Atangomaliza kuyankhula a Chimwendo Munanva zomwe anayankhula owonjezera uja?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 17 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 88

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona วันที่ผ่านมา +6

    Simunakhudzidwe ndi ANTHU munawapha Ku Chikangawa aja ndiye mukakhudzike ndi Namondwe wa Chido.
    Chipani chokumwa Magazi,Mikodzo,Malobvu ngakhalenso Mafinya mumapsyodza inu.
    Mr Smartmatic Chakwera and the Cabinet anthu Oyipa inu.
    Ukuyankhula so zaziiiiiii Chimkhumba 👹👹

  • @HamuzahRoben
    @HamuzahRoben วันที่ผ่านมา +1

    Km chimwendo ma speach ake amandivekela mwa usavega😂😂

  • @chikonditetheleya4758
    @chikonditetheleya4758 วันที่ผ่านมา +1

    Ndiwe galu kwabasi chimutu ngt chigubu Muthu otsava chisoni ngt iwe sindinakuwone ai

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx วันที่ผ่านมา +3

    Inu a chitsiru inuyo zikwanje zija matulutsa azanu amayankhulapo

  • @MenfordZimba
    @MenfordZimba วันที่ผ่านมา +2

    Dziko lija linaphulidwa pamoto ndi Bingu lija pano alitelekatso oo Chakwera

  • @PatumaCassim
    @PatumaCassim วันที่ผ่านมา +2

    Choka chi leg iwee mau osasawo ngat wagonerera pa tseche wa masese 😂😂😂😂

  • @DanielGeorge-l4h
    @DanielGeorge-l4h วันที่ผ่านมา +1

    Mundiphuzitseko chipani ndi party ndizosiyana Kodi 😂😂😂😂😂😂😂

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka วันที่ผ่านมา

    Paja inuyu ndi amene mwayamba lero.zakuwawani 😅😅😅😅😅

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz วันที่ผ่านมา +2

    Kambani za zikwanjeeeeee guys zimenezi zisakuwaweni mukuyambitsa ndinu nomwe

    • @JJ-in-the-hut
      @JJ-in-the-hut วันที่ผ่านมา

      Yeah otherwise his message is balancing

  • @RuthKakathera
    @RuthKakathera วันที่ผ่านมา

    Komatu dpp mukumva nayo pain😂😂😂

  • @DouglasDimingu
    @DouglasDimingu วันที่ผ่านมา +2

    Moses kumkuyu asamale nayo MCP

  • @leeonerecords8779
    @leeonerecords8779 วันที่ผ่านมา

    Ifenso tikudirq za imfa ya chilima 😢😢😢😢😢😢😢

  • @fatsankapitikitsa
    @fatsankapitikitsa วันที่ผ่านมา

    ifenso wathu chilima mutiyankhe

  • @HandEllah
    @HandEllah วันที่ผ่านมา +2

    😂😂😂😂😂😂😂😂 Aikanda pokhalira kapena? 😂😂😂

  • @AronLuka-ue5hl
    @AronLuka-ue5hl วันที่ผ่านมา

    Uwawuze ana ako ndi azibale ako akavotele chikangawa wakoyo,kwacha yagwaso kwacha yagwaso

  • @SimonBanda-b1f
    @SimonBanda-b1f 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwalephera a MCP mukuyendetsa boma ngati church.

  • @Jessica-tc7rf
    @Jessica-tc7rf วันที่ผ่านมา

    Tachokani mwasowa zochita zanuzi ndiye zopanda mutu😂😂😂Apm moto buuuu

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 วันที่ผ่านมา

    Achitsiru inu ndi Chakwera wanuyo,nzeru mulibe

  • @KennedyKManda
    @KennedyKManda วันที่ผ่านมา

    Inuyo achimwendo mlindivito kwabasi, yakhani zokupha anthu kuchikangawa inu mukanyongedwe musakhaleso ndimoyo .

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 วันที่ผ่านมา

    Iwe ndiye ukuzangoluza mcp ndiwaku wire basi

  • @JudithSadi
    @JudithSadi วันที่ผ่านมา

    That's a total no sense.... MCP yakupha, aliyense akudziwa

  • @JamesJaswabPhiri
    @JamesJaswabPhiri วันที่ผ่านมา

    Kodi bwanji chilichonse choyankhula kumawonela pa papers amakhala asanawelenge kale @ Chimwendo

  • @GOSH-c8y
    @GOSH-c8y วันที่ผ่านมา +1

    UNGAFANANE NDI GANGATA KU CENTRAL REGION IWEYO, PAMTUMBO PAKO

  • @hassammaulana4529
    @hassammaulana4529 วันที่ผ่านมา

    Basi ndiye panopa anthu akukhala bwino za ziii kugokula mitu koma dzeru mulibe eeeti black box ilikuti ..osati mukunenazi

