Namiwa,, you're the true son of the soil,, fight for us plz.. Malawi si wa Chikangawa party they must pack and go.. Anthu sangamadye chitedze iyeyo ndikumakayendera ng'ombe zomwe zili zakenso,,, that's nonsense chakwera pack and gooooooo
Mr namiwa, this country needs people like you to reform our country. One more time soldier said tough times do not last but tough people do last. Which means chikangawa & his followers there times is coming, painful time.
Anthu ofunika support aja ndi awa koma kuli ziii, koma kukaona ng'ombe nde chigulu misonkho ya amalawi eni ake kusakaza Basi, my question is Kodi inu amene mkumati ndinu atsogolerinu do you care about your people kapena mwangokhala ndi dyera Basi?? Amalawitu siopusa

Koma khani iyi ndiyovuta kuvesesa chondechonde ambuye bwelani nokha muzaweluze zikoli
Anthu ofunika support aja ndi awa koma kuli ziii, koma kukaona ng'ombe nde chigulu misonkho ya amalawi eni ake kusakaza Basi, my question is Kodi inu amene mkumati ndinu atsogolerinu do you care about your people kapena mwangokhala ndi dyera Basi?? Amalawitu siopusa
Zimenezo ndiye zofunika kwambili ature pansi udindo basi mcp yoipa kwambili chikangawa team yakupha
Tili pambuyo panu tiyeni tipange mademo
Ambuye sadzabwera kudzangopulumutsa malawi ,iye adzagwiritsa ntchito anthu omweo,wake up Malawians Mulungu alowerera pamenepo
More fire guys chimwendo anene bwino ndi milomo yake yofanana ndi nyini ija garu wamunthu
Stand up Malawi Stand up 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🎤🎤
More fire namwiwa
Ndikuthokozeni Anamiwa ndi mabungwe onse amene mukutiyimilila, timadikila inu ife tli okozeka kupita kumsewu cikangawa ndi mcp dzikoli alitenga ngati la a mawo. Tikufuna mabungwe onse amene anaticotsa mu boma limene timadya ka 4 patsiku ndikutilowetsa mkamwa mwa ng'onazi mubwele pamodzi mutilanditse ku ng'onazi .Tikufuna Anabero, Nrb ndi smart matic onsewa acoke kuphatikiza apo kalembela ayime cifukwa akungolembana a mcp okha okha. Mademo akhale dziko lonse la malawi cifukwa mcp yatitengela kumtoso
Malawians seems kuti mwayambako kulingalira mwa nzeru please more fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Rescue us Mr namiwa
Bwana namiwa timakumyadilani, koma Mesa Kodi Pali national enquirery? Ndiye bwanji achimwendowo akafusidwe ndi penguier yomweyo
Tili mbambuyo panu don't give up
Mwafotokoza moveka bwino limbikilan tili nanu limoz
Namiwa tiyeni chowona chipezeke ngati sanena zowona tikamuchosa tokha kunyumba yathu
Mademo akufunika
Ndipo ndikubwela koko
Funso lina nali kodi ngozi mpaka kuvula tayi kuchitsa lamba tikulira
Mr namiwa tikufuna chakwela achoke please
Chonde bomali likatuluka amangidwe onse from chakwela
Mwa Mr Namiwa muli kuthekela kokonza dziko LA Malawi koma a opposition ndi amene akuphweketsa
Marawi zafika panyas kwambili chakwera ndi nindaniso iyeyo kut azivuta patumbo pake posasambapo ine nimadana ndinyas am kenan
Kuzafika 2025 makadeti onse Akhara ali pambalambanda
Angakhale mfiti ataonedwa kuti wapha munthu ndi iyeyo sichapafupi kubvomera kuti ee ndapha ndiine nduna zoipazi ndi zimene zikumuuza chakwera zochita ndiye akabvomera zinthuzo ndi kuchitika ndi kobvuta kuti azisusana nayenso imakhala poloti ya anthu angapo omwe amuzungulira pulezident pofuna kukwanilisa zofuna zawo
Palibe chazelu apa kumalawi ndalama kilibe zakutumbo
❤
Namiwa ulime chimanga chako udzatchipitse mitengo ya chimanga ikugwirizana ndi fertiliser mmadimbaso uwauze alesi azakowo aziloma chimanga chimachaso
No Belo
X 😊😊😊
More fire namiwa