A Police Ndi A Army Ntchito Yanu Siyoopsyeza A Malawi - Bon Kalindo
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 11 พ.ค. 2024
- On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo want to speak with Malawi Security Agencies, telling them that their job is not to terrorise Malawians but to keep Malawi and Malawians safe and secure.
Pa Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo akufuna kulankhula ndi Nthambi za chitetezo ku Malawi, kuwauza kuti ntchito yawo si kuopseza Amalawi koma kuteteza Malawi ndi Malawi.
#malawi
Kalindo umatha..big up
The DC
The picture was designed by Junta club
Osati dzikwi za anthu? Times hot currents said it was filled with a lot of people.
I love you bwana bon kalindo
Kumbayani zikuvuta kupeza ma ID
Bon kalindo angalamule ziko kupamba chakwela ndi chilima
I love the DC
The D.C. ❤❤
Akalindo ndionga Palibe chomwe angatiuze chazelu or misala inachuluka mmutu
Ku Namiwawanso zikuvuta kwambiri kupeza ID
The DC ❤❤❤
The dc asiye achitetezowo aziona pasogolopa boma limasintha asaiwale
Army anzawo akulanda maiko uko, Malawi yomvetsa chisoni kwmbr ndi asilikali omwe tonse tulo lokhalokha
Malawi is one of the country that is still poor because of politics
Kumachinjili anthu alumapita 3aam ukapanda kulawla form suinumkha ATI anthu 250 ATI patsoko
Osangolowa dppyo bwanji kalindo
Dc❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤🎉
Ndi wandale siwomenyela ufulu ayi kambweee galu masa unali kale mdpp
It's called the abuse of power and intimidation just to oppress loyal descent citizens. Here at home the Bobby metropolitan police including the community police they protect us and arrest criminals not the other way around. Here we love our police and you feel secured and warmth around them, you can actually tell them anything very fast thus if you saw someone committing crimes.
The DC boni kalindo, kawawa
Achalume
The DC iiiiiiiiiiiiii mumaitha
KALINDO udziwe kuti mcp ndiyoyipa dzedi Abitsa ndalama ziko cholinga anthu adzitsauka iwowo adzigula dzinthu adzigawa mene akugawala Ufa kaya ndalama ndidzina dzotelo malo kodza chuma chadziko kuti anthuwo adzigula okha asaaa koma a mcp inu ndi agalu kwabasi
Nyamata omenyela ufulu alomue
Osasankha mtundu DC ifenso anthu aku mpoto timawakonda a DC athu not only for alomwe.
The DC ❤❤❤