ไม่สามารถเล่นวิดีโอนี้
ขออภัยในความไม่สะดวก

ZINA UKAMVA, ADZUKULU AKUMANDA OMWE ZIMAYI WADZUKA ATAMWALIRA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 25 ก.พ. 2024
  • updateZINA UKAMVA, ADZUKULU AKUMANDA OMWE ZIMAYI WADZUKA ATAMWALIRA

ความคิดเห็น • 56

  • @honourablemcgregorysc97tv
    @honourablemcgregorysc97tv 5 หลายเดือนก่อน +8

    Muli ndi ma Cameras aboh super HD 🔥🔥🔥

  • @user-qu9iu7hs8k
    @user-qu9iu7hs8k 5 หลายเดือนก่อน +3

    Kmatu explanation iri bwino kwambiri Hanifa you are the 1

  • @OleTaika-xl1tg
    @OleTaika-xl1tg 5 หลายเดือนก่อน +4

    Nzimayiyo ntengeni akagwilre ntchito ku radio afotokoza boh kwabasi

  • @user-zg4uu8mi9x
    @user-zg4uu8mi9x 5 หลายเดือนก่อน +3

    Prophet ameneyu ku Lilongwe ndi ndani dzina ??

    • @SumamiaDaud
      @SumamiaDaud 5 หลายเดือนก่อน

      Nane ndikufuna ndimudziwe

  • @DavieKaumphawi
    @DavieKaumphawi 20 วันที่ผ่านมา

    Wonderful story 😮

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 5 หลายเดือนก่อน +3

    Zimayi mukufusayo akufotokoza monvekabwino

  • @mackgozambia
    @mackgozambia 5 หลายเดือนก่อน

    Watching from KATETE Zambia

  • @CharlesMulikhiwa
    @CharlesMulikhiwa 3 หลายเดือนก่อน

    Hanifa go ahead is a good job u are doing ma media enawa kwao nkutamandira

  • @MtenjeHassan
    @MtenjeHassan 5 หลายเดือนก่อน +2

    Great job hanifa TV..hope mutipasila nkhaniyi mpaka kumapeto...

  • @henrychikuse1543
    @henrychikuse1543 5 หลายเดือนก่อน +2

    Koma chonde a Hanif muziyesetsa Kutionetsa munthu woukayo

  • @WhiskyMiti
    @WhiskyMiti หลายเดือนก่อน

    God is greater than all,

  • @JeniferKananji
    @JeniferKananji 7 วันที่ผ่านมา

    Amakhala kut muthuyo amuchosamo kumusandusa ndondocha zomagwila tchito za mudima kumanda timakasiyako Cha thochi ife timat TanyAmuka Muthu ai ndithu atamusunga

  • @user-gz9ej7ct7z
    @user-gz9ej7ct7z 5 หลายเดือนก่อน

    We need feed back here in zambia

  • @SilviaKamphonje
    @SilviaKamphonje 15 วันที่ผ่านมา

    God is good

  • @fosterkatemba1269
    @fosterkatemba1269 5 หลายเดือนก่อน

    Great job prophet

  • @user-yj3vj8wb3p
    @user-yj3vj8wb3p 5 หลายเดือนก่อน +2

    Ife tikudikira mutiuze momwe ayendera kulilongweko mukungoika zomwezomwe bwanji

  • @AFRICAHome-iv9bq
    @AFRICAHome-iv9bq 5 หลายเดือนก่อน +1

    Koma bwanji zimai ameneu nkhani zambili zimachitika pa maso pake. Is it acter kapena mutiuza
    Cox ndakhala ndkuonela ma video angapo Koma ekhaekhau

  • @GabrielNkhambule
    @GabrielNkhambule 3 หลายเดือนก่อน

    Sanamwalile mmayiyu aaaaa zitsamba zilipodi 😢

  • @user-dd8sk4wp4t
    @user-dd8sk4wp4t 5 หลายเดือนก่อน

    Illustrated well

  • @HamzahBandah
    @HamzahBandah หลายเดือนก่อน

    Mundipaseko nambala ya aprophert akulilongwe ndikuwafuna aprophert andithandoze

  • @G.Mpinga
    @G.Mpinga 4 หลายเดือนก่อน

    Ndipo akuyeneradi eni ma Radio Athedi kupangapo kanthu apa coz mzimayi uyu ndi super kumbali ya kufotokoza...

    • @user-yh2ji6si3x
      @user-yh2ji6si3x 4 หลายเดือนก่อน

      Zotsautsa. Ambuye azimekezeka. Thanks.

  • @edwardcomfort2085
    @edwardcomfort2085 5 หลายเดือนก่อน +1

    Apa Hanifa ndy wayamba kuyilumikiza bho TV 🤗

  • @KingstoneMnelemba
    @KingstoneMnelemba 25 วันที่ผ่านมา

    Prophet wanji opanda dzina?

