Chisale akumva zowawa chifukwa cha anthu ansanje but Chisale is the best Man in Malawi he spend his money to help the orphans and community, God bless you always and protect you Mr Chisale.
Interviewing a well trained professional soldier should be different with interviewing a well trained professional economist💪🏾💪🏾Bravo snipper Norman Paulosi Chisale🤣🎉🎉💥💥
Mr Chisale I hear ur story it's very bad and am very happy with u ustand with God dnt give up mukuyakhula kwako mulungu akumva ndipo mulungu amalora Kuti ana Ake andutse mmavuto ndicholinga Choti ukulu wake ukaonekere God will be with u mwaiwe muli usogoleri
Mukuyamikila chisale man? After all what he did now you're embracing his work.... don't you know people lost trust in DPP and one of the biggest reason ndi iyeyu
People never lost trust with DPP...anthu tinanamizidwa kuti tizaona zabwino...pano misozi yatha mmaso yayamba kutuluka ndi misozi ya magazi chifukwa Cha bodza la CHAKWERA ndi chilima.
Political prosecution has ever been in existence since our independence....please follow the rule of the law always! Clear conscious is the medicine...God is watching and will judge everyone right..
Mr Chisale i understand your pain please please firgive him isbus for your own good, you saud you are Christian our master jesus taught us to forgive those who do us wrong before we ask to be forgiven
He is very emotional and trying to run away from facing justice. No one accepts to be guilty in public and whatever is doing here is normal for suspects. 42years doesn't match with the way he looks unless he tells us kuti amasamba Nyanga.
1986 he was already working as a soldier but he is saying is 42 years old eeeeeish!!! 😂😂😂komatu munthuyu akuoneka ndiokakala mtima mayankhulidwewa atha kupanga zoophsya. He is saying kuti ndiopemphela koma akuti sangakhululukile aSteven Kayuni 😭😭 chonsecho amayenda ndi bible , mawu a Mulungu mwamunthuyu mulibemo.
Those who are saying bravo chisale you need special prayers..this guy stole our money tax payers money....he accumulated wealth within a short period of time....hotels cars houses etc he is backing himself apa he can't admit it.....and you are busy kumunyadira 😮Malawi ndife ogona too much.....he is lucky he is outside otherwise he belongs inside
Haters will always blame you my brother just because all the enemies of APM can't be happy with your speech. Even the way this woman is interviewing you just shows that she is one of the haters because of this ( I feel bad and hate those ones who are blaming APM for useless things or political reasons and I handle him as my biological father) but no stress brother you're a real and very strong soldier and you're humble man otherwise stupid questions this woman was asking you if it was I, I would just fu....k off from that interview. Your character is a real good courage and discipline soldier and we love you and everything is going to be good
Am watching this interview kachikenaso Norman Chisale yu ndi #1 kwa amene alipa chilungamo akudziwa kuti big wa ndi real man osangoti mwakati poti umadana naye.
Substandard journalism. Nkhani ya kuti ndalama anazitenga kuti sanayimalize. Amati kunali nkhani yina imene amayenera kugundako they didn't. Komanso kumusiya munthu using profanity language over and over on national osampatsa warning or even ending the program it's way below par.
Interview ili yonse imakhala ndi mayambidwe osiyana, iyi si program ya tikudziweni, muziyamika kuti mwa atolankhani achizimayi, Leah is one of the best.
Pajatu anthu odziwika ngati amenewa introduction sikhala yofunikira kweni kweni, komabe as far as ma dos and don'ts are concerned apopo sizinayende kweni kweni😂
i was riding in your ship until i took some time to regurgitate and i learn kuti amacheza naye ngati bodyguard wa Peter, his professional, and not as him as a person brian banda akucheza ndin Bushiri, 27th may times exclusive, followed the same lane yomwe anacheza ndi a Kapito pa 7th october anatero even yomwe anacheza ndi Dr. Joyce Banda
Achibale zimenezo ndizija mumkachita kwa anthu ena muli m'boma limodzi ndi DPP. Zimatelotu chisale, iweyo ndiye akupsote kumene galu iwe munthu oipa iwe
They are asking this guy what challenges did you face.. akufotokoza ma situations.. he was expected to mention political challenges, kapena professional dilemmas. Ayi, zopepela
Norman is right,the fact that aperson is working in the government does not bar aperson from being rich . Malawians justify poverty as being honest and truth
Why even giving him a platform to say this nonsense.? He was very powerful, kusowa umboni doesn't mean you re innocent...you did 99percent of what you were accused of .....we know you can see even his tone kuti angaombele munthu awa
Achisale ndakutsatani pa u tube Mumapemphela zinazi msiireni Mulungu akhale Mulungu Ambuye yesu amamunamizila koma samayankha kanthu mpaka anaphedwa Eksodo 14v14 Chonde chonde
The lady was carefully selected to handle this interview am impressed with how she has handled this heavy interview. Professional indeed
😊
Big up Norman Chisale ,I love your courage 🔥 Ambuye apitilize kukumenyeran nkhondo ,,,I'm one of your supporters
Ndpo nthawvyamayankho ikubwela big tipanga zobwezera ntoporao
Komano pa point ya human rights Peter Muthalika he really respects
Leah you the best journalist...well done to Me Chisale
Chisale ndimunthu wabwino kwambiri wamanga ma church wachita zambiri Ambuye akudalitsen achisale long live
Great man Norman Chisale. Oceans of luv to you and your family.
