Zikomo ndikudikila mwa chidwi next mr Gova n Kadewele kamba ka lutso lanu keep it up ❤ u guys kamba ka ma update anu kanyimboso kakuchita kumveka mo gunda ntima 😂😂😂
Zaboza zilibe umboni iziiiiiiii munthu kutenga futi is not means ndiwe mmbanva I'm from malaw guyz please next time u mus try to search before to do something
Ndimakonda kumvera Balanco Semanal. Estou em Blantyre, Malawi.
watching from south africa but am from malawi
Keep up the good work ,watching from durban
Dzianthu zaku Mozambique dzoipa Moyo kwambiri
Zikomo kwambili pakutidziwitsa zakwathu. José from cidade de Maputo
Good work from.....خيري
Ayi anyamata mukuesesa kugwira ntchito yotamandika yotiziwisa nkhani zosiyanasiyana ambuye azikudarisan
Apo Mulungu wawonetsa ukulu wake chilango chimenechi.
Following from malawi 🇲🇼 keep on updating..... next video please
Choipa chitsata mwini.Adatero akulu akale
Zikomo ndikudikila mwa chidwi next mr Gova n Kadewele kamba ka lutso lanu keep it up ❤ u guys kamba ka ma update anu kanyimboso kakuchita kumveka mo gunda ntima 😂😂😂
Please agova tapangani part3
Nice 1
Mumakwanila atsogo agova
Nkhani yopatsa chidwi...waiting for part 2.
Zaboza zilibe umboni iziiiiiiii munthu kutenga futi is not means ndiwe mmbanva I'm from malaw guyz please next time u mus try to search before to do something
Good reporting
😊😊khk😊
Kodi Ku Mozambique amayankhula chichewa chabwino chomchi abale?
akuchita kutiposa ife a kukaya 😂
Ntchito ya bwino anyamata anthu
Zikomo kwa mbiri potiziwisa pitilizan kutelo pls
Following
Please Agova tapangani part 2
Zikomo kwambiri BS let's wait next video 📷
Taika maliro dzana kuno ku dedza anali chigawenga choopsya kwambili
Zilibwino kwambiri timanhadira
Good
Mbambande plogramu
Mumakwana.pio apartir de Nzewe
Tiyamike balanso mumatipasira khani zomwesitimazidziwa ine Chimzy kumalawi
Koma dzovuta
Rest in peace
Zikomo mumapanga zithu mwaluso kwambiri
Ndipo amaigwira ntchitodi mwaluso awa not hanifa
Waiting part 2
Zovuta zedi
Tidikira part 2