Zomwe Wayankhura Patricia Kaliati Zadabwitsa Anthu

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 5 พ.ค. 2024
  • Zomwe Wayankhura Patricia Kaliyati Zadabwitsa Anthu

ความคิดเห็น • 246

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 หลายเดือนก่อน +9

    Pepani mayi, your time is gone. You are all failures. Now is time for DPP, UDF and AFORD. Enanu mukagwere.

    • @EllenLuwanika-tl5ck
      @EllenLuwanika-tl5ck หลายเดือนก่อน +1

      Dpp uDf AFoRD my vote

    • @chiluzbandah
      @chiluzbandah หลายเดือนก่อน

      Aah thawi ya Dpp inatha

    • @EllenLuwanika-tl5ck
      @EllenLuwanika-tl5ck หลายเดือนก่อน

      @@chiluzbandah mukunama

    • @chiluzbandah
      @chiluzbandah หลายเดือนก่อน

      @@EllenLuwanika-tl5ck tiyeni tidikire

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 หลายเดือนก่อน +9

    Bodza la 2019/2020 lija mwayambiranso? I don't know what you guys gonna say this time. You can't fool a Malawian again, your time is over.

    • @mustafailanga2585
      @mustafailanga2585 หลายเดือนก่อน

      Akaliati zauhule basi kuyela kogulako mbudzi yamunthu zausilu basi ndi galu wakoyo chilimayo

    • @user-hy4el8ov1l
      @user-hy4el8ov1l หลายเดือนก่อน

      Akuti nsomba zikaola mundengu nde kuti zonse zaona awa asatimize ayi zisilu zaathu

    • @user-hy4el8ov1l
      @user-hy4el8ov1l หลายเดือนก่อน

      Akwafusa athu kuti kondi simumadya kawili akuti zimene zija zodya kawili zo zinali za UTM akuti kasala kamozi komaso athufe timangosekelela zilizonse

    • @umalimaganga
      @umalimaganga หลายเดือนก่อน +1

      Chilima 2025 BOMA lanyowani

    • @umalimaganga
      @umalimaganga หลายเดือนก่อน +1

      Chilima 2025 BOMA lanyowani

  • @Creslevison-vj2sl
    @Creslevison-vj2sl หลายเดือนก่อน +5

    Tachionereni chikuyankhula ichochi apa manyaz bwanj isa upusa bas

  • @LovemoreSalima
    @LovemoreSalima หลายเดือนก่อน +2

    Chonde amalawi, amzanga osaononga vote kamba kokuti akukunazani ndi ma ti shet kapena msalu musamale.

  • @andrewchirwa2193
    @andrewchirwa2193 7 วันที่ผ่านมา

    UTM vote yanga

  • @LovemoreSalima
    @LovemoreSalima หลายเดือนก่อน +1

    Wazipeza zitsilu
    Ku chiladzuluko, osakuthamangitsa?

  • @JasonJackets
    @JasonJackets หลายเดือนก่อน +1

    Mmzimayi oipa manyazi alibe garu wen wen☝️

  • @eliaskhofielias8152
    @eliaskhofielias8152 หลายเดือนก่อน +1

    Anthu ena anangobadwa opanda manyazi ndikuyankhula.komanso anthu ena timasowekera wisdom from God kumangosatira zilizonse.zoona anthu omwewa ndiomwe anatipusisa leronso tikuwasatilanso bac atimbwititseso?koma aliboma momwemo palibe chomwe akupanga ndiye anthu opanda uzimu akuwatsatilabe komanso adzazivoteranso zitsiluzi.

  • @user-rd8vw1pc4b
    @user-rd8vw1pc4b หลายเดือนก่อน +5

    Chitan manyazi akwen 😂😂😂

  • @user-pb1yr1jx5g
    @user-pb1yr1jx5g 10 วันที่ผ่านมา

    APM MY VOTE ❤

  • @user-yk3wc9ei5g
    @user-yk3wc9ei5g หลายเดือนก่อน +2

    Wasowa chonena ameneyi.