Azodiak tamakhalani ndi ma bottle amadzi mukamapanga interview ndi anthu please
Komadi man
I support 😂😂😂good
Chisale akumva zowawa chifukwa cha anthu ansanje but Chisale is the best Man in Malawi he spend his money to help the orphans and community, God bless you always and protect you Mr Chisale.
Zoonad ol evn Ines zimandiwaw, km Amalawi if nsanje😢
@@AngellahKunsanama amalawi amamukonda munthu akafa, that's why dzikoli lili lobwerera mbuyo,
Titakhala ndi anthu 20 nziko lino ngati Mr Chisale Malawi atha kusintha I proud of you Mr Chisale ndimakunyadilani chifukwa chakulimba ntima kwanu
Norman ooooye.Please Please please Mr N Chisale keep it up God will help help you, always pray, praise him Amen Amen Amen
God bless Mr chisale komano mokupemphani ndithu pepani uyu akufuna kut mumukhululukileyu imvani kulila kwake kut ukulu wayehova ukhalebe pa inuyo yesu anat muwakhululukile chifukwa sakuziwa chimene akuchita
Musaiwale kut munthu payekha alibe vuto koma satana akamulowa amapangisa munthu kuchita zimene choipa chili mwa iyeyo chikufuna please ndikuziwa ndithu ululu ndi ochuluka kwambili koma khululukani ambuye apitilize kukupasani moyo wamphanvu madaliso avumbebe kut wamasiye apeze popumila
Interviewing a well trained professional soldier should be different with interviewing a well trained professional economist💪🏾💪🏾Bravo snipper Norman Paulosi Chisale🤣🎉🎉💥💥
The one who talk the truth doesn't fear and it's really true that the truth pains big up Mr Chisale
Am agree with you 💪
I agree with you.
Gud interview love you questioner and Mr interviewer Norman
Mr Chisale isn't my relative but ndawamvesa he is a real soldier, BRAVO CHISALE. BULL Sheet kayun.
Chisale your number 1 well trained soldier
Soldier never die chisale more 🔥
Mr Chisale I hear ur story it's very bad and am very happy with u ustand with God dnt give up mukuyakhula kwako mulungu akumva ndipo mulungu amalora Kuti ana Ake andutse mmavuto ndicholinga Choti ukulu wake ukaonekere God will be with u mwaiwe muli usogoleri
Msilikari adzakhare msilikari mpaka kare. Big up bro N. Chisare❤❤
Norman your statement is clear and comprehensive but what about Chthyola, Chimwendo Banda, Kunkuyu etc ??
Bravoooo big man chisale i salute you
Akuzuzika ngati yesu chisare ndi Good Samaritan athu abwino amazuzika
Mr chisale attitude in this interview shows kuti bambowa ndionama..😂
Ndipo sukunama uku ndiwabodza auze mtundu wa a Malawi kuti ma billions a chuma anawapaeza bwanji osamangobwebweta zopanda phindu, kufuna anthu akumvele chisoni.
Ndinu mabulutu guys
I like the energy tht u hv Mr chisale as a soldier...big up❤
Powerful talking and intelligent, proud of you @Norman Chisale
Intelligent ya ku machende amalawi mapanga support zingawenga bwanji, kupusa
Mukuyamikila chisale man? After all what he did now you're embracing his work.... don't you know people lost trust in DPP and one of the biggest reason ndi iyeyu
People never lost trust with DPP...anthu tinanamizidwa kuti tizaona zabwino...pano misozi yatha mmaso yayamba kutuluka ndi misozi ya magazi chifukwa Cha bodza la CHAKWERA ndi chilima.
Courage muli nayo...komano kusa kululukako kuchita kuoneseratu kuti muli ndi mtima wakupa
😢 or uli iweyo kut munthu akunamizele mulandu wa murder. Uthakumukhululukira?
Sukudziwa chomwe ukunena, sukuona kuti Chisale amuzuza popanda zifukwa?
