ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Komaso sinduona chifukwa choti wandale,kaya wotchuka akabwera ku church ,adziima PA gome,MPA anthu odzodzedwa APO...
Ndale amwene
Ameneyu akupangila chakwera campain
Wamisala uyu akugani ngati angafike Pachilima aaa bolaa
Or akuchepa kutali
Uyu amkawufunadi udindo wa SKC ndawona ine samkagona tulo ndi SKC
Usayese Yehova Mulungo wako amene owe uyenela kumugwadila
Ausi mwarambira fano lero mwayiwara kt lasabata linali zuro zamanyazi poti woweruza wolungama nimulungu tingodikira siku lomaliza 😢😢
😂😂😂😂😂 pita uko iwe what do you mean lamulungu ndizulo ....zanthawi yachina moses zimenezi ..now believe in Jesus christ as your lord and saviour and pray everyday..Mulungu sees the purity of your heart not umaphela tsiku lanji...muchedwa nazo
@@wisdom20mkango49😊😊😊
To those who are sided with Catholics in politics.Alwsys win elections
Nanu amipingo musawasekerere andalewa . Ndiamene akuwononga zikoli
Pamutu pake sipayenda uyu za ziiiiiii akuyithetsa dziko ndi iyeyo kusokoneza ku UTM
Timakukondani a Michael usi bola mzinena zoona zokha zokha msaputsitse anthu ndinu munthu wosazikudza
Aaaaaaaaa, akungotaya nthawi manganya, za ziiiiiii. Iyeyu nindani kuti akaime ku gome.
Somenezi nde akukana mabishonp kukenya kulambila mafano kumeneko
Umphawi siwabwino mulungu mutiyendere mwapadera ndikuwakhululukila azibusa onse ndi ma bishop
Ku chilimba musalole anthu awa. Akuvutitsa ndi kusaukitsa dziko.Akatolika khalani ndi Maso
Kkkkkkkkkk kuyalukatu ukuu kkkkkkkkkk akuganiza angaseke anthu pakamwa... Aliyense nkatolika akudziwa angodzivuta ubwino wake ndi musonkho yathu hiya...
amipingo onse kumalawi ngkonda ndalama sianthu abwino ayi akanatengera chisanzo chabwino kukenya
Tivutike ndi a ma brethlylizer, fuel, sugar
Zavuta ndi ndale..don't mess with Catholics.
Zomatiuza za dpp ai a Robin akukharano bwinot
Otsati kugawa ndalama chopeleka aMalawi mli ndi vuto Pena mmutu mwanu
Zopanda ntchito zimenezo olo mubwere kuzapephera nafe ma church mwathumu sitizavoterabe lazalasi chakwera ndi kongeresi yanuyo.
Manganya asakuputsitseni a Malawi please tsegulani maso mafuta kulibe iye alibusy anthu akufa ndinjala midzimu
Abusa odyola,,wapasifwa ndalama,,akupasani,,,koma fundo tilibe
Mumuuze aimbe nap kwaya
Koma zotiuza za mcp ndiye ife tikudana nazo kwambiri
Nyumba ya Mulungu mwayesa yopezera zofuna zanu.
Dziko ndi anthu ake
Anapita ku Mbayani kukapemphera chifukwa amadziwa kuti mu church munalibe misala yomugendera
Hindeeee anadziwa mu Tchurch mulibe zokangana ndi miyala
No conviced
Kuyenda m'ma church ndi cholinga choti mudzigula adzibusa shame on you🙄🙄🙄
Hahaahha koma ndale za awaaa aaah wangowaedzeka azibusa a SDA kut awapatsa neef akatero akufuna anamizenso ansembe😂😂😂😂
Komatu chiyambile mfundo mulibemo aaah chogwila mtima cheni cheni mulibe
Za ziiiiiii
Ausi mwayamba kulambira Sunday
Chisilu chaunthu ichi
Bodza limayambila povala magalasi akuda..
Ur right kkkkkk😅
Eeeeeeee zilope continues
Mumuphalile mavwalo yake
😂😂😂😂😂nisabatatu mwahuno iiiiiiii
Aroma anamutuluka uyu ,ndalama sizingachotse chilima mimtima mwawo who can do that is a witch.
Ndipo zoonadi simukunama akapusa amudyere basi
Aroma ndi ndani?
Inu ngati simkatolika musatiyike mawu mkamwa akatolikafe
@AlumakioChingalu ine ndiye obadwila mkatolikatu ndidzafelamso.mkatolika pa limber cathraw apo kkkkkk
@AlumakioChingalu tingomudyera basi

Ku chilimba musalole anthu awa. Akuvutitsa ndi kusaukitsa dziko.
Akatolika khalani ndi Maso