  • @Hendersonspoon
    @Hendersonspoon หลายเดือนก่อน +1

    Manyazi mulibe iyayi kkkkk

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 หลายเดือนก่อน +1

    Mmmmmm ayamba kunamanso koma amalawi tikamvera izi ndife omvetsa chisoni

  • @user-pl6it7zc7c
    @user-pl6it7zc7c หลายเดือนก่อน

    kuonera live from south Africa mumakwana more fire

  • @sthoramexjrsa902
    @sthoramexjrsa902 หลายเดือนก่อน +2

    Manyaka weniweni🥺🥺🥺

  • @PeterPhiri-nd6op
    @PeterPhiri-nd6op หลายเดือนก่อน +1

    Zaboza zokhazokha eshii amalawi ndiyeno mukusekelela mmmmm

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 หลายเดือนก่อน +1

    Zatha nfundotu, mungobweleza za kale mumawanamiza amalawi zija. Kuatengela amalawi ku mtoso basi. Olo manyazi mulibe.

  • @ThoccoBondo-mx7vt
    @ThoccoBondo-mx7vt หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂Sewelo latikufelanji anthu abodza awa

  • @MaliGomani
    @MaliGomani หลายเดือนก่อน +2

    😂😂😂😂😂Koma mbuzi Izi akatero awanamize anthu kena

  • @ishmaeldama8906
    @ishmaeldama8906 หลายเดือนก่อน +2

    Kaliat mulungu akulange😊

  • @user-hy4el8ov1l
    @user-hy4el8ov1l หลายเดือนก่อน +2

    Muthu wandale ndi satana lero akubwela ndi boza 😂😂😂

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr หลายเดือนก่อน +1

    Uyu adameza memory card eeeee!!! Wayambapo Zonama zakezija.

  • @user-jr1kq9vc7n
    @user-jr1kq9vc7n 24 วันที่ผ่านมา

    UTM my vote

  • @innocentnjoka7014
    @innocentnjoka7014 หลายเดือนก่อน +1

    DPP woyeeeeee❤❤

  • @LovemoreSalima
    @LovemoreSalima หลายเดือนก่อน +1

    Huleyutu wayamba
    Tikuthamangitsatu ndi maduka,
    Usamale hure iwe.

  • @HarryRefred
    @HarryRefred 27 วันที่ผ่านมา +1

    😂 zazi palibe chomwe ukukamba pamenepo 😂😂😂😂 kagwele uko

  • @StanfordGoda
    @StanfordGoda หลายเดือนก่อน +1

    🎉bodza bodza bodza koma ulibe manyazi.

    • @johnjoachim3820
      @johnjoachim3820 หลายเดือนก่อน

      Takambani zina, ndiye poti amalawi ambiri tinapoila sitimadziwa chomwe timafuna boza la 2024

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani หลายเดือนก่อน +1

    Ufiti ulipodi ku Malawi 😢😢

  • @hmshohagshohag9483
    @hmshohagshohag9483 หลายเดือนก่อน +1

    Palibe chanzeru mukukamba inu, Chakwera anakupeperesani kale apa Chilima wanuyo azamuvotera ndi ambuyake .kodi a Amalawife mumatitenga ngati zitsiru eti

  • @HarryRefred
    @HarryRefred 27 วันที่ผ่านมา

    Ukuzikolakola wekhatu 😂😂😂😂😂 muziwona katatu😢😢

  • @user-rd6zo8ry2d
    @user-rd6zo8ry2d หลายเดือนก่อน +1

    Mai opanda nzeru uyu kuwatenga amalawi ngati opusa eti

  • @lloydmalinga1198
    @lloydmalinga1198 หลายเดือนก่อน +10

    saulo Ali muboma chipanga iye ndi chani chanzeru.

    • @isaihmagani5697
      @isaihmagani5697 หลายเดือนก่อน +2

      Nzeru ulibe iwe sukuona adayimisidwa ntchito kuti ngwa Kuba, ndipo wakhara asakulamura nawo, pano mwina poti akuti milandu isapitilire umboni alibe siolakwa

    • @phirimacdonald8638
      @phirimacdonald8638 หลายเดือนก่อน

      😢tachokani okuba inu ,mumubelenso ndani mmanyamula thumba la fertilizer paphewa palibe mwachita inu

    • @Ferguson-Mdaka
      @Ferguson-Mdaka 10 วันที่ผ่านมา

      ​@@phirimacdonald8638Chilima wasn't given a chance to work. You know, and are a witness, to that. Think

  • @chikumbutsomarch4484
    @chikumbutsomarch4484 หลายเดือนก่อน +2

    Manyazi mulibe

  • @StanziaElias
    @StanziaElias หลายเดือนก่อน +1

    Mayi mulungu akukhululukileni kwambili koma ndili ndifuso kuti inu mumapemphela?

