cha masiye lija ili. Apa a UTM ndi Kaliati, Kampala ndi Usi. Bwanji atapikisana amenewa chifukwa ndiwo ana a Chilima amene Anastasia mphanje mundau osati ochenjera pa malilowo ayi.akakhala ndalama ndi zawo abwezereni. Ayame alima nawo zaka 5 kuti adziwike u UTM wawo
Ussi ndi osokoneza ,a kufuna asokoneze UTM . Koma iyeyo olo ataimila sangawine chifukwa ife sitikumufuna ayi
SkC ,ananenelatu kuti chipanichi ndichaliyemse ,musiyeni Kabambe tamukonda nayemsp ndi Malawi
Olo asapereke,abwelere ku Tikuferanji timamukonda.
Enawa anangofunika kukhara azibusa basi!!!! Koma usi uja timayenera kumutenga bwino chifukwa ndiye tizamulira
BELIEVE ME
Iwe ndi odwabwatsa usi ndi munthu oti mkudzamulila? Uganize bwino
Kwambili usi ndiwazelu muzamukumbukila ndithu@@courageouslondo1986
@courageouslondo1986 @ 05 Nov 2024. save the date
Aime payenkha moto iyeyo sakuziwa kut kunali gwirizano wakuchipani kodi usi ndiotani
@@courageouslondo1986 aise iweyo ndiamene u have to open your eyes and see ...that guy leadership in him his desire is just the same as SKC that why he was chosen. Adha the rest yachuluka ndidyela if they were good they supposed to let him, respect him as there president...mkuzamuchosa Ku convention....as i am saying mai kaliat amati she doesn't know kuti usi ndi president wa UTM....crazy how malawians don't want leaders than these idiots
Amene Ali ndi ndalama zMbiri ku chipani Cha utm akhale President wa chipanincho koma onse amachenje asatinyase
UTM yachuluka mkwizi ndi kaduka zonsezi zikuchitika kuonesa kuti ndiosasata malamulo komanso nsanjetu ndiye yakulamo
A Micheal Usi adawonesta mtima wopanda chikondi pa nthawi ya zobvuta za SKC,and through out he actions has been speaking for its self tonse Malawi tawona tokha
Konveshoni yopanda mtsogolo😊
Ussi ndi opusa akufuna asokoneze utm koma tikuziwa kuti akufuna achithese kapena achigulise ku mcp
Asatichedwetse uyu inu
Does Makosana view Usi as UTM leader?....kkkkkkkkkk......What has he done as UTM leader to show he is our leader?...he is not one of us. To answer your question, UTM will stand after the convention.
Malamulo agwire ntchito, owina ndi m'modzi
Chipani ayenera kugwirizana
Komaso chikondi Palibe ndiye convention imeneyo tsogolo lake ndichani
Manganya amayenela kukhala oyamba kukapeleka koma sakufuna ndipo mulekeni alindichake ameneyo odya zake alibe mulandu
Aliyese ndi mlendo ku UTM tinali ku DPP tonse ndiye Kabambe timuotere ndithu
Zaonesa kuti UTM tsogolo lake likhoza kuonongeka chifukwa ku chipqnichi kukuones kuti kukusowekera msogoleri wokhwima nzeru komaso yemwe akhoza kulimbikisa ufulu wa Democtracy . Mau omwe a Newton Kambala alankhula ndiotsimikizira kuti chipanichi chataya masomphenya a msogoleri wawo malemu SKC.
Usi alibe maso mohenya,komaso akusogoza zoti mgwilizano ulipo ndi mcp pomwe amzake anatuluka
Mwaona ailimvuto uyuyu
Azingopita kutikufelanji akumudikila ndipo iweyo usi sungasokoneze utm or utapanga njilazako zopoira izo
Maganya ndi munthu osokoneza kwabasi, awasiye anthu a UTM apitilize legacy ya malemu chilima basi!!