Ana achepa ulemu wanu bwana chisale 👏👏👏👏👏👏
Amalekano zikomo chifukwa Cha machezedwe anu ndi achisale mkazi odziwa kufusa ngati iwe thanks
I like sir Norman Chisale he's been good in speech osamaopa pa chilungamo
Wn am the of them amene ndimamva kuwawa ndikamva kuti mwamangidwa,sinakumane nanu ,sitinayankhulako koma zimkandiwawa koopsa
Political prosecution has ever been in existence since our independence....please follow the rule of the law always! Clear conscious is the medicine...God is watching and will judge everyone right..
One thing i like this guy he talk straight
Mr Chisale i understand your pain please please firgive him isbus for your own good, you saud you are Christian our master jesus taught us to forgive those who do us wrong before we ask to be forgiven
This woman is brave
He is very emotional and trying to run away from facing justice. No one accepts to be guilty in public and whatever is doing here is normal for suspects. 42years doesn't match with the way he looks unless he tells us kuti amasamba Nyanga.
Watching from zambia
great mtolankhani , kip the fire burning girl
1986 he was already working as a soldier but he is saying is 42 years old eeeeeish!!! 😂😂😂komatu munthuyu akuoneka ndiokakala mtima mayankhulidwewa atha kupanga zoophsya. He is saying kuti ndiopemphela koma akuti sangakhululukile aSteven Kayuni 😭😭 chonsecho amayenda ndi bible , mawu a Mulungu mwamunthuyu mulibemo.
Kkkkkkk aaa zoona. Msilikali kiching, amba chilungamo n how he's feeling with de way they r treating him
Those who are saying bravo chisale you need special prayers..this guy stole our money tax payers money....he accumulated wealth within a short period of time....hotels cars houses etc he is backing himself apa he can't admit it.....and you are busy kumunyadira 😮Malawi ndife ogona too much.....he is lucky he is outside otherwise he belongs inside
Kmat adakufikisani pamenepo ndi bambo anga mudawathokozapo ndi chani ???
Haters will always blame you my brother just because all the enemies of APM can't be happy with your speech. Even the way this woman is interviewing you just shows that she is one of the haters because of this ( I feel bad and hate those ones who are blaming APM for useless things or political reasons and I handle him as my biological father) but no stress brother you're a real and very strong soldier and you're humble man otherwise stupid questions this woman was asking you if it was I, I would just fu....k off from that interview. Your character is a real good courage and discipline soldier and we love you and everything is going to be good
Koma Chisale uyuyu eeeeeeh 🙌🙌🔥🔥🔥
respect to you both you building Malawi in this interview ..
This guy is some how mad
Definition of having readership, fire 🔥 chisale
Once a soldier always a soldier 💪💪💪💪
Once a soldier always a soldier❤❤❤
Kma this interview must be repeated even pa wailesi , nice Leah keep on going more fire
Norman chisale iweyo ndi number 1 moto kuti buuuuu!!
Chisale usatiuze kuti akhale wo opa mulungu suyo chakwera wo opa mulungu akutizunza
This was nice chisale seems a good one though ndindale
Am watching this interview kachikenaso Norman Chisale yu ndi #1 kwa amene alipa chilungamo akudziwa kuti big wa ndi real man osangoti mwakati poti umadana naye.
Chisale oopsya eeeee. Bible mmanja koma Bullshit pakamwa mbweee ashiii
Iwe umati atani? Uzaziona ukadzapeza ndalama
Tikukuvesesani mr chisale.
Once a soldier always a soldier
Exactly
Great man ,i like u
Ndamva chisoni pokumva nkhani yanu bambo Chisale 😢 koma chilungamo chilipo ndipo momwe mwadutsa inumo enanso adutsamo ili ndidziko. Abale whyyy a police athu mmatero, olo ndiliineyo ndingaophwezetu ndipo ndikanamizilidwa ndimakwiya kuposanso achisalewo 😂😂
Your the best Leah
Wabodza iwe umakhala kukawale pa rent bingu akulamula unalibe kanthu unaba chuma bingu atamwalira ku state house
Eeeeeeeeee ai zikomo kwambili koma Mulungu arimbariyakhe
Akunama uyu, wakupha komanso wakuba, chitsiru chimangidwa chisiyeni, sakudziwa kuti apita kundende.
Bravo Bravo 👏 😁 Soldier...
Substandard journalism. Nkhani ya kuti ndalama anazitenga kuti sanayimalize. Amati kunali nkhani yina imene amayenera kugundako they didn't. Komanso kumusiya munthu using profanity language over and over on national osampatsa warning or even ending the program it's way below par.