  • @MafkinSinjani-o7k
    @MafkinSinjani-o7k วันที่ผ่านมา +2

    Chitsiru cha munthu ichi MCP no room in Malawi

  • @UncleShopRite
    @UncleShopRite วันที่ผ่านมา

    Iweyo jeasy ubwere kuno kumwela tiwone ngati anthu sakupha

  • @shavielsiment-y9p
    @shavielsiment-y9p วันที่ผ่านมา

    agalu Inu mungozinenepera ndi misonkho ya amalawi

  • @MjombaMoosa
    @MjombaMoosa วันที่ผ่านมา

    Ndiwe chisilu kwabasi ngakhale manyazi ulibe

  • @crytoniegrantliffa2431
    @crytoniegrantliffa2431 วันที่ผ่านมา

    Aaaaaaa!!inu mwatisaukitsa ndithu

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkkkkkk zikuveka Zach ziiiiiiii😂

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 วันที่ผ่านมา +1

    Yokulirapo ngati chimutu chako chimwendo

  • @BirzetScott
    @BirzetScott วันที่ผ่านมา

    😅😅😅😅😅😅 osati inu munapha anthu 9 ,

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 วันที่ผ่านมา

    PANYAPAKO CHIMWENDO BANDA IWE NDI CHAKWERA NDAMWENE MWABWERETSA MKWIYO KUCHOKERA KWA MULUNGU UMUWUZE CHAKWERA PANYAPAKE

  • @McDonaldbeketeNkhata-n4l
    @McDonaldbeketeNkhata-n4l วันที่ผ่านมา

    MCP ndinu ankhaza satana weni weni

  • @ChrissieNyasulu
    @ChrissieNyasulu วันที่ผ่านมา

    A chimwendo dzudzulaniso za zikwanje.

  • @BirzetScott
    @BirzetScott วันที่ผ่านมา

    Tayamkhulani za mzelu inu Kodi ku m c p kulibe anthu amzelu.

  • @AliceChapita
    @AliceChapita วันที่ผ่านมา

    Koma ndiye mcp ayi tosa ponyenyerera chifukwa yakuwa

  • @CardoJustin-l7m
    @CardoJustin-l7m วันที่ผ่านมา +1

    Akufuna tiiwale za report la ndege ndicholinga kuti mmitu mwathu muziyenda izizi tiiwale za report

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mnyamata ameneyu RCB ndi anthu ake ndi opusa bwanji amangolankhula pokhapokha ataona kuti chipani chawo chawukiridwa? What hypocrisy kwa chipani choyimira Amalawi onse. Palibe za Chikangawa kapena apolisi okhala ndi mapanga. Amapitiliza kufunsa umboni akudziwa kuti apolisi aMCP.

  • @IbrahimMatola-k9p
    @IbrahimMatola-k9p วันที่ผ่านมา

    Achimwendo mudyelethu ndalamazo chifukwa Chaka chamawa mumangidwa MCP ikugwa

  • @UncleShopRite
    @UncleShopRite วันที่ผ่านมา

    Iweyo chimwendo udindo wakowo uzantha ngati adathela mkaka

  • @AbdulJohn-t7l
    @AbdulJohn-t7l 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uyu amandimvekela mwa uchisilu kamwendo

  • @SherifAubrey
    @SherifAubrey วันที่ผ่านมา

    Agalu inu membala wanu munamupha nokha atakuuzani kuti watuluka mu chipani chani agalu inu

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g วันที่ผ่านมา

    MCP mukuzinamiza kwambili ,kaya simumaudzana kuti ndife olephera ? 4yrs palibe chomwe mukupanga amalawi sakukufunani koma mungolubwa lubwa wanuyo muvotera koma amalawi tikuvotera tsogoleri wamaso phenya APM 2025 inu zakumvutani

  • @MustaphaCassim-t7g
    @MustaphaCassim-t7g วันที่ผ่านมา

    Apolice ayambe kufufuza imfa yachiwaya ndianthu ena 9 kuchikangawa b4 kundilande chimwendo

  • @GabrielJosua-r2y
    @GabrielJosua-r2y วันที่ผ่านมา

    Ziphanso mwachotsa a Nrb ku LL kamba ka chani?mwabisala mmbatata chimwendo

  • @LatifahShaffie
    @LatifahShaffie วันที่ผ่านมา

    Munthu wamkulu mutu uyu

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm วันที่ผ่านมา

    Eya akutibulen nanuso mumatuma azikwanje chimwedo Banda ndwe galu kwabasi

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 วันที่ผ่านมา

    Nyini Za Manu aganu inu Malo momakamba Za ifa ya chilima agalu inu anthu opanda chisoni akapoli inu tazikavalani akapoli inu

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 วันที่ผ่านมา

    Koma simachita manyazi mukamati MCP chipani chankhaza ngati chimenechi

  • @BusisiweMakhoba-d8o
    @BusisiweMakhoba-d8o วันที่ผ่านมา

    Chimutu kukula

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz วันที่ผ่านมา

    Inu minafotokoza za zikwanje zija????????????????