  • @isaacchipatala1618
    @isaacchipatala1618 22 วันที่ผ่านมา

    SKC my vote

  • @PleasantMagombo
    @PleasantMagombo หลายเดือนก่อน +1

    Anthu osowa zochita awo.

  • @user-iu3bf6oe1x
    @user-iu3bf6oe1x หลายเดือนก่อน +2

    Amp my vote

  • @llewellynkhungwa4712
    @llewellynkhungwa4712 หลายเดือนก่อน

    Kweee is back....💪

  • @samsonphangire1523
    @samsonphangire1523 หลายเดือนก่อน +1

    Akweni yokhayi yodya katatuyi Akweni sigwira ataaaaa or pang’ono kkkkkkkkkkk!

  • @user-vu9rt8gj3o
    @user-vu9rt8gj3o หลายเดือนก่อน +1

    Mbuzi iweee

  • @LinessiTambala
    @LinessiTambala หลายเดือนก่อน +1

    Mwachedwa

  • @StanziaElias
    @StanziaElias หลายเดือนก่อน +1

    Ulape mulungu akukhululukile

  • @WhiteRichard-cw2fo
    @WhiteRichard-cw2fo หลายเดือนก่อน +1

    Mai oposa iwe wasowa chonena watokhuta

  • @user-ow3tp3vu3c
    @user-ow3tp3vu3c 11 วันที่ผ่านมา

    Kodi chilima salim'boma penapake akweniwa asamatinamize ndithu aaaa

  • @user-wi9pe2hz7e
    @user-wi9pe2hz7e หลายเดือนก่อน +1

    Manyaz mulibe mai nd chilima wanuyo kagweleni uko

  • @YohanePatrick-lc2lq
    @YohanePatrick-lc2lq หลายเดือนก่อน +1

    Panyinipako hele iwe komatso nyiyamako nyiya iviyo

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e หลายเดือนก่อน +1

    Kodi kaliati uwe ndi munthu kapena chidzukwa muudze chilima anyamule thumba lafertilizer lija ulibe nzeru chilima wakhala akunama pano angamumvere ndani mbavayo okuba ndi sattar

  • @binalidjeyshabahzombamalawi
    @binalidjeyshabahzombamalawi หลายเดือนก่อน +1

    Mbuz yosafunikira kaliat

  • @user-rk3jx3kg8i
    @user-rk3jx3kg8i หลายเดือนก่อน +1

    Mai opanda nzeru akuwatenga amalawi ngt zisiru,

    • @user-oh5vs1gl4n
      @user-oh5vs1gl4n หลายเดือนก่อน

      ife pambuyo pa adadi osati onamawa ,achilimaso ndi kape anali kuti

  • @isaacchipatala1618
    @isaacchipatala1618 22 วันที่ผ่านมา

    UTM for life

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x หลายเดือนก่อน +2

    Kupepera zedi uku muuisova DPP ikulowa m'boma itchetcha afiti nonse okubanu

  • @EdgarBuleya
    @EdgarBuleya 20 วันที่ผ่านมา

    Kkk koma malawi eee alibe manyazi akwen inu mwano wake

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 หลายเดือนก่อน +3

    😂😂😂😂😂😂 so funny the take Malawian for granted. Wht is doing now is in the government mxm

  • @francisvisage2705
    @francisvisage2705 23 วันที่ผ่านมา

    Musagawe nsalu inu, gawani chimanga ndi kukwanilisa munalonjeza

  • @musamakanjira
    @musamakanjira 22 วันที่ผ่านมา

    Wati ma Mp ali ku boma komweko alephera nanga Saulosi si ali ku boma konko

  • @TressLuka
    @TressLuka 20 วันที่ผ่านมา

    Munatigwilitsa fuwa lamoto Inuuu aaaa😢

  • @fatsanichibwana9438
    @fatsanichibwana9438 หลายเดือนก่อน +2

    DPP WOYEEEE!!!

