ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Enanu mukuona ngati akulankhulawa ndiwosowa nzeru kapena amphawi muzazindikira bwino patsogolo ngatitu tikumadya nkumakhuta sionse akukhuta ayi anthu akunzuzika komanso mukamati kalimani kulima mwakuona lero bwanji simumanena muja mumamumatcha Peter kuti achoke pa mpando mulibe nzeru komanso ndinu ozikonda anzanuotu akudya inu tikuvutikira limodzi😂😂😂😂😂
Alima opanda fertilizer? Zavuta tivomereze anthu awa sitiwatha kuthupi koma pemphero ndipembedzero.
Awa saziwa kuyendesa dzikoAchakwelaAmalawi amagwila ntchitoAmalawi olimbikila ntchitoKoma asogoleri a akuba okhaokha Mulungu walange
Esh tavutika ndithu
Simunati muziona, timkakuwuzani ife kuti musavotere izii lero siizi mukutipwetekesa omwe tinaikana mcp ife
Zoonadi big yy alepela .kusowa sugar kuno ku Malawi. Sugar kufika pa K3500 zoona .kuno kwatu tikudalila tishuga wochokera Ku Zambia ,kulije sugar wa illovo .
Ineyo ndikadankhala akulu wa nyau malawi yonse ndikadalengeza kuti tizitulutse ndikukafika komweko ndikukavuta oopysa
Aliyense Amanena zomwe zikumuwawa
Walira Chokwedza Ochewa Tinanena Ife Kuti Chakwera Simunthu Lero Ndi Izi😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Chakwela mbava yahikulu achokee chilima bomaa
❤❤❤❤ bro
Amene amakonda MCP ndiamene akudya Naye chakwera tsopano taziwona tokha za MCP tikangoza Kuti MCP siyabwino
Munasankha nokha pakufunika chakwera yo akufinyeninso kwambiri
Chakwera galu wa munthu kungobwera kudzazuza amalawi bs
Chakwela mbava yahikulu chilma angamba kale zosangana mitundi hiteee
Muphunzire kuvotera munthu chifukwa cha ubwino wake, osati chifukwa choti ndi wakwanu.
Mmmmm pepan amwene mwazindikila mochedwa kwambli ubwino wake mumadziwakale kut zidzakhala chonchi nde tiyenazoni munasankha nokha pajatu mumafuna kusintha zinthu nde mwazisinthadi nde don't wary mukadzafunaso kusintha zinthu mudzasinthaso musalile ayi
Komatu moyo watsankhu umene mukuchitawu thawizina mudzafuna anzanu
koma zoona chakwera waononga dziko ndipo tikapanda kusamala tose titha psiti
8:14
Munyera muona simunati
Wa ulesi uyu akalime
Feteleza akwinitsa?
Wadyanayoo 😭😭😭🇮🇱
Akulu kalimani ndinu wawulesi
Fertilizer wa 100 thousand kwacha per 50kg bag umugulira?
Nthawi ya DPP mmati DPP yawononga panu mkuti waulesi kkkkk
More 🔥 braza man.
Olonsotuuu kumwera c onse amakonda dpp kulinso ena a Udf ndiye mukufuna muwanamize chani akuluuuu.......Mcp nchipani chakaleee kaleeee
Machende ako iwe
Zomangoti MCP MCP Zi mmalo momalimbikila kulima tomato tichedwa nazo guys
Aaah r u sure
Enanu mukuona ngati akulankhulawa ndiwosowa nzeru kapena amphawi muzazindikira bwino patsogolo ngatitu tikumadya nkumakhuta sionse akukhuta ayi anthu akunzuzika komanso mukamati kalimani kulima mwakuona lero bwanji simumanena muja mumamumatcha Peter kuti achoke pa mpando mulibe nzeru komanso ndinu ozikonda anzanuotu akudya inu tikuvutikira limodzi😂😂😂😂😂
Alima opanda fertilizer? Zavuta tivomereze anthu awa sitiwatha kuthupi koma pemphero ndipembedzero.
Awa saziwa kuyendesa dziko
Achakwela
Amalawi amagwila ntchito
Amalawi olimbikila ntchito
Koma asogoleri a akuba okhaokha
Mulungu walange