Aaa iwetso wamitsala nkhani ya mcp uphatikidza bwanji ndi za utm ifetu mcp yakoyo ayi KOMA NKHANI YA KU UTM ANTHU AKUPANGA CHIBWANA CHIPANI CHITHA PA 17 APA ANTHU 6 OFUNA PRESIDENT KKKK KOMA NGATI CHILIMA ALI MOYO CHIPANICHI CHINALI PA # 3 NSONO PANO KUKOKANA KWAKE UKU NDE MUCHITA BWINO AAAA ZAMATSIYE DZOMVUTA KUGAWANA ATI
Usi si mnsogoleri
They never know what people think outside there about them let's wait and see, nonse inu mulibe mbiri pa ndale munya muona🚀🚀🚀
Akafuna akapeleka makalatawo
Manganya yo basi musiyeni asapereke sitikumudandaula ndiwa MCP ameneuja
Umunthu wanu ulipati? Mmalo momupanga support Usi kuti chipani cha UTM chinkhale cha mphamvu, muli bizy kunyozana bas. Ngat mukuona kuti simukwanitsa kumanga chipanicho musiye Usi ndi Marry chilima aziyendesa chipanicho.
Mary Chilima ndi yemwe angamange chipanichi plus ena onsewa ngati nduna
Exactly saliwokha may patricla
aus achoke utm ife timachikonda chipanichi akungofuna kupha utm bas kom mulungu ali nafe
Dr DALITSO KABAMBE mnapanga mistake kutuluka Dpp ndiizii sopano
Osasankha munthu chifukwa kuti ndi mkhala kale koma mfundo ndi ukadaulo wake
Mau amenewa akuwopa kabambe ,koma asaiwale kut ndi omwewa amat khomo ndilosengula Ndipo akhoza kulowa,ndiye Lelo anthu anja alowa akumat ndi alendo aaaaaaa utm ndi ya anthu amene ali kumuz ndiye atipase pata tikasakhe tokha ku conversation,kay ndi mulendo tikasakha koma tikasata fundo zake
Ndindani amene angakhale kumbali ya Ussi than his families only
A ussi ndimunthu wantopola ndipo iyeyo ndiwadyera kwambiri sakuyenera udindo ameneyo abwererenso ku tikuferanji
Mayi Makuta sanayankhule bwino anayankhula mopusa
Njawala ndiosokoneza
Michael usi musavutike naye iyeyutu ndi amene akufuna kumakhala vice wa chakwera ndipo muzaona eyetu
Komabe it's true what if kabambe is sent by DPP to neutralise UTM
Manganya sitikumufuna ku chipani cha UTM ndi nthira kuwiri akhale komweko ku chikangawako
Alibe ndalama ndiye kuti komaso ndi wa MCP ameneyo
That's true democrats
Mhkukanganirana president muzilandila zingati
B KALINDO ANAKAMBA kut kuyendesa dziko sima drama
Ifetu tisapota munthu aliyense yemwe swine chifukwa ife tikutsa Tila Manfsto osati munthu
Chipani chathapo ichi ndizomwe zayambikazi,, that means kuwina kabambe kuzakhara kusagwilizana bas aaa mbola
Manganya akufuna kugulitsa UTM
Usi awina chifukwa anthuwa mngwirizano palibe
Anthu awa akunena zoona. Mukaonetsetsa muona kuti ambiri akubwera nkumati Chilima anali nzawo sanafune kumuthandiza Chilima nthawi imene idza ndipo anali bize kufuna u president ku dpp kapena ndi ma business awo. Mngakhale pamene Chilima amakumana ndi zokhoma ku dpp ndi ku Alliance awawa sanatulukile poyera. Atulukira poyera atamwalira Chilima. Ndigulu lija limalanda chuma cha masiye lija ili. Apa a UTM ndi Kaliati, Kampala ndi Usi. Bwanji atapikisana amenewa chifukwa ndiwo ana a Chilima amene Anastasia mphanje mundau osati ochenjera pa malilowo ayi.akakhala ndalama ndi zawo abwezereni. Ayame alima nawo zaka 5 kuti adziwike u UTM wawo
Ndizoona zimenezo
They are all confused
Usi akutsata constitution
Kupanga zinthu modekha 11:02 kumabweza mkwiyo . Usi sakupanga mopupuluma ai, iye amadziwa ukangano umabweretsa uchitsilu. Tiyeni tikhale chete kuti mawa tisadzakhale opusa. Usi pitilizani kudekha kwanu
Azawinira kuti munthu sadalembetse
Manganya ndi bulutu komaso oyipa mtima kwambili
Bodza
Munthu oipa uyu
Akungopanga campaign
Kabambe yemweyo
Zavuta
Anthu awa akumgovutika DR M. USI akuzawina pa Conversation. Ndiye pasazapezeke Wopepesa kwa President DR USI .Coz akulankhula mopusa ngati Blutoo.