😅😅😅😅😅 iweyo ndi amene ukuva kupwetek sukuona wekha bon kalindo Ali pano kuzang'alula u will still get pain until end of your life I'm show that because bon kalindo nde wabwela kuzakhala pano 😅😅😅😅 uva kuwawa machende akonso patiiiii
Inuso nde Kayatu ine sidavotepo ndipo am not a fun of any party koma pot ndili ndi mutu oganiza ndikuttha kusiyanitsa nthaw ya kale anthu sankazuzika chonchi kudya chitedze boma Lili pheee pano ndi nthaw yolima koma kuli feteleza kosadziwika njala yongobelekana Chaka nchaka katundu kukwera ngat afuna anene kut osauka nose chokan mmalawi muno.. so nkhan si Jane ansah or Anabel koma koma the leadership behind anthu akukayikilra so after all ansah anatula pansi ndipo uyuso atule simple like that . let the will of people prevail
Achitsiru amalawi Ake atiwo ukunena iweyo , Moyo mmene ukupwetekera panomu ukat akafune chakwera? Ulibe chison anthu kumudzi mmene akuvutukira ndi utsogoleri osaganizura umoyo wa anthu Ake kut akukhala bwanji? Basi just because iwe ukupeza cholowa akamasakaxa chuma cha amalawi azisogoleriwo nde ulibe nazo zamiyoyo yochiluka ikuzunzikayi ndi odzikonda heavy umunthuso ngopelewera . APM was better tikasiyanitsa nizomwe akuchita chakwera tidamukhulupira koma ndimavuto tidawayambawa so ndi bwino ENA atenge ulamuliro osatengelaso chipan Kaya si APM adzakhala wina we don't care Bola usinthe ulamulo and as matter of fact anthu zuoneka kut akukupatsan phuma ndi APM cuz mukudziwa anali better than you
Opposition is trash ,,,,,, we are cursed ndithu
The DC...Umakwana pitilizani osaopa,osafooka...❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Go ahead our DC help us❤
Dc pangolini❤❤❤❤❤
The DC!!!! Mwana wakwithuuuu
Ma Bishop okonda ndalama😂😂😂😂
Ishiii tilipamavuto ndthu😊
DC ❤❤❤
The Dc mwana owopsaaa kwambr 😂😂
The almighty God is all_knowing
Iyayi iyayi a mbuye tilinazo mtengo zathu zofunika pemphero ndi pemphera bwanji Muthu ndilindi njala
Akuti vitz osadzayiphweketsa😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
DC penaso azilowako live
Kuvomeleza kukuvuta chodabwisa mabungwe akutuluka ambili kuwaimila pac mipingo onse ali ziiii amalawi kuimbira mmanja zopepera
Ine sindinalembese 3 days kumangobwerera anali pa ufulu ndi ama id amapepalafe ambiri tabwerera bt
Vitz siyamasewra 😂
Mukanalira simunati
Mulungu ndi wamkulu sangalole kt tidzingolira masiku amoyo wwawo
Arandire basi nangakutani nimumene yavutira ndaramamo
Pa dziko la pansi palibe chinsisi zoona komanso wa bzness kumasekelera zopusa chonsecho daily katundu akukwera daily. Komanso zisankho izizi zikapitilira kuyenda mopusa chonchi kudzakhala nkhondo Ku malawi kuno. Iyiyi ndi nkhondo akuyuputayi azitsogoleri opusa
😂😂😂😂 ma Bishop Okonda ndalama
Ndimmene tikunena kuti 2025 zisankho kulibe, kusakhale zisankho
Umafuna uzilandila wekha ndalamazo , inunso mwafika popepera kwambiri
😅😅😅😅😅 iweyo ndi amene ukuva kupwetek sukuona wekha bon kalindo Ali pano kuzang'alula u will still get pain until end of your life I'm show that because bon kalindo nde wabwela kuzakhala pano 😅😅😅😅 uva kuwawa machende akonso patiiiii
Bodza kalindo...
Tangopitani konko mukachitenge chi machine Cho hiya
Afufuzeni azibusa awo ndimabishop olandira ndalama awo tiwaziwe dzikolose
Liberation is coming soon
Kodi ndalamazo ukufuna udzilandira wekha? Umakatapa ku page house, nawo mabishop ndianthu…zukupweteka pati? 😂
Sukudziwa comwe kuyakhula mulungu akukhululukire
Bon Kalindo perekani umboni....mumanena manyaka zopanda umboni
Kwa iweyo nzopanda umboni koma akunenaz zoona siwose alingat iweyo odana nchilungamo
Galu iwe, suphula kanthu ndizimenezo. Mcp sikuchoka muboma
kkkkkkk choka satana iwe mcp yagwa nayo bc pokhapokha uja mwamupha ku chikangawa uja adzuke kaye muzalowa mboma
ATI asaphule kanthu ndi chikangawa mbisa wa kumidima satana wapansi pa nyanja check fzite cosadziwa comwe akupanga
Chest pain
Mumatimvetsa kukoma aBon kalindo
Kkkkkkk DC.
Komatu Jane ansa nayeso anatizunza ayi zikomo poti dpp idachokamo boma
Inuso nde Kayatu ine sidavotepo ndipo am not a fun of any party koma pot ndili ndi mutu oganiza ndikuttha kusiyanitsa nthaw ya kale anthu sankazuzika chonchi kudya chitedze boma Lili pheee pano ndi nthaw yolima koma kuli feteleza kosadziwika njala yongobelekana Chaka nchaka katundu kukwera ngat afuna anene kut osauka nose chokan mmalawi muno.. so nkhan si Jane ansah or Anabel koma koma the leadership behind anthu akukayikilra so after all ansah anatula pansi ndipo uyuso atule simple like that . let the will of people prevail
Iwe bon kalindo ngakhale utayankhula mwantundu wanji anthu ambili sakunfuna pita muthalika akukumbukila mene anawazunzira nde iweyo uli mbali yomweyo dungatikope kut tilowe dpp
Achitsiru amalawi Ake atiwo ukunena iweyo , Moyo mmene ukupwetekera panomu ukat akafune chakwera? Ulibe chison anthu kumudzi mmene akuvutukira ndi utsogoleri osaganizura umoyo wa anthu Ake kut akukhala bwanji? Basi just because iwe ukupeza cholowa akamasakaxa chuma cha amalawi azisogoleriwo nde ulibe nazo zamiyoyo yochiluka ikuzunzikayi ndi odzikonda heavy umunthuso ngopelewera . APM was better tikasiyanitsa nizomwe akuchita chakwera tidamukhulupira koma ndimavuto tidawayambawa so ndi bwino ENA atenge ulamuliro osatengelaso chipan Kaya si APM adzakhala wina we don't care Bola usinthe ulamulo and as matter of fact anthu zuoneka kut akukupatsan phuma ndi APM cuz mukudziwa anali better than you
Kodi wadzola manyi eti
Wht goes Round comes round
Inu bwana ife tatopa nd zonena zanu pangani mademo kd mtambo alikt pamodzi nd inu mungokhala chete osapanga action
Sibwanaso uyu amwene ulemuwo mkupeleka kumunthu olakwika munthu woti IQ yake yili below 20% nkukhalaso bwana? Uyo ngwamisala ndithu
Siya ngati watopa.
Alekelenji kulandira?mawu akuti landilani idyani, pakuti izi ndindalama zamisonkho yanu.....
Bon kalindo usamangoyankhula iwenso upite nawo kumademoko