Ndichikhala Chilima Sindikanalola Kuti Mulandu Ungotha - Bon Kalindo
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 4 พ.ค. 2024
- As News is circulating that corruption charges against Vice President Saulos Chilima are to be dropped, Bon Kalindo says it would be wise for the Vice Presidenrt to not allow this happen becuase it might do more harm than good to his public image.
Pomwe nkhani ikumveka yoti milandu ya katangale yomwe wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Saulos Chilima idanenedweratu ichotsedwa, Bon Kalindo wati chingakhale chanzeru kwa wachiwiri kwa pulezidenti kuti asalole kuti izi zichitike chifukwa zitha kuvulaza kwambiri mbiri yake.
#malawi
Chakwerayu akufunika bomba basi apo ai ndiye tichita kupha ndi miyala ngati stefano
Kalindo is a great and intelligent man Malawians let's support this man he is very wise
Aliyense yemwe akumadana ndi kalindo sakonda dziko,kalindo akusegura amalawi maso🎉🎉🎉
Ulemu wanu Malume. Chilima anayenera kukana kuti mulandu wake uthetsedwa kufikira chilungamo chioneke
Mr chakwela akuziwa chimene akufuna kuthetsela mulandu ndichani chakwela nduwokubatso
Anthuwa onse ndi akuba, apa akuberekana kumbuyo chakwera is also involved.. 💔💔
That's why wathesa mulandu, mbava zokha zokha izi
Athuwa ndyakuba ndithu chilima mulungu amuyendele padeladela chifukwa naye ndiwakuba wazuza a Malawi kwabasi
Tikufuna akulamulireso paja ndi wachigawo chapakatitu Chili mayo, ndipo udakalira iweyo sunati
Bon kalindo umakwana ndipo malibeso
Umatha born ndpo umamusengula mutu muthu ngti ali akumva achilima amve inu lero ndiinu advance wako ndpo amve ngti samva azamva ataphikira muphika
Abon musayambepo kt mukhale mbali yachilima ayi mukaymba izi mutitayisa hope painu. Khalani wachilungamo ndipo chilungamo chanu chizakhuthandiza kt mukhale pule coming years
More fire 🔥🔥🔥
Zabodza zimenezo, kuti komwe Munthu woniziridwa anayamba wanena kuti ayi ndikufuna mukandiyimbe Milandu?
Ndikuona ngati Chilima is tired of everything. At this point he just wants to live peacefully. If it’s money nde he has enough moves going on. Long live SKC!
More fire more fire
Munthu woti akuziwa kuti anachitadi angakane kuthesa mlandu? Kuteloko Chilima wasangalala kwambili.
Milandu siola tionesana September next year mr chilima
Zakhala bwino coz chilimayo akakana kuthatsa mlandu zitenga nthawi ife tikufuna akhale pule mmalawi muno
vuto bushiri safuna kuzaima ngati president
Chilima next president 2025
Yes ask Mr cassim chilupha this malawi ,
The DC bon kalindo
Tamenyelani ufulu anthu osauka basi nanga mwayambaso kumenyela ufulu chilima
Advisor was Chilima ndiwe Bon Kalindo ndipo iwe Chilima ukatsata zimenezi,BOMA iri udzalamula tsikulina.
Boni kalindo the D c
The DC
Machine
Onsewa ndi mbava zokhazokha so zikuopana kuti angaululanepo apa😂😂😂😂😂
Mmene ndimamuonela chilima ndi mfana ofoila kwambili, izi kwa iye zatha bsi why ati ndi mfana oganiza bho za ziiiii . Asayankhuleso za nonsense zokhuza mlandu wake. Amakanika kuyankhula za mavuto womwe amalawi akukumana nawo , ndie akatiuza za mlandu wake za chani, anthuwa ndi amozi palibepo wabwino apa
That's why ndiwe mbuli iwe Bon kalindo because you don't understand the incompetence of Martha Chizuma based on how she presented and compiled the evidence in order to strengthen the state's case way back from the beginning. The problem with you Kalindo is that you think the top leadership has a hand in this decision without understanding that the office of Director Of Public Prosecution(DPP) has the prerogative to discontinue a case that lacks validity and stems from insufficient evidence, and that any evidence collected illegally can't be submissive in a court of law. Chizuma rushed to do what wasn't supposed to be done, hence the need to discontinue the case. So kalindo, please do not pause as a benevolent advisor to Saulos Chilima because you lack the understanding of the whole case. You are just a Copycat of what was debated on a Hot Current program of Times Television, and you want to exhibit some wisdom out of that program. Presenters of that Hot Current program of May 5th also lacked understanding the reasons behind the discontinuance of Chilima's case, but showed emotion and a biased approach to the same. Kalindo please shut up because you know nothing but ranting.
Acb singamange vice president chakwera asakuziwa
@@awardjafar2928 You don't know what you're talking about. ACB gets consent from DPP( Director Of Public Prosecution) who is independent of the executive. The president only follows proceedings thereafter , but has powers to offer clemency after conviction.
Mukamva izi muzimwa madzi ambiri zimathandiza, achipatala adatero, mqtupi odzadza mafutawa sachedwa kulefuka. Maka ukafuna kukonza zinthu ngat izi.
Mukulakwitsa chifukwa mulanduo siwanu musaoneke ozindikila ndinuo musireni mwiniwake aganizepo mofatsa osalankhula ngati mwamuona kuti chilima ndichitsilu
Non Kalindo , was Chilima found huilty of theft by the court of law ?
And even I Chilima declines the discharge, the DPP still has the authority to discontinue the case....without chilima's consent
Timakunyadira DC
Chilungamo chanu timakondwera nacho ife osauka
tha DC😂😂😂😂😂😂...NTHAWI YA GYM😂😂
Chakwela akuopa kt wapatsindwi angaulule wapadzala
Abon nayo asamale asakhale kumbuyo kwachilima ayi
iweyo kalindo ndiiiwe waphuma lopusa kwambiri that's why umasusa zinthu lero mawa nkumavomeleza nkhani yomweyo! suuziwa zimene uli ...sungakhale chilima ndipo sungamake pachilimaa that's why after all insults none answers you because they use 'kumenyana ndi wamisala nonse mumaoneka amisala'. onse omwe umaanyoza samakuyankha to avoid foolishness!! amene amakusapota iwet mmmmm kkkkkkk😂😂😂😂 ife tinakutuluka kalekale!! olo Mandela anamangidwapo but still he was voted into power!!! uzipaanga zakozo tizingokuyang'ana
Panyapako
Kkkkkkkk ok
Mwayamba ndale za a chilima Mr bon kalindo
Our Lovely Malawian Redeemer and wise man Kalindo, keep the fire burning
Mr bon kalindo ,if the case has no mature evidence there's no need to continue with the case.and also bringing false information to the case is also illegal.mr chilima is innocent man.
Dzimachende dzako bon mathanyula
Tchende lamako phwala lako
@@WilsonLimited-fh1mz pamtumbo pamako nachende iwe , dzi ma refugees dzothawa nkhondo ku Mozambique
I don't trust any politician in Malawi
Another problem ndiyokuti us people we don’t differentiate between stealing and bribery.
Those are two different things.