Mai wonena chilungamo. Ngakhale ine mupaka pano sindikuvomereza kuti chisankho cha 2019 sichinauende bwino ndi aboza chisankho chinayenda bwino according ndi chisankho chobwereza kusiya penalibe koma chifukwa cha umbuli kumalawi timavomereza ndi aboza zomwe wina akatinamiza
Yeah well spoken MAMA, Malawian we need people who can develop OUR COUNTRY ,osati izi Za MCP and Tonse ALLIANCE, Malawian voted for MCP And Tonse ALLIANCE what is happening today is what???? is very SAD NEWS😂Anzathu Akunja amati akawona kuti chipani chao sichikupanga zabwino next time they will vote the other part it can bring food on the table and development in the Country its up to US to DECIDE.
The Bible Speaks about Daniel as a servant of God who served Him faithfully , his role was a prophet but later it pleased God that he should serve in Babylonian kingdom as a prime minister. But this did not cause Daniel to change his character from being a faithful servant before his Master. Faithfulness is an offspring that shoots out of the good character of a person. Mother - Mrs Jane Ansah can server God in political carrier if it pleases God just as Daniel. Both Daniel and his people benefited alot from both prophetic and political roles he played. Though people may change, corrupt and become unfaithful and evil, but still there are some good persons out there. That's why Noar and his family was saved from flood, and Lot and his daughters from Sodom. I wish her well... Let God lead your path -Mother- and good Luck!.
Mai akukunamizani anthu kuno sitikukufunani. Ngati muli ndi timatambala chonde gwilitsani ntchito ina osati kundale muzalila. Muli ndi mbili yoipa kale kudziko. Ndithu kuno ku Ntcheu Mai pa u MP simungadzawine.
It can't be the same because of natural factors, there's just no way that the statistics would remain exactly the same bcoz we of issues such as accidents, kudwala kwa munthu or sudden death or travelling and so on. So figures can't be ndende nde 12 million the other time and months or years the same million?
Koma upelezident abale basi kungozuka kwanuko basi tiye uyime upule yooh nda ndi mmene akuyankhuliramo angakhale pulezident inuso mukumuyikila kumbuyo mayiyu nzeru ndi zopelewera mfunika ku mental basi
I love this woman very much.
Welcome J ansa your matured woman in law weldone
This woman akuyenera kukhala Vice president wa DPP ndi machine
Keep it up mama brave 😮😊❤
Zoona ndimbava yopanda manyazi komaso alibe chifundo adaledzera ndi dpp musiyeni aziona zotsatira
Mai wonena chilungamo. Ngakhale ine mupaka pano sindikuvomereza kuti chisankho cha 2019 sichinauende bwino ndi aboza chisankho chinayenda bwino according ndi chisankho chobwereza kusiya penalibe koma chifukwa cha umbuli kumalawi timavomereza ndi aboza zomwe wina akatinamiza
Welcome mai, Mai wanzeru, wozichepesa, wosakwiya
Ife tili pambuyo panuuuuu
Kulimba mtima uku ndi koopsa kwambiri.
Ndipo koopsa ishhhh
I support you Jane vote yanu ili ndi ine
Keep it up mama, bravo
Kwamene sanaoneko satana abwele apa
Keep it up mama...mukawina anthu lero azindikila kt ndinu Mai wabwno.. ❤❤❤
Yeah well spoken MAMA, Malawian we need people who can develop OUR COUNTRY ,osati izi Za MCP and Tonse ALLIANCE, Malawian voted for MCP And Tonse ALLIANCE what is happening today is what???? is very SAD NEWS😂Anzathu Akunja amati akawona kuti chipani chao sichikupanga zabwino next time they will vote the other part it can bring food on the table and development in the Country its up to US to DECIDE.
Mbava iyi isatinyase. Imativotera mmalo mowerenga mavoti athu. Lowani dpp yomweyo mukagwe nayo.
Munthu wachilunngamo dziko limadana naye ndithu, koma Chilingamocho chimamusiya pabwino zedi. Sagona ni njala
Tikudikilaso tsiku lomwe mudzacheze ndi Mai Anastasia Nsosa
Mai amene uja anari katundu,,,,,,sizingafane nd iziz
The Bible Speaks about Daniel as a servant of God who served Him faithfully , his role was a prophet but later it pleased God that he should serve in Babylonian kingdom as a prime minister. But this did not cause Daniel to change his character from being a faithful servant before his Master.
Faithfulness is an offspring that shoots out of the good character of a person. Mother - Mrs Jane Ansah can server God in political carrier if it pleases God just as Daniel.
Both Daniel and his people benefited alot from both prophetic and political roles he played.
Though people may change, corrupt and become unfaithful and evil, but still there are some good persons out there. That's why Noar and his family was saved from flood, and Lot and his daughters from Sodom.