Kkkkkkkkkk Norman Chisale !!!!! Ur a big Man. Wandiwaza kwambiri Msungeni all the way from Zambia.
Iwe interview sayamba choncho aaaaa introduction first
Interview ili yonse imakhala ndi mayambidwe osiyana, iyi si program ya tikudziweni, muziyamika kuti mwa atolankhani achizimayi, Leah is one of the best.
@@Littlefair7😂😂😂 koma ndi fact
@@alfredbanda1693
Samala Alfred upalamula🤣🤣🤣
@@Littlefair7 ndaleka😂😂
@@alfredbanda1693
🤣🤣🤣🤣
I love you Mr noman❤
True leadership timakunyadilani mr
Interview without introduction 😂😂😂😂😂😂Lea be professional plz
Ndipo ineso ndikudabwatu interview yanji yotero no introduction
Kkkkk I hope akuphunzira adzitolera
Pajatu anthu odziwika ngati amenewa introduction sikhala yofunikira kweni kweni, komabe as far as ma dos and don'ts are concerned apopo sizinayende kweni kweni😂
i was riding in your ship until i took some time to regurgitate
and i learn kuti amacheza naye ngati bodyguard wa Peter, his professional, and not as him as a person
brian banda akucheza ndin Bushiri, 27th may times exclusive, followed the same lane
yomwe anacheza ndi a Kapito pa 7th october anatero
even yomwe anacheza ndi Dr. Joyce Banda
Kkkkkkk ndipo etiiiiiii inuuuuuu iiiiii
Kulavula Moto munthu wamkulu, Lord have mercy on him
Mulungu akhale patsogolo basi Mr chisale Angoni
Komatu chisale ndye akumulakwla
Leah ndikadziotche apa adakamenyedwatu
42 years old? Did I hear that well? 🤔 Interesting.
😂😂😂 so in love with his courage 🤦🥰
Achibale zimenezo ndizija mumkachita kwa anthu ena muli m'boma limodzi ndi DPP. Zimatelotu chisale, iweyo ndiye akupsote kumene galu iwe munthu oipa iwe
Bwana chisale ineyo ndikuti pepani kwambili pa zomwe munazunzidwa
Ifenso timamvanso kuwawa
This lady, knows how to calm somebody. Mamuna wake anapata.
😂
Aaaa😮zaka 42 ndeine ndili 15 years 😂😂awa ngabodza
Leah try to write questions to be asked and kungoti bwana chisalewo amachita kokuwongoleranso plz plz plz interview opanda introduction aaaaaaa 😂😂😂
munazolowera zoloweza, muziganiza.
Ndipo live akunenazo ndi zoonad km Malawi kusamva😂😂😂
Kkkkkk ayayaya malawi tingogulisa tigawane dollar zo
Koma poti APM ayimezo nde tasephana basi aaaa..mwachidure kumalawi ndare zithe
Iweso khala chete mapazi opotokawo ngati milomo yako ikuyankhula mopotokayo
😂😂😂😂😂😂😂moto kuti buuuuu L malekano umatimilila koma bwinotu akubandula mbakela bwana ameneyo 😂😂😂😂😂
Bravo Mr Chisale
MCP ikazachoka m'boma idzazunzika kwambiri
Uyu mafunika brain Banda osati ana awa
Munthu ukulempera to forgive while holding bible
Kkkkkkkk😂😂😂😂😂😂
They are asking this guy what challenges did you face.. akufotokoza ma situations.. he was expected to mention political challenges, kapena professional dilemmas. Ayi, zopepela
Norman is right,the fact that aperson is working in the government does not bar aperson from being rich . Malawians justify poverty as being honest and truth
chisale ndi chitsiru. nkhani ya chilima ikukhuzana pati ndi kuba kwakoko
Leah , bravo 💪
Dpp yangoyenera kubweler 💓💓🙌🙌
Akuti thats totally bullshit yes yes
I like the confidence.
Chisale ndikatumdu🤗
This was a hot 🔥 one lol 😂
Brother chisale takumvani...Proud of you now.
The real legend khaaa wauuza ngamo
Chisale💪💪💪🇲🇼🇲🇼
Why even giving him a platform to say this nonsense.? He was very powerful, kusowa umboni doesn't mean you re innocent...you did 99percent of what you were accused of .....we know you can see even his tone kuti angaombele munthu awa
Achisale ndakutsatani pa u tube Mumapemphela zinazi msiireni Mulungu akhale Mulungu Ambuye yesu amamunamizila koma samayankha kanthu mpaka anaphedwa Eksodo 14v14 Chonde chonde
mbuzi chisale ukuona ngati bambowakowo sangawine ameneyo wapha albino wakwa na