    • @user-le9su3mt7r
      @user-le9su3mt7r หลายเดือนก่อน

      Dpp tatopa nawoo apanga Chali mbili zakale

  • @user-jp9ip1dl5h
    @user-jp9ip1dl5h 22 วันที่ผ่านมา

    Anthu akuyankha mofookatu mphamvu alibe.... Njala
    Mmmm

  • @rynordmagoli
    @rynordmagoli หลายเดือนก่อน

    Padiko pako garu iwe

  • @user-hy4el8ov1l
    @user-hy4el8ov1l หลายเดือนก่อน +1

    Mayiwa ndi aboza 😂😂😂

  • @KereeditseMotsetse
    @KereeditseMotsetse 15 วันที่ผ่านมา

    Amayi kaliyati pakholopako

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 หลายเดือนก่อน +1

    Kukamwa konyasako mai iwe osamakayamikira amuna ako bwanji mxiii!

  • @PeterThawi-jc7zl
    @PeterThawi-jc7zl 11 วันที่ผ่านมา

    Kodi fredokiss akutaniko uku😂😅😂😂😂😂😂😂😂

  • @user-xv3ju8yi9n
    @user-xv3ju8yi9n หลายเดือนก่อน

    Ingobwererani ku dpp musowatu cholankhula campaign ikubwerayi.

  • @user-qe2lv3hs8q
    @user-qe2lv3hs8q หลายเดือนก่อน

    anthu andale ndinu oipa inu mulungu azikukhululukilani 100% tikuvutika chifukwa cha anthu andale inu

  • @user-zv9ud1dx3j
    @user-zv9ud1dx3j 14 วันที่ผ่านมา

    Kodi mulibe manyazi ndithu?

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 13 วันที่ผ่านมา

    Kodi mwanva speechyi anzanga ine sinkunva mpaka ndaika bluetooth ine 😢

  • @allanchangalusa6662
    @allanchangalusa6662 หลายเดือนก่อน

    Galu uyu, ung'omboka 2024

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 หลายเดือนก่อน

    owinawina SKC

  • @PeterPhiri-nd6op
    @PeterPhiri-nd6op หลายเดือนก่อน

    Sopano apa muli muboma bwanji osapanga zosezi agalu inu

  • @user-gx8or3yz9u
    @user-gx8or3yz9u หลายเดือนก่อน

    Mzimai oipa uyu za dpp unasunga zija ukabweze kwa eni aka adad mzimai oipa iwe

  • @JamesMalango
    @JamesMalango หลายเดือนก่อน

    Kuyankhula kwa bwanji uku mukamati munangowalawitsa anthu, kusowatu chonena uku

  • @user-is5dl7np9g
    @user-is5dl7np9g หลายเดือนก่อน +1

    Palibe chamzeru chomwe mukunena mayi opusitsitsa inu, a malawi mwawatola

  • @WitnessKambwiri
    @WitnessKambwiri 24 วันที่ผ่านมา

    Hule uyu ali ndikukamwatu kobowoka kkkkk

  • @KereeditseMotsetse
    @KereeditseMotsetse 15 วันที่ผ่านมา

    Kalonga ndi chilima machendako nose agalu ndionukha kumatako kaliyati mayi

  • @lingstonenagoli7729
    @lingstonenagoli7729 หลายเดือนก่อน

    Mayi asazampatsabe mpando,anthu oipa akuononga dziko ndi awa

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 หลายเดือนก่อน

    Onse Alliance sopano, eeeeh! Mbuzi zokhazokha.