I wish her well... Let God lead your path -Mother- and good Luck!.
Mmai wozichepetsa kwambiri ❤❤❤
😂😂😂aaaah kulankhula kuphweka koma kuchita agalu andale inu,mukufuna mutisokosele tsopano,ndi mmene mumadyela ndalama
Mmayi uyu zinthu anayendetsa bwino kwambiri ndpo statement samaisintha komano osamataya ntima agalu akulamulawa ankangofuna kumuchotsa mutharika uja mpake zikuwavuta
Ndipo mayi uyu ndi mbambande
I wish I could have strong woman like you mum never give up
Siinu woyamba mayi kulankhula zimenezo,
Nganganga ndi Mai mkulu🎉❤❤❤❤
Thanks mama good idea
Tipex tipex tipex
Ntcheu patsogolo ndi chitukuko Mai wa mphanvu Jane
Welcome mama,developments at its best
She is a true woman of God
Dandaulo lalikulu ndi matochi😂
Ndi mlomwe munthu uja..... no wonder.
Tazifunsani mafunso ngati munapita ku school!!! Ndekuti Mr Banda aja samakuwazani?
Ine i would like kuti apikisane pauPresident
Kodi ndingalibeze nawo Bukhuli?
Mayi malawi
Timakunyadilani mama
Mama well done keep it up amalawi unatikulila ndiumbuli
Mayi wathu wabwino
Amalawi mulibe pa bwino walakwa chani mayiwa
Welcome back, you are capable of fulfilling your words . We still trust you Mama
Okay do you mean even mfumu atha kukhala MP
Kulongosola komveka bwino
ndipo ndizona anawinila chifukwa anamphatikizana
Mai wabwino uyu
Malawi Malawi very shame! Are we going to find good leaders like our neighbouring coun
Lero ndi izi
Mama Tippex
People came to see the evil
Zoonadi mmayiyu anali osalakwa
Waboza uyu wa dpp mesa anali pamozi ,chinangota chisankho amajambulisa limozi ma photo
Kodi jaji wa khoti mdziko ngololedwa kuyimirira za ndale
Yes he/she allowed to do so as long as that person is retired or resign from that office bt this beautiful mama she is retired.
Wina aliyense ndiololedwa as long as wapanga retire/resign ku ntchito yomwe amagwirayo
@@EvanceEdson-fz1vnchabwino atsogoleri. Ndimaganizatu kuti mfumu ndi oweluza milindu kukoti ndi midiator citizens sangalowelele zandale
Mau akuti former chief justice mwamva
@@JalasiLucasJalasi indeetu mchifukwa ndimafuna kudziwa mafumu atha kusiya ufumu mkupitha kundale
Are you related to Brian Banda?
Wa DPP uyu remember anakhalapo ngati attorney General during peter munthalika regime
Ndiye
@@sheikhjaffarwhyte2688 ndiye bankha wanuyu amakana chani kuti alibe chipani?We all know she is blue
chisankho chithee
Mai akukunamizani anthu kuno sitikukufunani. Ngati muli ndi timatambala chonde gwilitsani ntchito ina osati kundale muzalila. Muli ndi mbili yoipa kale kudziko. Ndithu kuno ku Ntcheu Mai pa u MP simungadzawine.
Mukudya bwino ndi mp amene Ali kumene ndakuona
That is not meaning of 50+1. This woman was really a judge??
Kodi timamva kuti kwao mkukampata komanso kumulanje ndiye apa ntcheu zikuti bwanji
Listen the whole clip your will get the answer she has explained properly you will understand without any Questions.
It can't be the same because of natural factors, there's just no way that the statistics would remain exactly the same bcoz we of issues such as accidents, kudwala kwa munthu or sudden death or travelling and so on. So figures can't be ndende nde 12 million the other time and months or years the same million?
Dyela mayiyu ndalama zimene anakupasani peter yo simnankhute siyilani achinyamata mwakula
Does the constitution in Malawi allow a former judge to do politics??? In Zambia it's not possible. The constitution does not allow.
In Malawi, it is allowed
In Malawi its not a crime...
This woman is dangerous, mbamva
Anakuberani zingati
How she is dangerous??
Koma upelezident abale basi kungozuka kwanuko basi tiye uyime upule yooh nda ndi mmene akuyankhuliramo angakhale pulezident inuso mukumuyikila kumbuyo mayiyu nzeru ndi zopelewera mfunika ku mental basi
Eti eti inu ishhhhh
Nfiti yaikaz I iyi
Mmmmm zabodza ukadzangowina basi kenako mwano
Kaligwichi meaning plz
Nkhwidzi.....mangawa.
Zopusa
What a Waste of resources. Time , bundle.
Did anyone force you to watch
A very stubborn woman I have never seen in my life
Akufunikadi ku mental uyu nda ili nde tsoka lenileni la a Malawi satana kuwaonekera poyera