  • @YasmeenYalabi-e8g
    @YasmeenYalabi-e8g วันที่ผ่านมา

    Nachimutu tiye uko azikwanje ukuwatuma aja kukhapa anthu munyeratu simupita kummene kummwera ndi kumpoto tikutemani

  • @LoydBanda-b5q
    @LoydBanda-b5q วันที่ผ่านมา

    Ifa yachilima mwapangapo chain???

  • @MphatsoLuka-gn3lr
    @MphatsoLuka-gn3lr วันที่ผ่านมา

    Athu sadya misewwu

  • @PatrickDiness
    @PatrickDiness วันที่ผ่านมา +1

    Mwatitola aMalawi

  • @GoldenNamanguya-b1f
    @GoldenNamanguya-b1f วันที่ผ่านมา

    Mapwala ako athu okuba inu

  • @GOSH-c8y
    @GOSH-c8y วันที่ผ่านมา

    MUDZANYA MANYI KLA SMARTMATIC KANU SIKADZAKUTHANDIZANI

  • @GOSH-c8y
    @GOSH-c8y วันที่ผ่านมา

    DPP SINGAKHALE KUNJA 26 YRS PAMTUMBO PANU

  • @SamwaJohn
    @SamwaJohn วันที่ผ่านมา

    Zawawani lero nm

  • @hassanfaizadaffer2421
    @hassanfaizadaffer2421 วันที่ผ่านมา

    Iweyo chomwe chinakupangisa kut usakwere ndege ndichani unathawa ifa mumayenera ukhale ufere popo,anthu Inu munapanga business yofoira monakakhala azaru munakaikamo mu ndege muja akuluakulu a mcp angapo kut mwina anthu asakukaikireni

  • @bobkatas1974
    @bobkatas1974 วันที่ผ่านมา

    Tikudikila mwa chidwi kuti tizawone m'mene moyo wanu udzakhalile muli kunja kwa boma,it's very unfortunate that you talk like there's no tomorrow,,,be careful my dear brother,,,analipo ena akomedwa choncho koma lero kulibe

  • @DaflenRedi
    @DaflenRedi วันที่ผ่านมา

    koma ndye kuwelengatu bwino ngati nkhani zamaboma

  • @ELLENZAPS
    @ELLENZAPS วันที่ผ่านมา

    Mumati dxiko munayamba ndinu agalu inu dxiko ndi lamanu mikongo yanu mbava mfiti xawanthu

  • @JohnMeleka-s1t
    @JohnMeleka-s1t วันที่ผ่านมา +1

    Aaaaaaa pansete pako chimwend

  • @KapitoDaire-n1h
    @KapitoDaire-n1h วันที่ผ่านมา

    Machendako chimwendo 2025 dpp boma

  • @KapitoDaire-n1h
    @KapitoDaire-n1h วันที่ผ่านมา +1

    Nanga kuchikangawa??

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm วันที่ผ่านมา

    Chimwedo chimulomo chako chachikulucho bwanji iweyo osazizura azikwanje boma lanu akulifuna

    • @JJ-in-the-hut
      @JJ-in-the-hut วันที่ผ่านมา

      Akuonesa kupanda nzeru.

  • @KossimasiMaluwa
    @KossimasiMaluwa วันที่ผ่านมา

    Chimwendo masiku asala ochepa ukafela kundende satan

  • @FelixKChisale
    @FelixKChisale วันที่ผ่านมา

    Ulemu wanu achimwendo a dpp asatilembele malire opangitsila misonkhano Malawi ndiwa tonse

    • @JJ-in-the-hut
      @JJ-in-the-hut วันที่ผ่านมา

      Koma inu mwalembere malire opangisa misonkhano , since ndinu azikwanje?

  • @StoniaMoyo
    @StoniaMoyo วันที่ผ่านมา

    Mmm galu iwe yankhula nzako zakupha fosek

  • @Kradle-h4o
    @Kradle-h4o วันที่ผ่านมา

    Nyengatoni😅😅

  • @AmosiChauluka
    @AmosiChauluka วันที่ผ่านมา

    Kkkk mbuzi

  • @LydiaMushala
    @LydiaMushala วันที่ผ่านมา

    Shame😢

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka วันที่ผ่านมา

    Za ziiiiiiiiii

  • @Maxielyies
    @Maxielyies วันที่ผ่านมา

    Zaziiiii

  • @LameckNgwangwa-g3p
    @LameckNgwangwa-g3p วันที่ผ่านมา +1

    Koma sanatenge dzikwanje tu

  • @ErnestsMoshu-c6k
    @ErnestsMoshu-c6k วันที่ผ่านมา

    Mutu oumao

  • @donexmakande5979
    @donexmakande5979 วันที่ผ่านมา

    A mcp niyahlanya mpela niyaphuma niyanya

  • @LindaChikwawa
    @LindaChikwawa วันที่ผ่านมา

    Agaru akuru mitu inu pakunya panu

  • @rashidkandulu290
    @rashidkandulu290 วันที่ผ่านมา

    Masiku atha