CHIZASO GONDWE KUFOTOKOZA UMBAVA WACHAKWERA MOMVEKA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 5 พ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 26

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o 2 หลายเดือนก่อน +2

    Yes we talk and talk but nothing on the ground

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 2 หลายเดือนก่อน +2

    Tiyamike ndimesegi yanu big ife tatopa nd mcp

  • @henryhenry6632
    @henryhenry6632 หลายเดือนก่อน

    Mwalilan ngati mwatopa

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 หลายเดือนก่อน

    Inu mwanapiye anawonera make kunyera mnyumba

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r หลายเดือนก่อน

    Chekwela bagamoyo

  • @user-ln5ob6ki5g
    @user-ln5ob6ki5g หลายเดือนก่อน

    Iwe ndi munthu amene ukuwononga dziko ukutiphunzitsira

  • @user-xe5lb4uf3n
    @user-xe5lb4uf3n หลายเดือนก่อน

    Kodi mabungwe omenyera ufulu akutani pankhani zimenezi

  • @jonathanmalanda7742
    @jonathanmalanda7742 หลายเดือนก่อน

    Amalawi ufulu wonyasa womwe timaonetsa a pule akale ananyozedwa lero awa akunyozedwa azelu alipo koma opadongosolo

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 2 หลายเดือนก่อน

    Mtsogoleri aliyense ku Malawi amafuna kudyapo basi. Tiyeni tizingoyembekeza kubwera kwa Yesu basi.

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l หลายเดือนก่อน

    Galu iwe , ukulemekeza America ngati ambiyako galu ndiwe chitsiru. Nyasi munthuwe

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 2 หลายเดือนก่อน

    Malawi 🇲🇼 dziko lomvetsa chisoni kwambiri.

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 หลายเดือนก่อน

    Guys wake up Malawi panopa wafika powawa chifukwa apule ndi mbamva yotheradi mulungu atikhululukire tinangochosa Peter munthalika munthu wabwino

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mbusa cakwera sanalowe mboma kuti asogolere amalawi ai koma kuononga dziko kuna kusakadza ndipo tikalekerera kuti 2025 apitilidze ndithu tlnse amalawi tikutha tiyeni tidzuke amalawi president uyu ndi wasatanic onani sakukhudzik ndi mmene anthu tikuvutikira akungoba mopanda manyazi cakwera anthu tatopa naye anwerere ku church

    • @user-zg7iw8kq4r
      @user-zg7iw8kq4r 2 หลายเดือนก่อน

      Ndipo nkhumba imeneyi yandikwana kwabasi

  • @iamandypandy
    @iamandypandy 2 หลายเดือนก่อน +1

    Koma a phumbwawa ?

  • @George-zd5le
    @George-zd5le 2 หลายเดือนก่อน

    Tikungomva ma vn every day but nothing to do with actions on the ground paliphindu apa

  • @DicksonBlack
    @DicksonBlack 2 หลายเดือนก่อน

    Kkkkk menus mwanabwa tone mbuyake

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk หลายเดือนก่อน

    Never again for MCP

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy หลายเดือนก่อน

    Dziko laipa ili

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 2 หลายเดือนก่อน

    Koma zoona anthu daily tikumva zoyipa za Boma la Tonse Alliance ndi President Chakwera, but tikungoyang'ana osachitapo kanthu kuyiopa MCP

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r หลายเดือนก่อน

    Masiku osiliza zayambila kumalawi or ufulu dairly tizingova zonyoza basi zauchisulu kusowa ntchito eti ndi atumbuka womwe ife kumpoto timadalila kulima not kunyoza ai ndimwe vizeleza

    • @user-rf4br1fv2z
      @user-rf4br1fv2z หลายเดือนก่อน

      Abale every day kunyoza kunyoza kodi alipi munthu wabwino pa dziko pano chonde amalawi tidxiganiza pena tilimbikile kudziyimila

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 หลายเดือนก่อน

    Inu mwanapiye anawonera make kunyera mnyumba

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 หลายเดือนก่อน

    Inu mwanapiye anawonera make kunyera mnyumba

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 หลายเดือนก่อน

    Inu mwanapiye anawonera make kunyera mnyumba