  • @godfreysingini1508
    @godfreysingini1508 20 วันที่ผ่านมา

    Palibe zonamizananso ayi agalu inu stupit

  • @user-lg1bw8fx5m
    @user-lg1bw8fx5m 22 วันที่ผ่านมา

    Zakudya katatuzo tazisiyani izo yambani Zina komaso ngat ndale mwatopa nazo muyeseko business ya kaunjika musatichimwitse

  • @farlenmkorongo
    @farlenmkorongo หลายเดือนก่อน

    Vuto simumaziwa kuti vice president ku malawi amachita kutumidwa ndi president, nde ngati president anamuyimisa iyeyo akanatani

  • @MAPAGASTUDIOS
    @MAPAGASTUDIOS หลายเดือนก่อน

    Tentiyo a dpp anakubwerekani yosachapatu komaso zakuti mukutibera misonkho mubomamu zodziwa chilima wanuyotu osangobwerera pambuyo bwanj mpepeseni APM basi

  • @Mike-du7zt
    @Mike-du7zt หลายเดือนก่อน

    😂😂😂 koma anthu andale eeesh

  • @PeterThawi-jc7zl
    @PeterThawi-jc7zl 11 วันที่ผ่านมา

    Ku Malawi kuli zipani ziwiri...osamanamizana ma kape Inu.MCP and DPP basi.enanu mukutaya nthawi😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg หลายเดือนก่อน

    Mau amati awiri sayenda limodzi asanapangane, inuyo m'mene mumalowa mu alliance munagwirizana lero musayambe kusintha chichewa kamba koti zakuvutani. Zipitani tiyese anzanu, anzeru si inu nokha ndi a Chilima kulinso ena.

  • @LemaniKhimba
    @LemaniKhimba 18 วันที่ผ่านมา

    Uzauza abale abale ako zodya katatuzo

  • @TywellShumba
    @TywellShumba 12 วันที่ผ่านมา

    Galu isiyen izikuwa yakhuta mafupa

  • @InnocentJavelo
    @InnocentJavelo หลายเดือนก่อน

    Olo mayi wakuyandikirayo wakhumudwa nawetu kwambiri😢😂

  • @StanziaElias
    @StanziaElias หลายเดือนก่อน

    Mungosiya kupemphela mwamva

  • @user-wl3nb1mq9t
    @user-wl3nb1mq9t หลายเดือนก่อน

    Zaziiiiiiii

  • @westednyachikadza6353
    @westednyachikadza6353 หลายเดือนก่อน

    Koma, mfiti iyiih

  • @beinhardkausiwa7107
    @beinhardkausiwa7107 หลายเดือนก่อน

    Apm ❤

  • @MackdonaldMilanzi
    @MackdonaldMilanzi หลายเดือนก่อน

    Mayi opandanzelu kwambili

  • @MphatsoIshmaeladam
    @MphatsoIshmaeladam หลายเดือนก่อน

    Tsopano ngat manufesito onse mudalonjeza alipo ndindani akudya ndikugula fertilizer pa mtengo omwe mudalonjeza?Koma Mcp mukuiona bwino ubale wanu mmansomo ukuupenyetsetsa? DPP plus UDF more fire

  • @PeterThawi-jc7zl
    @PeterThawi-jc7zl 11 วันที่ผ่านมา

    Mwachedwa kutuluka mu tonse alliance ...UTM is a dead party.ndipo palibe angavotele UTM😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @ThoccoBondo-mx7vt
    @ThoccoBondo-mx7vt หลายเดือนก่อน

    Aaaaaaaa nanunso mwasowatu zokamba wadya katatu ndani inunso anthu ndi omvesa chisoni kwambiri fertiliser wosaka mtengo mwamugula kuti mitu yanu mwaiwala nsanga nsanga

  • @user-ow3tp3vu3c
    @user-ow3tp3vu3c 11 วันที่ผ่านมา

    Anthu sadya mfundo

  • @user-vp5mf6bd3o
    @user-vp5mf6bd3o หลายเดือนก่อน

    Ndinu mai ovesa chisoni mulungu sakondwera ndi boza ngati limeneli

  • @WilliamMsimuko-mx7fu
    @WilliamMsimuko-mx7fu หลายเดือนก่อน

    Apm my vote❤❤Dpp

  • @user-fm5fk1zt1l
    @user-fm5fk1zt1l หลายเดือนก่อน

    Adadi woyeeeee

  • @jeremiahmemmanuel9988
    @jeremiahmemmanuel9988 หลายเดือนก่อน

    Anthu amodza inu