  • @CharlesMulikhiwa
    @CharlesMulikhiwa 3 หลายเดือนก่อน

    Kutamandira akuba misomkho ya amalawi

  • @Esther-yv1mf
    @Esther-yv1mf 3 หลายเดือนก่อน

    God bless

  • @PetroJack-me8wn
    @PetroJack-me8wn 5 หลายเดือนก่อน

    Padziko pano eeeh pakuchitika zinthu😢😢😢

  • @lazahmaunde8877
    @lazahmaunde8877 4 หลายเดือนก่อน

    Km chifukwa chani anthuwo akt akubabwera ngati amisala

  • @Annah-wh1gg
    @Annah-wh1gg 5 หลายเดือนก่อน

    Eshhhh koma kuli zinthu kunjaku

  • @Mateustaulo
    @Mateustaulo 2 หลายเดือนก่อน

    Zonama zauchiwanda zimenezo

  • @ShorishKenneth
    @ShorishKenneth 5 หลายเดือนก่อน +1

    kumalawi paribe kupuma tikapuma kumwamba komweko kukapqnga zibwanaso tikazunguzaso

  • @HenrySiame-zf8xx
    @HenrySiame-zf8xx 2 หลายเดือนก่อน

    I'm

  • @user-wq9fq1yn6l
    @user-wq9fq1yn6l 5 หลายเดือนก่อน

    Eish zina ukamva

  • @user-qu5gf7cd5i
    @user-qu5gf7cd5i 4 หลายเดือนก่อน

    Kodi zimayo amabwelesa nkhanizambili samanama ameneyo

  • @user-dk8ey5pu5w
    @user-dk8ey5pu5w 5 หลายเดือนก่อน

    September si kale anthu sangakuiwale,si iyeyo

  • @user-oe4gp9ln7w
    @user-oe4gp9ln7w 5 หลายเดือนก่อน

    hanifa mumatiziwisa zambiri mupitirize zikomo

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 5 หลายเดือนก่อน +3

    Ndizowona wanthuwa akumagulisidwa ndiponso kumene amapita amakhala ndondocha zolima, zotenga ndalama, koma inenso ndiri kuno kuna bweranso Munthu wa nzimai Koma iye anati ndimakhala ku Blantyre mu shop koma nkumalire kuno Kwa Zimbabwe Ndi Mozambique, panopa Dziko siriri bwino za U satanic zavuta

  • @user-cm4wk6td1d
    @user-cm4wk6td1d 5 หลายเดือนก่อน

    Zili bwino

  • @yohanestainly6340
    @yohanestainly6340 5 หลายเดือนก่อน

    Pitani mukamujambule

  • @user-zl1xz9kt5s
    @user-zl1xz9kt5s 5 หลายเดือนก่อน

    Komatu mZimai uyu apole moto suja ankati anavundukura mvula mu mtsuko uja uyu😂

    • @iankuchaga5967
      @iankuchaga5967 4 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂😂😂 eyaaa ndiyemweyooo

  • @MartinsilverChirwa-fv9wn
    @MartinsilverChirwa-fv9wn 4 หลายเดือนก่อน

    Unbelievable

  • @user-xv3mw3ov8x
    @user-xv3mw3ov8x 5 หลายเดือนก่อน

    Zilibwino musasie kutelo

  • @ZakeyoCjere-bd1gj
    @ZakeyoCjere-bd1gj 5 หลายเดือนก่อน

    Koma zikuvhitikazi

  • @PatrickCarol-xe2zb
    @PatrickCarol-xe2zb 5 หลายเดือนก่อน

    mmmm

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb 5 หลายเดือนก่อน

    Koma mziyi uyu sieamvula uja

  • @AdamSalimu-tl3ts
    @AdamSalimu-tl3ts 5 หลายเดือนก่อน

    zowopsa mmmmm

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 5 หลายเดือนก่อน

    Kusapota MCP ndi ufiti

  • @user-zj3wi2zs5c
    @user-zj3wi2zs5c 5 หลายเดือนก่อน

    Koma kuli zithu

  • @Billi5
    @Billi5 5 หลายเดือนก่อน

    mzimayi ataona munthu akupala moto anakomoka,from there anapita kuchipatala atamwalila,,,question is who told the story kuti anaona bambo chanchan,,,anaifotokoza nkhaniyo ndan yet munthu mwiniwake anakomoka ndikufa at the moment

    • @user-hy3ig3nm6h
      @user-hy3ig3nm6h 5 หลายเดือนก่อน +2

      According to my understanding akut zoti anaona munthu akuzapala moto wanena yekha mayiyu mmene wabwelamu

    • @RebeccaKapira-xs7xj
      @RebeccaKapira-xs7xj 5 หลายเดือนก่อน

      Wafotokoza mmene wabweleramu,,, zimene zinachitika Kuti amwaliire

    • @user-gz9ej7ct7z
      @user-gz9ej7ct7z 5 หลายเดือนก่อน

      I think they have to answer

    • @isaacbandah3617
      @isaacbandah3617 2 หลายเดือนก่อน

      Fuso labwino kwambiri bigy